Amene amafunika mu inquiry. Pastor chumba .enock chihana .bon kalindo. Namiwa bakili TV tanyiwa akubanja mubusa wa ccap uja anamangidwa .mutumiki yasini gama. Mafumu ayi ose ndi adyera pamaunikaso jb abiti maness mery navisha suleman anthu amewa ndi amene amafunika mu commission of inquiry
Micah stood alone against 400 prophets and so was Elijah. See that you are Elijah of our time. All eyes are on you . Keep yourself holy and be blessed ✝️🕊️
Poika Namiwa mu commission of inquiry kunali kulelesa mademo Amawona ngati achenjera Koma apapa nde azipalasila makala amoto 😂😂😂😂 Pitani mukaike chilungamo pambalambanda Mr Namiwa our only hope in the entire inquiry Osaopa! Osatopa! Osafooka!,💪💪💪
Am the one to believe and trust Mr Anamiwa to handle this issue by fearing God, make it transparency and accoutable. Ndipo make sure kuti the inquiry must be on the heath.
Musavutike kupita kutali even akaliati atengedwa koma umboni is very safe respect to Mr boooooon kalindooo the DC anamiwa even outside the country ma audio mmmmm pray for Malawi guys
You are saying the truth and please am Zambian but I have been following this issue since June 10 ,chilima was killed so please stand for the Malawian s so that the truth must come to an end otherwise it was a plan move for chakwera why he changed his mind to stand 2025
Commission of Enquiry imeneyi ( maka maka its composition) sikundipatsa chikhulupililo olo pang'ono. Kwangodzadza ma delegate aKhongelesi basi. Don't expect any justice from these party loyalists. Namiwa, extricate yourself from this pantomime.
Comrade anamiwa chonde chonde maso athu kudziko lathuli lilipa innu chonde ima pa chilungamo musadye nawo ndalama izi za magazi cha chakwera inuyu please we love you ❤❤❤😅
All we need family members to be involved radios and tv have to inform us live accept MBC radio and TV we don't trust them go well mr nawiwa All the best
Nanga akumabanja bwanji mulibemo inu a namiwa banji simunawauze aikemo? Why is it almost only namiwa included? Why not opposition and media? Madya mabanz inu nyari sanafike ma band akubwera trust me
1) Funso langa ndilakuti kodi mukudziwa anthu amene mudzikawafunsa mafuso - mwina ngati aku army, a president, anthu a kumudzi kufupi ndikumene kunagwa ndege, anthu a ku Mzuzu ndi ku Lilongwe airports ndi ena onse amatumiza ma nkhani zakusowa kwa ndege? 2) Kodi ndi zowona kuti anthu ena amafuna kekwera nawo ndege koma ena anaudzidwa kuti mundege munalibe malo. Kodi nkhani yimeneyi ndizoona?
Alright, Koma musazatinamize Kuti anthu Aja ,anangochitidwa Ngozi chabe chifukwa,ndegeyo inagwa,ndikuwomba mtengo osagwaso mtengowo,zimenezo ayi ,zichepe. Koma mutiwuze Kuti mwawapeza , chifukwa Chilima anaphedwa ndi zigawenga,mopelekedwa ,ndi President wa ziko la Malawi Chakwela. Mukazaloza Kuti President ndi amene ,anatumiza anthu aja,ndikugwilizananso ndi aUsi
Mr namiwa mulungu kusogoleleni koma osakaiwala mafutso awa 1 ndindani anati ndege inatdzaza 2 ndani anatenga black box 3 ndindani anamuudza president kuti ndege inafika ku mzuzu 4 ndindani analoledza ndege kuuluka yopanda zoyenelela chifukwa chani chimwendo anakane kukwela ndege ndindani
Mukadya banzi tikudziwani kusitha mayakhulidwe koma muchite mene mukyankhulira apa ai ambuye akutsongoleleri koma muli azibusa Ena muzikawawonesesa ndi azibusa okonda ndalama tikudziwa komanso mafumuyo ndiokonda ndalama muzikawawonesa muzolakhula zawo zinazo ndi njoka
Pandale you can say that you can not accept enybig position but if it happens then a namiwa mulungu azapanga bugwe lanu kugwa pansi but for me people from my home khonjeni TA kapichi sanama we trust you please
Amene amafunika mu inquiry. Pastor chumba .enock chihana .bon kalindo. Namiwa bakili TV tanyiwa akubanja mubusa wa ccap uja anamangidwa .mutumiki yasini gama. Mafumu ayi ose ndi adyera pamaunikaso jb abiti maness mery navisha suleman anthu amewa ndi amene amafunika mu commission of inquiry
Ndipo live
Iwe khala chete
Samasankha mbuli,,, achina ntanyiwa nde ndani ??
