Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
I love Moxy, Kamtande, profet, sauzande, love D ndi Phweteka, ma gys amenewa amakwana Ka padzaso nako
Kodi a Jah man akufuna kuyamba uchifwamba 😂😂😂
Tichosa ntchito uyu 😂😂
Ndayamba kuonera series iyi chifukwa chankhope ya Lucy
Mkanaonesa bho mwomwe anaphulira Lucy
Mafana okutha mesa, mpweteka ndi friend wake uja
Ngolombe samadziwa kt aprophet amatimba
A jah man sound up prz
Uncle k .alikuti yawo ija ndi luse
Big up Lucy,Noxy amapanga zopoyila apa waganiza mochedwa
Gate mn yuuu ati acting imeneo aaaah mwatinamiza
Km noxy mumandiwaza kwambir mumatha mn iwe nd one kwa ine
Kma m'prophet ai ndithu matama kwa eni ake zoona
Apulefeti apeza udindo kwa 2mins
Watching from boksburg north SA 🇿🇦❤
Yaulendo uno camera mbola so udindo mbola pls tikhozeren zimenezo mabige koma inali mwala hvy☠️💪
Gusys tima film tanut mwayamba kuchepesa ma mnts tingoonela scine yamunthu mmozi bac
Midrand Pretoria am here watching Getto ting
This week sound mukodze km zili mwala🔥🔥
Km Lucy munvele noxy ndiwako
Kma mission ichitike mwachangu kma
Ina insachedw tikudikilil 😮😮😮
Uncle k mwabisala kwakwana tuluklani😊
Eeeshhh koma Prophet saxatheka😂😂😂 kkkk jaman alibe ganja angofuna abande nawo basi 😂😂Noxy wapepelatu apa kkkk okapepesa hahaha
Move ndiyabho koma ikumachedwa kutuluka try to make fast or realise more episode
Magetters mumakwana guys ❤
Where is kantande episode iyi sinakome bwanji
Massive
Kodi apolofeti makhalidwe anji ameneo ndi Lucy yo😂😂😂mpaka kuwombana miyendo 😂 Polan moto...Timakunyadilan guys keep it up
😂😂😂 kodotu a Noxy apapa no mpata 😂
Tafika kale 🔥🔥🔥
Lucy walemeraso nthawi zanji plizi
Gate-man wokula mtimaso😂
Mwayamba bwino kwambili guyz kamo aRass next week muwonjezele mawu wezisitikukunvani kwambili maka pa mission pokhapo muyesese mawuwo tinvenawo sitikakunenezani ku police ayi iii 😂😂😂😂😂
Inenso mpaka ndinatenga ma head phone
Tobias wonjeza kwambili
Kkkkkkkk kom nox abale wayamba kuvesa chisoni abale iiiiiiiiii
Live from Dubai
Kd izatha lit gn imeney? chifukwa ndye ikupitabetu
Koma voice ikumazatsika hvy pena... Plz kozani zimenezo
Lucy ndiwooneka bho koma
Too much shot 😢Mu episode tima event mzikhakhako tingapo....
Timadxikonda idzi ifeee
This is what I wanted
Watching from joz
Hope you enjoyed it!
Tsopano Lucy walemeraso nthawi zanji,,, a noxy ndika T-shirt kawo kokwinyikako olo true love yo uyambira pati
Ndipo Lucy walemera liti abale
Koma Noxy😅😅😅😅😅
Koma phrophet
Mmakwana
Km Ana a xool awawa ai
Camera shooting lero sidali bo gyz.Koma deal ikupana achina Nakinaki iwathandiza?A Lucy kkk vacancy yake yatuluka lit 😅😅😅😅😅 Koma nonse muli bo gyz
Mumatha guys
Aporofhet mumakwana😂😂
AA a prophet makani bc ah akamuchosa tcheto Muthu osamuziwa kuti akulandira zingati 🤔😂😂😂😂😂😂😂😂
Aaaaaaa achiko aja nda serious Plus atha kupwetekesa munth😂😅😂
Eh guys noxy why life akulida noxy Pano eh no balance at all 😕 what you luce now you know what is life 😁 sorry
Lero sindsiya comment iliyose apa guyz 😂😂😂
Wasiya kale
🎉🎉🎉 9:24
Noxy game yatembenuka
I ddnt like this episode crc guy although am a fun
ife yatisangalatsa vaya uko iwe
@ kod nd milandu?
