Zimene akuganiza a mcp ndi zopenga ,chifukwa President Peter Mutalika sakaimila ku nyumba ya munthu akuimilira amalawi. Ngati atumidwa ku satanic azikapha abale awo,zonunkha amalawi sakufuna anthu sakukufunani mukuwakakamira bwanji? Zopusa ife sitikufuna amalawi, Peter Mutalika ndiye amene ali chiyembekezo cha amalawi.
Mayz oro atatenga chileso ife wathu ndi adadi bs kkk
@@StephanoIssah 💙💙💙💙
Whether there's no Peter or Peter, but dpp will make it, win win❤
@@CharlesMotloung-w3n until forever 💙💙💙💙
Malawians we are God fearing county..tikupempherera ife dzikoli president tikusintha ife.. Mulungu akuoneni amene mukuzunza anzanu inu
Ndipo ukunamatu iwe APM alowa alore alore akane akane
Ukunama adady 2025 Boma😅
Peter muthalika is a retired president he cannot stand whether u like or not
Who told you that he is a retired president?
Who told you he's retired?
@@EmmanuelJoseph-lj5eu ask him my brother
Mukumuopa APM..mulungu sakulola
@@RosinaPatel ndiponso sangalile
Agalu a MCP MWATIKWANA musatinyasepo kazingopakilani ulendo chaka ichi
APM kaya wina afune olo asafune akutenga Bomaaaa chakwela kodi bwanji kuwakaka milila a Malawi tatitu sitikuyifuna watizunza kokwanila kafike bwino
inu. chakwela zikoli silake. zimuvuta yekha. koma pano sakuwinaso. zamuvita zimolino silske komaso kuno sikurwanda. kuno ndikumalawi.
That is no sense papa PM his has to stand as a president of Dpp and Malawi 2025 to 2035 🎉🎉🎉❤❤
@@CharlesMoffat-u1i 💙💙💙💙💙💙💙💙
Panyapanu amcp
Zimene akuganiza a mcp ndi zopenga ,chifukwa President Peter Mutalika sakaimila ku nyumba ya munthu akuimilira amalawi. Ngati atumidwa ku satanic azikapha abale awo,zonunkha amalawi sakufuna anthu sakukufunani mukuwakakamira bwanji? Zopusa ife sitikufuna amalawi, Peter Mutalika ndiye amene ali chiyembekezo cha amalawi.
Trump
Zikoli silanu musatitengele kuntoso mwamva a mcp ndi President wanuyo siife anthu anu ayi akutumani zolakwika satanayo chiseko chikupanani simunati
Age Limit tinathana nayo.Kungotu nfti zikuteri angofuna chisokonezo m,Dziko muno.Abale Atsogoleri mulibe Chisoni Kodi m,ene AMalawi tikuvutukila?
Koma ndiye ziliko
Akunama ameneyo tikulephela kudya ife aziona
Moyo wa munthu uli mmanja mwamulungu ambuye kumwambako amutetezela apm
Bola tadziwa tizaona poyambira pake ,mwatchukatu koma
Ambuye akuwateteza adad mulungu ndi wa dongosolo palibe chida chosula chimene chigwire ntchito pa APM mu dzina la yesu mwazi ukumphimba wa yesu
@@GraceLimani-zw7dx mulungu awakonde add💙💙💙💙💙💙
Tatopanaye chakwera
@@EmmanuelChaluka komanso sitikumufuna
Munya manyi nose
Pamsanapanu munya muona aima
Ziwasata okha mcp amufuse mble wake gagame ngati asamunyonge ndi mwayi wakw
@@NdaonaMsowoya komanso AWA angozinamuza💙💙💙
Mapwaka wa mcp
Sizingatheke mudzina la yesu
@@EmmanuelGodfreynkhoma ndipo zoona zake ❤️😘❤️
Jesus christ
Chikangawa akuchoka avuneaza fune
@@YassenYasin-v6o ndipo alibe thawi
Mulungu simunthu ndipo sangayang'anire mfiti kuzunza anthu ake
@MosesTangwe-q8o 💙💙💙💙
Adad omweo
Sizitheka ndinthuuu
@@TinasheKamanga-p9c komanso Ife sitilola
Koma sizitheza, munalanda Boma, muona nyekhwe simunati Mr Chikangawa, Viva Malawi 🇲🇼 ♥ ❤ Malawi 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼
@@eunicesaiti ndipo anya.manyi ameneyo
Mulungu alipo
Ndipo awatetezera adadi
Alomwe mukulongolola kwambiri
Tiyenera kulongolora iwe umati
@@ShillaShamil-v2y ndifusileni Kwa ameneyo