Nkhanga zaona: Chakwera wagawa futi zoti amuphele Kalindo. Machine obela alowa dziko muno

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 184

  • @KingfrahMachado
    @KingfrahMachado Місяць тому +2

    Nde mfuti kuphela anthu kumalawi mesa Malawi ndiziko kamtendele😢😮😮 zimenez zosathek ife tikamuteteza President wathu Bonkalindo❤🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-rm2xv8ys1i
    @user-rm2xv8ys1i Місяць тому +9

    Ndipo mulungu akuone iwe chakwera ife tizimva kuwawa iwe uzinjoya zoona mulungu ndi mulungu

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Місяць тому +9

    Am not sure if MEC will do good for all malawians

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz Місяць тому +14

    Olo atazabela tizavotanso zomwe anawapanga anzawo a dpp nawonso azaziwona zomwezo mark my words

  • @HannifordWitness
    @HannifordWitness Місяць тому +14

    Tithokoze ntchito yabwn a Comrade Ntanyiwa ...km pena zikumaoneka ngt propaganda mukamanena cfkwa simukumatipatsa umboni ogwirika Mr Ntanyiwa mwachitsanzo what's group mukunenayi pakanakhala voice yotsimikizira zimenezi wosangonena ndi pakamwa panu ai km pena muzitipatsa umboni wogwirika ngt mmene amachitira wa Bakili Muluzi.

  • @user-cn3gi2vf5n
    @user-cn3gi2vf5n Місяць тому +17

    All plans will cancelled in Jesus name amen

    • @SifatiMoses
      @SifatiMoses Місяць тому +1

      Ayelekeze kuzaomba chipolopolo, pa 8 pano apeza polekera. Tili pa sewu pa 8 pano ngati amapha akape pa 8 pano.

    • @PromisNtaba
      @PromisNtaba Місяць тому

      @@SifatiMoses 0

    • @YohanePaul
      @YohanePaul Місяць тому

      Amen

  • @user-hs2dw7ly2c
    @user-hs2dw7ly2c Місяць тому +2

    Amuphe Bon Kalindo awone momwe Malawi 🇲🇼 iyalukira kuzakhala nkhondo ya mipaliro

    • @Dysonkhofi
      @Dysonkhofi Місяць тому

      Angayambitse nkhondo ndani?

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w Місяць тому +2

    Following from south africa

  • @Yaqub-nk4pu
    @Yaqub-nk4pu Місяць тому +4

    With respect Mr Ntanyuwa, no one will reward u only God knows how much to reward u my brother

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Місяць тому +1

    Mayi uyu ndiwoyipadi mtima eti Yoo 🙌🙌🙌

  • @YasinElias-q3z
    @YasinElias-q3z Місяць тому +2

    But why can't you play the audio of their conversation timakusatilan koma zinazi timagona ngat mukakhala mwakhuta chabe

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Місяць тому +3

    yes ndakunyadira sweet

  • @johnmponda9070
    @johnmponda9070 Місяць тому

    I love Limpopo fm, Com Mtanyiwa, we love Bon the DC ng'alulisation K. Kalua i love Malawi's keep going God always flights for his children.

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Місяць тому +1

    ❤❤ antanyiwa pitilizanj ntchito yanu god bless you please amalawi let's fight for our country palibe angatimenyele dziko lathu please

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Місяць тому +5

    Koma ntchito ilipo ndithu koma komaaaaa komaaa

  • @chiletsokazembe-ri4ic
    @chiletsokazembe-ri4ic Місяць тому +2

    anthu amisara mukuchuluka, komaso bwanji mukukhara alone nokhanokha? Ndiyet dpp sitivotera coz mukuonetsa kt dpp alone mumadya bwino eti?

  • @ronnexthyoke7947
    @ronnexthyoke7947 Місяць тому

    Comr Ntanyiwa please keep the fire burning, Malawians deserves to know the real truth about SKC ,.the DC Bon Kalindo #MALAWI FIRST #LIMPOPO FM.

