Namiwa has an important point to make but our interviewer is disturbing him. At this stage I think its needless to push him heavily on irrelevant questions. Please give him a chance to explain so we the listeners will follow him
Namiwa be strong dont be like the so called pastir Evangelist Ty Nyirenda wakomedwa ndi ndarama,am very disappointed with my pastir from north and wa seventhday shame shame shameon you pastir Tulukanimo mmenemo
The big problem anthu amene anakulila muthawi yamuma 70s and 80s amafuna kubisa chilungamo mumalo moziwa zowona forgetting this is 21st century which is 2024
Gabriel Kamloma mhhhhh very partisan, tinkakupatsani ulemu kale kaloweni ku MBC! Journalist umayenera kufufuza koma inuyo mukuoneka kuti simukudziwa za anthu...Namiwa akukamba zomwe zili pa ground
Namiwa you are a genus, we are really taking bags of maize sneaking them into our hostels in these Universities, kumaphika mobisa we can not afford to buy meals
Soka kwainu amene muli mu enquiry imeneyo ndichochilinga chopeza phindu not to produce the truth,mind you your days are counted by God,we have few days to leave in this earth.
Anamiwa niganiza kuti ndinu abugwe loyima palokha liyimililira anthu koma mukukamba kwanuku zawonetsa kt ndinu oyimirira zipani zotsutsa go ahead for your job to help opposition party.
Namiwa nkhani iyi India miyoyo ya anthu si ndi spots mulimafunso ambiri oti ayankhidwe mumenemo kuyankhaku ndi kwawutambwali nenani kuti munapitako ndi phuma, kumadekha bwino tu nanunso akhodza kukuyitanani kuti mukayakhe, mupite ndi wumboni
This man namiwa ndimunthu ofunikila kwambiri
He is doing well , keep it up Mr Namiwa
Yaaa namiwa maonetsa chilungamo God bless you
This is God speaking through Namiwa
Namiw pamenepo mwaonetsa kuti mumatikonda ife amalawi mubomamu mukufunika anthu ngati inuyo mwaonetsa chikondi ndipo mapangazi anthu ambili akukhulupiliani komaso mwaonetsa chikondi ambiye azikudalitszni iwyo ndi mbambande❤❤❤
Anamiwa ndi inu munthu wachilungamo and GOD BLESS YOU 🙏🙏🙏🙏
Chilungamo chiyende ngati madzi osaopa osatopa osafooka namiwa god bless you.
Anamiwa mulungu akudalitseni kwambiri you are the person who look forward with our country
Abambo. Namiwa God bless you ❤❤
Audzeni anamiwa kuti smart martic machine no more , akozeke Anabel ntalimanja kozekani tikubwera konko ndi mademo anyooooo well done Mr Namiwa
Very good reporter & asking tough & professional questions 😂
Mr U are a true Malawian and Christian bravo big
Ooo God protect Mr Namiwa
Akulu invitation was for Mr. Namiwa as a whistle blower.
Anamiwa ndikatundu komano chikangawa akanango vomereza zaifa basss osachedwa apa aaa chirungamo chikunena chokha akuruwo adya ndarama anamiwa ayakhe mbwerera
Namiwa God bless you. Will close my shop to follow you during demonstrations
Mulungu azikitetezani Mr namiwa ❤❤❤
Namiwa ndiwe munthu wanzeru kwambiri ❤❤
Zikomo Sylvester Namiwa, you are a great man.Chilipo akubisa.RIP Saulos.
God bless you Mr Namiwa
Namiwa has an important point to make but our interviewer is disturbing him. At this stage I think its needless to push him heavily on irrelevant questions.
Please give him a chance to explain so we the listeners will follow him
God bless you Namiwa🎉
More fire 🔥. Achilungamo sakondedwa pamalo.
Inuso abambo inu mukufusa mafuso opusa kwambiri kom nokha chilungamo simukuchiona koma kukunyunso ndindani munthu wakupha uja. Aluza chani inu munthu akufotokoza moveka bwino,
Mr Namiwa now 100% keep it up
❤❤❤Congratulations Mr namiwa
If I were a billionaire I would have invested in this guy so called namiwa...
Namiwa deserve to be Presidential Adviser. Mumatiimilira
Be blessed Mr Namiwa....
