BON KALINDO THE DC 19/5/24-ANTHU AKUNCHINJI ALIMU LOLE KUPITA KU NSONKHANO WA AFORD ATUMIDWA NDI MCP
Вставка
- Опубліковано 18 тра 2024
- #malawipolitics #numeroyapastorntambabazi0788554028 #news #duet #bongotv #zodiaktv #31march #aford #march2019 #humour #live
#livestream #livenews #livetipsandtricks
watch ZODIAk CRUISE 5 WITH MLAKA Malilo part 2 here
• ZODIAK CRUISE 5 NDI ML... - Розваги
MCP mwabisala Mmbata, ufumu wanu wankhanzawo mudz iwe kuti siwukupita patali ayo
Komano mcp ikupangilanji zimenezi
Koma emusipi
Moses kunkuyu anapha a Allan witika chifukwa cholimbilana nkazi
Osayiwala msewu wa Neno
Alhomwe pamtumbo panu, central region is not alhomwe belt, anthu othawa nkhondo inu dzitsilu dzimachende dzambuyanu
True ndima folena
Exactly awo ndima fouraner
Aford akanalamla kale kale koma ndichipani chovesa chifundo zoona angapange alayasi ndi chipani chakupha abale achilbino mkhalabe kuja zikuvutani adpp analonjeza kuti amanga sukulu ku edingeni kodi anamanga kalindo ndwe chisilu
Nanga chakwera wako mchani wapanga pazomwe ankalonjeza , chomwe wapanga mbuye wake ndi devaluation, high cost of living, nepotism amawanena a dpp iyeso pano akupanga zomwez, corruption nde yangokhala ngt chikhalidwe, afford mesa inali mu mcp momo nde ngt aganiza zolowa chipan china zakuwawa bwanji, mulimbana mkumanga anthu kumakhapa anthu instead of kukoza pomwe mukulakwisa kt amalawi akukhulupiliren kma busy kumaba ndalam mkumanga anthu akakuuluran nyasi zanu
Mmamnyoza mtambo pano poti naye wayamba kunyoza ndimbwenzi kalindo satanic ndipo amagwilizana ndiwina amene walowa mgulup la kunyoza satanic kalindo adpp akupasa ndalama dairy koma iye akuwona ngati anthu sakuziwa chisilu or utayankhu boza lannji mcp satekeseka
Panyapako iwe mutu waukuluwo ngat chimwendo banda
Kkkkkk