Mwaimvera speech ya president wa UDF inu ma Cadets a DPP komaso chitsiru Enock Chihana? This is a powerful speech, speech yosanyoza a Chakwera komaso MCP. Congratulations Atupele, you have my vote 2025. Shameful to DPP and Chitsiru Enock Chihana
Aisha mambo iwe galu naweso kama gayezi UDF bas itulukidwaso Nkhankha zaona mwaona Zina chitika interview ya acheya zimene amawafusa ndimumene amanenela mungandiuze kuti zimene
congratulations. boy.

Mukupita konko 😂😂😂😂😂
Siyani kuphatikiza ndale ndi mpingo wa chisilamu komaso za kubanja
Amen allah akudalisani ulendo uno tupere awina musi allah
We need to change the system of government federal no Party will get 51/%
Bravoo!!!
Chipanichi Cha udf ndi mcp zimandinvesa kukoma ,koma chipani Cha alomwe sindifuna nitachionaso Malawi muno chipani chopanda khalidwe
My vote❤
We need alliance please 🙏😢
Amen
My love vote ❤
Congratulations ku UDF
atupele my vote
Amen
DPP is UDF enemy number 1. DPP killed UDF. Pakanapanda Bakili Muluzi bwezi kulibe DPP. Chipani chosayamika zomwe UDF inapanga. Chair Muluzi spent his energy inorder to sell out Bingu, koma mbizi za DPP kumumangaso Chair Muluzi. Anthu oipa agalu mxiieew
❤❤❤❤❤
🎉🎉🎉🎉🎉chipani ichi chili mbili yabwino mukanayesesa koma chifukwa kuthekera kulipo kozatenga boma eeshhii our last hope is in you Malawi sali bwino
Aisha mambo iwe galu naweso kama gayezi UDF bas itulukidwaso Nkhankha zaona mwaona Zina chitika interview ya acheya zimene amawafusa ndimumene amanenela mungandiuze kuti zimene
Zakhala ngati zaufumu