That's violation of Human Rights to freedom of expression and association. Every Malawian has the right to campaign everywhere in Malawi. Ndirande is a township in Malawi and NOT a country on it's own. Let the Law take it's course.
Kodi DPP ili ndi studio yakeyake yojambulisila nyimbo zake🤔? Chifukwa nde ee nyimbo zonse zomwe zimaimbidwa kutamandila chipanichi zimakhala zobhebha heavy 😂😂.
A Malawi kutengeka, kusayamika, kulephera kusiyanitsa that's why we put someone in office who doesn't deserve to be the president and now Malawians are in big problem in their own country
Thank you my Beloved Rev for protecting the A noiting God gave you ,
Moto kuti buuuu🔥🔥🔥
Zikutheka❤❤❤❤ Moto kuti buu vot yanga mwatenga
Victor musowa my mp l will give you my vote 2025
🎉🎉🎉 Koma kunachema
Zomat peter wakalamba sfundo izo Khan ndikuyendetsa bwno dziko
Zikomo kwambiri mau aphavu
More fire 🔥 DPP and achepa
Moto moto❤
Boma ilo❤❤
This is where my vote belongs to
Boma 🎉🎉🎉🎉🎉
Dpp ❤❤❤❤ mbambande
❤❤❤❤❤ APM my vote
APM my vote 💙🧢
Tayahkulani mfundo osati kuyambitsa ziwawa anthu awuzeni mfundo kut mukatenga boma simudzawonongaso anthu a chalbino?
Ndiposo
Auzeni Athu fundo Zomwe mudzapange Osanyozana
A peter a betha loya more faya ambuye aaunge moyo wa a peter apulumutse dziko😊
That's violation of Human Rights to freedom of expression and association. Every Malawian has the right to campaign everywhere in Malawi. Ndirande is a township in Malawi and NOT a country on it's own. Let the Law take it's course.
DPP more 🔥
APM my vote
Amuchacha ndembela imeneyo siya dziko palibe phindu ndizomwe mukunena tayakhulani fundo
No any party to vote rather than DPP
Apm my vote 🎉🎉🎉🎉
Mcp yagwa basi tiyiwale tineneretu pano
Ng'ona ndi mcp. Zomenyana anayambitsa ndi a mcp ku Lilongwe.
Ife MCP ayi yatiphela chilima ndi Anthu 9
Adad my vote 🎉
2025 boma professor. Auther peter muthalika moto kut buuuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Dpp yomweyo ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉
Hie
Za kwacha azikapqnga ku Lilongwe
Mukunenazowona bro a MCP ndiwodelera.
Koma ngati atawine chakwela ine ndizafuna inu
Kuyankhula mupusa ngati kumuneku mungatenge boma,makamaka mp ameneyi ndiwamwano kwambiri
Angopusisana anthu akuba awa, muja ankabera akuona ngati adzabaso?
Nanga mwano amaugeya achimwendo uja bwanji??omwe mwawona ndi uwu
Chabwino a DPP amaba koma angafanane ndi zigawenga za MCP kuba kupha kugwesa kwacha,zinthu zikungokwera tsiku ndi tsiku ndiye mukuti chani inuyo chani
Mafuta 12500 nkhuku 10 pin bread 2400 sugar 2700 soap wa tablet 700 mayches 150 eeeishh
Mkumati boma ndilomweli, ayi zikomo ndinthu.
@MathewsJanuary eee ndipo mbali zakuno akazi anga amakukonda mbusa amenei
Zobeba ipase moto Dj ukoooooo😅😅
Ndikumva kukoma ndi apm
DPP boma basi!!! 🎉🎉🎉🎉
Woyeee!
❤❤❤❤❤❤
mau, km, ameneo, dpp,idikile, zaka, 26, kuti, idzawine, km, 2025, mukunama
Zikukuwawani tu akamachokako kwanunuko, kuwina ndikomweko dpp 2025 yikulowa boma
Naonso akazanva DPP azaona mochitiranso mwake
DPP woyeeee ❤❤❤
Makape
Chikangawaaaa woyeeeee
Manyaz agwire Satana
DPP woyeeee
sitingavotele, dpp, mcp, tikuyiwona, akatiphele, alobino, ine, aui
anthu,a,dpp,mulibe, kukhazikika, nokha, musapote, dpp, komaso, utm, nokhanokha
Nkhani yabwino
mukhululukileni, apm, wakalamba, zolakhula, sizikivekatu tsopano
MCP ndi akatundu munya muona, Joyce Banda yemwe uja munamubera uja not MCP
Ndithu masiku ano anthuwa akamabwera kuzachita misonkhano Awuzeni achitiretu chitukuko chifukwa mbava zokazoka zimangofu kuba
Mwaponda ajomo
Kumaloku kunakoma heavy
Zitsiru zakumana inu nokha kwanu kunatha simuzabwereranso boma inu
Ajomo muja mukampha malubino inu? Mukuona ngati anthu nzisiru?
Dpp moto woyeee
Ndava kt aNchacha akupita kwa kabande ku utm
Dop my vote
Tiuzeni fundo
Koma guyz nde kwazaza, imagine kulibeko apm. Nankha akazabwera apm. Kuzakhala bwanji.
A c p ❤❤❤❤
Kakakakaka ayambakake yemweyo moto kt buuu
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Bola tameki
Ndi zigwe zizakutalkreni 2025 cuz ee mwatengekatu
Kodi DPP ili ndi studio yakeyake yojambulisila nyimbo zake🤔? Chifukwa nde ee nyimbo zonse zomwe zimaimbidwa kutamandila chipanichi zimakhala zobhebha heavy 😂😂.
