Times Exclusive..A Nicholas Dausi kuwakana a APM as 2025 presidential Candidate

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 26 сер 2024

КОМЕНТАРІ • 199

  • @ibrahimwezely-pn6te
    @ibrahimwezely-pn6te Рік тому +4

    Komatu dpp isamale izizi sizingabweretse chipambano, chipanichi ndichamphanvu ngati onse ali limodzi united. Chiyembekezo cha amalawi chili ku dpp koma nd🎉immene zikuyenderamu kaya tiziziona. Koma asawadelere adausi ndi ena omwe akutsutsana ndi akuluakuluwa

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk Рік тому +5

    Hie guys no politician in Malawi will come to save our interest, they will be saving their own interest with their families.
    Let's go out there and work hard and support our families these guys akupanga Michele yawo ife tizingovutika nazo chabe.

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 Рік тому

      Koma achinyamata ndi amene akumva kuwawa dziko, yet ndi amene Safuna kulowa ndale, dziko la malawi panopa likufunika andale atsopano.

    • @Asidibrahim
      @Asidibrahim Рік тому

      U are right

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Рік тому +6

    Brian akuluwotu abwera ndi nfundo zosanveka
    Chifuwa akugwilitsa ntchito may oti, AKUTI, zikuonesa zokha adausi ndi ndioononga,
    Akuluwa ndi osusuka Msonda 2, Ukufuna uwauze Anthu chani😂😂😂 akuti akuti akuti
    Interview yonse yathera ndi mawu oti AKUTI kkkkk koma ndiye publicity secretory abambo Inu ndi ofuntha

  • @evansedgarmatope2463
    @evansedgarmatope2463 Рік тому +10

    I have started to love Nicolas H.Dausi, he speaks the truth now....

  • @norabanda3891
    @norabanda3891 Рік тому +2

    I think B ans D should get married..they really get along well...they understand each others political language and share a great sense of humour ...bless them 😂😂😂😂😂🎉🎉🎉uluuuuuu

  • @chisomombeta6446
    @chisomombeta6446 7 місяців тому

    Powerful interview.....koma nkhani ndiyakuti onse amene anasumira chipani no chance ....Ayambitse chao

  • @user-fw8so5st6d
    @user-fw8so5st6d Рік тому +1

    I wish could understand language, but looking and listening at the clip shows that here is a serious thing going on

  • @patrickmubiana9505
    @patrickmubiana9505 Рік тому

    Independence. Of Zambia. Was on 24. October. 1964. Not 1963. Thanks big Man. Following you from Zambia.

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 Рік тому +5

    A dausi ngati mukufuna kusiya chipani dzingopitani Ku MCP komwe munaliko sitikukudandaula wava

  • @teddienamabande671
    @teddienamabande671 Рік тому +3

    Dausi ndiosokoneza.

  • @chipi892
    @chipi892 Рік тому +2

    Yambani chipani chanu Mr Dausi to ease your pain

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Рік тому +5

    A Brian inunso ndi munthu osokoneza adausi ku nsonkhano sadapite zimenezo azitenga kuti ? Adausi zawavuta chifukwa zofuna zawo sizidatheke akatengane ndi nankhumwa akaone kopita

    • @esthergweje4038
      @esthergweje4038 Рік тому

      Munthalika akumufunatu ndi anthu mmamidzimu ndi nkona amzanu anaona kuti azangoimira Munthalika yemweyo bwanji a Dausi mungoyambitsa chipani chanu at least mukamasuke musawasokoneze anthu tikuvutika ndi ifeyo osati inu ovuta ndi ife amalawi osati inu

  • @lyiemax
    @lyiemax Рік тому +3

    Dausi ndiwa MCP palibe chanzeru chimene anganene chomanga chipani chathu cha DPP

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Рік тому +2

    Brain mumawaitanila chiani amenewa. Nthawi Yao inatha. Tinatopa nazo nzeru zao zoononga dziko

  • @towellabanda2218
    @towellabanda2218 Рік тому +4

    Dausi have learned his lessons
    I support him 😂😂😂😂

  • @StevenPongolani-pp9by
    @StevenPongolani-pp9by Рік тому

    Brian banda continue doing your good job

  • @joyceellis9045
    @joyceellis9045 Рік тому +5

    Anthu awiri awa tsiku lina adzagwirana pa manja 😂. Koma they are like Tom and Jerry. They need each other's presence 😅.

