DR MICHAEL USI KUYANKHULA KWA NYOO!!!__24 November 2024

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 161

  • @LeonardChimbaza-n4l
    @LeonardChimbaza-n4l Годину тому +4

    Mmmmmmmmm
    President comes after conversation.

  • @kaitanokagalu
    @kaitanokagalu 2 години тому +4

    Hahahahaha no commission of enquiry 😂😂😂😂 mukumufunayo wapezeka ndi Dr Usi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂, you have made my day Bwana Usi.

  • @kaitanokagalu
    @kaitanokagalu 2 години тому +4

    This is the Malawi we wanted, ufulu wokhala ndi omukonda 😂😂 ngati mumutukwane Dr Usi ,alipo omukonda hahahahahahahaha! Wina alira magazi. Go go go go go Dr Usi!

  • @BenjaminKamanga-p8w
    @BenjaminKamanga-p8w Годину тому +1

    Chofunsira kuti kodi mwadya ndi chani ngati you're really doing your job good, zikuonekeratu koma they are can'ts

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 Годину тому +2

    I'm just enjoying all of this drama in UTM, kaya mumutukwane athu akumukondabe kkkkkkkk

    • @CuthbertChinseu
      @CuthbertChinseu 42 хвилини тому

      Politics plus women equals confusion at its best

  • @TasiyanaChinula
    @TasiyanaChinula 2 години тому +4

    I il pretend as if I dint see this....
    I il pretend as I dont know Mr Usi aaaa zosayenda......azimai ndife otengeka..

    • @khoviwaedward
      @khoviwaedward Годину тому

      Kwambiri azimai inu ndiophesa ndithu. Kunamidzika azimai muli easy kwambiri

  • @SteveNyson
    @SteveNyson 2 години тому +4

    Komatu apapa zikuonekelatu kuti azimaiwa alibe nzelu.chifukwa apapa Usi ndiye wamasuka kuti sakupangaso za UTM.

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 Годину тому +2

    Akuti abwera ngati a UTM. Apapa kuulula kuti anthuwo si A UTM. WABALALIKA

  • @PatriciaChibwato
    @PatriciaChibwato 2 години тому +2

    Munthu uyu ndiwanzeru kwambir, muzazindikila patsogolo. The weak minded are seeing drama

  • @TanangachiMkhala
    @TanangachiMkhala Годину тому +1

    They are exercising their rights leave them

  • @patrickMakhumba-yc7rb
    @patrickMakhumba-yc7rb Годину тому +1

    Koma this mmm no comment but God alinaye cholinga ndiyhu

  • @IbrahimWezely
    @IbrahimWezely Годину тому +2

    Dr usi ndimtunda wina, achina kaliat anazindikira mochedwa kuti wabetsa chipani

  • @GeoffreyPhiri-qy5gq
    @GeoffreyPhiri-qy5gq 2 години тому +4

    Uyu mzeru alibe osangovomeleza bwanji

  • @BenjaminKamanga-p8w
    @BenjaminKamanga-p8w Годину тому +2

    Ngati akugwira ntchito bwino bwenzi anapita kunsika akafunse kuti thin la chimanga ndi zingati

  • @wisdom20mkango49
    @wisdom20mkango49 2 години тому +2

    if only UTM could remain with this guy...2030 boma amatenga

  • @AffectionateGeyser-fm7dl
    @AffectionateGeyser-fm7dl Годину тому +2

    Anthu ake amenewo kkkk koma anthu andale mapusisika bwanji

  • @BiliatMzungudala
    @BiliatMzungudala 2 години тому +3

    😂😂😂😂 koma kumalawi adah ndi dziko lokoma kobas

  • @limbikanil.i.mmtewa7595
    @limbikanil.i.mmtewa7595 9 хвилин тому

    It's a tactic to divide UTM ...this is MCP members in UTM attire

  • @GiftNkhoma-n2w
    @GiftNkhoma-n2w Годину тому +1

    Iwe atengeni azimaiyo opita nawo Ku odya zake alibe mulandu fundo ulibe iwe tangonenani chilungamo kuti bas ndachoka Ku UTM

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy Годину тому +2

    Ndikutha kuona chipani China chikutuluka😂😂😂😂

  • @AbdulMalik-o7n1q
    @AbdulMalik-o7n1q Годину тому +1

    Kausi mkafiti apa ndiye zadziwikilatu moti manyazi or amodzi samugwilako iyeyu umunthu alibiletu anamuletsa ndindani kuti asapite kukomvetion

