Azibusa aCCAP koma ndi chani,ndine wa ccap koma mukutichitisa manyazi kwambiri ndinu mimbulu eti ija amanena Ambuye wathu Yesu eti?dyelanitu Moto ukukuyembekezani posachedwa,mulibe manyazi poyenda ndizina la ubusa mukutchulidwalo?mulibe mantha ndi Mulungu chifukwa chani?asatanic inu ,mundilakwisaso ,Mulungu alowe ndi nkwapulo munyumba ya m'busa aliyense mwalowa ndalama ya mwaziyi,mdzina la Yesu
Komano pa nkhani yobera anthu muma kampani,kuzunza powagwiritsa ntchito anthu mwakalavuala gaga ndi kuwapatsa malipiro ochepa,zakhala zikuchitika kwa nthawi yayitali ndipo maulamuliro onse akuyenera kudzudzulidwa posapangapo kanthu. All the past regimes have to take the blame.All the governments have never taken any company accountable when the citizens are being exploited by their companies.And surprisingly most of these companies are depended by govt
Let the opposition register all fertilizer beneficiaries and find out from each if he or she received all two bags of fertilizer if not then all who were responsible to be accountable otherwise this is theft.
Bola inuyo zilibwino zikukuyenderani komatu akuyankhualazi ndizowona anthu akuvutika, nkhani si DDP nkhani si MCP or UTM nkhani ndi a Malawi akuvutika ndipo zintbu sizikuyenda mu dziko lathu lino.
I always support you just because you stand for the truth may God always be with you the DCCCCCCCCCCCCCC from mulanje southern Africaaaaaaaa malawi
😂😂 Chilungamo chimamveka Pena ngati mwano kkkk
Makwana Mr DCCCCC ulemu wanu
Azibusa anakulodzani ndani koma?? Mene Malawi waonongekelamu kumalambila munthu zoona a ccap? Zooona
CCAP ndi amfiti Bon kalindo avala zoyera koma mkati mwa mtima ali akuda 🎉🎉🎉
Chilungamo chiyende ngati madzi
iwetu nde adakoza
Mumakwana big
Mitumbo yawo azibusa a nkhoma synod machende awo kutigulitsa ife kamba ka 10 million
Azibusa adyera akakowa awapasa nthumbwana basi akut bwana zilibwino azibusa a ccap adyera omasangarara anthu akuvutika
Thana nawoni mu tea Estate muli nkhanza aoneseni afisi amenewo
Kodi azibusa bvuto lanu ndi chani,,,makamaka aaaa mbuye akuyendereni,,,thawi yokhala limodzi ndi apulezdent.yatha inuyo simukuona mene awonongera zithu muno Malawi nde mumakatani kumeneko....ntengo ukakhota ngakhale utakula simungaungole awa ndi anthu oyipa,,azibusa opanda masophenya...
Azibusa aCCAP koma ndi chani,ndine wa ccap koma mukutichitisa manyazi kwambiri ndinu mimbulu eti ija amanena Ambuye wathu Yesu eti?dyelanitu Moto ukukuyembekezani posachedwa,mulibe manyazi poyenda ndizina la ubusa mukutchulidwalo?mulibe mantha ndi Mulungu chifukwa chani?asatanic inu ,mundilakwisaso ,Mulungu alowe ndi nkwapulo munyumba ya m'busa aliyense mwalowa ndalama ya mwaziyi,mdzina la Yesu
Apa ndiye akunyazisa mipingo anthuwa palibe kukhulupilira opemphera Maka mazibusa onse
Ndiwe kape
Komano pa nkhani yobera anthu muma kampani,kuzunza powagwiritsa ntchito anthu mwakalavuala gaga ndi kuwapatsa malipiro ochepa,zakhala zikuchitika kwa nthawi yayitali ndipo maulamuliro onse akuyenera kudzudzulidwa posapangapo kanthu.
All the past regimes have to take the blame.All the governments have never taken any company accountable when the citizens are being exploited by their companies.And surprisingly most of these companies are depended by govt
Let the opposition register all fertilizer beneficiaries and find out from each if he or she received all two bags of fertilizer if not then all who were responsible to be accountable otherwise this is theft.
Auncle bon kalindo mulungu aonjedzere masiku anu popanda inu amalawi titha. Ndibu yemwe mumatidzindikiritsa ndi kutiunira
Inuyo the DC ndiwakulu❤
Zitsiru za abusa
MAZIMBUSA NONSE MUNALANDILA NDALAMA ZOTI MUZIWUZA ANTHU MA CHURCH INUYO KAYA MUKUDAMBA MACHIMO YA CHAKWERA NDIPO MUKAYANKHA PAMASO PA MULUNGU CHIFUKWA CHAKWERAYO ANASANKHA KUPHA CHILIMA MALO MOFUNA KUPITILIZA UDINDO NOKHA INU MUZIFUSE KUTI CHIFUKWA CHIYANI SATANAYI AKUTIPATSA NDALAMA IZI KODI TSGWILA NTCHITO YOTANI KOMA CHIFUKWA CHOFUNA KUTI CHAKWERA ASAKALANGIKE YEKHA PAMENE AKUGAWILANI NDALAMA YACHIPHIMBA MASO KUTI MUSAWONE PATALI NOSE INU MWALANDILA NDALAMA MWAMVOMERA KUTI MUNAPHA NAWO MR CHILIMA AMEN MU JESUS NAME AMEN
The DC katundu zenizeni azibusa aminewa ndi mbuzi kwambiri
Powerful message
This is the truth ❤
YOU DESERVE RESPECT
A Nkhoma synod anthu awo akumva bwino boma ili. Ndi chifukwa anapita kukafunila Chakwera zabwino.
mwatero
Kuyankhula mopanda mantha
DC munabwera kuzaimilira malawi
Kalindo iweso ndi mbuli kwambiri .Chiyambire sunagawepo chimanga .keep on shouting
Azigawa chimanga cha chani nanu inu....mutu okhotawo
😂😂😂😂😂😂😂
Dpp never again ndipo ulira zeni zeni, uli ndi zaka zina 5 ,ukulakhula zopusa zakozo
Ulila ndiweyo pulpet wa chabe chabe
Wopusa ndiiweyotu chifukwa ukuyikila kumbuyo zopusa.
Bola inuyo zilibwino zikukuyenderani komatu akuyankhualazi ndizowona anthu akuvutika, nkhani si DDP nkhani si MCP or UTM nkhani ndi a Malawi akuvutika ndipo zintbu sizikuyenda mu dziko lathu lino.
I think ndiwe osabala.
@@codeoflife1398 mpaka mwapeza chipangizo zoyezera kusabeleka kwa anzanu tikumana September 🤣