Germiston Paradise Choir CHITILENI CHIFUNDO (Malawi Gospel Music Update)

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 19 вер 2024
  • Artist : Germiston Paradise Choir
    Title : CHITILENI CHIFUNDO
    Video Prod : ########
    Audio Prod :########
    Record Rebel: Independent
    Malawi Gospel Music Update

КОМЕНТАРІ • 11

  • @TomHardy-b4x
    @TomHardy-b4x Рік тому

    Amen munthu ndiwovuta

  • @frankkaumba
    @frankkaumba Рік тому

    God's time is the best.Amen

  • @ettahchipeta4795
    @ettahchipeta4795 2 роки тому +1

    Amen munthu ndiovuta

  • @moriahquilayah5684
    @moriahquilayah5684 2 роки тому

    Zoonadi Munthu ndiovuta

  • @ingridmokwena4495
    @ingridmokwena4495 2 роки тому

    zinthu zimenezi ndizoipa pamaso pa ambuye

  • @ingridmokwena4495
    @ingridmokwena4495 2 роки тому

    tsitsi limeneli lidapangidwa ndi satana chotero mukavala zimamukonda zedi amadziwa kuti onse ochita zimenezi sakalowa kumwamba

    • @aliciamajamanda
      @aliciamajamanda 3 місяці тому

      Inu mudamuwona Satan yo akupanga?😂 nde mukatero ndekuti chilichonse chidapangidwa ndi Satan ngakhale zovala mumavalazo zidapangidwaso ndi Satan yo 😊 osamayankhula zinthu zopanda umboni

  • @JihnMathera
    @JihnMathera 9 місяців тому

    Zilibwino tikamabvera nyimbo Zanu kuno sA.

  • @tsankhulojamson6202
    @tsankhulojamson6202 Рік тому

    excellent

  • @ingridmokwena4495
    @ingridmokwena4495 2 роки тому

    nyimbo zabwino koma chimodzi chokha zomwe amavala azimayi kumutu zomwe ambuye sasangalala nazo ndi pastor matiasi kuchokera kuno ku joni

    • @aliciamajamanda
      @aliciamajamanda 3 місяці тому

      Inuyo ndamene simukusangalala nazo osati Ambuye 😅 tiyeni tiphunzire zinthu kuyamikira osati kuweluzana 😊 anthu wa akuyimba za Mulungu osati zazimene avalazo ku mutu kumasiyanitsa zinthuzi