  • @user-wp2bp4hx5g
    @user-wp2bp4hx5g Рік тому +1

    Koma mukungoona kuwada a Dausi,Munthuyu akulankhula zoona mmene multiparty imakhalira

  • @TrysonChimenya4-fm8nt
    @TrysonChimenya4-fm8nt Рік тому +1

    Dausi is showing signs ,of going back to MCP, Politics indeed is a dirty game, Never trust these recycled politicians.

  • @walusungukayange8759
    @walusungukayange8759 Рік тому +1

    This is one of the best interview. I always like the interaction between Brian and Dausi.... You're really democrats. ❤❤❤❤❤

  • @thondoyaenterprise3795
    @thondoyaenterprise3795 Рік тому

    😂😂😂 big up Nic , i agree with you the party doesn't belong to a person .

  • @user-xd7kw4ze6h
    @user-xd7kw4ze6h Рік тому +1

    Anthu awa ndi ma brothers😂😂😂

  • @victoryganizanimwale9046
    @victoryganizanimwale9046 Рік тому +1

    Brian Banda you are very good in this field of interviewing people..Keep it up good work sir

  • @user-tx7ms9xs9q
    @user-tx7ms9xs9q Рік тому

    Akuti akuti akuti akuti akuti,akutiyo ndani

  • @jonathanchirwa3297
    @jonathanchirwa3297 Рік тому +1

    ❤❤😂😂😂 Mr Banda you're super

  • @patrickmsendema4982
    @patrickmsendema4982 Рік тому

    The best interview

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt Рік тому +1

    Dausi bwinotu osazimangilira muyankha bwanji zithu zoti inu kunalibe kkkkkkkkk

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 Рік тому +3

    this is again one of the best interviews. Dausi ndi Brian amayakitsa moto ahahahaha

  • @user-zc4wl5pc3m
    @user-zc4wl5pc3m 7 місяців тому

    Politics devide and rule

  • @frankkuluunde
    @frankkuluunde Рік тому

    You are doing good so not forget kuti these people read more people while Brian zidamukanika Ku State

  • @user-ij6nq4dr3s
    @user-ij6nq4dr3s Рік тому

    Awatu alindimbali yawo Mr Dausi mukwaziwa sanganene zabwino ku Dpp

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 Рік тому +4

    Dausi wa kwathu ku Mwanza koma zochita zanu mulibe chitukuko and zokamba zanu mmmmmm manyaka

    • @robertrichman9376
      @robertrichman9376 Рік тому +2

      Nduona ngati akutumidwa ndi MCP galu uyu kuti ayipite DPP, komaso akufuna kuti milandu yake ikhululukidwe

    • @edsonnyirenda-uv3sb
      @edsonnyirenda-uv3sb Рік тому +1

      Pena muzingokara chete basi,osamangoyankhira zili zonse

  • @patiencetebulo
    @patiencetebulo Рік тому +1

    Dausi ndiwe chitsiru bas ok

  • @edwardmusamba8173
    @edwardmusamba8173 Рік тому

    Hon Dausi were u there ? If u were not there I will appreciate u investigate properly B4 u comment. U hv a very good base for your argument but u were suppose to attend that meeting so that u tell them your opinion.

