Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Nyimbo ivuta mmaukwati iyi asakunamize anthu. Akuvina mobisa akalowa nyumba ndaziona ine kuno
Ndipo live onse akuti muthuwu wapala akavina mmaukwati sure.
@@EllardMidule-t9o With time anthu aziyimba nawo.
Kwanu komweko zimenezo
ua-cam.com/video/b8iOeAAM3Aw/v-deo.html
Mene ndavinira ine 🎉🎉🎉🎉
Sheli banana eeee zivumbuluse wekha phoda asanathe ululu wamunyanya princess kunoEish nyimbo iyi yitiyambisa uhule ndithu nice tune 🙌
Kk
@@DorothyTaumbe-zk3ki kwachema 🔥🔥
Khangat ndayamba kumukonda Emmie ❤❤❤❤
Inenso I Love her
From Gwamba. Let's gather here
We here🔥💃
Apapa mwaimba kwaya , it's giving CCAP vibe .
It's giving Masintha Chigwirizano
@@fortunemumba1508😂😂😂😂 ndipo its giving Stella mwanza
It's giving thoko katimba anaphi
Ineso ikundinvekela mwanchitaitsimuso choncho eeeee😂😂😂
😂😂😂
Cape town watching umatimvetsa kukoma kwambir deebo fire 🔥🔥🔥
From Kelly kay let's gather here ❤
😂😂😂😂😂
Talent promax ,Akometsi on fire . Upcoming ndiyemweyu enanu zilimbanani kwinako
Nyimbo iyiyi iribho koma poti ndi Amalawi msanje too much koma osafooka mwana iweyo umatha ♥️♥️.
Kwambiri
Anthu nsanje mfana uyuyu amatha kuyimba heav
Mikozi fan anthua akuti Emmie deebo akufunika ching'aning'ani Ngati top security
honestly, if it had a different beat, different melody, different lyrics, different sound effects, different artist, different message and a different genre; it could've gone hard🔥🔥
Broo😂😂
@@GiftSambani-n8p 💀💀😂😂😂😂 🏃♂️
i agree with you, it would have been a different song 😂😂😂
@@DysonLembani-m2r I know right💀😂😂
Bro spitting 🔥🔥
Nfanayi wayamba kutha zinthutu… apa ndamvela osakaka… a new fan here.🎉
From akometsi let's gather here
We here 😂😂❤
Ndipo here we are
Ife pano
We here akometsi
Ife pano 😂
Her voice is beautiful
Ndikhale pati ndimvere nawo Sheli Bananayi🍌🔥🔥
Kuseli kwa nsuko 😅
Emmie again!!!! Zambians 🇿🇲🇿🇲 where are you 👊👊🔥
On top akometsii km mukukometsadiiii more life
I like this music from ethiopia
Úzbekistan🇺🇿🇺🇿🇺🇿🇺🇿🇺🇿
Iwe ndthu ukanawina miss culture global😁😁🔥🔥
Komatu nyimbo wapha iyi emmie
Ndilondola eh👍
Kamwanaka kukuoneka kuchepa koma kali ndi nkhani zondipangitsa kumwetulira pandekha ❤❤❤😂😂😂
Nyimbo abwino❤❤❤❤
Gud pa gud .. Or pa made on Monday tikanati ili bhoo man joy
Best song of the year Best female artist if the year Best management of the year akometsi ntchito mukuyigwira receive ur flowers 🤗🤗🤗🤗🤗🤗
Emmie.. My favorite being😘... Keep the fire burning my dear
Mwa uyu yekha muli luso la nyoo.. What an achievement 💥
i like your songs Emmie keep this local vibe forever
❤keong Kadango amatha ntchito
Nyimbo ya bwino yachi Malawi🇲🇼🔥🔥🔥
Akadaimba wa kunja mudakanva akuyamikira
Talent that is not supposed to be over looked.More blessings and favor upon your career ❤
Makonda kusiyana, sindinayikonde tikumana pompa next release
Akaso nde kabweratu🥰🔥🔥🔥 sheli yemweyo
why people are hating this massive song in town 🔥🔥🔥🌹❤️❣️
We are from Akometsi, ndipo nane ndilondola wanga
Nyimbo iyi mwa para
Kwambiri 😂😂
The talent is natural any one to like my comment I will come back to watch this video ❤
Wow! This song has the love vibe 🔥keep on elavating deebo😎
