Monga mulungu adatuma yona kukalalikila ku niniv iye nkuzemba koma chinsomba chitatumeza chidakamulabvulila mbali mwa mzinda omwe iye Yehova adamuuza kuti akalalikile, mulungu sathawika, chomwechonso nonse mudathawila ku zipani Zina dziwani kuti kubwelela kwanu ku DPP sinu ini ayi koma mulungu afuna kuti nonse pamodzi muthandizane kupulumutsa malawi yemwe lelo lino wagwidwa mu ukapolo wazaoneni.
Mukamati dpp singabweleleso m'boma mukutanthauza chani NGATI inuyo anthu oyipa a Mcp mwabwelelaso nde what more DPP? Koma ine ndiwa utm ndimangofuna kukozapo
Most welcome
Yes Apm is coming soon to be president of this country Malawi 🇲🇼 🙌
Mwaona ino Dr HKabambe kudzikweza kwanu!Awakubwerera kwao ku DPP.
Kubwerera kwamakolo sikulakwisa ayi ndipo mwalandilidwa kwambiri
More 🔥🔥🔥 adadi tikukufunanidi tatopa ndi mavuto
My vote 💙 my vote 💙
A Henry,akoloko nonsenu yesetsani ,aYonamu nonse bwerani inu kuChikwawa bwererani APM Musamnyoze Iye ,Mulungu ali patsogolo pake.Mose ndi Yoswa walero.Pakati,kumpoto ndi kumwera onse afuna APM abwerere.
Anthu adyela awa, zipitani ife tikhalabe chonchi komanso mudziwe tikuvutikila limodzi bcz nde mukuoneka opelewedwa ngati ine ndemwe
Zikusiyana zomwe mwalemba
Tidzasiya kutsata page yanu
Ndipo zoputsa zomwe akumachita this days akumalemba Mutu osiyana ndinkhani cholinga munthu ungotsegula basi
Zokongola
Monga mulungu adatuma yona kukalalikila ku niniv iye nkuzemba koma chinsomba chitatumeza chidakamulabvulila mbali mwa mzinda omwe iye Yehova adamuuza kuti akalalikile, mulungu sathawika, chomwechonso nonse mudathawila ku zipani Zina dziwani kuti kubwelela kwanu ku DPP sinu ini ayi koma mulungu afuna kuti nonse pamodzi muthandizane kupulumutsa malawi yemwe lelo lino wagwidwa mu ukapolo wazaoneni.
Guys mutu sukusiyan akutanthauza kt kucoka a UTM ku cipani cawo kupita ku DPP ndy mwanowo inu simukumvetsa Pati
Powerful
Kkkk
Mukamati dpp singabweleleso m'boma mukutanthauza chani NGATI inuyo anthu oyipa a Mcp mwabwelelaso nde what more DPP? Koma ine ndiwa utm ndimangofuna kukozapo
Tatoos ndi MCP we'll come a dad
Mulanje wa khala wa moyo tsopano.Inu aku MULANJE WACHITA BWINO KUPEPESA.
Komano tingokozapo kuti awowo sanali a UTM awo anali a Manganya ndepaja anathamangitsidwa chifukwa anali a Mcp amaona NGATI UTM angaipusitse
Mutu WA nkhani mulembenge makola please
Komatu mwalakwitsa Heading ife timatsatila UTM osati zomwe tikuonazi
Vauchindere naleka kujula page yinu muli wazereza mwalemba utm uku VA dpp mwagongowesa namufumani
Page iyi pang'onondipang'ono anthu asiya kuyipanga follow...aka ndi koyamba ndikomaliza ndasiya kutsitira page imeney.
Kusonyeza kuti UTM ya Kabambe sizinthu alibe chikoka bwenzi tulandira alendo ochokera ku DPP komwe adaliko iyeyo
MCP ilipheeee ikudziwa zochita inu batekesani
Mwano=kusiya UTM atasankhidwa ku convention. Koma panopa inu a DPP mulimbanne ndi SMARTMATIC yomwe inavotera kale Chakwera.
Ok
Mazila ako galu iwe zmenezi ndye zichani
HOT 265 be careful
Tiyeni tizinena zoona iyi ndi proof kuti arowadi ku dpp carakwika ndi cani komaso ambiri akubwerabe nde mutani
😂😂😂😂😂 Anayika pusi nyumba
😂😂😂😂😂 ndale zakumalawi ndi choncho.
Koma alendo ake osasamba kkkkkkk or muphatikizane simumaka mcp ndi machine
You will regret
Machende ako uwonaso tili Malawi momuno tonse
Mwanapiye wabwelera mmapiko amche
Pamtumbo pakuda ngati tambala wakuda Chikangawa zithupsa
Apa angochokelatu mbusa uja bas
Koma anthuwa sanalembese sazavota
❤❤❤❤
Why MCP is ruling again? don't cheat your self let us wait and see
Agogo team kkkkkk dpp will never win again MCP pachiwongolelo
Page yopanda nfundo kkkkkkk
We are not here to sheck never what you need to know is that this is political manner oky we need food for our loved ones not party
Kwachema
Diedly party
Inu nda modzi agalu inu
Boma ndilomweri
Uziona ndi chikangawa crocodile
Munya Chaka chino
chisankho chabwino
DPP will never rule again
You are dreaming dude
😂😂😂😂 muchila chikangawa team.
Ndiwechisilu amenesazalamula ndi amako.
In your dreams
Batukwana ine ndilibejthaw yolimbana ndi kape iwe@@FelixNyirenda-c4y