AKU DPP NDI AFITI GUYS...MPAKA CHAKWERA KUMUTELE KU PARLIAMENT ABALE?

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 54

  • @Steven-q4u
    @Steven-q4u 14 годин тому +12

    Chule iwe chizungu ndi nzeru yoyendetsera dziko umbuli okha okha akulu inu !!!

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 13 годин тому +5

    Mukutiuzakut tigulise chimanga tigule fetereza chimanga tichitenga kut anthu tikusowa chakudya

  • @KalimaImedi
    @KalimaImedi 2 години тому +1

    Mmmm Achakwela Kupha chilima chifukwa cha ndalama. Ayi zikomo popeza ndiwe wamuyaya Zonse tisiyila mmanja mwa Mulungu mwini wake 😢

  • @RuthJopilo
    @RuthJopilo 12 годин тому +2

    Mfiti ndi chakwera ndi boma lake.

  • @Marymahendra
    @Marymahendra 2 години тому

    That’s his job not just getting paid for nothing by the law he should go to permanent every day

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 12 годин тому +1

    AAAAAAS IWE UKATI A DPP NDI AFITI UFITI WA DPP UNGAPOSE UFITI WA MCP WAKUPHANAWO CHILIMA MULIBENZERU AGALU INU ANA ACHIKANGAWA ,CHAKWERA NDI MCP NDI AFITI OTHERATU ANTHU OPANDA CHIFUNDO NDI NZIKA ZAWO ANTHU ONGOFUNA KUKHUTITSA MIMBA ZAO , MUMAIKIRA KUMBUYO MCP CHONSECHO MUKUDYA CHITEDZE , FERTILIZER MULIBE , MUKUTUPIRANA NDI NJALA KOMA KUMAKAMBA ZOPUSA KUIKIRA KUMBUYO AFITI A MCP MUNYATU SIMUNATI NDIYE WAKANIKATU KUFOTOKOZA KUTI KODI NJALA INGATHE BWANJI KUSONYEZAKUTI MUDAKADYABE CHITEDZE NYEKWE YENIYENI

    • @RichardHetekere
      @RichardHetekere 6 годин тому

      Ine ndilibe chipani komano chikangawa no no no non no 😂😂😂😂😂

  • @JimmyMaster-l1x
    @JimmyMaster-l1x 12 годин тому +1

    Chakwera mutu wake sukugwila kuyankha mafutso si solution yothesera njala

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO 14 годин тому +2

    Ndale za ku malawi ndi nthabwala zeni zeni 🤣🤣 President wadziko kukayankha mafunso kunyumba ya malamulo yomwe mtsogoleri wake ndi wachiwiri wa president ku chipani. 🤣🤣🤣 A Malawi tilinso ndi vuto losadziwa malamulo athu a dziko

  • @JohnChitsulo-q6f
    @JohnChitsulo-q6f 10 годин тому +1

    😂we don't have leadership in our country

  • @zamanmwachumu554
    @zamanmwachumu554 8 годин тому

    The sound from the house is very poor sitikunva BS plz

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  8 годин тому

      @@zamanmwachumu554 Oooh sorry, next time we will try to improve

  • @FelixMakumbi-r6k
    @FelixMakumbi-r6k 4 години тому

    2bags yachimanga ichokela kuti akulu igwa kumwamba

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu 15 годин тому +7

    Ku opposition kulibe wodziwa kuyankhula bwino chingerezi ngati chakwera

    • @CvgGgbnb
      @CvgGgbnb 14 годин тому

      Kulimbedi simukunama kkkkk

    • @Shariffsa
      @Shariffsa 12 годин тому +1

      Iweyo ukudya chizungu?

    • @HenryBanda-wh6gg
      @HenryBanda-wh6gg 12 годин тому

      Komaso amenewa akhala ku opposition mpaka kale kale asathamangire kukwiya

    • @HenryBanda-wh6gg
      @HenryBanda-wh6gg 12 годин тому

      Awonda asanati

    • @gkay-striker
      @gkay-striker 11 годин тому

      ndipo ​@@Shariffsa

  • @wisdom20mkango49
    @wisdom20mkango49 13 годин тому

    dpp ikawina will be a mistake of malawians....this guy is humble forget what propagandas

  • @phillipkazembe7281
    @phillipkazembe7281 12 годин тому

    Ben NDI machine 🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @KalimaImedi
    @KalimaImedi Годину тому

    Mukamat ku oposion kulibe oziwa chingelez Anthu amadya chingelez? Anthu akufuna mafuta,chakudya feterizer osat chingelez chanucho ayi .Zija zachitika ku chikangawa zija zabwino? Kupha chilima zabwino? Oziwa chingeleziwo amapha Anthu mmbusa otan

  • @FrankChimphepo
    @FrankChimphepo 4 години тому

    Boma ndilomweli palibe kusitha opposition yomweyi.....namalomba uzingovutika ......boma ndilomweli anthu sitikusitha

    • @Steven-q4u
      @Steven-q4u 4 години тому

      @@FrankChimphepo Koma utsilu uwu si utha boma Lake liti kkkkkk Koma Zina izi ndi mphwepa !!!!

