SINDIKUDZIWA CHOMWE CHIDAPANGITSA KUTI NDEGE IGWE NDIKUPHA VICE PRESIDENT/MAU DR CHAKWELA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 187

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk Місяць тому +21

    Wuyu si president ndi chiboli boli cha president

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 Місяць тому +10

    Akuyenera kufunsidwa,, coz asilikali achilendo amakatani ku Chikangawa 😢... Mudzayankha pamanso pa Mulungu

  • @AhmedHchipelesa-zm8oe
    @AhmedHchipelesa-zm8oe Місяць тому +9

    Uyu akudziwa mesa adati ndi chifunga ndiye sakudziwa so lelo wayamba kudzilumaso

    • @MoosahChikwakwa
      @MoosahChikwakwa Місяць тому

      Silent means (yes) wapha ? Chete, anthu akudabwa ndiye kuti wapha, key questions are, why silence? What people should expect? Do you have death results? Why did you delayed investigation of death? Why you don't know but you put inquiry for this?😢😢😢 But you, you, you, your days are numbered wallah.

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb Місяць тому +2

    Kodi lwe chikangawa umadana Naye chani kwen kwen chilima mpaka kuimisa asilikali kt asiye kumusaka chilima way way Lazaro lweyo umatha kupha galu fit

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f Місяць тому +2

    Hule iwe umapephelaso kod munthu ndiwe wa mcp kale Nde ujoyinaso bwanji hule

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Місяць тому +3

    Ndiye ngati sakudziwa zomwe zidapha Chilima nanga akumangiranji omwe akunena za imfayi.

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 Місяць тому +3

    Chomwe chinakupangitsani kuti muchedwe kukayamba kufufuza ndi chomwe ife sitikuvetsetsa ,komaso kuleketsa asilikali kuti basi tiyambaso mawa nchifukwa chiyani ? Keep Resting in peace Mr Saulos Chilima and all the other pipo who died in Chikangawa Continue to be Resting in peace and fight for justice for malawias so that choona chioneke

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh Місяць тому +5

    Mbuziiiiiiiii,,ikudya ufa koma sikudziwa kuti ndi ufa.

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Місяць тому +7

    Kulibe chobisika kuseli kwa thambo

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Місяць тому +4

    Komatu chakwera mau msamatha, RIP Mr president chilima 😭😭😭😭😭

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef Місяць тому +3

    Chakwera ndi wakupha basi, bwanji amachedwa kumafufuza Za kugwa Kwa Ndege. Akudziwa kanthu

  • @PaulineIsmael
    @PaulineIsmael Місяць тому

    Nfiti yamunthu okupha amatelo kunamizila chilunga uzafa ukuyeda mulugu Ali nawe konse mizimu ya anthu 9 unia uwona
    May your soul continue resting in peace Mr saulos and eight others
    I'm in Mozambique

  • @user-hu7qs5be4j
    @user-hu7qs5be4j Місяць тому +3

    Kkkkkkkkk Malawi dziko lonvetsa chison kwambiri ndipo amene anatembelela dziko ili mulungu amukhululukole sure, chifukwa ndidziko lonvetsa chison kwambiri

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 Місяць тому +5

    Udzachidziwa chimenecho 😭

  • @JonathanMsiska
    @JonathanMsiska Місяць тому +3

    Mafumu anthu azamenyani musamale mukuthamangila kulandila ndalama mumalo mosova zinthu musamale.

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Місяць тому +2

    Chakwela wakupha Mr chikangawa 😢😢😢😢

    • @AnnieBanda-rb2dk
      @AnnieBanda-rb2dk Місяць тому

      Mr chikangawa galu uyo chigawenga chamunthu kuchita kuwadula mapisimapisi azake galu iwe chakwera chikangawa chinkhope ngat chikangawa

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Місяць тому

      Umbuli wanu nde mwafika nawo pa 💯 😅😅😅

  • @lingstonenagoli7729
    @lingstonenagoli7729 Місяць тому +4

    Mmalo mokapepetsa ku Ntcheu kwao Kwa Chilima

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Місяць тому +2

    Iweyo kiungu ukunam
    Ngakhal kt asayankh pal chiyan chomwe awapangako zosonyez kt chifukw chakusayankh kuj wachit izii

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Місяць тому

    Chakwera ndimunthu oipa kwambiri dziko lonse lapasi 💔💔💔💔💔 anapha Chilima

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope Місяць тому +2

    Ife ngati amalawi mafumu ndi atsogoleri azipani ngati simukhala ofuna kutumikira anthu simuzapatsidwa ulemu

  • @user-hl1jt6eo3d
    @user-hl1jt6eo3d Місяць тому +1

    ntchito Yake yauganayongayo mkumati MCP ntchito wabwino fodya bas

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Місяць тому +1

    Bodza ili U TM sitikukangana Adyela ndiomwe akuchoka

  • @ChrissPhiri-kh3bd
    @ChrissPhiri-kh3bd Місяць тому

    U can be clever on this world but one day it's one day God is watching U baba h!

