BRIAN BANDA, WONDER NSISYA, CATHY MAULID KUYANKHURAPO ZOMWE ZACHITIKA KU CONVENTION YA UDF LERO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 2 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 41

  • @LiamMwinga
    @LiamMwinga 11 годин тому +4

    Cathy maulidi umatha ndipo Malawi muno ngati mu best female journalist nde ndiweo

  • @merryMaele
    @merryMaele 16 годин тому +2

    Mrs Lilian Patel mai wandale wosagwedezeka chiyambire UDF nganganga May God continue showering favours on You Madam Patel

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 17 годин тому +1

    A Brian akunamizira kuiwala kuti UDF siinakhalirepo limodzi nanga paja pano anakwera ya DPP. UDF INAPANGA ALLIANCE NDI MCP SAKUDZIWA ZIMENEZI?

  • @bazalikasokomera
    @bazalikasokomera 15 годин тому +1

    Mukhala ngat sa malawitu mwaiwara kare kut UDF inaphatikizana ndi MCP 2009 pamene akafuna kuchotsa BINGU

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane 14 годин тому +1

    Mzimayi wosanzunza mutu wake ndi zomangamanga koma wapa ntchito yake yapamwamba, ulemu wanu a Cathy Maulidi

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 16 годин тому +1

    Komaso akangopanga part ndi mcp basi aononga abakili amulakwira mwana wao sazalamulira dziko lathu

  • @Sofi-p1v
    @Sofi-p1v 18 годин тому +2

    UDF akwatirana ndi MCP

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 15 годин тому +2

    Kuyima paokha nkuzinyenga ndi chala sure,matama a chule 😂😂

  • @RobsaiSaidi
    @RobsaiSaidi 7 годин тому +1

    Your videos trips bwanji makosana... improve...tiziva mosaduphadupha...pena tikumaona ma blue, names scrolling 😢😢 i enjoy watching your videos but zikhala smooth to match others

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 3 години тому

    Ulemu wanu guys 👦 best of the best 👌 TV 📺

  • @drbanda6105
    @drbanda6105 17 годин тому +1

    UDF...2025🎉🎉🎉

  • @kearabetswemashego3084
    @kearabetswemashego3084 15 годин тому +1

    Kunena chilungamo atupere sanazifotokoze bwino

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 4 години тому

    We need alliance please 🙏😢

  • @RobertGoliat-gt2qh
    @RobertGoliat-gt2qh 16 годин тому +1

    UDF siingawine paokha tisanamepo apa akapanga chibwana ithera pompo

    • @cynthiakananji1608
      @cynthiakananji1608 16 годин тому

      Ndipo abakiri akufuna kupanga part ndi MCP ndiyetu Anya aona anthu sangavotereso

  • @NoreenNaituri
    @NoreenNaituri 6 годин тому

    UDF yapanga kale ngwilizano ndi MCP ine ndaziona kale and zikuchita kuoneka machitidwe ake

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 3 години тому

    UDF payokha siingawine, they should join either DPP or MCP,one of these two parties will win next election,,, ndale sitinayambe lero😂😂😂😂😂

  • @DerlinNyirenda
    @DerlinNyirenda 11 годин тому

    Brian is the kadeti

  • @AhmedJali-xf3rw
    @AhmedJali-xf3rw 38 хвилин тому

    Koma wonder umandisangalasa kwambili uli ndi fundo kwabasi

  • @AndyChiwina-x8i
    @AndyChiwina-x8i 16 годин тому

    Brian Banda kodi ndiwe mtolankhani? Kapena cadet? Mumazinongera mbiri ya utolankhanitu, umadana ndi boma chifukwa anakuthamangitsa ku state house?

    • @victorbanda9039
      @victorbanda9039 15 годин тому

      Munthu amene akuononga Malawi ndiameneyu

    • @RanoKanyoza
      @RanoKanyoza 9 годин тому

      ​@@victorbanda9039osati a zbs

  • @DerlinNyirenda
    @DerlinNyirenda 11 годин тому

    Brian Banda kadeti
    You have sankho. Very bad mtolankhani.
    Remove hatred

    • @RanoKanyoza
      @RanoKanyoza 9 годин тому +1

      Mwaiwala aku zbs alimbali yaboma mukuona kumodzi brian akutiyankhulira mtundu wamalawi

    • @KhooMadex
      @KhooMadex 43 хвилини тому

      Katengeni khoswe wanu chawezi adzikuyankhulirani afisi okupha inu

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 4 години тому

    Atupele anthu amakukondani koma tikuuzileni mayeso anthu amadandaula bwana kuumila plz plz tayambani kufewa manja anthu anu azinva kukoma plz

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 2 години тому

    Anyamata inu simulibwino😂😂😂😂mpaka udandaula kuti kwina simunadyeeeeee eishiii 😅

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv 13 годин тому

    Apapa pokha watinamiza ndevu zamwayi wowo mpaka nyelele kuseza golo wa disl 😂😂😂 kmabe kumalawi palibe chipani chomwe chingatenge chokha Boma

  • @sulagrey
    @sulagrey 6 годин тому

    Brain ndi one cathy ndi 2 andevuuu ndi 3

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 16 годин тому

    Ang'alureni sangawine paokha iwowo😅

  • @TrigaKadango
    @TrigaKadango 17 годин тому

    Chosatheka ndi munthu chitheka ndi mlengi

  • @BiliatMzungudala
    @BiliatMzungudala 18 годин тому

    Tangovomelan ajesie kabwela si anzanu guso 😂😂😂

  • @sulagrey
    @sulagrey 6 годин тому

    UDF BOMAAAA

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Годину тому

    Mmesa munaponya kale zulo izi

  • @mikebernabechimundi3472
    @mikebernabechimundi3472 14 годин тому

    Ma dolo awawa ndi a mabodza heavy kkkk

    • @RanoKanyoza
      @RanoKanyoza 9 годин тому

      Ma bodza amakambira pa air

  • @JoelKacheche-x6i
    @JoelKacheche-x6i 15 годин тому

    ❤Chilungamo ndichakuti udf pakalipano ikuziwa kuti mdani wawo wamkuru ndi chipani cha dpp,chipani chokhacho chomwe angapite nacho kuchisankho ndi Mcp basi,a dpp muli mmazi kulibe kulowanso mboma boma ndilomweli sitikusntha anatero mayi wamphamvu Dr Jessey kabwira❤❤❤😂😂😂

    • @Kelvin-hj5qv
      @Kelvin-hj5qv 13 годин тому

      Kkkkk 🤣🤣 Oooh km Yaa ndipo inu UDF Dani wake ndii DPP bwino km sizingatheke KT angawine a MCP never akupitaso kuja 30 😢

  • @MasterJailos-kv5sd
    @MasterJailos-kv5sd 18 годин тому

    Udf wili win

  • @MasterJailos-kv5sd
    @MasterJailos-kv5sd 18 годин тому

    Udf wili win