ZOMWE WAYANKHULA LERO KAMLEPO KALUA ZI AKAPANDA KUZITENGA BWINO AMUMANGASO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 92

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 2 місяці тому +3

    Mr kamlepo don't worry nthawi yaanthu mukuwadandaulao yatsala yochepa misonzi mukugwetsayo owo adzagwetsa x7

  • @CEDRICJIKA
    @CEDRICJIKA 2 місяці тому +5

    Thanks so much Dr we respect you from the past 80s and 90s. I hope these idiots has forgotten these because they are young. Keep it up to let us know the trueth

  • @MasterMwandira-q8v
    @MasterMwandira-q8v 2 місяці тому +5

    A honorable Foniyo msayivomele, akungopasani ndalama mkagule yina nokha

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 2 місяці тому +8

    Kamplepo kukhala maiko ena bwenzi akupasibwa ulemu chifukwa adagwila ntchito yaikulu kuno ku malawi

  • @supa4dupa
    @supa4dupa 2 місяці тому

    May God protect you and your family,daily prayer is the key,have your lawyers get your phone,you are a great Malawian treasure.🙏🏾

  • @MariaWilson-gq8st
    @MariaWilson-gq8st 2 місяці тому +9

    Dziko ndi anthu Ake ndi conco mulungu akupulumutse iwe kamlepo ufike tchaka CA mawaci bass God protects kamlepo kaluwa and other family

  • @mussolinechiwotcha4124
    @mussolinechiwotcha4124 2 місяці тому

    This Kamlepo Kaluwa is a real Malawian let's respect him and let our money return

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 місяці тому +3

    Unuyo osawopa anthu awa atikwana ndipo tiwaponda aziwe sopano kuti tatopanaqo agalu amwnewa Mr chikangawa

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 2 місяці тому

    Amenewo asiyeni Akaluwa

  • @dysonmasiye5736
    @dysonmasiye5736 2 місяці тому +2

    Akuti a boma mwaba 3 trillion ndipo mukubisa m'ma bank osiyana'siyana, mukumangira nyumba zibwenzi, zina mwasunga ku Cuba....koma mukupangiranji izi pomwe a lot of Malawians akuvutika ndi umphawi? Muzionatu

  • @FunnyBasketball-er3vc
    @FunnyBasketball-er3vc 2 місяці тому +1

    They hate him because he spill beans which is good for poor Malawians

  • @johnmponda9070
    @johnmponda9070 2 місяці тому

    Keep going mr KK we're really following you and all you are speaking out is all true thise stupid people they taking Malawi like they own it

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala 2 місяці тому +3

    Apolisi analowanso gulu la zigawenga lotchedwa MCP 🐊 zam'mabango

  • @CaptainLusky
    @CaptainLusky 2 місяці тому

    Why background music

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 місяці тому +3

    Ayi bwana phone musalandile anthu awa ndimamafiya tiwonana chaka chama I hope to remove this nyasi

  • @chilungamosimkonda79
    @chilungamosimkonda79 2 місяці тому

    May God continue protecting you fadah

  • @Stevekatiwa-tp3oq
    @Stevekatiwa-tp3oq 2 місяці тому +1

    Don't worry father kamlepo Mulungu afungatila Satana ndi olephela bas

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya 2 місяці тому +8

    You don’t know why Salima have two barracks 😂

    • @EdnahShantell
      @EdnahShantell 2 місяці тому +2

      ⁉️😂

    • @JervisDicksonMzinda-vu9vr
      @JervisDicksonMzinda-vu9vr 2 місяці тому +1

      If a boat were sinking on Lake Malawi today , do you think they could have any capacity to go and rescue people quickly as , for example, ZAMBIAN soldiers can do? If they can't, what is the point of having two barracks?