  • @VincentTry-cv4hu
    @VincentTry-cv4hu Місяць тому +1

    Iwe uli mbuz ukut chiuta aziwa unamukana kale chiuta poya zachipani

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Місяць тому +1

    😂😂😂😂😂Nde mafumu ndiwoyima mituuuuu onsewa akuwabera mitsokho yawoooo nde ndikumakamupepesa mr chikangawa yooo 😂😂😂😂😂nimayikondatu

  • @AnnieBanda-rb2dk
    @AnnieBanda-rb2dk Місяць тому +1

    Galu iwe chakwera fiti yamunthu manyi ako ukazuse kaye anthu amene unapha aja galu iwe, okay umaganiza ngat kut amalawi saziwa kut wapha ndiwe anthu galu iwe osatchulapo mulungu apa pomwe mulungu unatikana, galu iwe chikangawa chakwera fiti zamanyi basi

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Місяць тому

      Ukuziwa wekha ndi mbuli zizako 😅😅😅😅

  • @user-xc2zm9bu1i
    @user-xc2zm9bu1i Місяць тому +1

    We respected you chief alot but on this brutal murder,chakwera knows
    No resignation
    No cabinet reshuffle
    No someone to be fired
    No

  • @BrightKuyaka
    @BrightKuyaka Місяць тому +1

    Bwanji munachedwa kulengeza, munadziwa 10am kukalengeza 11pm mumadikila chai?

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b Місяць тому

    Sakuziwa kod mesa anatiuza kuti ndi chifunga kmaso akawapepesa bwanji ma mfumuwo chikangawa usamawawone anthu kupusa wamva iwe upepesa bwanji ma mfumuwo ma mfumuwo ndi adyela ngati iye yemweyo 😂😂😂😂😂

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Місяць тому +1

    Evera yudasi wachikaziiii😂😂😂😂😂😂😂 eee koma kutukula dziko kuti latukukako dzikoli njara ilithoooo uphawi uli thooooo umbanva uli thooooo kupha athu nde nyanye kumanga nde akungo lakalaka kumanga dziko lonse

  • @TheaKayikani
    @TheaKayikani Місяць тому +1

    Simuthu wabwino chikangawa chakwera uyu

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Місяць тому +1

    😢😢 yah akayenela kufunsidwa and uyu si president koma chilombo chowopsa

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b Місяць тому

    Ma mfumu maso tong'oo kulandila mr chikangawa mesa chilipo chimene akumeneko 😂😂😂😂

  • @mwaiwaobanda2691
    @mwaiwaobanda2691 Місяць тому +1

    Ndi Mulungu wanthawi...choonadi sichipheka ...

  • @ZondoChirwa
    @ZondoChirwa Місяць тому +1

    Ulikoma iwe kupusa

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Місяць тому +1

    Mbiri yabwino yachani nawe kachimagrass?mbiri yakuphayo kuchikangawa?

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Місяць тому +1

    Kamtukule adakikale wa MCP

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli Місяць тому

    Tell us 😭😭 what is happening in chikangawa plz plz

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Місяць тому

    KAMANSO CHAKWERAYO SAKUYENERA KUMAYANKHA KUMENE CHIFUKWA OLAKWA SAKHALA NDI MAU CHIRICHONSE CHIMENE ANGAYANKHULE ADZETSA NKWIYO KWA ANTHU, IWENSO NDIWE MBUZI CHAKWERA ALI NDI ULAMULIRO WABWINK KUTIKO AGALU INU

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x Місяць тому +1

    Mmene umagwetsa ndege muchikangawa mulungu analipo ndipo alipobe mulungu akuika poyera ndipo uchidziwa pompano

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r Місяць тому

      Munene kuti zose akudziwa ndimulungu osati zinazo moyo wachilima unali mumanja mwa achakwera kodi or mafuso mulibe kuti mwini moyo anazilola bwaji kuti zichitike moti inuyo kwanu anthu samwalila amalawi tiyeni tikhale ndi umunthu chosecho ambiri mwainu mukutukwana pano pa social media pankhani ya achilima makolo anu ndi afiti bwanji osaweluxa makolo anu uko

  • @WupeKamwambi-od6dn
    @WupeKamwambi-od6dn Місяць тому

    We have to wait from German to deliver the commission of inquiry.

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y Місяць тому +1

    Tidayika satana wakupha pampando,lero akukhuta misokho yathu chonsecho ndi chigawenga

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona Місяць тому +1

    Kamtukule wa tsata chibwenzi chake ku MCP

  • @AnnieZiba
    @AnnieZiba Місяць тому +1

    Anangodziwa kuitana asilikali akunja?

