This song has done something last Sunday night was listening to it with a prophetic spiritual sight.The testimony came yesterday 3days later. May God bless the one who sung this song.....
This song!!! 😢😢omg she sang my life testimony! Glory to God for his faithfulness over my life!!😢😢🙏🏽🙏🏽🙏🏽 Thank you Jesus! Ndinu Yahweh pa Moyo wanga Yehovah, Palibe ofanana nanu! Mwandichotsa kosadziwika ine!😢😢
Am smiling 😂 like mumu becoz of this powerful song iwish people akanaipanga recognize nyimboyi momwe amapangila za secular just that anthu timakonda zadziko than zakumwamba but this song it's powerful and I love it
This song has done something last Sunday night was listening to it with a prophetic spiritual sight.The testimony came yesterday 3days later. May God bless the one who sung this song.....
Ndinu yaweh patsogola langa, Just focus on God, sachedwa safulumila, zambiri zizakutsatila ❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉Dzina lako lizasinthaa 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
This is beautiful l'm so blessed thanks melifa may God bless you as you continues comfort us
You are indeed Yahweh. Jehovah nditama inu
Kukwalapula nyimbo osati chibwana iyi ndiyo gospel yokhudza kukusendeza chifupi ndi Ambuye.
This song!!! 😢😢omg she sang my life testimony! Glory to God for his faithfulness over my life!!😢😢🙏🏽🙏🏽🙏🏽 Thank you Jesus! Ndinu Yahweh pa Moyo wanga Yehovah, Palibe ofanana nanu! Mwandichotsa kosadziwika ine!😢😢
Yes Ambuye ndinu yahwe,mumapanga njila popanda njila❤❤❤
I even don’t know how did i get myself into this song it has turned into my daily routine
God bless you
Nyimboyi yandisangalatsa ndipo ikundidalitsa kwabasi ojambula zidayoso amayidziwa ntchito yake
Ambuye akutsogoleleni pawutumiki wanu chemwali
👏👏👏
Komatu anthu munangobadwa ndimawu olalikira mmmm.best song
Indeed ndinu yawe pa chilichomse,ambuye mumaona ovuti mthawi pitilizan kutipatsa mzeru kuti tipitilze kupeza zosowa,ambuye ndinu wazatheka bwanji
I always crying when listening to this song ....eeeeee imandisuntha kwambiri....O.M.G.❤
From nobody to somebody.God you are great.
I just come to know this beautiful song, but indeed Lord is Yahweh in my everything. Can't stop listen to this song❤❤
ndinu yaweh pa moyo wanga indeed . yaweh in my everything.
To say the truth ndachoka kutali I like the song it has changed my life. God loves all of us his name should be glorified amazing
😢😢timaiwala pachomwe tibadwila mulungu timamusiya behind
This song always gives me hope & courage that with God anything is possible
Am so blessed with this song ndisaname
Ndamvetsela thau whole day lero. Zoona ndinu Yahweh pa moyo ndi banja langa
Mwayankhula ndi moyo wanga amen 🙏 amen
Ndinu Yahweh pa banja langa...that's powerful
Beautiful song, watichotsadi kutali kosadziwika. Yahweh
You are the GOAT Ndirande Anglican Voices❤
This sonf touches my heart,nyimbo yotsitsimutsa kwambiri,😢 amen and amen
Mwayankhula ndi moyo wanga this two ladies ai ndithu proceed to praise your God
Amen
Ndinu yaweh PA moyo wanga... Amen amen!!
My past and what I am presently is a good proof that God is so loving. Let others mock but I will live to testify of your goodness'
I feel blessed when l listening thing song oooo thank you juses 🙏🙏
Great ladies, this is what we call Gospel, keep it up ladies ❤❤
powerful song inuyo ndimdalitso..... tikaona komwe tikuchoka iyeyo ndi Yahweh muzonse .... more Revelation ladies .... love u
Amen... Milefa sisters really appreciate you
I like this Song, imandisuntha mmoyo wanga ndithu.
Ndinu Yahweh pa moyo wanga, Yahwe pa banja langa..
That's powerful mum n may the Good Lord continue blessing you
Ndinu yahwe paciliconse canga ❤on repeat
Nyimbo yamphamvu mama, komaso ikundidalitsa🎉🎉🎉
Ndinu yaweh zoona ndikuti mutamandike muzinthu zonse zamoyo zonse 🙏🙏🙏🙏🙏
Yes Yahweh you're the game changer!!!!!