    • @AbdulmajeedHajj
      @AbdulmajeedHajj 2 місяці тому

      Tell us why

  • @EliasManthenga
    @EliasManthenga 2 місяці тому

    Zomati ndizaulula ndizaulula zii, ife sizmati sangalasa ai lelo si mawa ai ndibwino kuulula lelo a malawi tizziwa

  • @AARONCHISUKAMZION-we3vp
    @AARONCHISUKAMZION-we3vp 2 місяці тому

    Hands of to Kamlepo and his son.
    Anthu inu Malawi siwanu,it's for the people who were born in Malawi.
    A president mukuchitisa manyazi mulungu,azisogoleri anzanu mumipingo, Assemblies of God,pamozi ndi ine Deacon,mukumangosainila nkhanza zina zilizonse,nyansi zokhazoka pangani chilungamo .
    A president pangani reconciliation ndi mulungu,resign from politics.Mulibe mtendere inu ngakhale mukudya bwino,mwaonda nazo mkati mwa mtima.
    Apolosi ovutika anzathu siyani kuzunza ife Malawi anzanu,you are just the bread winners like us.
    Akakutumani siku Lina simkabwerera, people will overcome your power.
    Umaliro wake wazakumubondani na misi,nthonga ,umaliro wake lakusizgika ni banja linu.
    Amalawi wavuka imwe atopa
    Chakwera resign Kuli Moto kumwamba.
    Zokoma zazikoli zakutengerani koyipa .
    Ana ang,ono,akupweteketsani
    Bwerani Kwa Yesu a president.
    Yesu akudandaula pantanda.
    Mwazunza amalawi osauka,anthu opunduka,amasiye,amayi Ali pa uchokolo,ma compasation anamfedwa ndi zambili.
    Misozi ya Yesu Khristu yagwera pa inu
    Soka😢😢

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 2 місяці тому

    Mr kamulepo ulemu wanu , gulani phone ina iyo itayeni atenge chikangawayo

  • @MoosaChirwa
    @MoosaChirwa 2 місяці тому

    Keep it up
    Kom back ground track takozani ikumasokosa

  • @MercykanchureJohnson
    @MercykanchureJohnson 2 місяці тому

    Wosadanda bambo anayamba kudana ni Yesu

  • @HassanKhebo
    @HassanKhebo 2 місяці тому

    The big man

  • @thomasbotha9790
    @thomasbotha9790 2 місяці тому

    Kudandaula yayi adada ka mulepo Kaluŵa, Chiuta nimukuru awo wamubilani foni ndarama walije, Chiuta wawezgerepo foni iyo, awo walikumupokani foni Chiuta wawalange wose

  • @ChimeWe
    @ChimeWe 2 місяці тому

    Amalawi akuvutika kusowa makwala mu hospital ndalama zogulila makwala mwazigawana ayi amuye atengepo gawo

  • @DysonNakhaphe-bo4dl
    @DysonNakhaphe-bo4dl 2 місяці тому

    Ndi a kuba ayikoda phone

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 2 місяці тому

    It's matter's of time one will take off this cruel government

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala 2 місяці тому

    Kkkkkk akulephela kugula phone kkkkk apolisi ndichanikoma

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Awuzeni achikangawa fogs amenewa malume 😂😂😂, they're too young for politics

  • @stevenbanda6665
    @stevenbanda6665 2 місяці тому

    Iyooooo 😮

  • @stevengeorgechakhumbira1508
    @stevengeorgechakhumbira1508 2 місяці тому +2

    Mcp 2025 0vote kunoko ku Ntcheu khulupirini

  • @JawaduDivision
    @JawaduDivision 2 місяці тому

    Ndi mene amadyela agaluwa

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 місяці тому

    I love u mr kamulepo

  • @HaliJana
    @HaliJana 2 місяці тому

    KODI MAYI YOLAMU CHAKWERA ZIKHALI MKAKA USI KOD CHILIMA UJA SANAKUKWANENI NDI ANTHU 8 AJA

  • @BlessingsMwale-k4s
    @BlessingsMwale-k4s 2 місяці тому +2

    Waku Nkhatabay yo ndiye eeeee eeeeee eeeee 😂😂😂😂

  • @SkeffaKaifa123
    @SkeffaKaifa123 2 місяці тому

    My father mungule 4 ni yina basi

  • @VioletNguluwe
    @VioletNguluwe 2 місяці тому

    😂😂😂😂koma kamlepo😅

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj 2 місяці тому

    But Why Salima have two baracks?? ..ndalama angoyenda nazo mmisika kusokoneza akut maganizo a a Malawi..kutiona kuvutika kwambir koma Mulungu awaone mwa padeladela

