Це відео не доступне.
Перепрошуємо.

Bon Kalindo Ndi Guru lake la Malawi first ayankhura izi pamene anapangitsa press conference lero

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 сер 2024

КОМЕНТАРІ • 172

  • @user-mg5yy5hk9t
    @user-mg5yy5hk9t Місяць тому

    Anganga Alula malawi fist member all the way from mangochi mamatiyimilira mr big man keept up mangochi yosaopayo

  • @Moses51
    @Moses51 Місяць тому +3

    The Dc bon kalindo keep up update 💪💪🇲🇼🇲🇼💯 osawopa

  • @VungaQueen
    @VungaQueen Місяць тому +9

    Boni Kalindo munthu wotiyimilira 🔥🔥🔥

  • @user-ez8uk7py8n
    @user-ez8uk7py8n Місяць тому +3

    That is true it needs all Malawian to vote as long as he/ she is Malawian Mr president keep continue loving your poor people abd our country Malawi proud of you thanks

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Місяць тому +8

    Ndipo athu inuyo tchito mukuigwila mulungu azikusungani ndi moyo maka Mr boni kalindo simutopa mwamangidwa kambili mbili mukanakhala wina bwezi mutatisiya ife athu osauka sikuti ndinu Muthu ovutika ayi koma mumasiya pogona pabwino zakudya zabwino kukagona Malo onyasa chifukwa Cha ife aphawi kuzipeleka m,sembe pokhapo mulungu adzikudalitsani ❤❤

    • @RiyemaDomybusiness
      @RiyemaDomybusiness Місяць тому +1

      Exactly 💯💯 bon amatiyimirila ampwawi

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d Місяць тому

      @@RiyemaDomybusiness sure tidziwapephelela ndithu athu amenewa

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Місяць тому +4

    I respect your Mr nkalindo together with Malawian fest and the cautrry everyone DC is so powerful as well and you are always welcome to our team of Malawi wholld my Allah bless you always about the what happened with Malawian

    • @esaMoha-dm4kj
      @esaMoha-dm4kj Місяць тому

      I am a Malawi but now I'm in the sauth Africa estan about working on

  • @WysonJalamu
    @WysonJalamu Місяць тому +8

    Big up the DC osatopa, osafowoka, osawopa malawi ndi wathu uyu, tili limodzi pa nsewu basi.

  • @user-ml4bl2ll2g
    @user-ml4bl2ll2g Місяць тому +9

    Please please ife TIKUFUNA ufulu wathu wovota a MCP asauchotse ponamizira ma id, aliyense akuyenera kukavota popanda id

    • @Franklifo2217
      @Franklifo2217 Місяць тому

      Nzelu mulibe enanu! Anthu omwe mumalephelesa malawi kutukuka🙌

    • @hudycorex1893
      @hudycorex1893 Місяць тому

      Inu amzeru kwambiri?​@@Franklifo2217

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Місяць тому

      Anzeru ndinuyo? ​@@Franklifo2217

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm Місяць тому +1

    This is our president kalindo thanks so much for your help Malawias

  • @DavieBinzih
    @DavieBinzih Місяць тому +1

    More fire mr kalindo we proudly of you keept up we love you

  • @WezzieChimuzi-ek7bk
    @WezzieChimuzi-ek7bk Місяць тому +1

    Good job my people Ambuye azikutetezelani ndi mwanzi wawo nthawi zonse ..

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 Місяць тому

    Lets presure dem evo!....aluta continua!

  • @YousufMpunga
    @YousufMpunga Місяць тому +3

    Ndine Yusuf wakumangochi kmnso amalawi amene Ali kumaiko akunja apasidwe mwai wovota kuchokera kunja konko kumene ali

    • @patrickmacheso5062
      @patrickmacheso5062 Місяць тому

      That's true, we need to vote and choose the President that we want not this Manyaka Government, but the problem is Akazembe athu sathandiza or kuwapempha kuti atipatse mwayi ovota.