This is worship at it's best am blessed amen and amen
What a beautiful song,,nyimbo iyi nsaname mumayankhula kwambili ndi moyo wanga,,Yesu akukongoletsa moyo wanga..
Mmavera pa ZBS Pano takumana , very nice message
Indeed you are Yahweh baba so blessed with this song
Mbambande mayi mwakwapula and I'm blessed
Powerful muli uthenga waphamvu
Full gospel music
So blessed
Will be a born again cz of this song 😢cz wowwo
Ndimasunthika ndikamamva nyimbo iyi amen 🙏🙏
The powerful do g and my spiritual anthem each Day I can see the glorious of God
Ndinu Yahwe pa moyo wanga❤️❤️
Very NYC song with revelations
Good vocals. Respect is inorder chemwali. Mumatitsimutsa! Bravo
I like this song.. Eish there's a strong message in it...
Mukundiyandikitsa pafupi ndi mulungu ❤❤
Nyimbo iyi imandizendezera chifupi nda mbuye ambuye azikudaritsani ndithu cc
What a song!talking about my real history ❤
I have been looking for this hit
Powerful
Yahweh pa banja langa
Good work nyimbo Zanu ndizodutha🙏🙏🙏
Paul Sagona
May the good Lord bless you it's arevalation
Wonderful sisters
My mom tiyese,,ndi kakumbikila tikuyimba limodzi ku senga-bay singers mama,mumatha inuyo,
Beautiful song keep it up mumie inuyo ndi makina
You are yaweh to my situation 🙏
Amen indeed ndinu Yahweh pa moyo wanga
Ndinu Yahweh pamoyo wanga , gory to be the lord
What a beautiful song…HE is GOD in everything indeed!!!
Nice song
This is a very unique praise song. The message is so invigorating and soothingly sweet!
I like this song
wer
It's best track.. listening from Mozambique
Nyimbo iyi imandisuntha kooopsa🎉❤
Nyimbo iyi imandidalitsa zedi, sinditopa kuimvera.
Very Very true Yahwe ndi chilichonse pamoyo wanga
Ndinu yahwe pa moyo wanga🙏❤️❤️❤️
Mwandichotsa kutari yahwe amen 🙏
Ndinu yahweh pamoyo wanga,,wandichotsadi kosadziwika
Iiiii nyimbo ndaikonda bwanji.
Ambuye akudalitseni
Powerful song God bless
Amen, ndinu YAHWEEE pamoyo wanga YEHOVA
This is so touching song. Keep on sister
Oh yes!!! Your name is yaweh
what a blessed song .to God be all the glory, ambirife tuchokera kutali sure 🙏 🙌
I like the song it touches all the corners of my life
Amen! Indeed Jehovah you are Yahwe pamoyo wanga!Glory be to God in Jesus Christ name!
Share me the audio am failing to download it NOT the video
Inspirational song, ndinu yawe pamoyowanga. I like this song. God bless you ladies. May He remember you, amen.
Nyimbo iyi imasintha Nyengo zanga komanso imadzetsa Chimwemwe pa Moyo wanga
Ndipo powerful song yachirimbikiso
Dzina layehova lizilemekezeka nthaw zonse
Nyimbo iyi imandirimbikitsa, pitirizani kuenda ndiambuye kuti zamphavu zipitirire
Kuimba koma uku....mumatha inuyo
Zoona zake ndinu Yaweh, Amen Amen
I salute your Faith ladies. Mwaimba bwino kwambiri. Am blessed 🙌💃
Sweet spiritual beat with absolute soul healing.
Nice song l like it so much
Thanks and Amen
@@josephtchika❤❤
@charlesmuwanya7845 Amen
My life definition
Yahweh can only be understood through his revelation.
Powerful!
Beautiful song may God bless you mama
Uuuuuuuuuuuu zikomo kwambili mai wanga ndimakukondani kwambili...lelo tsiku loyamba kuionelela vedio imeneyi ..ndinkangovela nyimbo iyi imandisuntha kwambili
I like your song, it's so amazing may God bless you
I like it maimbidwe apamwamba
Ndatsitsimuka kwambiri keep it up sister
Glory🎉🙂..He is Yahweh
It`s my prayer that He be Yahweh in all aspects of my life, So help me God
Blessed with the song... feeling like playing it again and again
I like this song..I listen to it everyday
Am smiling 😂 like mumu becoz of this powerful song iwish people akanaipanga recognize nyimboyi momwe amapangila za secular just that anthu timakonda zadziko than zakumwamba but this song it's powerful and I love it
Amen and Amen
Ndinu yahwe ndidzakhara mfulu ndi kukongoletsa moyo.