Even me especially when it comes this so called prophet, he doesn't know his side, always mixing things 😢
I love Moxy, Kamtande, profet, sauzande, love D ndi Phweteka, ma gys amenewa amakwana Ka padzaso nako
Kodi a Jah man akufuna kuyamba uchifwamba 😂😂😂
Tichosa ntchito uyu 😂😂
Ndayamba kuonera series iyi chifukwa chankhope ya Lucy
Mkanaonesa bho mwomwe anaphulira Lucy
Mafana okutha mesa, mpweteka ndi friend wake uja
Ngolombe samadziwa kt aprophet amatimba
A jah man sound up prz
Uncle k .alikuti yawo ija ndi luse
Big up Lucy,
Noxy amapanga zopoyila apa waganiza mochedwa
Gate mn yuuu ati acting imeneo aaaah mwatinamiza
Km noxy mumandiwaza kwambir mumatha mn iwe nd one kwa ine
Kma m'prophet ai ndithu matama kwa eni ake zoona
Apulefeti apeza udindo kwa 2mins
Watching from boksburg north SA 🇿🇦❤
Yaulendo uno camera mbola so udindo mbola pls tikhozeren zimenezo mabige koma inali mwala hvy☠️💪
Gusys tima film tanut mwayamba kuchepesa ma mnts tingoonela scine yamunthu mmozi bac
Midrand Pretoria am here watching Getto ting
This week sound mukodze km zili mwala🔥🔥
Km Lucy munvele noxy ndiwako
Kma mission ichitike mwachangu kma
Ina insachedw tikudikilil 😮😮😮
Uncle k mwabisala kwakwana tuluklani😊
Eeeshhh koma Prophet saxatheka😂😂😂 kkkk jaman alibe ganja angofuna abande nawo basi 😂😂Noxy wapepelatu apa kkkk okapepesa hahaha
Move ndiyabho koma ikumachedwa kutuluka try to make fast or realise more episode
Magetters mumakwana guys ❤
Where is kantande episode iyi sinakome bwanji
Massive
Kodi apolofeti makhalidwe anji ameneo ndi Lucy yo😂😂😂mpaka kuwombana miyendo 😂 Polan moto...Timakunyadilan guys keep it up
😂😂😂 kodotu a Noxy apapa no mpata 😂
Tafika kale 🔥🔥🔥
Lucy walemeraso nthawi zanji plizi
Gate-man wokula mtimaso😂
Mwayamba bwino kwambili guyz kamo aRass next week muwonjezele mawu wezisitikukunvani kwambili maka pa mission pokhapo muyesese mawuwo tinvenawo sitikakunenezani ku police ayi iii 😂😂😂😂😂
Inenso mpaka ndinatenga ma head phone
Tobias wonjeza kwambili
Kkkkkkkk kom nox abale wayamba kuvesa chisoni abale iiiiiiiiii
Live from Dubai
Kd izatha lit gn imeney? chifukwa ndye ikupitabetu
Koma voice ikumazatsika hvy pena... Plz kozani zimenezo
Lucy ndiwooneka bho koma
Too much shot 😢
Mu episode tima event mzikhakhako tingapo....
Timadxikonda idzi ifeee
This is what I wanted
Watching from joz
Hope you enjoyed it!
Tsopano Lucy walemeraso nthawi zanji,,, a noxy ndika T-shirt kawo kokwinyikako olo true love yo uyambira pati
Ndipo Lucy walemera liti abale
Koma Noxy😅😅😅😅😅
Koma phrophet
Mmakwana
Km Ana a xool awawa ai
Camera shooting lero sidali bo gyz.
Koma deal ikupana achina Nakinaki iwathandiza?
A Lucy kkk vacancy yake yatuluka lit 😅😅😅😅😅 Koma nonse muli bo gyz