Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Iyiy ndi moto I wish patoranking akanaimba nawo💥
My wish too
Uyu ndi patoranking wa ku Malawi 🇲🇼 seriously 🎉
Iwe this tune sili bho off course adawa ndima wa fila km na iyi yokha mmm ayi nd panja
Muli ndi ndivuto ankolo
😂😂😂 are you joking?@@VyberKhama
Ndimafila Malinga km this year award mwatenga boss ❤❤
Kwa amene tanvera pa speaker yaikulu tipange like apa 🔥🔥
Martse foundation fans let's gether here
``Too ghetto too gutter``🔥🔥🔥
Gether or gather
@@SceloMsweli-e6n paka gramma ummm bro I don't have time to play
Chaka chino award akatenga wina ndekut atibera, this is dancehall ❤❤❤
Nkhani ndi kuvota
Ngat Sean Morgan sitimpatsaso award this Year Ku Malawi zinyengo sizizatha
Legend of all time ndi fadah Sean 😂😂😂🎉🎉mwangofka Inu kukuzizira kwatha mesa Inu ndi 🔥🔥🔥🔥
Ndiwe dolo ngati Patorunking who agrees with me???
Real tings🎉 quote zawudolo wanga yisakhale funso
@@AdamsonSembo in Martse's voice🤫
Iyi ndi 1, ichi chimayimba like patoranking I hope when he hear this song mupanga chi bale heavy 👌👌👌🤞🎶🎶🎶🎵🎵🎼🎼🎧🎤 Talent boy, Unabwela kuzakha, young n free🎶
Mzuzu pple let's gather here uyu ndi wathuwathu
Timanena mobwelezabweleza..... Sean Morgan ndamene ama runner dancehall ku Malawi kuno!!!
Uyu wabwela ngati coming 💥
Mukazangoti zii ife tizagendaaaInu mmawona ngat amacheza 🎉🎉🎉 Sean akasiya tizinvera chan
Ndipo kusiya iyeyo kaya tizimvera chani 😅
Sean Morgan iwe ndi dolo aise ndimakufira hvy ndipo nyimbo zako kwa ine palibe yoipa siku lina uzabwereko kuno Cape Town 🧘♂️🔥
Kwa amene taimvera full brast mu galimoto like tione
Panyimbo zonse koma iyi ndiye eee waomba bro ngati anointed ija bwera pa casualinapa umwe umodzi
This man deserves an award 🔥🔥
Uyuyu et aaaa anamaliza masewela❤much love my favourite dancehall artist here in mw🎉
Mwatipanikiza ndima hit🔥
Director Kante palibeso! Za FADA Sean nde mukudziwa kale ndi chilombo
Iwe ndi dolor aise🎉
Nyimbo yowinira ma award 🎉
Fully Sean dih Ghetto Icon 🙌🏾🔥
Commenting for the second time...this guy is really something else 🔥🔥🤝
Dadament sopanooo 🔥🔥🔥🔥🔥
Level yachina Patoranking🔥🔥🔥🔥
Uyuyu anabwera 🔥
RIP too ghetto too gutter Zaudolo wanga fadah lisakhale funso 🫡Iyiyi yaphedwa eeh
Uyu ndikutunda Ku mountain 🔥🔥
the boi deserve a lot of Awards 🙌
Fadda amvera kwambir patoranking.... Keep it burning son of the Big league representing Getto 🔥🔥
Ndiwe dolo kwambili bro 🔥
Our own Sean Paul🥳🥳🥳🥳 iweyo Sean Morgan ndiwe dolo aseeee🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
🎉🎉 Iweo umatha Sean Morgan
Mr Morgan 🎉....pezani malo opita mphepo. Ntchito yagwilika . Big tune !!
Za udolo wanga pano lisakhale funso legend recognize legend 😂❤❤
Machine anga awa🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤ iweyo award chaka Chino ilimanja mwako
The hit and the vibe ngatidi ta-winner lotto🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mwatipanikiza ndima Hit Dada
Chinyimbo chovinika amwene🥳🥳🤸
Nyimbo iwe 🔥 Big league ife tili mkati
Ndiye zomwe waipanga #kantezo 🎉🎉🎉🎉
Osamangolubwa kut muma runna Dancehall. Bwerani kuno Dancehall icon akuphunzitseni kuyimba 🔥🔥🔥🔥🔥, @Sean Morgan to dee world
I think dolo wa dancehall akhale emweyu basi big up big league
Eeeeh bigy up broh unabwera iweyo
Iweyo ndi level Ina AdaInternational material
Iyiyi yakungidwa. Siza chitelera ayi😎
Big league ....Iwe ndikatunda aise though ndafikako mochedwa koma sinachedwe ulemu onse and lero kwatuluka nyimbo yako yokha😊😊😀
Patoranking wachi malawi 🇲🇼.... Umaswepo ndi brasto 1 day
❤❤ Dadament kwayaka moto ndi KuNo ✊
Ndiyemweyu bas Morgan on fire 🔥
Sean Morgan fans let’s gather here 🔥🔥🔥
Fully active
Izii nde ndinyimbo ozati dzina zija 🔥🔥🔥
Sanapalepo mwangonuziwa kumene😂
Katundu waku Malawi uyu💥💥🔥🔥
Uyu ndi dolo❤
Fire iwe ukooo moto hit after hit unambwera sitizagendansotu apa 💪💪💪🔥🔥🔥
Director wa video iyi ndi shasha guys 🔥🔥🔥🔥🔥
Tizagenda nthaw izakwana komabe uli 2fa nd Kuno 🔥🔥🔥
Kukabwera ophwekesa Liza Siren 🚨🔥🔥🔥
Dada wa ma dada onse , inetu iweyo ndamene ndikudziwa kuti umayika dancehall
Ernegy ngambwingambwi....Moto kuti buuuuuuuuuuuuuuuuuuuu!!!!!