  • @FrankSpison-o7o
    @FrankSpison-o7o Місяць тому

    The Dccccccc Booooooooon kalindo inu nde anthu oti mzika zamalawi tizikupemphererani kwambili 🙏

  • @AnussaAlli
    @AnussaAlli Місяць тому

    Big up the DC Bon kalindo continue timakunyadlan❤❤❤❤❤❤🎉🎉

  • @ChristopherMadulira
    @ChristopherMadulira Місяць тому

    Congugulations Mr DC ntchito mukugwila anthu inu only God bless you ❤❤❤❤❤

  • @user-uf4db7im7d
    @user-uf4db7im7d Місяць тому

    Every malawian should be in a possession of ID, If the NRB is failing to reach all malawians for ID registration, you should expect Malawi to be on fire, because voting results will not be accepted, People have rights to vote for who they want not rigging.

  • @jogechawa6192
    @jogechawa6192 Місяць тому +2

    Bon Kalindo and malawi first our hope basi

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Місяць тому +1

    I respect your nkalindo bisid ashankwela and everyone else has been in the path of mcp I don't respect anyone anymore because the people who keep and keeling Malawian people 2025 mashall Allah bless you nkalindo 😮😮😮

  • @harrisonlowheat6569
    @harrisonlowheat6569 Місяць тому +1

    My president

  • @user-uf4db7im7d
    @user-uf4db7im7d Місяць тому +1

    This government must go

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e Місяць тому

    Good move Malawi First ❤

  • @NellieKabvina
    @NellieKabvina Місяць тому +1

    Pa ziphatsopo ndie zikudabwitsa zikupezeka kuti anthu ambiri akumadziwa tsiku lokuti akumaliza kupanga ma ID,,,sakulengeza tsiku loyamba anthu ambiri akudandaula

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Місяць тому +1

    yaa wa mcp ngati akunyasidwa ni boni karindo asavere khani zake ayi chonde ife anthu osauka tiyeni tizimuvera boni koma uzayime iwe boni tizakuvotere

  • @RemaniNkhoma
    @RemaniNkhoma Місяць тому +1

    boni karindo tingopita mawa bwanji pa sewu kuti agaru awa tiwakhawurise

  • @SamKaposa-i5c
    @SamKaposa-i5c Місяць тому

    Viva malawi first Richard mphepo umadziwa kuyankhula more fire dc

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Місяць тому +5

    Wa mcp ngt born kalindo amakunyasa usamaver nkhan Zak iwey ndy opanda zelu ife tikufuna dziko libwerer ngt kal osat mukumakambo shem on you 😢😢😢😢

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence Місяць тому

    Ulemu wanu Mr Born 🙏🙏🙏🙏

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 Місяць тому

    Well done guys kpt up

  • @user-uv5rf4zt5q
    @user-uv5rf4zt5q Місяць тому

    Malawi first all the best u are representing poor people. To be honest Malawi is the poorest country in the world our leaders are selfish we are going backwards.

  • @BacklinebwanaliBwanali
    @BacklinebwanaliBwanali Місяць тому +2

    Akupatsen moyo was utali

  • @dawsonwaya4722
    @dawsonwaya4722 Місяць тому

    Za ziiiiiiiii munthu unalephera kuimirira constituency ndiye ukati amalawi osauka aaaa zangokuvutani Moya, .

    • @robenallie6985
      @robenallie6985 Місяць тому

      Ndizako zimenezo dc number 1

    • @FatimaAyami
      @FatimaAyami Місяць тому

      Vuto ndi bomalo iyeyo amangopanga imprement

  • @Samu-q3z
    @Samu-q3z Місяць тому +1

    Boni karido ndikatundu

  • @YohaneChitapini
    @YohaneChitapini Місяць тому +1

    Mumakwana ndipo ndinu nokha boss ndagwada ndikumvesela

  • @user-dq9oe8sp8k
    @user-dq9oe8sp8k Місяць тому

    Ifetu though tilibe ma ID kma tikazavota
    Angoona kuzinamidza agwapewa
    Fireeee the DC❤

  • @AndrewNyondo-ut3gk
    @AndrewNyondo-ut3gk Місяць тому

    King David bon kalindo the DC❤

  • @AlidWidon
    @AlidWidon Місяць тому

    Wosawopa bon kalindo tili limodxi 💪💪💪🔥🔥🔥👆👆

  • @Okalekale
    @Okalekale 27 днів тому

    Tikufuna tidziwe kuti ndi ndani amapanga sponsor gulu lanuli Mr.Kalindo?.The nation should know if you claim to advocate for transparence.