@@FrankMsiska-i9j mbuli ndi izi zimamena kuti ndege inafika kuno ku mzuzu ndipo anayibweza mdipo inagwera kutali ndi muzi komaso inazaza kaya inazaza ndindani zimagula fertilizer kubucha zinapereka ndalama ku foundation bridge zimezi ndizo mbuli zazikulu kuno kumalawi
Wapatower
Bravo Sylvester Namiwa ,mawu amphanvu,God bless you
Micah stood alone against 400 prophets and so was Elijah. See that you are Elijah of our time. All eyes are on you . Keep yourself holy and be blessed ✝️🕊️
Zoti muli pakati pa mikango simukudziwa anamiwa nfusen chilima ku gwilizano anapanga ndi mcp uja
Zoona timamva pa Bakili Muluzi TV ndlam idyani kwa Mulungu kulibe chibazi guyz
I trust you namiwa God be with you in this journey
Mr namiwa mukayelekeza kukalandir ndalama kt mutseke pakamwa mizimu ya athu idxakwiya kms 🇲🇼 sadzakhulupirira no chinyengo ulendo uno tidxiwe zoona mulungu akuonat
Anthu anakukayikirani km powerful speech Mr namiwa ❤❤
100%×100. Wow! Mr. Namiwa takunyadilani kwambiri. Eish! Thank you so much, keep it up.
We are giving you benefit of the doubt, Namiwa. You are outnumbered. The rest of the team has MCP DNA.
Amen mulungu akutsogolelen paulendo wanu panokha simukwanitsa chilungamo chimamasula
Mr Namiwa please kagwireni ntchito yachilungamo, amalawi amakhulupilira bungwe la Cdedi limeneri. So Anamiwa mukakhumudwitsa amalawi Cdedi idzathera pompo chifukwa amalawi adzasiya kukukhulupilirani
Even if you will be in there Mr. Namiwa you cannot influence the Team to stop manipulating because you will not be a Leader
Anthu oipa😢
For this special speech Mr Namiwa God be with you and help you in all battle ❣️
Mr Namiwa u the last chance of Malawians plz try ur best ambir ife zutiwawabe😢
Poika Namiwa mu commission of inquiry kunali kulelesa mademo
Amawona ngati achenjera Koma apapa nde azipalasila makala amoto 😂😂😂😂
Pitani mukaike chilungamo pambalambanda Mr Namiwa our only hope in the entire inquiry
Osaopa! Osatopa! Osafooka!,💪💪💪
Ndipozoona zake
May the good Lord continue blessing you aseh😢😢we lost our comrades indeed en still more our hearts remained blocken😢😢
Bravo Namiwa, be strong, my home boy, fear God and He will bless you, I like ur saying " I wii expose who ever tries to bribe me,"
Am the one to believe and trust Mr Anamiwa to handle this issue by fearing God, make it transparency and accoutable. Ndipo make sure kuti the inquiry must be on the heath.
Ngati mukufuna kuti anthu akukhulupireni, tengani andale alowepo, achibale oferedwa alowemo
Inu izi sizandale ayi awa ndimalilo
@jamesch nanunso ndiakape mmesa ndi maliro amunthu wandale?
❤❤❤
Andale ake ATI , azikanama?
I'm worried for you Mr Namiwa , we can't lose you again? What if they have a plan to kill you, please almighty God be with Mr Namiwa and protect him
On that list, i trusted you mr namiwa please do this for us,as a Malawian 💪💪🙏🙏
Zikharedi live......tizizamva.....ndinthu. Takuldalirani..mr Namiwa...,. osaopa
Its my pray anamiwa mulungu akuchotsereni mantha in Jesus name
Mr Namiwa can you please 🙏 just exclude yourself from this crew
Ayitu apite abweletse report ife tudikila
Coach is in the field of play endeed, let's support the Namiwa the great go bring the truth of Our late vice president SKC mlungu akusogoleleni
Bora nawe namiwa ukapange zachilungamo kumeneko
Lero bwez ali Timoteyo Mitambo😅😅
Anamiwa ife takukhulupilani koma mukhale wachibale was anthu ofeledwawo akhalemo
Mr Namiwa uli olimba ntima wandikumbutsa Julius Malema ❤❤ big up
Exactly 🎉🎉 ndaikonda comment yako comrade❤
I don’t trust this Namiwa guy, but he needs to be very careful with this sensitive issue
Namiwa...the only Hope of Malawians now....❤
Chifukwa ndi mlomwe?