Wow !! This song has the vibe🔥keep on elavating and entertaining us deebo😎😊
Great piece of music. Thanks akometsi.Bravo Deebo
Uyuy akufunika award ndithu 🔥🔥🔥
From mikozi let's pano ❤
Sheli banana wanga phulizi dzibvumbulutse ndatopa mkukusaka chonde 🥰🥰🥰
Kuimba mukuyimba bwino koma eeeeeeeeee every week mwatulusa aaaaaaa
nyimbo ngt izi ndizimene zimakometsa mma show muu ...nice tune💥💥💥💥💥💥
Good song am enjoying it - from lusaka Zambia
Nde pali Lady Aika... Simple. Talent kumalawi ilipo
Guys ngt mukufuna kubwelaso muzangosegura UA-cam app yanuyo ndikupanga search kut jetu waimanya bas zatheka musiye zomati like my comment aliyese wabwera ndi mofaya wake kuno😂
Naneso ndikupita ndikukamusaka wanga❤❤❤
Umatha Emmie ❤🎉
Nice tune, we listen to music for different reasons like, to dance, to get a lesson, for entertainment.. This one tivinadi.. Ilibho
Ndilondora wanga mesa?❤🔥❤🔥❤🔥
I never knew this girl has potential like this until this song ❤❤❤ Umakwanaa hop🔥🔥🔥🔥
Zosangalasa chifukwa ❤ video inali pa home ❤❤❤
Mwalawitsatu 🔥
Akometsi nane ndisayineni nditchuke ngat emmie, this is a big tune 🎉🎉❤ uyu apitilize manganjewa akumukhala eeh ❤❤🎉
Ukali wako Emmie industry ilipa dangerous 😀
Levels
Dolo kwambiri iweyo ndimahop anga ❤
Mu industry yi muzitero ndithu hit after hit,,,,sheli wanga kayaa uli kut😎
❤❤❤ ndazikonda 🥳🥳🥳
Km ka munthu aka ndika beautiful kanangolakwisa kukhala kopanda hip🔥
Tafka all the from akometsi🤗
Akometsi aja ankangokuchedwesa mammie 😂😂😂🤗🤗🤗🤗
😂😂 inu zoti nyimboyi yayamba ndi akometsi omwewo simunawone.?
Mwana ndi Dolo uyu.... Sher banana on fire 🍌🍌🍌🔥🔥🔥
From Kell Kay 💃💃💃💃let's dance the tune... Girl u are talented without forcing
Masiku sakoma onse apapa ndye ndye ai aaahh
I don't get it why people hate this kid,, She is talented
Jealous amaona kuti mfanayi amapanga zinthu zosempha ndi sinkhu wake
Akometsi mwana mwamunola ndi grinder uyu🔥🔥🔥🔥🔥
It is a blessing to be a namadingo fun❤
Iyi nd mbambande!!
Mwana uyu alibwino ❤️❤️❤️❤️
Sounds good specifically for weddings and zinkhoswe Nice song 🔥
Eeeeeeeh 😍😍😍😍😍😍😍😍😍 iyiyi simunaiphonye
Thise sounds exactly like that of Sly C track titled ine ndi wako..go check it out and come back here again.
AKOMETSI sheli bana🤣🔥🔥🔥
Koma mwana kaziii umakwanisaaaa mesa 🔥🔥🔥
From gwamba who else?
We here
Best artist of the year She never disappoits Actually my favourite 🔥🔥🔥
Emmie deebo umatha 💕 n video mwapha
The only bad thing about this tune is that it ends
Mbwelela zen zen
Iyi nde ndipa repeat ndaikonda nyimbo iyi oooo
Ndivineko ine💞💖💖✨🌟🌟umatha emm d
Kuli Gwambayo eeeh akukwezatu mutengo😂😂😂😂😂😂😂😂🤩Anyway Sheri banana bs💓💓💓💓💓
Simomwe kuliri ❤❤❤❤❤❤ umatha iweyo mamiiie
Wandikumbutsa padzana👌💚
Wow congratulations that's good job well done young lady
Stella mwanzaa appaaa🔥🔥koma ilibhoo
Iweyo ndi nyimbo izizi nde ndi khethekhethe2🔥🔥🔥🔥🔥
Upcoming uyu akutenga bs
Umatha Keep fire burning
Not my cup of tea, but still, it's a wonderful song. The filmography & directing is soo good. Great job Emmie. Always rooting for you ❤️
This tune is on repeat in my playlist❤❤
Anthu tachimvereni chi nyimbo muma zima Speaker 🔥🔥🔥
Nyimbo ngati chitelela
Nduganiza zongomukwatila azikaimbira kunyumba🔥🔥🔥🔥🔥
Timenyanetu eti?