  • @mussolinechiwotcha4124
    @mussolinechiwotcha4124 2 місяці тому

    Amuputa dala uyu anati ziii ngati kunalibe

  • @Raph-kayRaph-kay-g5v
    @Raph-kayRaph-kay-g5v 2 місяці тому

    Nsambi kwambili chakwera satana yehova akuona

  • @HaliJana
    @HaliJana 2 місяці тому

    NDIYE MULENGEZE KUTI TIZIPHANA CHIFUKWA MWATIONJEZA CHAKWERA SUNGANDIVUTE INE NDI SIKU LIMODZI INE ALILA AKWANU IWEYO ZIKHALI N'GOMA IWEYO NDIYE NDI MAMINISI KUPHWESA INE MIMBAYO WAVA TIMAKUPASA I ULEMU KOMA NDINU MAVI ONUKHA KWAMBILI PANYO PANO CHAKWERA IWEYO USAMALE CHIKANGAWA SIPANAPITE NTHAWI KUTI MWINA ANTHU AIWALE KOMA IWE ULI BUSY KUCHOSA MOYO WA MUNTHU MBOLO YAKO CHAKWERA NIPHANYA CHIMUTU CHAKOCHO WAVA MAVI PONYELA PAMATAKO PAKOPO

  • @MasterDaniel-n1g
    @MasterDaniel-n1g 2 місяці тому

    It won't happen tilinanu madala

  • @NelsonMarley-m6p
    @NelsonMarley-m6p 2 місяці тому

    Aliense azafa,,,, mark that words zitsilu za mcp

  • @felixbandawe892
    @felixbandawe892 2 місяці тому

    Tangoing'alulani akulu

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 місяці тому

    😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂 is the eeeeee,eeeee,eeeee,for me😅😅😅😅😅😅😅

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 2 місяці тому +1

    Vuto lake andale ena amuiwala kamlepo

  • @savinapili7185
    @savinapili7185 2 місяці тому +1

    lankhulani bwana kamlepo

  • @JoshTech-h4r
    @JoshTech-h4r 2 місяці тому

    Chiona ndi chipande powomola

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Muzingodomola one by one basi malume 😂😂

  • @SalaJawali
    @SalaJawali 2 місяці тому +1

    Muwasumile amenewa ku bwalo lamilandu a galu amenewa

  • @HamzahMiles
    @HamzahMiles 2 місяці тому

    Ndazipeleka kukhala lawyer for free, kasumeni mulandu ndipo iwiri, okunamizilani plus phone yanu

  • @CharityChirwa-t1e
    @CharityChirwa-t1e 2 місяці тому

    Apolice akusunga phone yanu chifukwa cha chakwela ndiamene amatuma apolece kuti azimanga athu chifuwa alindimatha panyasi zimene akupanga enawo ngongotimidwa koma ambuye akuwona chifukwa akanakhala kuti iye sakuziwapo kathu phone yanu akanakupasani thawiyomweija koma alinayo cholinga kuziwa akuziwa chakwela kuti phone yanu andi apolece bwanji akukhalachete ndemawa azizati palibe chomwe akuziwa chimuthu choyipa kuyipa kwachinkhope ndintimawomwe kuyipa nkumati ndibusa busawake wakuti wakumidimatu ma bafomet amitu 6

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika 2 місяці тому

    You won't die prematurely in Jesus name.don't worry God is protecting you. Chilungamo chikuyenda ngati madzi apa dzikoli talisambira mmanja kuti Mulungu wathu achite nalo basitu.

  • @BrightPhiri-bt6ev
    @BrightPhiri-bt6ev 2 місяці тому

    Koma akamlepo kutha samatha choncho ndithu anthu ankakupasani ulemu koma mpakana apapa ayi ndithu.