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e Місяць тому

    Chakwera akudziwa chomwe chinagwetsa ndenge ndipo tose tikudziwa zimenezo ndichifukwa achita manyazi kutulutsa report

  • @CHESOLO
    @CHESOLO Місяць тому

    Palibe chomwe angatiudze uyu..ngati report lama Albino mpaka pano kuli ziii 3 years atalikhalira

  • @FrankBaison
    @FrankBaison Місяць тому +1

    Wapkuphabe iwe chakwera

  • @EmmanuelNgamuti
    @EmmanuelNgamuti Місяць тому

    The only witnesses to the tragedy r those that were in the plane & lost their lives, let's not fight over this, truth shall alwez prevail, it's just a matter of time!

  • @ClementKhomba
    @ClementKhomba Місяць тому

    Ndimmene mfiti imanenela.adapha wanthu uyu

  • @EviChio
    @EviChio Місяць тому

    Ameneyu akuona ngat sitikudziwa kut anapangitsa ndege kut igwe ndiiyeyu.

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf Місяць тому +1

    akantukule ndi hule kupemphera iweyo hule tazingonyengsna ndi achakwera chigawenga

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Місяць тому

    Iweyo Mkaka umiyedzekerense mlam wakoyo
    Ngt mnene munamuyedzekera chilima
    Ubwino wake ndiwanu kale simungamuyedzekere....poti ndachibwenz abwana anu..nde simuyedzeka😅😅😅😅

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Місяць тому

    Akudziwa kuti ndege anagwetsa chili chonse akuchidziwa koma sangavomeke

  • @MeriaMasinga
    @MeriaMasinga Місяць тому +1

    Gwenembe kupha chilima

  • @user-hb2hr5oc9l
    @user-hb2hr5oc9l Місяць тому

    mulungu alipo wamoyo zizaziwika osadandaula ifa ikubwela muzaziona

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Місяць тому

    UYU ANAPHA CHILIMA ASANAMEPO APA AKUDZIWAPO KANTHU CHIKANGAWA UYU GALU, KOMANSO CHODABWITSA NCHAKUTI KODI MAFUMUWA AKUMUPEPESA CHAKWERA NGATI NDANI ? KOPITA CHIPEPESO MESA NDI KU MABANJA OFEREDWA ? MAFUMU SO NDINU OPUSA KWAMBIRI ZITSIRU ZAMAFUMU AGALU

  • @AllanJentala-g6h
    @AllanJentala-g6h Місяць тому +1

    Palibepo Umboni wakut apule ndiwolakwa kungot anthufe tikuyenda okwiyakwiya pa zifukwa zanthu

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika Місяць тому

    Mafumu awa zikazangoziwika kuti achilima anaphedwa mafumuwanso azaweruzidwe

  • @user-ei5kv4fr2g
    @user-ei5kv4fr2g Місяць тому

    Mafumu Ena amaoneka ngati anzeru but ndimazoba kyungu oneka ngati wanzeru uja mpaka kupera chonchi? Eishi ndalama yavutadi

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9j Місяць тому

    Nigalunji uyo wavala magogosi akuti chikangawa chakwera ali nd mbiri yabwino

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Місяць тому

    Akuopa ma minster kuti akakhalabe ku utm akhonza kuluza mpando ndi xm mene ine ndikuonera

  • @user-oh9bh1cl3b
    @user-oh9bh1cl3b Місяць тому

    Which ntchito yomwe akugwila anyakwawa?? Mwalandila chi banzi vuto lake

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya Місяць тому

    Anthu Ena andiodabwitsa, are you saying kuti anthu akulowa MCP chifukwa chambiri yabwino ya Chakwera?? Mmmh kuteroku zoti kuli Mulungu mwaiwala chifukwa Cha misonkho ya Amalawi??

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa Місяць тому

    Mrs chikangalawa akufuna athandize mamuna wake kuti awine kawiri chisakho koma it won't happen in our country

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v Місяць тому

    Ubwino ndi otii olo chakwera atalamula bwanji koma mathero ake imfa ilipo naye azalawa imfa

  • @DaveMtepa
    @DaveMtepa Місяць тому +1

    Hule iwe Vera

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm Місяць тому

    Galu iwe chakwera unapha nzako kapolo iwe dikira siku la chiweluza ukomana ndi moto wa sufure ndpo mcp chipan chakupha sitikuchifuna ife

  • @MonicaSembo
    @MonicaSembo Місяць тому +1

    Amakatengako ndalama basi

  • @DavieChiwale
    @DavieChiwale Місяць тому

    Chakwerayo chikumbu mtima ngati chimapha chimuphe

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Місяць тому

    The response to the incident was questionable.