  • @user-yt2op5rl2q
    @user-yt2op5rl2q Рік тому +1

    Daus ndiwa nankhumwa akulankhulira nankhumwa team yanankhumwa mbuzizawanthu

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 Рік тому +2

    Dausi ndi brian aaa anthu inu mukakumana ayi 🤣🤣🤣🤣ndimaseka

  • @frankkuluunde
    @frankkuluunde Рік тому

    That's political science

  • @user-cq5zb4lb4d
    @user-cq5zb4lb4d Рік тому

    i love this dausi mpaka ndayamba chifuwa ndikuseka kkk

  • @patriciondadzela2869
    @patriciondadzela2869 Рік тому +1

    Dausi is just ranting? He has a court case to answer so seeking sympathy of MCP .

  • @darrenduisel3683
    @darrenduisel3683 10 місяців тому

    Iwe Nicolas Dausi usatenge ngati Amalawi opepera which party you're belongs D P P kapena M C P ? Ndiwe gwape kwabasi ukuwasokoneza Amalawi maganizo ngati ulj wanzeru bwanji sunapite ku meeting??????

  • @KenkingsChidumula-pc3oj
    @KenkingsChidumula-pc3oj Рік тому

    Mr Brian

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Рік тому +1

    Kodi adausi mukuona ngati boma liri pa Times Radio abambo inu mulibe chopanga ndithu pitani ku konko ku MCP

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Рік тому +1

    Inu adausi ku dpp amene asakufuna achoke zipani ndi zambili mukonza kukajoina

  • @MitengoFrancis-sp9ox
    @MitengoFrancis-sp9ox Рік тому

    MR DAUSI.
    Chimenene. Mwayankhula APA ndi zosamveka
    Ngati inu mukufuna kubwelera Ku. MCP tangopitani musachuluse zokamba APA

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 Рік тому +3

    Mr dausi we don't like you, zizungu zanuzo sizingati thandize kulibe oti tongamubvotere ku dpp apart from Peter mutharika , age is just the number , we need matured people like him , inuyo a dausi mwapanga chani ku chipani , Inu ndi wa mcp tonse tikudziwa ndipo we know you mumkayenda wapansi mukupanga driving school yanu mu Blantyre mu , kukambisana satero program siyanu , musadzawaitanenso awa , palibepo chamzeru

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 Рік тому +1

    Brian ndi Dausi😅😅 mumamvana Kwambiri, mumandiwaza😂😂

  • @merviselias6230
    @merviselias6230 Рік тому

    Iwe dausi unayamba kale ndale, ngati ulindi mzeru osayambisa chipani chako bwanji,munthu osokoneza,adausi inuyo mulingati hule, kumene mungaone Kuti zikuyenda mumathamangira komweko, tikufuna APM ndiifeyo anthu akumudzi amene tiliamphawi osati inuyo Adausi

  • @rachidermak8827
    @rachidermak8827 Рік тому

    Mupite,kuchipani kuano. Nanga pamenepo mulankhula ni ndani inuwo kukula mtima basi

  • @Mbwanaayami-hp3xk
    @Mbwanaayami-hp3xk Рік тому

    Dausi libe nzeru tsogoleri ndi APM omwewo kagwere uko iwee

  • @violetmanasecheonga4495
    @violetmanasecheonga4495 Рік тому

    Amen 🙏

  • @user-di4om7sh8w
    @user-di4om7sh8w Рік тому

    Daus ndikatundu mmadzi ndipo akunena zoona ndipo APM ngt sasamala chipanichi chikutha

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Рік тому

    Mr. Dausi akunena zoona koma, APM should step aside and pave way for new blood. DPP ikuonetsa poyera kupusa kwa amalawi.

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 Рік тому

    Ine Dausi ndi Brain mumandiwaza muzipanga izi deile kkkkk😅😅

  • @SamsonGood-cw7pp
    @SamsonGood-cw7pp Рік тому

    Zonse mchabe wabwino ndi yesu yekha basi

  • @user-om9de3hr2x
    @user-om9de3hr2x 6 місяців тому

    Munthu ndi uncle ake

  • @funnykatchenga-uk5mf
    @funnykatchenga-uk5mf Рік тому

    Dausi opole moto, siwe wa DPP. ukanakhala nsomba ukanakhala nkholokolo, maoazi ako.