  • @MercyJohnsonkanchure
    @MercyJohnsonkanchure Місяць тому

    Mr Kalindo Mulungu azikupansani zeru zakuya ngati Solomon ❤

  • @MikeKoloko
    @MikeKoloko Місяць тому

    Mumatiimilira, big up

  • @ShariffAbdul-m9t
    @ShariffAbdul-m9t Місяць тому

    I salute you

  • @RanaQari-py4bd
    @RanaQari-py4bd Місяць тому

    Mumakwana guys we love you all the time 🙏🙏🙏🔥🔥🔥🔥

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 Місяць тому

    Mulungu azikhala namu guy's 💪💪

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo Місяць тому

    Never give up guys let's see what happens

  • @lastonkandiyado4526
    @lastonkandiyado4526 Місяць тому

    Respect 🎉🎉🎉

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Місяць тому

    The DC ❤

  • @MuhammedNtaba
    @MuhammedNtaba Місяць тому +1

    ❤❤❤ The DC

  • @ImanRashidi-so4oo
    @ImanRashidi-so4oo Місяць тому

    Congratulations mr DC

  • @KeftonChimaliro
    @KeftonChimaliro Місяць тому

    Iyayi zonsezitu akupangazi akufuna ndalama mtambo samachitaso chocho anango kuwapatsa zochita ndikungokhala duuu osayakhulaso amalawi anthuwo ndi amodzi Lucia's. Anayimba kale

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Місяць тому +3

    Pick up guys chilungamo ndimwano

    • @patrickmacheso5062
      @patrickmacheso5062 Місяць тому

      Ndimayesa ngati mukhala kumbuyo kwa a name anu kkkkkkkk let's fight together, this country is belongs to all Malawians not MCP only.

  • @RanaQari-py4bd
    @RanaQari-py4bd Місяць тому

    🙏🙏🙏🙏🙏 Thnx good work

  • @GodisoneNoel
    @GodisoneNoel Місяць тому

    Asirikali achirendo muzikorathu zichepe mr DC

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Місяць тому +2

    Akumangeni ngati mwaphwanya malamulo dala mbuli

    • @kenmasta
      @kenmasta Місяць тому

      Ndiye mmene akumamumangamo ndiye akumamupeza ndi milandu yanji,,,,..ndaletu zisakusokonezeni mchimwene andale amabwera amapita koma Malawi adzakhala yemweyu ndiye let's love Malawi.

    • @user-bd5kw8oq1r
      @user-bd5kw8oq1r Місяць тому

      @@kenmasta mwanena nokha awa asiyeni koma akanalankhula zinthu zambili ndi za against popeza ine ndinapanga nawo compain ndiye sanandipatse udindo awona, zimenezo ndi zabodza,chikuwawe sichimanga dziko amwe awa ndi a ndale musokonekera sayamika ndi ankhwidzi amafuna zawo ziwayendere kalindo akudya makobidi inu mukudya nawo 🤗🤗 ayi so bola yesu

  • @user-dy5bj9ck5e
    @user-dy5bj9ck5e Місяць тому +3

    The DCCC

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli Місяць тому

    Good move bafethu salute you

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf Місяць тому

    Only GOd Bless you DC

  • @SueWahna
    @SueWahna Місяць тому

    Big up Malawi first 💪💪

  • @TiyamikeMakande
    @TiyamikeMakande Місяць тому

    Mumatiuankhulira ndinu bwana ,mutiyankhulireso za ndrama za masiye ku Capital hill Chaka chino nchachitatu ndrama sakutipatsa tikuvutika ndi ana

  • @HarrisonMangani
    @HarrisonMangani Місяць тому

    They need to address those issues other wise Mmmmm panunkha mphira

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni Місяць тому

    Firr the DC

  • @EliasMcray
    @EliasMcray Місяць тому

    Go go ahead

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 Місяць тому

    Point of correction not guru lake koma Born kalindo ndi guru la Malawi 🇲🇼 first

  • @nelsonmhango7515
    @nelsonmhango7515 Місяць тому

    Inu ndi king

  • @gracetjomane-jj3ib
    @gracetjomane-jj3ib Місяць тому

    Kutundu uyu the DC❤❤❤❤❤❤

  • @YohaneChitapini
    @YohaneChitapini Місяць тому +1

    Guys inu musazafe mulungu azikudalisani

  • @user-tw2zf7bj3e
    @user-tw2zf7bj3e Місяць тому +1

    ❤❤❤❤ guys

  • @AnockyDavidd
    @AnockyDavidd Місяць тому

    Congratulations to all

  • @Malambia
    @Malambia Місяць тому +1

    Mr kalindo ulemu wanu

  • @KhalidwePentani-c6q
    @KhalidwePentani-c6q Місяць тому

    Zopanda ntchito izo akalindo mumangofuna udindo ngat mungakwanitse kutumikila dziko aaaa zawumbuli