Never disappointe iwe ndi machin❤
Kuno 🔥🔥🔥 tinvera mwez onse 🎧
Dolooo!!🔥🔥
Ndili kutali level uko, zaudolo wanga lisakhale Funso "REST WELL MARTSE"
Level ukoo🔥🔥🔥🔥
Unabwera kudzakhala aise💥
Iwe ndi shasha🔥🔥
Ulemu wanu bgy mumapha sound 💪💪
Ichichi chimaimba danso yaukali jonas. Big up bredda Sean
NyimbO yabho..Pure lyrics, nice visuals.
Morgan ndichifaya amwene 🔥🔥🔥💯
Katswiri yo ndi inuyo fada 🖐️🖐️ nuff respect and blessings ras
Iweyo ndi shasha ase 👌👌
Son of the big league🔥🔥🔥🔥
Dude is something else 🔥🔥
Fadah munabwera kuzakhala 🎶
My hero sean Morgan ulemu basi 🔥🔥🔥🔥
the only malawian. who doesn't disappoint
Yeah apa ngat ndawinad loto
Eyetu izi nde nyimbo, composure 100%
Big league,,,dadament ikupanga zinthu.. next vids ku North bas nafe tili moto tizayasa🔥
Iyiyi yokha mkuluyu waipha ❤
Moni kwama fans ofira dancehall
Sean you're too talented Ndiwe dolo 👊
Mafuna ofira dancehall chaka chino tachiva kukoma💥🔥🔥🔥🔥☄
Ndipo heavy, apa pa repeat chan 😀
Nyimbo ili bh guys
🔥🔥🔥🔥Wayatsa iweyo shasha
Uyuyu ndi dolo
Pena ngati ndawina lotto🔥🔥
Woooooooooooow Mr Morgan respect kwa hiyi New hit Song International.
Ndiwe dolo kwambiri, RIP MARTSE MARTIN NKHATA
Tili nkati mwa gettoh🔥🔥🔥
Zopitira ku xul izi🔥🔥📸
Son of big league ❤❤❤
Son of a big league
Ghetto izirandira maulemu osatha ..mwafikado man Sean 🔥🔥🔥
Dolo katatu🔥♥️
Iyiy ndi moto I wish patoranking akanaimba nawo💥
My wish too
Uyu ndi patoranking wa ku Malawi 🇲🇼 seriously 🎉
Iwe this tune sili bho off course adawa ndima wa fila km na iyi yokha mmm ayi nd panja
Muli ndi ndivuto ankolo
😂😂😂 are you joking?@@VyberKhama
Ndimafila Malinga km this year award mwatenga boss ❤❤
Kwa amene tanvera pa speaker yaikulu tipange like apa 🔥🔥
Martse foundation fans let's gether here
``Too ghetto too gutter``🔥🔥🔥
Gether or gather
@@SceloMsweli-e6n paka gramma ummm bro I don't have time to play
Chaka chino award akatenga wina ndekut atibera, this is dancehall ❤❤❤
Nkhani ndi kuvota
Ngat Sean Morgan sitimpatsaso award this Year Ku Malawi zinyengo sizizatha
Legend of all time ndi fadah Sean 😂😂😂🎉🎉mwangofka Inu kukuzizira kwatha mesa Inu ndi 🔥🔥🔥🔥
Ndiwe dolo ngati Patorunking who agrees with me???
Real tings🎉 quote zawudolo wanga yisakhale funso
@@AdamsonSembo in Martse's voice🤫
Iyi ndi 1, ichi chimayimba like patoranking I hope when he hear this song mupanga chi bale heavy 👌👌👌🤞🎶🎶🎶🎵🎵🎼🎼🎧🎤 Talent boy, Unabwela kuzakha, young n free🎶
Mzuzu pple let's gather here uyu ndi wathuwathu
Timanena mobwelezabweleza..... Sean Morgan ndamene ama runner dancehall ku Malawi kuno!!!