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Рік тому +1

    Chisiyeni Chipani cha DPP a Dausi chifukwa mukugwira ntchito ndi MCP

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 Рік тому

    Brain ndi Dausi aphana 😂😂

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363

    Dausi ngosokoneza nkale akatelo akufuna adyekonso kwinaku uyu kumusatila uchimwa naye limodzi uyu sanalape ndiye zikumuzunguza mutu

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Рік тому +1

    Adausi ingochokani ku dpp mulibe phindu ku chipaniko tazingopitani ku mcp komweko

  • @user-gn1xn3js4l
    @user-gn1xn3js4l Рік тому

    Adawusi ndi galu alibe fundo kodi sakupitilanji ku m c p ko bwanji kodi amasetenga ngati aliyeka

  • @emmanuelkenneth4768
    @emmanuelkenneth4768 Рік тому +1

    Akulankhulatu zomveka koma nkuluyu ngati chipani ichi sichisamala chitha ngati ma katani, Munthu wanzeru mamayenera kumva maganizo a ena ndikupereka maganizo ako then kupanga chiganizo chabwino chokomera anthu onse.

    • @robertrichman9376
      @robertrichman9376 Рік тому +1

      Don't trust Dausi, don't forget ali ndi milandu yoopsa yomwe akuyankha, nde don't expect kupanga zinthu zokomera DPP, akufuna MCP izinva zoipa za DPP kuti akhululukidwe milandu yake

    • @alfredbanda1693
      @alfredbanda1693 Рік тому

      ​@@robertrichman9376inuso nde abodzatu dausi akuyakha milandu iti muli mumalawi inu koma

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Рік тому +1

    A Dausi ndinu a MCP tonse timadziwa kuyambira kalekale ndiye za DPP zisiyeni eni wake agwilizana

  • @WinnerChisambi
    @WinnerChisambi 6 місяців тому

    Koma Brian ma video Anu ambiri sakutha bwino why amangoyima basi kumapitirila ndimau okha bas why

  • @user-pq5bo5ch3m
    @user-pq5bo5ch3m Рік тому

    😅😅😅😅😅 woza nazo,bring it on

  • @kamwendoderek6567
    @kamwendoderek6567 Рік тому

    adausi ngati mufuna upuresident ingonenani

  • @edwardmusamba8173
    @edwardmusamba8173 Рік тому

    Brian I love and enjoy your interview. Keep it going u are are too genius.

  • @user-kj8kj1kr9t
    @user-kj8kj1kr9t Рік тому

    awa kumvetsetsa kwangowavuta. ineyo sindikuona vuto iliyonse. komanso is this the right proceedures yonenera zinthu? bwanji iwowa a dausi sanapite kwa a president awo mkukakamba nawo? kukula mtima akuruwa. kkkk

  • @merviselias6230
    @merviselias6230 Рік тому

    190%B B Dausi ayambise chake munthu osokoneza ndi amsonda ,Malata,Mavote siinu adausi,Mavote ndiife anthu akumudzi,NGCmuli angati adausi,ukayambise chipani chako dausi nonsense

  • @Phaless-ur6en
    @Phaless-ur6en Рік тому

    Dpp ithelalimodzi ndi amuthalika

  • @thondoyaenterprise3795
    @thondoyaenterprise3795 Рік тому

    Heated interview

  • @peterchilewa380
    @peterchilewa380 Рік тому

    Asatinyase dausi wa mcp

  • @collingsjambo658
    @collingsjambo658 Рік тому

    Kkkkk adausi inuyo anthu akumakambilana mulikuti kkkkkkk 😂😂😂😂😂😂

  • @samuelsergio5343
    @samuelsergio5343 Рік тому +1

    A Dausi ali mugulu lofuna kuti amalawi adzivutika.president ndi muthalika yemweyo