  • @InnocentKavalo
    @InnocentKavalo Місяць тому +1

    Zoona big umakwana dc

  • @ambeweburton
    @ambeweburton Місяць тому

    Timenyeleni nkhondo please mulungu imvani kulira kwathu

  • @PetroMatias
    @PetroMatias Місяць тому

    Amarawig fct muri nbi mfunbo zabwini timakuyamikirani

  • @Fridayasani
    @Fridayasani Місяць тому

    Osawopha Bon kalindo tikukupembela kwamulungu Kuti anzikala nawe kwina kulikonse komwe udziyenda

  • @ntandokazindzwana3083
    @ntandokazindzwana3083 Місяць тому

    Fire fire tili pa mbuso pa malawi oyambirira

  • @ritchardchakuma5725
    @ritchardchakuma5725 Місяць тому +1

    Apomwayikwanisa maiko enasaziwa Chichewa pakufunika ayaluke mbavazi 💯🔥🔥🔥🔥🔥

  • @Samu-q3z
    @Samu-q3z Місяць тому

    Zikomo boni karindo umatiyimilila big Kom amalawi sitimayamika

  • @chikoko-uj2tt
    @chikoko-uj2tt Місяць тому

    Salute 🫡 The DC

  • @user-dy4gc2hr5e
    @user-dy4gc2hr5e Місяць тому +1

    Good move

  • @HajaSande
    @HajaSande Місяць тому +1

    Zikomo kwambiri umawona patali

  • @AgnessChiwalo
    @AgnessChiwalo Місяць тому

    Your good man bon

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Місяць тому

    The DC'S mwana woooopsa kwambiri chilungamo chiyende ngat madzi.

  • @AgnessChiwalo
    @AgnessChiwalo Місяць тому

    ❤❤❤ good news

  • @JafaliAjusa-zg2xi
    @JafaliAjusa-zg2xi Місяць тому

    Respect Mr

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i Місяць тому

    ❤❤❤💯💯🔥🔥🔥

  • @LukaJaulanchirwa
    @LukaJaulanchirwa Місяць тому +1

    You people you thinking harder that is good Diction thank chakwera is not thinking

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj Місяць тому

    Following with all my chidwi

  • @shephardlonex3371
    @shephardlonex3371 Місяць тому

    Booooooooni kalindo

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo Місяць тому

    Go konko bwana DC❤

  • @kurhikhoza8298
    @kurhikhoza8298 Місяць тому

    Tipiya pa sewu akapanda kuyakha

  • @sarahmphande6108
    @sarahmphande6108 Місяць тому

    I'm sure, the government you will grant our request

  • @PreciousKARINGANIZA
    @PreciousKARINGANIZA Місяць тому

    Tilikomweko

  • @shephardlonex3371
    @shephardlonex3371 Місяць тому

    Munene kuti ife ngati A Dpp

  • @MaryNgola
    @MaryNgola Місяць тому +2

    Mmene wafikira Malawi alipodi amene akumamuona uyu kt akupanga zolakwika? Iweyotu wa MCP nkana akukubowa

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo Місяць тому

    Go konko..

  • @PiusMpando
    @PiusMpando Місяць тому +1

    Tikukunyadilani kuno

  • @DaglasUseni
    @DaglasUseni Місяць тому

    Well

  • @kashmirmohakashmirmoha8659
    @kashmirmohakashmirmoha8659 Місяць тому

    Ulemu wanu DC😊😊

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Місяць тому

    Wina Aliyense amavota kumene adabwadwira Ndipo amfumu amadziwa Wanthu wao,apapa wina Ali yense azavota amene ali mbadwa ya Malawi zama I'D za chani?zopusa

  • @ShadreckChimaimba-l9y
    @ShadreckChimaimba-l9y Місяць тому

    Osatopa big

  • @user-ru6fc3qy5n
    @user-ru6fc3qy5n Місяць тому

    Zilibwino kwambili osaopa