Boni kalindo akunena zoonadi koma poti m,dima umadana ndi kuunika muzazindikila bwino patsogolo ife timamuvela chifukwa chili chose chimene iye amanena chimakhaladi chona chokhachokha
Kodi nkhani iyi yachoka kwa Kalindo Yifika ku Dpp😅😅😅, koma nkhani zake. MCP yikupangaso chimozizi, tiyeni tidzudzule awa a mcp, Dpp tinayitchotsa kale😅😅
Very nice speech
Nzeruizonzeru🎉🎉🎉🎉
Mzibwela bwela big man
Izinso nde ziti zopanda nchere basi
Bon kalindo ndioyambitsa maudani mdziko ,Omenyela ufulu samakhalandimbali
Amene mwayandikana ndi yemwe wapanga Audio iyi mutengeleni kuchipatala mngopenga uyu.... Opanda mbali DPP yaipa bwanji... Udikile akung'alule Kalindoyo
Boni kalindo akunena zoonadi koma poti m,dima umadana ndi kuunika muzazindikila bwino patsogolo ife timamuvela chifukwa chili chose chimene iye amanena chimakhaladi chona chokhachokha
Abon kalindo amayima pachilungamo
Akulu chakwela ndi chilima akanakhala kuti amakhala bwino chilima akanafa? akulu penapake mukumveka chi mcp eee
❤zoonadi zomwe mukunenazo chakula ndi umbuli basi
Ndichisilu chiboni kalindo chigalu
tizikondana bwanji ndi yemwe akutipha akutizunza......??? Ndinu makape kwambiri ku nyasa
Kodi nkhani iyi yachoka kwa Kalindo Yifika ku Dpp😅😅😅, koma nkhani zake. MCP yikupangaso chimozizi, tiyeni tidzudzule awa a mcp, Dpp tinayitchotsa kale😅😅
Komaso anayamba bwino yakathera koonetsa kut akupepha nthandizi from mcp
Tinakuwonelera bonikalindo ngati uchitazanzeru koma waonekela kuti ndiwe njoka yoluma kuyambanitsa anthubasi
Muuze zoona kalindo akusochelesa anthu Koma iyeyu kupambila kale ngakhale Ku tikufelanji ndiyeyiso amene amakhala munthu waziwawa pambali imene amapanga palipose amakonda phokoso
Aboni kalindo ndi achisilu boni kalindo siwomenyela ufulu ndiwogawanisa tosefe ndi amalawi koma tangosiyana zipani
Akulu mulungu apitilize kukupatsani mzeru, inu mukuwonetsa kuti dziko lamalawi mumalifunira zabwino
Inunso mwatumitwa kachilungamo kakuthawani
Bon kalindo ali ndi mbali ndi wa dpp asamatipusitse kuti ndi omenyera ufulu
Bonikalindo ndi manganya monga onse azisudzokuyambilakale adasiyana pachisamalirochakumakolo.Bonikalindoanalekeleredwa mwina adakula popanda bambo pamene manganya adakula ndikhalidwe mwina bamboake ndabusa mpake lero lino manganya akukwela mipando yabwino while bonikalindo akuvala maunyoloabwino (kusiyana kochokela)
Muwuzeni Bon kalindo ndi kape ndiposo mbiri yaadziko sayidziwa, UDF idamenya nkhondo kumupangila Bingu campaign aatawina mkuthawa ku UDF kukayambitsa chipani chake,ndiposo ndale zawo ngat zingaakhale ngat izizi saawina komaso zikapitilila zilowa m'mabanja tose amene tidakwatila kumwela a chewa tiyamba kuwaleka a zichemwali awo
Bono kalindo sitsogoleli wa athu osawuka ameneyo ndi wa dpp asaputse anthu ameneyu asiye uchitsilu umeneyu
Mwalakhula bwino aboni kalindo ndiwosokoneza udf ndichipa cha athu awumuthu
UDF yathu ikutha chotchi ndichifukwa cha DPP
Mukutisokonezatu khani yanuyi zosezi Bon kalindo?
Mukumazanveka ngat mukumenyeraso khondo mcp mukutisokonezatu
You are a fool Mr. What transpired after mcp itasemphana ndi chilima , where is chilima today??? mcp ilibe umunthu sidziwa democracy