  • @samueljere4997
    @samueljere4997 2 години тому +3

    Pa dziko lonse la pansi anthu ambiri aku voter ndi azimayi

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 2 години тому +2

    Uyu mutu wake sikugwira ndinthu dzilope dza biyeni💔💔💔

  • @patrickMakhumba-yc7rb
    @patrickMakhumba-yc7rb Годину тому +1

    😂😂😂😂😂 akuti agwire tchito nd Benjamin?😂😂😂

  • @ElickNasiyaya
    @ElickNasiyaya 2 години тому +2

    Pangani zanu - wakutukwanani ngati? Manganya more fire!

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx Годину тому +1

    I understand now that empty tin makes alot of noise

  • @JacksonclementWasili
    @JacksonclementWasili Годину тому +1

    Ndiwe savage ussi

  • @georgealabih8979
    @georgealabih8979 2 години тому +1

    Ndipo UTM yeniyeni ndi ya Dr. Usi Yi inayo it's irrigal UTM

  • @mercymagaleta9672
    @mercymagaleta9672 2 години тому +3

    Nkhani ndi njala chilungamo chili mmitimamu

  • @kaitanokagalu
    @kaitanokagalu 2 години тому +3

    Hahahaha Dr Usi,omutsatila akachulukilachulukila, this guy is something 😂😂😂😂. Ada Mulungu alipo ndipo he is good to you amd all of us who loves this country!

  • @MariaNyamwera
    @MariaNyamwera Годину тому +1

    Vi azimayi voduka mutu akungofuna ya ufa awa aaaaa

  • @EzvizHome-z2v
    @EzvizHome-z2v Годину тому +1

    Kungosonkhanitsa anthu a odyazake alibe mulandu mkumati a utm😅😅😅😅

  • @OSCARChimthethe
    @OSCARChimthethe Годину тому

    Usi usachedwe ndi anthu amenewa akukunamiza
    Find where to be after general elections
    Tithokoze kuti palibe izo wawauza

  • @FrunkNjunga
    @FrunkNjunga 12 хвилин тому

    My leader

  • @GiftNkhoma-n2w
    @GiftNkhoma-n2w Годину тому +1

    Zichitsilu zopanda zeru azimai awa mudya saluzo mukhuta 😂😂

  • @limbikanil.i.mmtewa7595
    @limbikanil.i.mmtewa7595 7 хвилин тому

    Malawi open your eyes this is not UTM but rather MCP

  • @limbikanil.i.mmtewa7595
    @limbikanil.i.mmtewa7595 11 хвилин тому

    As far as I'm concerned...these women are of MCP..don't fool malawians

  • @denniskalambo-fv4ou
    @denniskalambo-fv4ou Годину тому

    Uyu agwetsa utm uyu i think he is being sponsored

  • @ThomasShuga-z5p
    @ThomasShuga-z5p 35 хвилин тому

    Manganya ngopusa kwambii Garu wamunthu osadziwa chimene akuchita!!!😡😡 RIP late Dr chilima 😢😢😢

  • @RaphaelShasha
    @RaphaelShasha 2 години тому +2

    A Angofuna ya soya pieces ndi okoman awa iya tiyeni tione

  • @DumisanPhiri
    @DumisanPhiri 42 хвилини тому

    😂😂😂😂😂 manganya iiiii wandichosa nkhawa

  • @KingsleyChingwalu
    @KingsleyChingwalu 3 години тому +2

    Apite ku Ndix akapangile mnsokhano kumeneko tiwone kuti ayendako bwanji?

    • @jacquelineboya9529
      @jacquelineboya9529 2 години тому

      Ndipo misokhano yake akungopangila kunyumbatu pa ground zero😂

    • @JohnmarkNazombe-hi9xd
      @JohnmarkNazombe-hi9xd 2 години тому

      Akhodza kupita...what is so special with ndilande...is ndilande not part of Malawi???

