That was a big mistake that supposed not be happening in the history of Malawi to work and joining MCP,are these opposition parties doesn't know the history of MCP how they operate MCP is like leopard who can never change its spot eve he can go a different mountain.
APAPA..AKUNA BANJA A ANTHU OMWE ANAPHEDWAWA..ATSOGOLELE MTUNDU WA A MW KUPANGA MATCH,FORCING THE GVT TO COME CLEAR ON THE REPORT THE MIN OF INFORMATION,THE ARMY GENERAL AND THE PRESIDENT HIMSELF...WHY HAS NOONE BEING FIRED OR ,HEARD RESPONSIBLE FOR THE DEATH OF MW VICE AND THE 8. . OTHERS.. ..
Mzimuwanga ndiokondwa kunva mawu a transparency udzakhala wokondwa kwambiri Choonadi chikazaonekera❤ thank you Comrade
Ukumba zenje ekha azagwelamu ambuye akudalisen ndi moyo wa utali adan anu azachite manyazi❤❤❤long live adad🎉🎉
Vuto la alomwe ndilimenelo simuzakamulanso olo mukakhala zipani 20
Powerful message my Richard Mphepo 💪🔥
Bushiri ndi chisilu,asanamalize kupha anthu omwe akunenawa ayamba iyeyo kufa,muzina la yesu khristu.Amen.
Yesu sangaphe anthu
Wayankhula zambili and i like zomwe wanenazo komaso ndi chilungamo chokha umu kung'alura ngat @Bon Kalindo
Powerful massage
Mawu amphamvu, Ambuye akudalitseni chifukwa chachilungamo. You must be the high court judge, comrade
Well spoken Mr malawi first
Well spoken ❤
Ili si boma ayi, ndipo anthu a ku Chikwawa, keep it up,
Amwene pitilizani kuwatsegula maso amalawi chifukwa ambiri maso tilibe, wishing you all the best AWA ATIMALIDZAMOTU MDZIKOMU
Usamasokoneze anthu ndi bodza iwe , cholinga Chako ndi chani panga zothandiza tsogolp lako bodza supindula nalo
Mwainu muli nzeru eishiiiiiiii ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndakukonda kwambiri walankhula bwino kwambiri thats good no more mcp
Police inawola kalekale coz iwo alibe choice pakuchita zithu,,, amayendera chomwe alamulidwa ndi andale not zomwe anaphunzira
Very good walankhula bwino mwana
Bravo brother Mphepo
That was a big mistake that supposed not be happening in the history of Malawi to work and joining MCP,are these opposition parties doesn't know the history of MCP how they operate
MCP is like leopard who can never change its spot eve he can go a different mountain.
This is true story from you bro keep it up.
Bola anakamuchosa diso 😂😂😂😂 inamuphonya bwanji mwala uja 😂😂😂😂
Exactly achokedi
Usatipusitse aise dziko sililimonga mwakale ukuza mwana ?aliyese pano akufuna ndalama ukajamajama ndikulubwalubwa kwakoko utipeza kumastand kuno ife tikuwonera game yakoyo tili pheeeee😂😂😂😂😂
Uyu uyu ndi number one atitsekula mmaso
President amamulephelesa ndi anthu ngati amenewo ozinva zisiru za anthu mbuli agalu a chabe achabe. Machende anu nonse maka director of youths wa mcp.
Panonso mcp ichoka pa mpando Ulemu wanu Achihana koma munakakamidza Chilima kuti alowe Ku mgwilidzano Pano kulibe
Zelu mulibe mwakanika fundo zonena mwabisala Ku ndege kkkk
Aziyamba dala ndiye asamphe anthu aBushiri ndipo iwo simulungu ayi
Walankhula ngati Peter Fote
Zoona zake mbwapini nisijowela kabi
Zoonadi brothe mwaimapachilungamo ndipo ifeyo timakunyadilani mumatiimilira
Mwamasura Inu ndithu eeeeeee Chakwera Ambuye amuone
Panalakwika kwa mbiri tikhale okondana osati izi sitingapindure nazo.
Kulila kwa cadet kumeneko mukanakanda
Ndikuwona ngati mamvuto samatha ndikulira
Koma or dpp inkazura mbendera za Mcp... Nde zisaipe lero
Akanamuchosa diso chakwera samasuzula anthu Ake akalakwisa
Iwe ndiwe wa bodza owe usamananize Malawi
Ana chitabwino kuwagenda nanga phindu lawo ndichani
APAPA..AKUNA BANJA A ANTHU OMWE ANAPHEDWAWA..ATSOGOLELE MTUNDU WA A MW KUPANGA MATCH,FORCING THE GVT TO COME CLEAR ON THE REPORT THE MIN OF INFORMATION,THE ARMY GENERAL AND THE PRESIDENT HIMSELF...WHY HAS NOONE BEING FIRED OR ,HEARD RESPONSIBLE FOR THE DEATH OF MW VICE AND THE 8. . OTHERS.. ..