  • @TriciaSeleman
    @TriciaSeleman 2 місяці тому

    Sim card yokha abweze... Wa police wationjeza

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 2 місяці тому

    That's the kamplepo kalua i know, amatakasa madala wa,

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 2 місяці тому

    Akamlepo nkhani yizktha kodi osapita kupolice koko bwanji ndinu munthu wamkulu

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya 2 місяці тому

    Mmmm this one is a real legend

  • @BlessingsMwale-k4s
    @BlessingsMwale-k4s 2 місяці тому

    Ayoswa kunotu yanu..
    Ija mmati muimba phone ku police kuti mwana Wa Kamlepo amangidwe.

    • @AliceYankhoKakusa
      @AliceYankhoKakusa 2 місяці тому

      Ndipo pokhapo mneneri eee watenthedwa🤣🤣🤣

  • @ishmaelchirwa9303
    @ishmaelchirwa9303 2 місяці тому

    MCP sizasintha, kamuzu Banda anaonga chipani

  • @HENRYCHAONA
    @HENRYCHAONA 2 місяці тому

    Phone pelekani siyanu

  • @HalimaShafie-o7g
    @HalimaShafie-o7g 2 місяці тому

    Apolice akumalawi ndiotsauka akufuna kuti aziyendela 4n yanuyo vuto samalandila ndalama yoti athakugura 4n zakulandila apolice o

  • @JuliusAndrea-iq6xc
    @JuliusAndrea-iq6xc 2 місяці тому

    Eeeee guys 3 Trillion kwacha 😢😢😢

  • @SueWahna
    @SueWahna 2 місяці тому

    Ampase telephone yake chimene asakumpasila munthu ndi Chan kod

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 місяці тому

    Osawopa tikudziwa ntchito zawo zokupha

  • @OwenMajoni-qv3eg
    @OwenMajoni-qv3eg 2 місяці тому

    Ndiwe wa mtopola iwe

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 місяці тому

    Zosayendatu kwabasi

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 місяці тому

    Ayaluka 2025 hold my words

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 2 місяці тому

    Mowa Tizimwa mwa size or fodya kumasuta mwa limit

    • @SalaJawali
      @SalaJawali 2 місяці тому +1

      Wasuta fodya ndani

    • @TroubleMuthala
      @TroubleMuthala 2 місяці тому

      Wamwa mowa ndani?

    • @Stevekatiwa-tp3oq
      @Stevekatiwa-tp3oq 2 місяці тому

      Ndan iwe kod ukufusa zopusa iwe? Wamwa mowa ndan?????

    • @TroubleMuthala
      @TroubleMuthala 2 місяці тому

      @@Stevekatiwa-tp3oq eeh eeh man mpaka opusaaa? Ochenjelanu mulibho. Ulemu wanu 🙏. Ine ndimawafunsa awo akuti mowa Tizimwa size or today kumasuta MWA limit

  • @AlbertEngelbercht
    @AlbertEngelbercht 2 місяці тому

    Kamlepo osaopa pitilizani ntchito,

  • @Manlymw
    @Manlymw 2 місяці тому +1

    Auzenii

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому

    Afiti a MCPigs ndi ufiti. Pamtumbo panu a MCP.

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 місяці тому

    Gulani Ina basi boma iyi mmmmm

  • @JuliusAndrea-iq6xc
    @JuliusAndrea-iq6xc 2 місяці тому

    😢😢😢😢

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 2 місяці тому

    Za lero kapena za dzulo izi abale

  • @DamianMoses-tj6zi
    @DamianMoses-tj6zi 2 місяці тому

    Musamantchuluse sounds sizikumavekaaaaaa

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 2 місяці тому

    Chonde chonde phoni yo musarandile Bambo. .. ... Anthu wa ali cholinga....kma inuyo ndi 1

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb 2 місяці тому

    4n Yao apaseni basi

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh 2 місяці тому

    Tsono boma likumva pa u.tube.wasowa chochita galu uyu