    • @JOHNOlesmasCosmas
      @JOHNOlesmasCosmas 26 хвилин тому

      Agendedwa kale kumeneko ndix sipanga nawo zaphada kkkk

  • @macleanldzimkambani7773
    @macleanldzimkambani7773 Хвилина тому

    Akutitu "Mulungu ndiwabwino" ? 😂

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale Годину тому

    You are just a member of UTM keep on campaigning for Kabambe or else kapitilizeni odya zake alive mulandu

  • @chimwemwebanda9939
    @chimwemwebanda9939 51 хвилина тому

    Viwazimayi vopenga ivi😂😂

  • @Gladm-sy1se1tn6r
    @Gladm-sy1se1tn6r 34 хвилини тому

    Aaaaa😂😂😂 stop giving this man force hopes😂😂

  • @London-wb2ql3of9d
    @London-wb2ql3of9d Годину тому

    Tikuferanji part 2

  • @StephanoIssah
    @StephanoIssah 3 години тому +3

    Kd uyu ndiwazimayi okhaokga aaah utm iyiyi ndee ayii yazimayi okha

  • @chimwemwebanda9939
    @chimwemwebanda9939 49 хвилин тому

    And awawa akuoneka kuti akufuna gulu limeneli Liliwe mcp

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 3 години тому +2

    UTM motooooo Uwoooooo

  • @MuhamadMpate
    @MuhamadMpate 35 хвилин тому

    Kupusa chitsiru Ichi kusowa chochita uku udya zake alibe mulandu

  • @jacquelineboya9529
    @jacquelineboya9529 2 години тому +3

    Kodi adindo a UTM osamtengela ku Court uyu bwanji wayamba kubowa

  • @musah-j6m
    @musah-j6m 2 години тому +1

    Sonotu awus mukutichitisa.manyaz takutoperani sopano panyopanu kwinako😅😊😊😢😂🎉😊

  • @ruthmissi7766
    @ruthmissi7766 41 хвилина тому

    Hmmmmmm no leadership in him

  • @Nelie-k4z
    @Nelie-k4z Годину тому

    Zaziiiiiii manganya ndi kasongo akukwatani

  • @LevieMwanayaya
    @LevieMwanayaya 2 години тому +3

    Palibepo ndimzibambo yemwe azimai okhaokha osaganiza kuti asowa yasugar afuna angokukawa

  • @dalisoulphiri3094
    @dalisoulphiri3094 Годину тому

    Munthu yekha akunena kuli njala koma nkumati ndagula nsalu popita mutenga anthu opepera nkumaombera mmanja hmmmm eeeeee amalawinso penapake kodi anatiloza ndindani

  • @JacksonclementWasili
    @JacksonclementWasili Годину тому

    Kodi palibe kungowapatsa mbama awA osokoneza

  • @BenjaminKamanga-p8w
    @BenjaminKamanga-p8w Годину тому

    Onsewa angovala zigoba za utm, onse ndi a mcp awa a utm tikuwaziwa ife

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 3 години тому +1

    Kodi osamanga bwanji kapeyu,akuononga chipani tu

    • @georgealabih8979
      @georgealabih8979 2 години тому

      Iweyo suukudziwa akuyenela kumangidwa ndi Kabambe coz convention ija ndi ya illigal

  • @DumisanPhiri
    @DumisanPhiri 49 хвилин тому

    Ndewu iyi ikathela patali

  • @isaacthawani5442
    @isaacthawani5442 Годину тому

    Munthu uyuuu amatamba ndipo anthu awaaa sa UTM agowaveka zitsilu za zimayi

  • @josephchikweni1857
    @josephchikweni1857 11 хвилин тому

    Kuswakuswa

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef Годину тому

    Palibe masapota a UTM apa, akulu awa apenga

  • @MebleKalitsilo
    @MebleKalitsilo 2 години тому

    Ine wanga ndi ndipo nawina 636 votes w

  • @kittymalambo1853
    @kittymalambo1853 Годину тому

    Kodi madam ussi amakhala kuti?

  • @EstherBauleni-g8p
    @EstherBauleni-g8p Годину тому

    Akufunika CPZ basi

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno 2 години тому

    Chonchi azimayiwa angamalephele kutichindila samalani azimuna nonse amene axikazi anu amene amayengeka ndiandale azingojuchindilani anthu andalamawa ambiri axikaziawo ndinkhwangwa ndiye akawona anuwo azingokupakulilani nyemba zanuzo

  • @TywellShumba
    @TywellShumba 2 години тому

    Ine ndimazidyesa ndekha sunayambe wandipasa chakudya chako 😂😂😂😂 galu iwe

  • @LevisonMalulu
    @LevisonMalulu 2 години тому +1

    Looks like a new Tikuferanji drama group

  • @chimwemwebanda9939
    @chimwemwebanda9939 54 хвилини тому

    Kutulo ndithu

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt 3 години тому +1

    Akusowa kolowera anthuwa!! Eti abalalika

    • @StarfordKAMOTO
      @StarfordKAMOTO 3 години тому

      Akufuna ma 5pin basi azimupitira daily

  • @emmaculatemenzeiwa
    @emmaculatemenzeiwa Годину тому

    My poor beloved women

  • @elizabethbalalasdp721
    @elizabethbalalasdp721 2 години тому

    Koma abale! Koma anthu awa mitu yawo ikugwira? Si misala iyi koma?

