Andale inu mitu yanu koma imagwira kapena nonse ndinu amisala komanso a Satana? Zoona mmene tikuvutikira a Malawi moyo ukulimba komanso misonkho ikutifinya. Zoona kukula mitu yanuyo mkumaseweletsa misonkho choncho? Nkhani iyi si ya otsutsa kapena olamula koma ndi mu malawi aliyense. Feel shame. Tidzabwera kumeneko kudzakuumbudzani nonse kumeneko. Mwachulutsa chibwana 🤮
We need MP like this one,she has spoken on behalf of many MALAWIANS who voted for CHAKWERA today are crying bcoz of his leadership style that has pushed us into in an inconsolable state due to the high price of local products, forex crisis,alot of aliases which are not addressed,pationias
Chimwendo Banda akuyitenga Parliament ngati ndi nyumba yake ndi MCP ndichifukwa chake amadelela wina aliyense. Kikanakhala kuno ku RSA akanawombeledwa ndi futi.
English ilibe kanthu bola tamva mfundo zake mai uyu , komanso sindimaona chifukwa chomwe amalankhula English coz amaimilira ifeyo a Malawi kaya okhala ntauni komanso kumuzi
Ma mp wose palibe akuchitako ku parliament wonse akungowononga misonkho mutawafinsa kuti ma 200 million mumalandira every year mwapanga po chani ku constituency kwani akuwonetsani chimbuzi cha million, bwanji zinazo kutsegulilako minda, kuti ikakukwapulani mudzikatengako nkumapatsa akudya kalongonda wo? Malawi heyiii dzukani

I love you my sister,,so brave and Intelligent,am behind. Youu ,,ashoshe a Mcp. Mbava izi
Here is another woman representing poor Malawians out there,we need more of them.
We need MP like this one,she has spoken on behalf of many MALAWIANS who voted for CHAKWERA today are crying bcoz of his leadership style that has pushed us into in an inconsolable state due to the high price of local products, forex crisis,alot of aliases which are not addressed,pationias
Madamu l love your speech ❤
Very shameful MCP and Chakwela government
Mai jolobala mumatiyimilira kudela lathu, ndipo chimwendo ngati siukumudziwa Mai ameneyo umufuse DC wamachinga akuwuza bwino bwino ataba ndalama yogulira chisulo
Madam 2nd deputy speaker utsogoleri wa Nyumbayi unawakulira today
Madam don't withdraw the statement Chimwendo hinself is involved in fuel deal.
Mzimayi wanzeru,,adabwitse akuba awo
Mama we silute you ❤❤
Chimwendo Banda akuyitenga Parliament ngati ndi nyumba yake ndi MCP ndichifukwa chake amadelela wina aliyense. Kikanakhala kuno ku RSA akanawombeledwa ndi futi.
Pajatu DPP imafuna manual. Auzeni iziimika zala mmwamba they are good at it.
Anakubala enieni... salute 🫡
Mwanenepa ndi milomo yomwe
Its not denting,,chilungamo
English ilibe kanthu bola tamva mfundo zake mai uyu , komanso sindimaona chifukwa chomwe amalankhula English coz amaimilira ifeyo a Malawi kaya okhala ntauni komanso kumuzi
Parliamentary Members pls polish up ur English
Woow 50billion dollars 💰💰 fuel 🤔🤔
Mama openga mugodya ndalama palibe chimene mpangako kumeneko ma mp
Am understand for mother arankhura bwino kut mitini ipitirire mawa akaiganinzire bwino amkuru akuruwa kuti nziyende bwino
Mama umatiyimilila ife timangokupemphelelan kt mulungu zikhala nanu inuyo kwanthu Kuja ngt ku kusitha nkhani ndinu bc
Mcp icoke kumene ikuba kwambiri ndipo cikangawa panyoo pako ndi mcp yako yonse 4tsake
Aphungu ambiri ndiosazindikira kulephera kugwiritsa ntchito computer ndi kukumva ambiri ndi aDPP. POFUNIKA KU PARLIAMENT MINIMUM QUALIFICATIONS IDZIKHALA DEGREE IZITU ZOCHITITSA MANYAZI
Waboza iwe wukuvakwandani?.
Ma mp wose palibe akuchitako ku parliament wonse akungowononga misonkho mutawafinsa kuti ma 200 million mumalandira every year mwapanga po chani ku constituency kwani akuwonetsani chimbuzi cha million, bwanji zinazo kutsegulilako minda, kuti ikakukwapulani mudzikatengako nkumapatsa akudya kalongonda wo? Malawi heyiii dzukani
misonkho ya amphawi ija kuno...................
Chimwendo Banda ufiira Maso sudati uziona wayamba zosayamba
More fire mum
Try not talk with hands
People are suffering with hunger but your busy talking nonsense.
More fire 🔥 🔥 🔥 🔥
osathawa ngongole zomwe tinaziputa tibweze basi iya
Poor English in parliament 😅😅😅😅 alimo ambiri
Motor
Kamtonga ko kangotha kulankhula apako ndiwausilu,sitose atonga ndife ausilu koma yekhayo mp wa MCP ndiwausilu