Namiwa wapangitsa kuti ndidzapezeke pa ma demo koyambilira pa mbiri ya moyo wanga. Andale akutitenga ngati ife mbuzi 😢
God bless you Mr namiwa🙏🙏
Anamiwa mulungu azikudalitsani potiimilira, inuyo mumantha ndipo mulungu akutetezeleni chifukwa anthu akuyang'anani ndi diso langati nkhwezule?
Keep it Mr Namiwa.
Ndichoncho akulu ofunsa mafunso mukufunsa chinyezi ku bafa
Ulemu wanu Mr Namiwa pitilizani kutiyimilira
Tili ndiotiimilira😢😢😢😢😢😢😢😢😢❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Keep it up namiwa
Uyu ndidolo kwambiri muli uthenga wanyooo
Namiwa changuwa makola kuti Mbakuchenjera and mbakuti wangalongozga chalo yayi
chonde mr namiwa ine ndimakutsatani kwambiri ,,Koma ngati mukufuna kuti tikonze malawi chonde ndipezeni ine ndikuuzeni zifukwa zimene amalawife timalephera kupita patsogolo ,chonde
Iweso ukuumiriza mafuso opusa kwambiri ndiwe wa MCP eti?anachita bwino kutuluka iweyo usamuulize ayi.
NAMIWA si munthu wamba amaganiza bwino kwambiri samafuna zopusa
Ofusa mafusoyu ndi kape kwambiri, mwina ndi wa😂 chikangawa party ameneyu.
God bless you Mr namiwa
❤❤anganiza bwino asalemo wokha a mcp wokha wokha agalu a mcp
Mr namiwa you a lone bigger than hrdc
Namiwa be strong dont be like the so called pastir Evangelist Ty Nyirenda wakomedwa ndi ndarama,am very disappointed with my pastir from north and wa seventhday shame shame shameon you pastir Tulukanimo mmenemo
Very shame😭,afookesa achristu ambiri
The big problem anthu amene anakulila muthawi yamuma 70s and 80s amafuna kubisa chilungamo mumalo moziwa zowona forgetting this is 21st century which is 2024
Akulu ofusanu ndinu achitsilu bwanji, mukufusa mafuso opepela kwambiri......Anamiwawo simukuwavetsa pati.....
Ndikape ameneyu
Ineso akundimwetekesa ntima ndamafuso akewa akumubalalisa muthu aaaaa😂😂😂😂😂
Gabriel Kamloma mhhhhh very partisan, tinkakupatsani ulemu kale kaloweni ku MBC! Journalist umayenera kufufuza koma inuyo mukuoneka kuti simukudziwa za anthu...Namiwa akukamba zomwe zili pa ground
Mr namiwa inuyo munali ngati chikwangwani anzanuwo zochita adauzidwa kale ngati ndalamaso adatenga kale and mudakakamira akasapangq plan yokusowetsan.
Namiwa you are a genus, we are really taking bags of maize sneaking them into our hostels in these Universities, kumaphika mobisa we can not afford to buy meals
You are big man mr Namiwa
Mafuso opusa opanda phindu
Anamiwa adpp ndiye panali vuto kuti akhale nawo gulu limeneli ndi achisilu
Soka kwainu amene muli mu enquiry imeneyo ndichochilinga chopeza phindu not to produce the truth,mind you your days are counted by God,we have few days to leave in this earth.
Keep it up mr
Mr namiwa we are together with u interview iyi yandisangalatsa zedi mukutanka boh kwambiri
Supumatu chikangawa guy iwe 😂😂 tikamaliza commission inquiry tili ndiwe annabel mtalimanja 😂😂😂😂
Umatiimilira
Namiwa you are right, komanso zokhala live ananena ndi aku banja la Chilima, ndie iwo akufuna za nseri chifukwa chani???
Namiwa the great,rebuild the nation
Madzi achita katondo😂😂😂
True - instincts is greater than reason!