Tikudalira inu a namiwa pliz, we love you so much
Indeed time is the best judge
Point Mr Namiwa❤
Mr namiwa i don't trust this issue i think best way u have to go their with mr bone kalindo the DC mwana wowopya kwambili
U r right it can be a plot take care Mr namiwa u r going to work with crocodiles
Musavutike kupita kutali even akaliati atengedwa koma umboni is very safe respect to Mr boooooon kalindooo the DC anamiwa even outside the country ma audio mmmmm pray for Malawi guys
Inuyotu Mr Namiwa timakukondan komano ifeyo a Malawi tikukuwopelan inuyo MCP ndiyakupha inuyo nonkanonka kumeneko mukuwona kut mulisefu(Namiwa)? Ndi m'mene inuyo umaiziwila MCP ndinu otetezeka?
Ineso ndili ndi nkhawa kwambiri munthu akaphedwa uku ndi mcp
Tiwayikize mapephelo Anamiwa😱😱😱😱
Zoonadi amalawi ambili sitimakhulupirila munthu , komano chonde, Anamiwa tiwakhulupirile sikuti munthuyu sanalandile ndalama ai , tiyeni timukhulupirile.... Be blessed Mr Namiwa....❤
😊God bless u mr namiwa, ndipo takukhupirani,
God be with you ❤❤❤
I like the speech of u brother Namiwa keep the fire burning
We also expected people like Kalindo, Kamlepo Kaluwa or his son Penjani and Enock Chihana
Is that commission of enquiry an independent or chakwera commission of enquiry?
In Namiwa we trust
You are saying the truth and please am Zambian but I have been following this issue since June 10 ,chilima was killed so please stand for the Malawian s so that the truth must come to an end otherwise it was a plan move for chakwera why he changed his mind to stand 2025
Mind the challenges your country is facing bro
Anyway Mr. Namiwa wishing you all the best and may God guide you.
God bless you always
Commission of Enquiry imeneyi ( maka maka its composition) sikundipatsa chikhulupililo olo pang'ono. Kwangodzadza ma delegate aKhongelesi basi. Don't expect any justice from these party loyalists. Namiwa, extricate yourself from this pantomime.
I like you Mr Namiwa what you said l'm under whith you
Comrade anamiwa chonde chonde maso athu kudziko lathuli lilipa innu chonde ima pa chilungamo musadye nawo ndalama izi za magazi cha chakwera inuyu please we love you ❤❤❤😅
Thanks Mr. Namiwa but my aim went want UTM and the family we lost the people to be together for equirely
God ahead u my brother
All we need family members to be involved radios and tv have to inform us live accept MBC radio and TV we don't trust them go well mr nawiwa All the best
Raw deal indeed !
Nanga akumabanja bwanji mulibemo inu a namiwa banji simunawauze aikemo? Why is it almost only namiwa included? Why not opposition and media? Madya mabanz inu nyari sanafike ma band akubwera trust me
Vuto ndinu kusadzitsata zinthu
Power full speech Namiwa
Powerful speech
Pakufunika kuonjezera like Bon Kalindo DC, relationship for die pple thats good to additional Namiwa
Komanso zikayendani mosamala, Tisakuluzeni Mr Namiwa.
God bless you Mr namiwa
Truth is truth whether one person or 2 but i will see 18 people fearing one true man.
Mwayankhura bwino we are waiting for the results
Akupatsani Bazi inu Mark my words born kalindo alikut umu
This commission is fake
Namiwa ,God first plis
1) Funso langa ndilakuti kodi mukudziwa anthu amene mudzikawafunsa mafuso - mwina ngati aku army, a president, anthu a kumudzi kufupi ndikumene kunagwa ndege, anthu a ku Mzuzu ndi ku Lilongwe airports ndi ena onse amatumiza ma nkhani zakusowa kwa ndege?
2) Kodi ndi zowona kuti anthu ena amafuna kekwera nawo ndege koma ena anaudzidwa kuti mundege munalibe malo. Kodi nkhani yimeneyi ndizoona?