  • @JervisDicksonMzinda-vu9vr
    @JervisDicksonMzinda-vu9vr Місяць тому

    KODI KYUNGU AMAFUNA CHANI KWENIKWENI? KUTEROKO WANYAMUKA KUCHOKERA KU KA ATI APULEZIDENTI AKANDIONE KUTI NDINE WABWINO?

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka Місяць тому +4

    Mulungu salakwitsa kalikose

  • @AffectionateGondola-cv7qj
    @AffectionateGondola-cv7qj Місяць тому

    In this world some people the know you than you know yourself that's he said only God knows

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx Місяць тому

    Chakwera akudziwa akudziwapo kanthu munthu oipa

  • @AudettaYohanie-fl3oc
    @AudettaYohanie-fl3oc Місяць тому

    Rest in peace Saulos Klaus Chilima 😭😭

  • @lenardmakuya
    @lenardmakuya Місяць тому +1

    Mudzacidziwa thawi ikubwera

  • @ChachuHomi
    @ChachuHomi Місяць тому

    Mapwala anuwo akutukulu dziko lake lithi

  • @frankdomingo1109
    @frankdomingo1109 Місяць тому +1

    No nsense at all

  • @ChiccoChunga
    @ChiccoChunga Місяць тому

    Mkakayo maso ngati mbolo

  • @UlemuChipompha
    @UlemuChipompha Місяць тому

    Ana amahule inu simuziwika chipani chimenene muli

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Місяць тому

    Eya akantule akuonaka kuti chakwera nzeru alive,mbiri yabwino yokupha anthuko NDE mbiri yabwino fiti ngo'ona inu

  • @clementlungu4514
    @clementlungu4514 Місяць тому

    Palibepo tsogolo pamepo kungobweretsa umphawi basi ndziko mwanthu

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 Місяць тому

    Mkudziwapo kanthu, why delaying kufufuza

  • @StewartGoma
    @StewartGoma Місяць тому

    Those chiefs went to condolences to the president they are stupidly crazy mind the chiefs they could to pay their condolences to Ntcheu

  • @jamesmsonkho4830
    @jamesmsonkho4830 Місяць тому

    Asowadi mtendele nanga report mpaka lero zithu za mu June

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 Місяць тому

    Who is to comfort who?

  • @FelixChikaondagama
    @FelixChikaondagama Місяць тому

    Kkkk koma pankhope ya apule mene akuonera pakuziwisa kuti ili ndi matha ndi china chake
    Munthu amaziwika pamaso kuti or uyu akukana komabe akuziziwa
    Maso a chakwera zikuonesa kuti mumtima akuziwapo kenakake

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m Місяць тому

    ndiye Ngati simukudziwapo Kathu apuresident ndiye mutitulusile lipoti Mesa mumanena Kuti kwabwela anthu akujelemani lipoti mpaka pano Ife chilungamo tidzachidziwa Muka Tulusa lipoti

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson Місяць тому

    Chakwera unapha sidiki mia saulos chilima ndi anthu ena aja

  • @edsonjohnbakaimani
    @edsonjohnbakaimani Місяць тому

    Institute an independent commission of inquiry

  • @MauriceTayali
    @MauriceTayali Місяць тому

    Ndikovuta kuti mafumu dziko lapansi akalowe UFUMU was kumwamba

  • @ZaithwaMatchado
    @ZaithwaMatchado Місяць тому

    Mmmmm mbiri yokupha mmmmm

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 Місяць тому

    Kodi maliro aChilima anachitikira ku ya boma,nanunso aKyungu mwadya banzi

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 Місяць тому

    Palibe zopatsana ulemu apa akudziwapo kathu pa za imfayi

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Місяць тому

    Harry mkandawiri nde mpha anthu wakarekare

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Місяць тому

    Palibe chamzeru pamenepo, akukapepesa Mafumu, kapena akukawapatsa ndlama? Chilima munachita kumupha musakane ndipo mzimu wa Chilima ndi anthu ena 8 anafa pa ngozi ya ndege ija plus Raff kasambala idzakhala ikufuula pa mitu panu kwa nonse munatenga nawo mbali pa kupha kumene kuja

  • @KennethDzama
    @KennethDzama Місяць тому

    Panyapako chakwera

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Місяць тому

    Saakudziwa bwanji poti ali ndi report? Akulubwalubwa bwanji?

  • @ReginaMulipa
    @ReginaMulipa Місяць тому

    Mbili yabwino yake yokuphayo ose akulowa chipani ichi ndiokuphaso naye kuti mufufuze uzayakha pamaso pamulungu mizimu yathu amene aja ngati ikuona ikukwapule chisilu iwe

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya Місяць тому

    Come out with a report ya ngozi ya ndege please please please.