  • @yohanebotso
    @yohanebotso Місяць тому +1

    We're with you boss

  • @stevenbanda6665
    @stevenbanda6665 25 днів тому

    Following from south africa tienazo comrade ntanyiwa

  • @KingfrahMachado
    @KingfrahMachado Місяць тому +1

    Kom mavote awawa ngt sangayendeso bwino ndekut mau tilibe ife anthu osauka cz akusangalala ndiandale okha bc kom Malawi ikubwera munthawi ya Tsamunda😭😭😭😢❤🙏

    • @cynthiakananji1608
      @cynthiakananji1608 Місяць тому +1

      Ndipo ineyo ndimalira ndikupemphera, Malawi ngat bodza ichichi cha pasi pa nyanjachi chaisandusa Malawi kukhala dziko la umphawi komaso lopatsa mantha

    • @KingfrahMachado
      @KingfrahMachado Місяць тому +1

      @@cynthiakananji1608 end panop dziko lathu muli nkhondo yachinsisi imene akupanga galu ameney Dairy kupha anthu😰😰😰

  • @ChrispinEdward
    @ChrispinEdward 23 дні тому

    Matishit ayambile komwekuno am here at cape town DC samukwanitsa asake wina

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Місяць тому +3

    Ludo NDI UTI ndizachindemo

  • @user-bi5lg8mg9y
    @user-bi5lg8mg9y Місяць тому +1

    No more secret on ground nowadays 😂😂😂

  • @OmarHassan-q8k
    @OmarHassan-q8k Місяць тому

    Osaopa ,osatopa ,osafooka Mademo tichita mosogozedwa ndi Mulungu osaiwala ku vala Mask ku ziteteza komanso kuvala zovala zofanana ku avutike pofunafuna munthu yemwe akumufuna kumuchita chipongwe moto kuti buuuuuuuu❤❤

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Місяць тому +1

    No wonder Joyce Banda adakali ku Alliance akufuna azipanga zauchitsiluzi.

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona Місяць тому +10

    Mumtanyiwa gwirani ntchito yolemetsayi musatope mulungu akuthandize

    • @KingfrahMachado
      @KingfrahMachado Місяць тому +1

      Kwambli chifukwa mukasiya ndekut ife bc tathela pamenepo Mcp izakhalebe ndiulamulilo

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f Місяць тому

    Pitirizani big brother. Mukuchenjedza champhongo

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 Місяць тому +6

    Mmm

  • @MphatsoIshmaeladam
    @MphatsoIshmaeladam Місяць тому +8

    Vuto ndi amalawi tili ndi ufulu kukana chairperson wa mec koma tingovomeraza zili zonse

    • @MarthaPhiri-q8m
      @MarthaPhiri-q8m Місяць тому

      Ndipo Zoona amalawi tinachenjera moputsa aaa timangoziwa kutukwana

    • @KingfrahMachado
      @KingfrahMachado Місяць тому

      Ngt mukunama inuyo vuto ndiimeney kya tinakhala bwanj kya

  • @user-ri2vi2fd5v
    @user-ri2vi2fd5v Місяць тому +4

    Mwachepa nazo mafana

  • @ChisomoamitoniSauzandeamiton
    @ChisomoamitoniSauzandeamiton 25 днів тому

    akungo usowa zocita chakwera pomalimbana ndi BON KALINDO musiyeni

  • @JustinBlackChiwaya
    @JustinBlackChiwaya Місяць тому

    God bless Malawi 🇲🇼

  • @MphatsoIshmaeladam
    @MphatsoIshmaeladam Місяць тому +1

    Ine ndagwirapo ntchito mu 2004 ndipo chisankho kudziwa yemwe awina ndi simple as long as zowelengera pa poling stains zisasinthe

  • @LuciusMakupe
    @LuciusMakupe Місяць тому +1

    Mizimu ya yathu sizingatheke Kuti tisamaziwe zinsisizi Lero Mulungu waziuluranso

  • @PeterSuwack
    @PeterSuwack Місяць тому

    Mbambande big man ❤❤❤❤❤

  • @elishamael-shadai
    @elishamael-shadai Місяць тому +1

    😂😂😂😂😂😂😂 koma ndale za pa Malawi zabwerera chikale

  • @AsiyatuAkila
    @AsiyatuAkila 26 днів тому

    Kmn zomwe akupanga apule aaaaaa gyz simunthu wabwino uyu km chomwe iye akufuna azingowaophweza anthu bs mutu owumawo 😊😂