Awa adakakumana ndi Brian banda zidakamuvuta ndi wa dpp ndamuwona uyu mbuli yamunthu
Opangisa interview ndiwe wa MCP ndakuona ukufusa zopusa ngt sukuva zisiye
Iwowa ndimagulu amene amauza amalawi kuti anali ndimaumbani asathawemo
Yeah wanena chilungamo 🙏🙏🙏🙏
Ofusa mafunsowo ali bias sakuyimira mbali ya a Malawi,koma akuonesa zoti akuyimira mbali ya onwe akususana omwe ali against Namiwa
Namiwa ulemu wanu ❤❤❤
Anamiwa niganiza kuti ndinu abugwe loyima palokha liyimililira anthu koma mukukamba kwanuku zawonetsa kt ndinu oyimirira zipani zotsutsa go ahead for your job to help opposition party.
Azibambo opanda mantha kuyankhula ngati wakhalila mfuti
Well done for dumpling the iquery team
musatiphere mwava agaru inu 😂
Namiwa ukhaledi nganganga pa ife amalawi mpaka choona chidziwike
Anamiwa sakuyankha zomveka iwowa akuiopa chifukwa iwowa anali mmodzi oti akanamuiyata Kuti azafusidwepo mafuso chifukwa iyeyu Namiwa amayankhula Ngati alindiumboni .amangodziwa kuyankhula Ku cdedi Koma mafuso amene mukumufusawa Namiwa akulephera kuyankha .zikuoneseratu Kuti ndimunthu oyambanisa kwambiri
Chonde anamiwa osalora ndalama za chinyengo mkagwira bwino ntchito Mulungu azakudalitsan
God bless namiwa
Mmmmm chosecho Kuli abusa Malawi ukoko akudya ndalama zaulele koma auzidya zochita
Mtola nkhani uyu sakuvetsa pati ndi mmene akufotokozela anamiwa zikumveka bwino koma mulungu alipo 🎉
Munthu uyu ndi wabwino kwambiri coz akuganizila otsalafe mwatphera kholo
Namiwa uli ndi mfundo zogwirika, why osaima pa wekha upange campaign ulitenge ndzikoli
Namiwa a true son of the soil
Namiwa ndiwetandisoratu❤❤❤❤❤❤❤❤❤🎉😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢chodetiphukute misozi
Namiwa simunthu wanna ndakhulupirira ine lero
Kuitenga nkholokoro mu vuwo wa chambo.. Ndizi
DR chakwera muziona anthu owatenga
Namiwa on fire
Namiwa koma akanasangalala kwambiri akanakumana ndi Brian Banda chifukwa onse ali chipani chimodzi
Kumalawi tidzaswane Kaye
Osokoneza namiwayu.
Ife amalawi commissioner of iquiary imeneyo siyathu ndipo asamvutike chifukwa zikuoneka kuti anthu adauzidwa zochita kuti mubise ife tiyaluka komat tizaziziwa anthu muzathawa dzikomo muno chifukwa chopha chakwera
dziko lamalawi lili pamavuto ochuluka chifukwa anthu ife tikudodedwa kwambili ndipo dziko lathu lawonongeka kwambili panopa
Namiwa God bless you
Uyu namiwa ndi wa dpp chilichonse kususa kma xa dpp sangasuse
Mean kuti commission yomwe yakhazikisidwayo nja mcp
Ineso ndikuwona Chocho akufinyika kwambi
@@GloriaKaduya-q1ykhalangat ndizomwe akutanthauza zilibwn pot tadziwa kut commission ndiya mcp
Umafuna azingovomera zilizonse kmans ukat ndiwa DPP wat do you mean? Ndekut commission ija ndiya congress?
Ma journalist a zodiac ndimbuzi za athu radio ya mcp
Anamiwawo sayakhabwino bwino aaaaaa
Dolodolo wacani citsilu ici kuzolowelakutsutsa zaziiii yikapongonowako paphandopo kkkkk
inu ndachitsiru
I pity you broz, open your eyes
Ndinu m,bulundi bwana
Iweyo ndichisilu galu wachabechabe
Iwedi ndi bankha
Namiwa nkhani iyi India miyoyo ya anthu si ndi spots mulimafunso ambiri oti ayankhidwe mumenemo kuyankhaku ndi kwawutambwali nenani kuti munapitako ndi phuma, kumadekha bwino tu nanunso akhodza kukuyitanani kuti mukayakhe, mupite ndi wumboni
You are missing his point wawa, pangani follow nkhani bwinobwino. Malawi needs the truth.
Mtolakhani Inu watumidwa ndi mcp mbuzi yamuthu mafutso wopepela kwambili
Namiwa🔥🔥🔥🔥