Kodi mukukambirana za kukweza magetsi pamene a president analonjeza mtundu wa amalawi ndi nfuna yawo kuti mavuto amagetsi okhala mbiri munthawi yawo pa nthawi yomwe anapita ku Borabassa ku Mozambique. Can't there be a follow up why we haven't started tapping Mozambican electricity up to this time ?
Chilungam ichi ,ndipo chizikochi chifunika 4 mat kuyambila kutundako paka mus
Malawi it need reset button sure kuyambira president nduna
Kodi mukukambirana za kukweza magetsi pamene a president analonjeza mtundu wa amalawi ndi nfuna yawo kuti mavuto amagetsi okhala mbiri munthawi yawo pa nthawi yomwe anapita ku Borabassa ku Mozambique. Can't there be a follow up why we haven't started tapping Mozambican electricity up to this time ?
MERA, and ESCOM need an audit to bring about trust to justify the hikes .
Wawoladi Malawi chilungamo chake🔥🔥🔥
Kankwatira
Ndalama za Escom zimathera ku zipani
Malawi wawola zoona, 100%
What is wrong with tnm and Airtel
Mcp imaona ngati dziko ndi church hhhh
Chonsecho agwape amanewa magesi tikuwagulila ndife amalawi iwowo alibe nazo ntchito 😢😢😢
ESCOM or EGENCO?
Thus the problem of devaluation
Is not devaluation vuto yaola dzikoli ikufunika reset button kuyambira president nduna kuchapako ndi boom ma position onsewo
Mmmhu koma ma salary kumakweza ndi 5percent🙌🙌