Bon Kalindo - Are Malawian Politicians Aware of the Impacts of their Policies
Вставка
- Опубліковано 10 лют 2025
- President of Malawi first Bon Kalindo in his latest audio discusses what is happening in Malawi’s urban centers where traders are allegedly being abused by city council officials. Bon kalindo asks if officials at the Ministry of Local Government are aware of the impacts of their policy on the welfare of Malawians.
Mtsogoleri wa dziko la Malawi a Bon Kalindo poyamba amakambilana zomwe zikuchitika m’tauni ya Malawi pomwe amalonda akuchitiridwa nkhanza ndi akuluakulu a khonsolo ya mzindawu. Bon kalindo afunsa ngati akuluakulu a unduna wa maboma ang'onoang'ono akudziwa zotsatira za ndondomeko yawo pa umoyo wa Amalawi.
#malawi
Salutation to you the DC who is the voice for the reasons while continuing the struggle in solidarity with all who are from unprivileged backgrounds and all the pains and sufferings of extreme poverty. Ambuye akudalitseni and and greetings from North London UK 🇬🇧
Much respect the DC 🔥 tikuvutika koma dziko lililanthu
Congratulations mr Booooon kalindoooo ❤
Mulungu akusogolereni a Kalindo tili ndi boma la mikango longofuna zao ziende osati anthu ake asangalare
Mr tilinanu nanu gagaga ndi akalindo paseu tilikomweko tiwuzeni bwana titani
Double salute Kalindo
Mfundo zabwino Mr. Kalindo
Nkhan yokhudza malipilo
Kwa anthu amene akugwila mu ma shop tisalimbane nao chifukwa amwenyeo akupanga business yao and amwenyeo sakulakwa kamba koti amawalipila malinga ndi business yao mmene ikuendera.
So sizingatheke aziwalipila mk200,000 pomwe sadagulitse chifukwa atha kuwalipila ndalama zambili nthawi yochepa business singapitilile.
Nkhan ndiyoti boma lidawanamidza amalawi kuti azawalemba ntchito awalemba?
Boma lidanena kuti lisisa mitengo ya zinthu yasisa?
Boma lidati lisekula ma company yasekula?
So musalimbane ndi anthu amene akupanga business kuti aziwalipila anthuawo ndalama zochuluka chonsrcho business zao sizikuenda.
Mupange zomwe mudawalonjedza amalawi.
🎉❤
Chilungamo chokha chokhaThe DC !!!!!??
😂😂😂 koma ndaseka ameneyo nde ndigaludi
Koma boni karindo mumawawonadi mavuto athu akuvutika mumalawi tuuu
😊😊😊😊
Gift Masenti,ngati mulibe data musamazipute.
Koma ndi boma lami kango eeeee akalido mulungu azayakha
Chisilu iwe kalindo munthu ali ndi ufulu wolowa chipani chili chose angafune mnawona kuti anakumanani udindu ndani amene sakuziwa
Chitsilu ichiiii kodi chomatopa nikubwebwetaku
Pa mako iwe ameneyu ndiwachilungamo the dc
Iwe Kalindo lamulo ndi lamulo basi...za human face zakozo ukapange kunyumba kwako...the law must be enforced kodi chisawawa mmizindamu chimakusangalatsa?
Patumbo wa bambo ako
@@XasankaalibeeyNuur Kaya utukwane kaya usatukwane the law is the law. Deal with it
Akalindo ndi chisilu akulimbana ndi boma anali amp anachipo chiyani mmasowa chonena kalindo ndi kambwe
Chakwera ndi ngwazi sigalu aliyense amakhala president mu MCP ndi ngwazi
The dc
observation mr Announcer too much pre comments we just want to hear the message u have brought we are not interested with your summary try to cut your talk.. its boring
ifenso kuno kujhoni tikuti musasiye kutumikila ife osawuka
Kodi iwe kalindo. Wanzelu mmalawi muno ndiwekha?? Kusukulu unapita? Amalawi nonse ndinu zitsilu
Amene wakutumayo Aku vulalisa ayse
@@GiftFrancesco uyambe kuvulala ndiweyo, anthu ansanje inu zitsilu
nanu introduction phwiii, aaaaaa
Introduction is too much mukungotithera dada
Wovutik iweo kkkkkk
@@cjaylucky nanga intro paka an hour zikutithera nthawi tili ndi zambiri zoti tizichita pa Malawi pano , Koma Malawi yu mwati wina sanamugulitse?🤕