  • @EmmJay931
    @EmmJay931 4 години тому

    Boma ndilomweli la MCP lotsogozedwa ndi Chakwera ndipo palibeso kusintha olo pang'ono... Dpp never again

    • @EnifarSeleman
      @EnifarSeleman 4 години тому

      Anthu onvesa chisoni Inu ,nde muthawatu next year

    • @KalimaImedi
      @KalimaImedi 2 години тому

      AAAA akulu please Anthu 9 anafa ndi chilima Aja amafuna Moyo mukamat boma ndi lomweli mukufuna kupha Anthu ena? Ndale zakupha Anthu zinatha kale ndi kamungu

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 6 годин тому

    Chakwela wayankha mafuso ndipo moveka bwino kwambiri. Macadet akungopanga phokoso basi. Kkkkk

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 14 годин тому

    Ndi afiti kumene nkhalamba zokhazokha muziwona nkhupe zija nkhope zoyipa sizisowa nte umadziwika ndichipatso chake

  • @AgnesNjikho
    @AgnesNjikho 14 годин тому +1

    Kkkkkkkkk sikidi munthu woziwa kiyankhula komwano ndindewo amafuna palipose pakhare ndeu or chipongwe kumeneku skukula muzeru choti tiziwe nichakuti chikondweresa muzinda sichikondwrresa aliyese ndiye awaa abambo awawa mwina akufuna achuke pazoyipa

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 13 годин тому

    Chakwera is a democrat. A Peter Muthalika anakhala zaka 6 koma ku parliament sanapiteko kukayankha mafunso. Kukula mtima ndikutsatsata malamulo.

    • @JohnChitsulo-q6f
      @JohnChitsulo-q6f 10 годин тому

      For ???

    • @MaryMlomba
      @MaryMlomba 4 години тому

      Ndiye kuti zinthu zimayenda bwino nthawi ya dpp ndi chifukwa samaitanidwa ku parliament kukayankha mafunso. Munthu amene amayankha mafunso ndiye kuti ndi olakwa.

    • @EnifarSeleman
      @EnifarSeleman 4 години тому

      Mumafuna azikataniko , fertilizer otchipa,sopo otchipa school fees yotchipa ,osati ndikubwera ngati adya nyama yagaru

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 14 годин тому

    Abwana bwanji kungosiya kupitako? Siulemu umenewo. Akungofuna kupedzelapo zoyankhula pa compen yawo.Muona mtsogolomu zimene atayambe kuyankhula
    Tiyeni tilitose pano.

  • @PhillipMacheso
    @PhillipMacheso 4 години тому

    Aaaa DPP akeeee

  • @michaelkunje5370
    @michaelkunje5370 3 години тому

    Mbuli ya president 🚮

  • @EnifarSeleman
    @EnifarSeleman 4 години тому

    Ine ndikuona kuti mr pule apite kaye ku Zomba mental sizikuyenda taa

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki 4 години тому

    Chakwera you must be mad enough! How dare you speaking stupid facts like that?

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 8 годин тому

    President uyu mutu wake wapoila bas 😂😂😂😂

  • @EdnaChidyaudzu-fx5eo
    @EdnaChidyaudzu-fx5eo 4 години тому

    Ndipo opposition youma mitu ngatiii iyiii sindinaioneko akuvaaa kuwawa kwambiri en zakuti mutenga mpando umeneu ndi kuopseza mukunama pezani za zeru zopangira campain not the way u are doing

  • @ThomChirwa-py8xo
    @ThomChirwa-py8xo 9 годин тому

    Kod akuyankhula chani uyu

  • @CvgGgbnb
    @CvgGgbnb 14 годин тому +1

    Wojambula mukunama mukutengela Mbali Koma Chakwera ndi BOMA basi mpaka a Malawi azavoteso mwamwayi Chakwera kuzawinaso ndiye muza lira chifukwa Mulungu amakonda aliyese❤❤ Chakwera

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe 3 години тому

    Basi ukatelo watsuta boma? Ponyelela Palo garu

  • @Bernarddavide-e1o
    @Bernarddavide-e1o 7 годин тому

    Chakwera watiponyadi ku chile

  • @phillipkazembe7281
    @phillipkazembe7281 12 годин тому +1

    Kkkkk koma chakwela kulephela kuyankha mafuso ngati Mwana choncho 😂😂😂😂