This is nice, pure childhood rhythm..💕💕
Emmie umatha 😭🥳
Amaimba izozo ali mkalasi?😂😂MhuuMuli voice eeh 🔥
Nyimbo ivuta mmaukwati iyi asakunamize anthu. Akuvina mobisa akalowa nyumba ndaziona ine kuno
Ndipo live onse akuti muthuwu wapala akavina mmaukwati sure.
@@EllardMidule-t9o With time anthu aziyimba nawo.
Kwanu komweko zimenezo
ua-cam.com/video/b8iOeAAM3Aw/v-deo.html
Mene ndavinira ine 🎉🎉🎉🎉
Sheli banana eeee zivumbuluse wekha phoda asanathe ululu wamunyanya princess kuno
Eish nyimbo iyi yitiyambisa uhule ndithu nice tune 🙌
Kk
@@DorothyTaumbe-zk3ki kwachema 🔥🔥
Khangat ndayamba kumukonda Emmie ❤❤❤❤
Inenso I Love her
From Gwamba. Let's gather here
We here🔥💃
Apapa mwaimba kwaya , it's giving CCAP vibe .
It's giving Masintha Chigwirizano
@@fortunemumba1508😂😂😂😂 ndipo its giving Stella mwanza
It's giving thoko katimba anaphi
Ineso ikundinvekela mwanchitaitsimuso choncho eeeee😂😂😂
😂😂😂
Cape town watching umatimvetsa kukoma kwambir deebo fire 🔥🔥🔥
From Kelly kay let's gather here ❤
😂😂😂😂😂
Talent promax ,Akometsi on fire . Upcoming ndiyemweyu enanu zilimbanani kwinako
Nyimbo iyiyi iribho koma poti ndi Amalawi msanje too much koma osafooka mwana iweyo umatha ♥️♥️.
Kwambiri
Anthu nsanje mfana uyuyu amatha kuyimba heav
Mikozi fan anthua akuti Emmie deebo akufunika ching'aning'ani Ngati top security
honestly, if it had a different beat, different melody, different lyrics, different sound effects, different artist, different message and a different genre; it could've gone hard🔥🔥
Broo😂😂
@@GiftSambani-n8p 💀💀😂😂😂😂 🏃♂️
i agree with you, it would have been a different song 😂😂😂
@@DysonLembani-m2r I know right💀😂😂
Bro spitting 🔥🔥
Nfanayi wayamba kutha zinthutu… apa ndamvela osakaka… a new fan here.🎉
From akometsi let's gather here
We here 😂😂❤
Ndipo here we are
Ife pano
We here akometsi
Ife pano 😂
Her voice is beautiful
Ndikhale pati ndimvere nawo Sheli Bananayi🍌🔥🔥
Kuseli kwa nsuko 😅
Emmie again!!!! Zambians 🇿🇲🇿🇲 where are you 👊👊🔥
On top akometsii km mukukometsadiiii more life
I like this music from ethiopia
Úzbekistan🇺🇿🇺🇿🇺🇿🇺🇿🇺🇿
Iwe ndthu ukanawina miss culture global😁😁🔥🔥
Komatu nyimbo wapha iyi emmie
Ndilondola eh👍
Kamwanaka kukuoneka kuchepa koma kali ndi nkhani zondipangitsa kumwetulira pandekha ❤❤❤😂😂😂
Nyimbo abwino❤❤❤❤
Gud pa gud .. Or pa made on Monday tikanati ili bhoo man joy
Best song of the year
Best female artist if the year
Best management of the year akometsi ntchito mukuyigwira receive ur flowers 🤗🤗🤗🤗🤗🤗
Emmie.. My favorite being😘... Keep the fire burning my dear
Mwa uyu yekha muli luso la nyoo.. What an achievement 💥
i like your songs Emmie keep this local vibe forever
❤keong Kadango amatha ntchito
Nyimbo ya bwino yachi Malawi🇲🇼🔥🔥🔥
Akadaimba wa kunja mudakanva akuyamikira
Talent that is not supposed to be over looked.More blessings and favor upon your career ❤
Makonda kusiyana, sindinayikonde tikumana pompa next release
Akaso nde kabweratu🥰🔥🔥🔥 sheli yemweyo
why people are hating this massive song in town 🔥🔥🔥🌹❤️❣️
We are from Akometsi, ndipo nane ndilondola wanga
Nyimbo iyi mwa para
Kwambiri 😂😂
The talent is natural any one to like my comment I will come back to watch this video ❤
Wow! This song has the love vibe 🔥keep on elavating deebo😎
Wow !! This song has the vibe🔥keep on elavating and entertaining us deebo😎😊