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Місяць тому +1

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂koma maboza akhala apa ai ayi dzinanamizani anthu akumulanje tcholo phalombe ndi chilazulu amenewa ndamene amabvela zanuzi zaziiu

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi Місяць тому

      Komanso inu mumataya thawi bwanji kumamvela ngt akukukakamizani? Pezani Zina zochita ife tizimvela mpaka chikangawa achoke

  • @user-yi2fg1lh8x
    @user-yi2fg1lh8x Місяць тому

    Ayi,, lord almighty will reward you

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Місяць тому +1

    Ukunena zoona opposition party si akuonesa chidwe ali gone azawo akuyenda mipingo kugura anthu. Koma Mulungu kumwamba wava kulira kwa amalawi

  • @user-fu3ni7fn1f
    @user-fu3ni7fn1f Місяць тому

    Proud of you

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s Місяць тому

    Mr chikangawa chakwera ndi a gwape azakowo mukunama zisankho simubera tikubwera ku Malawi komweko Joyce Banda ndi

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope Місяць тому +1

    Joice Banda joice banda ukuwaphwetekesa amalawi matako ako

  • @InnocentKadoma
    @InnocentKadoma Місяць тому +2

    Akunamatuuu😂😂😂😂 the DC amusiye

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f Місяць тому

    Adzinamiza amenewo .Teroni ndithu akatengedweko

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂 u are, the man eeeee

  • @violetkamvanthupi2443
    @violetkamvanthupi2443 Місяць тому

    Mmmmmm koma abusawa bwanji? Samauopa mkwiyo wa yehova

  • @user-pc7hj7hs5v
    @user-pc7hj7hs5v Місяць тому

    Takulandirani Mr Ntanyiwa mutimvesa kukoma

  • @ChisomoBanda-g5s
    @ChisomoBanda-g5s Місяць тому +2

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥👍👍👍

  • @ChikumbaLenzo
    @ChikumbaLenzo 23 дні тому

    mulungu wanthu siokufa ndiwamoyo zizitheka zimenezo

  • @user-lh6ou1vh5w
    @user-lh6ou1vh5w Місяць тому

    Koomatu kuli zinthu...ndalama zija .,.mmhuu

  • @MalikiAlex-wn8jc
    @MalikiAlex-wn8jc Місяць тому

    Yeah 😅 zikufunikadi tidzichangamuka a Malawa osamawopa yeah

  • @ivymakiyi
    @ivymakiyi Місяць тому

    Mukuluza track tsopano ndi mabodza anuwo aaaaa ,munaphunzira mpaka pati,mmmmmmmm mupusatu

  • @elishamael-shadai
    @elishamael-shadai Місяць тому

    Pliz Comrade release the audio

  • @MarieSoko-z2z
    @MarieSoko-z2z Місяць тому

    Chete ana a peter munthalika ndipo satibera ayi

  • @wadsoncontinue3017
    @wadsoncontinue3017 Місяць тому

    It's a sign of umbuli kumavera zopanda mutu izi. Tipase umboni iwe. Osatipasa meeting yo bwanj tiione

  • @Failoss
    @Failoss Місяць тому

    Antanyiwa t shirt musamuphonye Lezala kumachinjiri kuno. Thanks

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Місяць тому

    Ntanyiwa koma inu mulimbavinu kkkkk....anthueatu ndiwoyipa kwambili

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek Місяць тому

    Ndiye Ali busy mpaka watsup call
    Anthuwatu sakugona tulo

  • @MenardoJunior
    @MenardoJunior Місяць тому

    Mulungu si munthu mark my word

  • @ListerBarsonBanda
    @ListerBarsonBanda Місяць тому

    Mulungu watuma inu kuti muliwombole dziko lamalawi eish popanda inu sindikudziwa kuti zikanakhala bwanji mmmm osatopa please 🙏 please kumenya nkhondo ngati ya family yako 7:20 ukumenya ya dziko .Mulungu sakusiya choncho ndithu

