Sakutchika coz masiku ano miyoyo ya anthu ikufuna nyimbo za mau amulungu not za chikondizo ndi iyeyo ngati akufuna ku tchuka atembenuke mtima kumuyimbila ambuye yesu yekhanso uonanso mmensa mulungu atamutchukitsiletu coz apopo sakuyimbila mulungu tuyi
Ubrowa brother soon just keep pushing
It sounds like Truemel big up boss❤❤❤
Eeeee mbambande zedi❤❤❤❤
Ine I new him way back his songs were being played nd Mr president
Sanafikepo pa Amapiano
All it's about a time bro no matter what but you'll don't give up
Push bro
Sanamumwetse magazi
Keep it up bro. Blessings on your way
Nice
Nthawi sinafike ikazafika azatchuka
Chifukwa ndiwa ndwakumalawi
Akalowa atchuka
this guy is talented
Thumbs up bro
Apushe bax
Sakutchika coz masiku ano miyoyo ya anthu ikufuna nyimbo za mau amulungu not za chikondizo ndi iyeyo ngati akufuna ku tchuka atembenuke mtima kumuyimbila ambuye yesu yekhanso uonanso mmensa mulungu atamutchukitsiletu coz apopo sakuyimbila mulungu tuyi
Nyimbo za Chikondi tatopa nazo. Zikondi zake zosalimbazi?
😂😂😂
Low budget studio
Alowe Kaye satanic