  • @user-bc1zi6hz7g
    @user-bc1zi6hz7g Рік тому

    Daus ndikachan

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Рік тому

    Mwayamb kunyozan nokh nokha odya mbewanu kumasulir kt odya mbewa ndi Anthu opanda nzer? Mwatimasulat yapa

  • @user-kq8rb9jj7s
    @user-kq8rb9jj7s Рік тому

    😂😂😂😂 Braan ndi Dausi umandiwaza

  • @biza4111
    @biza4111 Рік тому

    kkkkkk eish ngati ndiibwereze

  • @user-jw3rs2fr9v
    @user-jw3rs2fr9v Рік тому

    Zachisoni nzeru za MP

  • @MilikaKilion-tn1bn
    @MilikaKilion-tn1bn Рік тому

    Brian ndi a Daus chonde thiti zanga zikuwawa mkuseka😂😂😂

  • @FelixKachera-je4yk
    @FelixKachera-je4yk Рік тому

    Mwati kubwera makadi!!! Eeeeee oooo mwati mchani Kodi??? Ohooo ahhhh mufuna makadi?? Chabwino mwakhalaso ngati kamuzu wakale uja?? Chabwino zioneka zokha...

  • @user-sx7fg1NEDG
    @user-sx7fg1NEDG Рік тому

    Waku ngona uyu kkkk

  • @rachidermak8827
    @rachidermak8827 Рік тому

    Munagulisa buluku ia polisi pá ntengo WA 2000000

  • @chisomockuwa6869
    @chisomockuwa6869 Рік тому +1

    Adausi pangani canu nd anankhumwa

  • @Misasi19
    @Misasi19 Рік тому

    Brian Banda walakwisa kumuitana kucheza ndi munthu oti kunalibe kunsinkhano,mukachezanso ndi wina tizamvanso zina

  • @tracymantchichi8347
    @tracymantchichi8347 Рік тому

    Muzaphana Inu😂😂

  • @KenkingsChidumula-pc3oj
    @KenkingsChidumula-pc3oj Рік тому

    Mr Brian tsopano

  • @chrispeter5256
    @chrispeter5256 Рік тому

    and i quote "iweyo usanabadwe 1992 - 1993"......kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

  • @crementnkhoma7735
    @crementnkhoma7735 Рік тому +1

    Daus choka mchipan usatisokoneze

  • @DanielJuly-dj2ji
    @DanielJuly-dj2ji Рік тому

    Brian ndi Dausi 🤣🤣🤣🙌

  • @KenkingsChidumula-pc3oj
    @KenkingsChidumula-pc3oj Рік тому

    Dausi....

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Рік тому

    Tikudziwa komano palibe angapeze mavoti kupotsa adad kkkk akufuna ndianthu kumudzi

  • @user-kq1pb8yl7f
    @user-kq1pb8yl7f Рік тому

    Owononga uyu

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 Рік тому

    Dpp ikutha ngati akukamila apeter aimeso ndipo izi ndi zoonadi

  • @MikeMadeya-xm4uy
    @MikeMadeya-xm4uy Рік тому

    Kodi Mr dausi inuyo ndi achipan chanji mukundidabwisa in siwa dpp ayi

  • @MATHEWSNKHOMA-jo2dn
    @MATHEWSNKHOMA-jo2dn Рік тому

    Inu a DPP samalani,chipani chikupita ichi

  • @jameboy3924
    @jameboy3924 Рік тому

    Uyu ndi wa mcp

  • @nelsonnkhambule6292
    @nelsonnkhambule6292 Рік тому

    Hon dausi ndi a yes bwana awo amangosusa chilichose

  • @louisgolden
    @louisgolden Рік тому

    Dausi akuopa mafuso😂😂😂

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Рік тому

    😂😂😂😂😂😂 ...dausi ndi ndi waboza eeich