Thanks Morton for shading more light on this, kungoti tinanamidziwa kuti mkaka ati umathandiza ma ulcers when it just makes it worse, mkaka creates an in environment in the body which requires the body to withdraw calcium from bones as a response to the situation causing fractures. At the end ndizithu ngati mikaka that add up to causing non communicable diseases koma pampanje yake ija they will blame kulozedwa as cause of these diseases.
True its a big problem for me. Even eating something with milk on it. I take when st home in case I open bowels Is it real milk though in the supermarkets in the west? Good topic. 😊
Ukunena zoona ine umanditsekulitsadi mimba ndikamwa mkaka wa fresh
Thanks pa ziphuphupo i can agree with you, zinanditulukapo
Ewe man tazingojani maphusizo kumeneko
Namachende wabodza uyu 😊
3:21 I can take a glass of milk in the morning with an empty stomach I still feel okay...
Thanks Morton for shading more light on this, kungoti tinanamidziwa kuti mkaka ati umathandiza ma ulcers when it just makes it worse, mkaka creates an in environment in the body which requires the body to withdraw calcium from bones as a response to the situation causing fractures. At the end ndizithu ngati mikaka that add up to causing non communicable diseases koma pampanje yake ija they will blame kulozedwa as cause of these diseases.
Koma bwana zovalazo mukutiposa aku Malawi fe😂😂😂
Kaya inu ikakwana thawi aliyense adzafa basi okumwa mkaka or osamwa mene umakomela ukatilidwa coffee ☕ isaaaa
Mesa ndi iwe umat mkaka ndiwabwino dzulo umatalikitsa etc...wekha wekha kuzikolwatu
Chimalaya please 😂😂😂
Ine ndmagodana nawo basi
Tawonga chomene Dada
Uzapangeso ya chiyawo nafeso aku mangochi muzitiganizila
Wabodza iwe kagwere ukoooo!
First to comment and like
😂 Ma top fan a molton
true ukamwa mkaka usanadye chilichonse munthu umatsegula mimbadi
Or utadya umatsegulabe
Those We Love Morton Baghaya
😂😂kma zlungamo za Maumau iwe 😂
Nde muli Bang Bang eish
🤣🤣🤣🤣
Ku bang'atu malile nselu kkkk
Tiyeni ku dziko la Mkaka ndi Uchi
😁😃😅😆
Tachoka lecture imeneyo uzikapasa makape
Thanks Koma nthawi Inayake iwe ngat M'malawi uzakhalepo ndi nthawi yotithandiza kut momwe kulili kwathu kuno zakudya zabwino ndizitizo?
Better kungokhala phee
Ine ndimadana ndi fungo
Zabodza izi ine ndangolemela kumene mkaka sindimamwa ndiye pano muziti mkaka siwabwino
Ndi achitsilu awaaaa, munthu usamwe mkaka ndiye uzimwa chiyani? Akagwere ndithu.....
Bodza ili 😂😂😂
True its a big problem for me.
Even eating something with milk on it. I take when st home in case I open bowels
Is it real milk though in the supermarkets in the west? Good topic.
😊
Ase stop confusing people
THANKS 🎉MORTON 🫡✅️
LECTURE
Tanva koma poti tilibe choice here in Malawi tizimwabe...nanga cow berro olo cremola tingakwanise
What a load of rubbish! 😔