Uyu wabwela ngati coming 💥
Mukazangoti zii ife tizagendaaa
Inu mmawona ngat amacheza 🎉🎉🎉 Sean akasiya tizinvera chan
Ndipo kusiya iyeyo kaya tizimvera chani 😅
Sean Morgan iwe ndi dolo aise ndimakufira hvy ndipo nyimbo zako kwa ine palibe yoipa siku lina uzabwereko kuno Cape Town 🧘♂️🔥
Kwa amene taimvera full brast mu galimoto like tione
Panyimbo zonse koma iyi ndiye eee waomba bro ngati anointed ija bwera pa casualinapa umwe umodzi
This man deserves an award 🔥🔥
Uyuyu et aaaa anamaliza masewela❤much love my favourite dancehall artist here in mw🎉
Mwatipanikiza ndima hit🔥
Director Kante palibeso! Za FADA Sean nde mukudziwa kale ndi chilombo
Iwe ndi dolor aise🎉
Nyimbo yowinira ma award 🎉
Fully Sean dih Ghetto Icon 🙌🏾🔥
Commenting for the second time...this guy is really something else 🔥🔥🤝
Dadament sopanooo 🔥🔥🔥🔥🔥
Level yachina Patoranking🔥🔥🔥🔥
Uyuyu anabwera 🔥
RIP too ghetto too gutter
Zaudolo wanga fadah lisakhale funso 🫡
Iyiyi yaphedwa eeh
Uyu ndikutunda Ku mountain 🔥🔥
the boi deserve a lot of Awards 🙌
Fadda amvera kwambir patoranking.... Keep it burning son of the Big league representing Getto 🔥🔥
Ndiwe dolo kwambili bro 🔥
Our own Sean Paul🥳🥳🥳🥳 iweyo Sean Morgan ndiwe dolo aseeee🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
🎉🎉 Iweo umatha Sean Morgan
Mr Morgan 🎉....pezani malo opita mphepo. Ntchito yagwilika . Big tune !!
Za udolo wanga pano lisakhale funso legend recognize legend 😂❤❤
Machine anga awa🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤ iweyo award chaka Chino ilimanja mwako
The hit and the vibe ngatidi ta-winner lotto🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mwatipanikiza ndima Hit Dada
Chinyimbo chovinika amwene🥳🥳🤸
Nyimbo iwe 🔥 Big league ife tili mkati
Ndiye zomwe waipanga #kantezo 🎉🎉🎉🎉
Osamangolubwa kut muma runna Dancehall. Bwerani kuno Dancehall icon akuphunzitseni kuyimba 🔥🔥🔥🔥🔥, @Sean Morgan to dee world
I think dolo wa dancehall akhale emweyu basi big up big league
Eeeeh bigy up broh unabwera iweyo
Iweyo ndi level Ina Ada
International material
Iyiyi yakungidwa. Siza chitelera ayi😎
Big league ....Iwe ndikatunda aise though ndafikako mochedwa koma sinachedwe ulemu onse and lero kwatuluka nyimbo yako yokha😊😊😀
Patoranking wachi malawi 🇲🇼.... Umaswepo ndi brasto 1 day
❤❤ Dadament kwayaka moto ndi KuNo ✊
Ndiyemweyu bas Morgan on fire 🔥
Sean Morgan fans let’s gather here 🔥🔥🔥
Fully active
Izii nde ndinyimbo ozati dzina zija 🔥🔥🔥
Sanapalepo mwangonuziwa kumene😂
Katundu waku Malawi uyu💥💥🔥🔥
Uyu ndi dolo❤
Fire iwe ukooo moto hit after hit unambwera sitizagendansotu apa 💪💪💪🔥🔥🔥
Director wa video iyi ndi shasha guys 🔥🔥🔥🔥🔥
Tizagenda nthaw izakwana komabe uli 2fa nd Kuno 🔥🔥🔥
Kukabwera ophwekesa Liza Siren 🚨🔥🔥🔥
Dada wa ma dada onse , inetu iweyo ndamene ndikudziwa kuti umayika dancehall
Ernegy ngambwingambwi....Moto kuti buuuuuuuuuuuuuuuuuuuu!!!!!
Never disappointe iwe ndi machin❤
Kuno 🔥🔥🔥 tinvera mwez onse 🎧
Dolooo!!🔥🔥
Ndili kutali level uko, zaudolo wanga lisakhale Funso "REST WELL MARTSE"
Level ukoo🔥🔥🔥🔥
Unabwera kudzakhala aise💥
Iwe ndi shasha🔥🔥
Ulemu wanu bgy mumapha sound 💪💪
Ichichi chimaimba danso yaukali jonas. Big up bredda Sean
NyimbO yabho..Pure lyrics, nice visuals.
Morgan ndichifaya amwene 🔥🔥🔥💯
Katswiri yo ndi inuyo fada 🖐️🖐️ nuff respect and blessings ras
Iweyo ndi shasha ase 👌👌
Son of the big league🔥🔥🔥🔥
Dude is something else 🔥🔥
Fadah munabwera kuzakhala 🎶
My hero sean Morgan ulemu basi 🔥🔥🔥🔥
the only malawian. who doesn't disappoint
Yeah apa ngat ndawinad loto
Eyetu izi nde nyimbo, composure 100%
Big league,,,dadament ikupanga zinthu.. next vids ku North bas nafe tili moto tizayasa🔥
Iyiyi yokha mkuluyu waipha ❤
Moni kwama fans ofira dancehall
Sean you're too talented
Ndiwe dolo 👊