A Malawi kutengeka, kusayamika, kulephera kusiyanitsa that's why we put someone in office who doesn't deserve to be the president and now Malawians are in big problem in their own country
💙💙💙
Dad woyeeee tilipambuyo pano
Musowa wandiwaza akuti ndirande sisunga kape
Amayi pangani za kabambe please
Musye kulota kt muzalamuliranso bomali agalu inu A DPP
Apm 2025 bomaaaaa
Ndiye tiziti akuyambitsa ziwawa ndi ndani pakat pa dpp ndi mcp
Ukamfunse chakwera
Mukafuse chikangawa bwa
Kkkkkkkk fusolimenero uziyakhe wekha
Anayamba okha Ku Lilongwe kutchinga nseuc
DPP youse nyapawo
😂😂😂 wagwa nawo iwe pusi
😂😂😂😂 @@alexjeremanuel2541
Ife tavomela chifukwa sitimalimbana ndi zitsiru 😂😂😂
Jommo ati Ng'ona ilibe mabere
Suleman lelo sanabwele bwanji?
Koditu mukana mtulutsa Pita Kaya azikwawa. Munthu adakula bwinobwino azipuma mukakamiza
Ukuona bwanji tidzangokusankha iweyotu
Kodi chakwela osango salande bwaji kuti noma ndalilephela chifukwa azafikapa akukhalangati Mutu wake sukugwila kapena mutu wake sukugwila kapena amakomoka
Kkkk amalawi atopa
Iyi ndi land slide mcp paulendo😂😂😂😂
masapota, a, dpp, fundo, alib, km, kutukwana
nanga,palifundo, yanji, apapa, yoti, mu2, atha kukopekanayo, kulankhula, musiile, mcp, akatundu
boma, ndlomweli, silikuchoka, olomwanamize, anzanuwo
Boma ndilomweli la malawi timangosintha chipani
Ati mukamva kuti kwacha muona mopangila make kkkkkkk.. DPP woyeeee
Kod anthu ena munakhala bwanji? Zona momwe znthu zikumaonongekera muno mmalawi Inu ndikumakhala kumbuyo kwazopusaz? Ot muzikamba nkhan yoipitsa dpp kumat amampha arubno zamaganizo mwanumo ndikupasiya nkhan yaifa ya chilimo yochita udziwikiratu anthu 9 osewaja adafawa sizikukhudzan ai koma ndikumabakila zoipa ngat iz? AAA kharan ndimanyaz gaizi chipswera Chanyowan ndichomwe chima Wawa.
Chikangawayo siimanamatu
Athuwa osadandaula nao amakhala apatsa timachenje kuti azizanyoza koma ose amaikila ku mbuyo MCP Ali ndi tsoka lalikulu ndithu sazapeza m, tendele
Akuti chitani mmomoooo kkkkk
Koma yaaa chala chikalodza chaloza palibe angadule chala cha yahwe kkkkkkkkk
Kungomva kuti kwacha,kuona mochitira mwache😂😂😂 ajomo eee Palibe chaulemu mukuchionapo apa😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂
a, dpp, kwanu, km, kudikulila, azimai, povina, fundo,mulibe
Pitar anakaramba inu ❤❤❤ msamphe alobinotu kuti mzapange ndiwo pano akukhara muufulu amalawi asakunamizen zaboza izo
Garu iwe ,ma vice president mwapha aja ,nanga nine ku chikamgawa.
Akalamba ndi mabvizi akowo
Akalamba ndi amako kwanuko
Umu uzuozeko panyapake
Fundo palibe
Ati nkazi ofuna mwanatu kkkk
DPP alibe fundo mau aZiwawa😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Wukunama kwambiri, wukunena fundo za Chikangawa Congress party zopha anthu mbuli iwe.
Chakwera ndiye Ali ndi fundo ....ndi zisilu zokhazokha zikuchita support chakwera chifukwa amakupasani ndalama zokuba .....iweyo ndi munthu wopusa kwambili ....chakwera wapanga chiyani mmalawi muno cholozeka
MBAMBANDE DPP KOMA MUSAMAONJEZE KUYANKHULA NANUNSO , MUKAMATIPASIRA
Oooh tamva. Timangofuna kupeleka zomwe zili mkati. Koma tichepesa
Munthu wa Dpp kulowaso Dpp
Kkkkkkkkk
Musowa umakwana😅😅😅
Nde kuyankhula kumeneku koyembekezela kutenga boma
Ayi koma zikwanje zijah ndizimene zikutenga boma. uko!
Iwe umat kkk
@@MuhaShaibu-x5x kkkkk
Iwe umafuna ayakhule bwnaji ....mcp out 2025 Apm my vote❤
Osafunsa Anyatu anu?
olomutatani, mcp,ndiakatundu,simatekeseka, zaka, 26, ikutsutsa, chipani, osapasuka,,komaso,osatukwa, mu2
Aaa zandale suzitsata ukuonekelamu iwe 😂😂
@@TysonMwenyetasiye akutopesa alipo anthu awiri okha axingo tumiza ma comment osusa paka ka 15
Kkkkkkkkk agogo
DPP can't win this time, mwatuzuza mokwana ndinu anthu oipa, chitipa can't tolerate this nonsense to support DPP, believe u me you can't win over MCP
If know win DPP who will win?