Great piece of music. Thanks akometsi.Bravo Deebo
Uyuy akufunika award ndithu 🔥🔥🔥
From mikozi let's pano ❤
Sheli banana wanga phulizi dzibvumbulutse ndatopa mkukusaka chonde 🥰🥰🥰
Kuimba mukuyimba bwino koma eeeeeeeeee every week mwatulusa aaaaaaa
nyimbo ngt izi ndizimene zimakometsa mma show muu ...nice tune💥💥💥💥💥💥
Good song am enjoying it - from lusaka Zambia
Nde pali Lady Aika... Simple. Talent kumalawi ilipo
Guys ngt mukufuna kubwelaso muzangosegura UA-cam app yanuyo ndikupanga search kut jetu waimanya bas zatheka musiye zomati like my comment aliyese wabwera ndi mofaya wake kuno😂
Naneso ndikupita ndikukamusaka wanga❤❤❤
Umatha Emmie ❤🎉
Nice tune, we listen to music for different reasons like, to dance, to get a lesson, for entertainment.. This one tivinadi.. Ilibho
Ndilondora wanga mesa?❤🔥❤🔥❤🔥
I never knew this girl has potential like this until this song ❤❤❤ Umakwanaa hop🔥🔥🔥🔥
Zosangalasa chifukwa ❤ video inali pa home ❤❤❤
Mwalawitsatu 🔥
Akometsi nane ndisayineni nditchuke ngat emmie, this is a big tune 🎉🎉❤ uyu apitilize manganjewa akumukhala eeh ❤❤🎉
Ukali wako Emmie industry ilipa dangerous 😀
Levels
Dolo kwambiri iweyo ndimahop anga ❤
Mu industry yi muzitero ndithu hit after hit,,,,sheli wanga kayaa uli kut😎
❤❤❤ ndazikonda 🥳🥳🥳
Km ka munthu aka ndika beautiful kanangolakwisa kukhala kopanda hip🔥
Tafka all the from akometsi🤗
Akometsi aja ankangokuchedwesa mammie 😂😂😂🤗🤗🤗🤗
😂😂 inu zoti nyimboyi yayamba ndi akometsi omwewo simunawone.?
Mwana ndi Dolo uyu.... Sher banana on fire 🍌🍌🍌🔥🔥🔥
From Kell Kay 💃💃💃💃let's dance the tune... Girl u are talented without forcing
Masiku sakoma onse apapa ndye ndye ai aaahh
I don't get it why people hate this kid,, She is talented
Jealous amaona kuti mfanayi amapanga zinthu zosempha ndi sinkhu wake
Akometsi mwana mwamunola ndi grinder uyu🔥🔥🔥🔥🔥
It is a blessing to be a namadingo fun❤
Iyi nd mbambande!!
Mwana uyu alibwino ❤️❤️❤️❤️
Sounds good specifically for weddings and zinkhoswe
Nice song 🔥
Eeeeeeeh 😍😍😍😍😍😍😍😍😍 iyiyi simunaiphonye
Thise sounds exactly like that of Sly C track titled ine ndi wako..go check it out and come back here again.
AKOMETSI sheli bana🤣🔥🔥🔥
Koma mwana kaziii umakwanisaaaa mesa 🔥🔥🔥
From gwamba who else?
We here
Best artist of the year
She never disappoits
Actually my favourite 🔥🔥🔥
Emmie deebo umatha 💕 n video mwapha
The only bad thing about this tune is that it ends
Mbwelela zen zen
Iyi nde ndipa repeat ndaikonda nyimbo iyi oooo
Ndivineko ine💞💖💖✨🌟🌟umatha emm d
Kuli Gwambayo eeeh akukwezatu mutengo😂😂😂😂😂😂😂😂🤩
Anyway Sheri banana bs💓💓💓💓💓
Simomwe kuliri ❤❤❤❤❤❤ umatha iweyo mamiiie
Wandikumbutsa padzana👌💚
Wow congratulations that's good job well done young lady
Stella mwanzaa appaaa🔥🔥koma ilibhoo
Iweyo ndi nyimbo izizi nde ndi khethekhethe2🔥🔥🔥🔥🔥
Upcoming uyu akutenga bs
Umatha Keep fire burning
Not my cup of tea, but still, it's a wonderful song. The filmography & directing is soo good. Great job Emmie. Always rooting for you ❤️
This tune is on repeat in my playlist❤❤
Anthu tachimvereni chi nyimbo muma zima Speaker 🔥🔥🔥
Nyimbo ngati chitelela
Nduganiza zongomukwatila azikaimbira kunyumba🔥🔥🔥🔥🔥
Timenyanetu eti?
This is nice, pure childhood rhythm..💕💕
Emmie umatha 😭🥳
Amaimba izozo ali mkalasi?
😂😂
Mhuu
Muli voice eeh 🔥