  • @georgealabih8979
    @georgealabih8979 2 години тому

    Musapusisike team yake ikuchulukilachulukila ngati mmene zidalili ku DPP mthawi ya malemu Chilima

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 години тому

    Wangokokola mbeta zosowa chochita chifukwa mkazi okwatiwa mwamuna wake sangapange zopusazi ayi ndi uchitsilu ukuchitikawo makosana.

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 3 години тому +1

    komaso mwasowa chochita usi pangani zanu ichi ndichathu chaife a utm ifeyo akubanja zikuti wawa unatiphera mwana wathu wagwanayo panga zako ndipo mzimu wabiyeni ukukatheni nose anthu woputsa inu nose's

  • @TywellShumba
    @TywellShumba 2 години тому

    Iwe maganya uzinamiza omweo ife siana wamva waukape kwambili

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno 2 години тому

    Guys tangokhalani chete kampeniyo azipangila kumpanda kwake komweko atipeza makwalalamu timupasamo makofi miyaya ikumudikililanso makomomu

  • @CrispineBetha
    @CrispineBetha Годину тому

    Michele usi you think you're very smart wena. Uyandama mcp ikaluza

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 години тому

    This is ridiculous Manganya chomwe akufuna sadzachipeza garu wapamtcheni kukuwa kwambri

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 2 години тому

      😂😂😂😂😂😂 what else more than being a vice president...saying someone that is suffering

  • @MaryZgambo-p5m
    @MaryZgambo-p5m 2 години тому

    A bale Kodi uku kuli nkumano wa zimayiiiii kapena kuli president wa zimayi chitsiru monga bambo a chisikonooo???

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri Годину тому

    Akudyera azimayi ameneo Iwe Manganya usamale nawo

  • @StarfordKAMOTO
    @StarfordKAMOTO 3 години тому

    Kodi kulimbe wa mkulu wa UTM pali azimai bwanji?

  • @ChrisEnos-to5uv
    @ChrisEnos-to5uv 2 години тому

    Manganya ndie Galu nfundo nje😂

  • @limbikanil.i.mmtewa7595
    @limbikanil.i.mmtewa7595 41 секунда тому

    This is total nonsense....

  • @KennKasonde
    @KennKasonde 2 години тому

    I think ukakhala very short kuganiza kumavuta

  • @IreenChilingulo
    @IreenChilingulo Годину тому

    Tangowapasa ndarama athuwo chomwe akufuna

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 3 години тому +1

    Manganya mcp woyeeeeeee mutu sukukugwira pati kodi

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 3 години тому +1

    Ngwa MCP

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 3 години тому

    Ndi Secretery General NDI ndañi pakuti kaliyati wachoka

  • @DavieChisale-w1z
    @DavieChisale-w1z 2 години тому

    We are not shaken with this group

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 3 години тому

    Wapengadi usi kod nsaluzo anthu mukuwavekeranji nsaru ya utm

  • @UchiMwakhuyu
    @UchiMwakhuyu 2 години тому

    He wanted now to make these statements

  • @MWASISAINI
    @MWASISAINI 2 години тому

    Kodi UTM ya azimayi okhaokhayi ndiye iti😅😅😅

  • @WindChipeta
    @WindChipeta 20 хвилин тому

    Koma nde ziliko zilikotu

  • @YusufMoyo
    @YusufMoyo 2 години тому

    Angofuna yodyela azimayiwa njala yakhaulisa

  • @marychipofya4945
    @marychipofya4945 2 години тому

    Zopanda tsogolo akuchitazi....tili pano kuona mathelo ake.

  • @Rashidlacasi
    @Rashidlacasi Годину тому

    😅

  • @TywellShumba
    @TywellShumba 2 години тому

    Pita ku Ndilande ukaone