KODI MNYAMATA OYIMBA WA TWIN M AKUDUTSA MUZOTANI??
Вставка
- Опубліковано 12 жов 2024
- After being quite in the music industry after the death of his twin brother, we made a follow up to understand what the remaining brother of the famous duo Twin M is going through.
I can imagine how you are feeling my brother...... Take courage ayise
So touching 😢
Koma Mulungu akukumbukire Aaron kuti maloto ako azakwanilitsidee
I can feel his pain 🥺. Nyimbo ina ya Angaliba, yachikhalidwe imandisangalasa pakana pano ❤
Zovetsa chisoni, koma limba ntima ndithu mbale wanga
Ndipo ine anyamata awa ndizawaokonda mpaka kale ❤❤❤
Ndizinthu zophweteka kutaya mbali imodzi yako😢😢 komade limba ntima mbale mulungu alinawebe sangakusiye
I can feel his pain💔
That's hard 😢😢
Zovesa chisoni kwambiri 💔💔💔💔💔🕊️🕊️😭😭😭😭.
Eish so sad ngat akupempha mpamba wa biznes ya zovala ,moyo wake wawawad sorry bro
I feel His pain
Maguys sadapangidwe support mokwanila awa koma luso lidalimo kwambili
Ndipo straight luso linalimo koma samapangidwa support anawa
Eeeeh zovta heavy
😢😢💔😭😭😭😭😭😭😭
Kom zoonad akusautsikad