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s Місяць тому

    Timakunyadirani a comrade ntanyiwa chakwera ndi a gwape azakowo mukunama mavoti simubera

  • @FelixMwakhula-cm2yy
    @FelixMwakhula-cm2yy Місяць тому

    Aululeni,tikufuna president owina mwachilungamo, Mulungu alipo kumwamba and tipemphera atikwana anthu amenewa

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs Місяць тому +1

    Limpopo yayamba bodza inu Rudo ndimpongozi wa chakwera ndy atuma bwnj boyfriend wake kkkkkkkkkkk

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi Місяць тому

      Nde akakhala mpongozi sangakhale ndi chibwezi???

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb Місяць тому

    Aunt joy nawonso

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m Місяць тому

    Ma audio muzitumiza ngati ma umboni

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa Місяць тому

    Ponyelela pa president chakwela fiti mulungu azakulanga

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s Місяць тому

    Mademo alipo wa polisi aliyense amene akayambise zopusayo zikamuonekera be owned

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s Місяць тому

    Nonse amene mudamvotera M.C.P ndinu zisilu za wathu mukupha anthu, kuba,kuonong,a

    • @FrancisMazamba
      @FrancisMazamba Місяць тому

      Ndipo zoona lne ndinavota ndinali ndilikumalawi Koma pano ndilikuno kujoni

    • @FrancisMazamba
      @FrancisMazamba Місяць тому

      Koma pano ndilindimaganizo kwambiri Kut ndikanadziwa ndikanangosiya osavota chifukwa ndinavotera mufiti

  • @user-cp4qt9hs8w
    @user-cp4qt9hs8w Місяць тому

    Apolice amene ananyamula machine km akuzuzikaso ndimunthu uyu chakwera nonse mitumbo yanu apolice ndimunthuso ameneyu ot adzalamuleso dziko lidzafika pat mbolizanu

  • @user-rl1ye8ki2x
    @user-rl1ye8ki2x Місяць тому

    Kkkk koma palibe chinsisi pa dziko lapansi

  • @AndreaLouis-wd8iv
    @AndreaLouis-wd8iv Місяць тому

    😂😂guys anyamata awa ulemu wawo

  • @MAFUNSOMOLESI
    @MAFUNSOMOLESI Місяць тому

    Kkkkkkk muli bhoooo kwambiri munthu wakulu

  • @PreciousHenderson-qc1hq
    @PreciousHenderson-qc1hq Місяць тому

    Jesus the nazarene knows everything chakwera you will immediately face the consequences

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Місяць тому

    Achita bwino kwambili ayambile iweyo kukupha 😅😅😅anthu omvetsa chisoni inu mufa mu zomwezo

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko Місяць тому +1

    ndpo maraw turo siizatheka

  • @mwale86
    @mwale86 Місяць тому +1

    Nde HE Dr Joyce Banda zikumukhuza pati munthu wachipani china aaaah koma this is cheap propaganda.nde WhatsApp call imakhala nde end to end encryption nde inuyo yagwela kwa inuyo how???

    • @user-lu5db5qk2o
      @user-lu5db5qk2o Місяць тому

      Koditu limpopo fm si ya mcp ndi anthu amalawi akuvutika ndiye inu a Congress musamabwere ndi ma coment amanyi mungotuluka we support nthanyiwa no matter what wamva iwe.

  • @AndreaLouis-wd8iv
    @AndreaLouis-wd8iv Місяць тому

    😂😂😂ana achepa

  • @kangungufoundation2020
    @kangungufoundation2020 Місяць тому

    Zambiri mwa nkhani izi zilibe umboni zimafunika kuti muziwonesanso proof kuti audio ndi iyi other wise it's just a propaganda nkhani zopanda umboni, we must our brain sometimes to think about these things