Namiwa iwe, ukhale ochenjera ngati njoka ndioona mtima ngati nkhunda, mau ako asathere m'mazira, adzalira ndithu
Alright, Koma musazatinamize Kuti anthu Aja ,anangochitidwa Ngozi chabe chifukwa,ndegeyo inagwa,ndikuwomba mtengo osagwaso mtengowo,zimenezo ayi ,zichepe.
Koma mutiwuze Kuti mwawapeza , chifukwa Chilima anaphedwa ndi zigawenga,mopelekedwa ,ndi President wa ziko la Malawi Chakwela.
Mukazaloza Kuti President ndi amene ,anatumiza anthu aja,ndikugwilizananso ndi aUsi
Mr namiwa mulungu kusogoleleni koma osakaiwala mafutso awa
1 ndindani anati ndege inatdzaza
2 ndani anatenga black box
3 ndindani anamuudza president kuti ndege inafika ku mzuzu
4 ndindani analoledza ndege kuuluka yopanda zoyenelela
chifukwa chani chimwendo anakane kukwela ndege ndindani
Mr namiwa we can't trust you anymore
Kod simunganditenge kukhala nawo ku commission Inquiry pliz
Ndiye mukamati wang'alura Chakwera ndimawu ATI ong'alura apapa😂😂 km anthu umbuli ukupwetekani ndithu
Ine I which mukamayamba commitional of inquiries tizimvera nawo azakhale live koma nkulu winayo amuikayo mmm ka Ty??
Am saying namiwaa titumikileni musamvere anthu opanda mzeruwo. Am saliute you!
Which Malawi do you save?
Namiwa iwe nchitsiru kotheratu ngati akusankha ukadakana iwe ndiwotembeleredwa kotheratu paja unazanama Kuti akuba pamapeto Poti anakutapira ndalama ine ndikungoti namiwa iwe ndigaru Kodi akubanja alipo Kodi mafumu alipo ambungwe omwe so aboma alipo namiwa mbuzi
The truth must prevail 😢😢😢
Sitikufuna tizamve kuti mwalandilako billion
Inenso maganizo anga ndi omwewa. Zayamba kukayikitsa kwambiri.
Namiwa you have our trust please don't let Malawian regret
Namiwa ❤❤❤ndipo ukapange zakupsa kumeneko akusankha Dara kut anthufe tizanene lnuyo
Powerful namiwa
Auuzen zoon amalawi adziwe chilungamo 🙏🙏🙏🙏💪💪💪💪
Zikomo kuti mukhala nao pa ulendo umeneu tidalira inuyo mukafukufuku ameneyu tipemphe Ambuye apitilize kukutetezani kukudalisani ndi kukuchinjirizani pa ntchito imene muyiyambeyi🙏🙏
Ndakukhulupira namiwa kagwire ntchito moopa yehova
We trust you more after you bring the truth not your speech today 😢
❤❤❤❤ great
Go on mr
Mr Namiwa chonde mafuso anthu a Malawi ali manja mwanu chonde ayankhidwe pa commission of enquiry iyi
Iwe namiwa take care Koma
Dr chilima anali wa ndale koma bwanji sinayikepo azipani ?
Mukadya banzi tikudziwani kusitha mayakhulidwe koma muchite mene mukyankhulira apa ai ambuye akutsongoleleri koma muli azibusa Ena muzikawawonesesa ndi azibusa okonda ndalama tikudziwa komanso mafumuyo ndiokonda ndalama muzikawawonesa muzolakhula zawo zinazo ndi njoka
Pandale you can say that you can not accept enybig position but if it happens then a namiwa mulungu azapanga bugwe lanu kugwa pansi but for me people from my home khonjeni TA kapichi sanama we trust you please
❤❤❤❤❤❤Nimiwa fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee
Mr Namiwa inquiry yoyamba mukapenge chakwera chifukwa mission yonse anayambisa ndi iyeyo kuti chilima afe, chilungamo chonse chili ndi chakwera pasapezeke bwamtasa wina omamubisa chakwera ameneyu ,
Mr chakwera you made a big mistake for not including just one of the deceased 9 people in the commission of inquiry
All the best mr Namiwa chomwe mungadziwe kut if u made a mistake kuzadzuka Namiwa wina inuyo muku Seva ndende ya chikumbumtima
Nuff respect comrade namiwa!...aluta continua!
Anthu 18 olo a Namiwa mutachita chilungamo atha kumakupinda kumakuzemba
Any way let's wait and see
Iwe ngati warandira kare ndarama kabweze panga choti akubanja akharepo iwe upitangati ndani
Bola osatinamiza
Amalawi akukhululupilira wekha Namiwa