Or ataphatikizana zipani zochuluka koma mcp sikuchokabe, Iweso ukamba izi zaonekeratu kuti ndiwe wa Dpp .koma or utamakamba zoipa bwanji za mcp koma anthu okavota akudziwa chulungamo. Ndiye report lidabweralo lakhudzako ndani? Iweyo ukuwonetseratu kuti ndiwe wa Dpp ndipo pangani mgwirizano wanuwo koma mcp simuitha.
Mcp singawine boss dzko analionpnga achakwela ine ndr SA chiyambleni sinayambe kwacha yagwela mene inagwela mu
That is true my big brother ulemu wanu umatimvetsa kukomatu big man 👨 💪
God bless you guys 👦 form Malawi 🇲🇼 fast 🙏 and mr president bon kalindo god give you long life mr DC be strong 💪 man 👨 💙 💪
Zikomo kwambiri mwatitsekula
Ndiye anthu 40 awamangawo amasulidwe
Pliz azipani zina lowelelanipo pa za anthu omwe amangidwa opanda chifukwa
Zilikotu 🔥🔥🔥
Ai zikomo
Ndizowona naneso ndinali komweko
zona zake chilungamo ichi
Athu oipa mcp chpani cha magazi
Inu ndiye mwanena zoona mmmmh ulemu wanu
Mulungu adzakulagani simutha kunena zoona ine ndinali konko izi ndizabodza
🤷♀️🤷♀️🤷♀️🤷♀️
Anabisa ndindani ndiboza lanu lonunkhalo
Koma vuto SI president koma anyamataWo afunika pachimeti
OSAMULOLA CHIKANGAWA KUPUSITSA ANTHU ATHAMANGE
Kodi iwe unalwelapo ndege ya asilikali
Wafotokoza bwinotu Aise
Mukunena zoona mfotokozi
Brov big
sindikuonapo apa zomwe mukunyankhulazo
Zoona izo
Chakwera amawasekelera anthu akewo
Ukuwuza. Mbuli
Zoona
achita bwino kuwagenda mcp ikungodziyika yokha pamwamba pamene amalawi mulibemo mu mcpmo
Wachamba iwe. Mukunamizana kuti train inabweretsa molasses pamene inabweretsa mafuta. Mudzavomereza liti anyaphaphi inu.
wabodza uyu
Galu iwe wa dpp
Anawaputa Dala anthu pozula mbendera za DPP masatana,amupweteketsa president ,,apolice nawo angoti butululu pakamwa ngati mbuzi,
Amalawi oganizabwino anamwalila , zasala ndi zinyalala
Ulemu wanu anthu a kuchikwawa mumakwana mwaonetsa kulimba mtima
Ameen
Ndie titani
Boma sitisintha koma tisintha chipani
ANAPHA CHILIMA NAYESO APHEDWE BANSI
Muli ndiumboni
Nde muziziwilatu kuti muoloseni nzanu azakutafuneni kukanakhala bwino kuti muphunzililetu kuzipangila zanu chifukwa kusogolo muzayamba kuinyoza DPP pomwe mukulephela dala kupanga zanu
Koma pazonse wayankhulazi chimene wayankhulapo chanzelu ndinkhani imozi ndiolose ndikakutafune ndi achina chihana ndianzao a UTM nditizipani tina tosaziwikati sakuziziwa kuti kuti akazaiwolosa DPP nayonso izawatembenukila sakuziwa nchifukwa chake pena ndimanena ine kuti Chilima anali ochenjela mopusa ndipo ine sindimamudandaula ndale ndichinyamata sizigwilizana ndale nzaanthu akuluakulu taganizani Bingu wamutharika anali ndi kachipani kake m'mbuyomu koma pena kamatha kupeza 5 vote the whole malawi koma abingu kuti aziwike kuntundu wa malawi ndi Bakili muluzi koma sono taonani zomwe zidachita bingu wamuthalika adawatembenukila abakili kuyamba kuwamanga kumawasegulila milandu palibeso mphavu yomwe abakili analinayo nde nonse amene munapana alliance ndi MCP nchimozimozi ndamenenso a DPP
Zopanda zeru!!!
Za mphavu
Akanangomupha abale amuoohonya pati galu satanic ameneu wakupha kuba ndi kuononga ameneu chitsilu kwambili
Amzanu nde safuna moyo
@@giftsululu4274 chilima anamupha uja ndi athu ena aja samafuna moyo pepeza mudikile afa ngati galu aneyo muziti muzimuombela m, manja chocho
Achinyamata musamachite umbuli pa ndale chonde chonde,olemera osati inuyo.
Galu
Chilungamo
Bodza. Ilo
AAA koma inuso mukuti ngozi anthu achita kupanga zimenezo achita bwino
😅
Useless mfundo
Fokofu you don't have source of information go back to school please
alone inu
Boma. Sitikusintha
😂
Zoona