Bon-Kalindo_Boma Limafuna Kundipasa Ndalama Koma Anduna Amalephera Kunena_Mademo Aliko Ku Mzuzu

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 вер 2024
  • Bon Kalindo Kuyankhula Ndi Amalawi Atamaliza Zokambilana Ndi Boma

КОМЕНТАРІ • 7

  • @gladysbonongwe7285
    @gladysbonongwe7285 2 роки тому

    More fire brooh kalindo,usamuope faraoh awombose amalawi mmavutowa

  • @williammhoni5729
    @williammhoni5729 2 роки тому

    Boni kalindo akubwera booh kwambili akufunadi kuongola ziko pamene silikuyenda bwino tiyeni akalindo tili pambuyo panu

  • @josephymtaya9048
    @josephymtaya9048 2 роки тому

    Akufuna kutchukirapo basi kkkk zinthu zakwera padziko lonse bwanji amalawi kupusisidwa muwonanga nazo dziko basi tiziti kusayenda or kusaphunzira mmmm

  • @angelicajoseph3080
    @angelicajoseph3080 2 роки тому

    It is possible just cut govt travelling and allowances expenses

  • @mlezanyirenda3993
    @mlezanyirenda3993 2 роки тому

    Koma msanyengeke ngati amtambo mtambo atampasa udindo sangalankhure panopa please kalindo usayerekeze kulandira ziphuphu

    • @leviphiri1547
      @leviphiri1547 2 роки тому

      MTAMBO ndi munthu wazeru alibe nazo ntchito zaukape. Mademo opanda phindu.timakhala pansi ndi boma dzikavuta ndipomwe timapanga ma demo. Osati poti chakwera ndi wofansa basi ma demo. Abwere Peter muzaone ma cadets azakupaseni zibakera ndi mademo anuwo.

    • @leviphiri1547
      @leviphiri1547 2 роки тому

      Mutambo anapita ku school sapanga nawo zawusilu