  • @ThulaniPrince
    @ThulaniPrince Місяць тому

    Zekariya 11
    15 Pamenepo Yehova anayankhula nane kuti, “Tenganso zida za mʼbusa wopusa.
    16 Pakuti ndidzawutsa mʼbusa mʼdzikomo amene sadzasamalira zotayika, kapena kufunafuna zazingʼono, kapena zovulala, kapena kudyetsa nkhosa zabwino, koma iye adzadya nyama ya nkhosa zonenepa, nʼkumakukuta ndi ziboda zomwe.
    17 “Tsoka kwa mʼbusa wopandapake, amene amasiya nkhosa! Lupanga limukanthe pa mkono wake ndi pa diso lake lakumanja! Mkono wake ufote kotheratu, diso lake lamanja lisaonenso.” ipite kwa apule

  • @SangwaniNkosi
    @SangwaniNkosi Місяць тому

    Ndipo mpaka kuvulidwa zovala?mlungu aliko ndipo mlungu azayankha.

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 Місяць тому

    Nanga pa chilimwe mumati bwanji

  • @MakawaSpliano
    @MakawaSpliano 19 днів тому

    Ok

  • @user-wu6vr6fk8n
    @user-wu6vr6fk8n Місяць тому

    Malawi wathu ali moto

  • @RitaKainga
    @RitaKainga Місяць тому

    Kuyankhula ndy mukuyankhula ,koma vuto ndatsogoleri athuwa sakudzuka,ativulalitsa

  • @user-lv9vf6rf8r
    @user-lv9vf6rf8r Місяць тому

    Timakunyadirani a Limpopo

  • @MveraNambala
    @MveraNambala Місяць тому

    Tiye. Nazo muthanyiwa

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m Місяць тому

    Zoona a opposition akugona kwambiri

  • @user-vp6fv2mu6i
    @user-vp6fv2mu6i Місяць тому

    Koma mfiti Chakwera mulungu akukanthe sure

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Місяць тому

    Naiyi yokha antanyiwa mwatinamiza chifukwa ngati mumamcera olo inali WhatsApp call bwenzi mutapanga record kuti a Malawi tizimvela ndikuti anthuwa ayalukedi zenizeni. Mesa samakupezani? Ndebwenzi tsiku lina mutawaika pa air ife ndetingaturukedi mwaunyinji not like this sizikubebanso

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Місяць тому

    awatu tithana nawo gen z sakuyiziwa ndipo sitizawapha Loma stroke😂

  • @user-wb9ji3oe5o
    @user-wb9ji3oe5o Місяць тому

    Ife chonde nafe tikufuna ma T Shirt ya MALAWI FIRST.

  • @HappyAntenna-sf9qx
    @HappyAntenna-sf9qx Місяць тому +1

    Koma anthu muli ndi bodza

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d Місяць тому

      Muthu ukuona kuti munthuu ndi wabodza osamataya thawi yako ndi muthu wabodzayo bola osamavela program yake

  • @MilikaKilion-tn1bn
    @MilikaKilion-tn1bn Місяць тому

    Kodi mukamati dzikoli akuliva kuwawa ndi Anthu akumpoto ndi akumwela apakati Fe sugar tikugula 200 kwacha thumba lachimanga tikugula 5000 nanga feteleza tikugula 20000 tamdimasulilani ine chifukwa kunena zoona aliyese akuvutika chifukwa cha Boma ili ndiye mwina tili ndi zigawo zapakati ziwili pa malawi. Pano koma naa dela lakwathu palibe akuva kukoma

  • @rhodahjere8747
    @rhodahjere8747 Місяць тому

    Kkkkkk agwa nayo achakwera

  • @BlessingsMassi
    @BlessingsMassi Місяць тому

    Mulungu odziwa kuteteza azikutetezani a mtanyiwa

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma Місяць тому

    Joice banda upole moto panyini pako

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s Місяць тому

    Wapha chilima ndi anthu onse anali mu ndege ija ndi chakwera, Joyce nayenso ali mommo anthu a satanic Inu nonses

  • @JudithAbinaele
    @JudithAbinaele Місяць тому

    Hmmmm guys zinazizi mungofuna ma views eti??? Nanga ndi Boni yemwe kuchita kumusonkhanisila mfuti? Munthu wakufa kale uja inu?

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s Місяць тому

    Palibe kubera mavoti sitifuna Malawi akhale wa satanic zidzitheka