Skeffa Chimoto -'' Ine Si wa sataniki'' kuchoka kogulisa zipewa Pano Ndi Billionare

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 жов 2024
  • Kupatula kuyimba, Skeffa amapangano ma business. Iyeyu ali ndi MAGalimoto ambiri omwe amanyamula katundu . Mu kanthawi kena, anayamba kutchuka ndi mbiri yosakhala bwino yoti iyeyu ndi mmodzi wa anthu a Satanic ndziko lino.
    kuchoka kogulisa zipewa Pano Ndi mponda matiki
    from sellingTsotsi Hat to a multi-millionaire
    the story of skeffa chimoto

КОМЕНТАРІ • 86

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 6 місяців тому +2

    Asikefa kodi kalata anasiya chinga sipanatuluke zina lanu kumbukilani kalata imeneyi mboni ndi grace chinga anasiya kalata dziko lonse likuziwa ndithu

  • @victorkazembe9631
    @victorkazembe9631 2 роки тому +15

    Vuto la ife amalawi munthu akatukuka timayamba kupeka nkhani. Skeffa wavutika pamoyo wake. Pano mulungu wamuona anthu mwayamba kukamba zambili.

  • @ngomajohn1751
    @ngomajohn1751 2 роки тому +2

    Watching live & direct from zambia , chipata , kasenegwa district - John Ngoma..skefa chimoto my blessing

  • @asmaljames9323
    @asmaljames9323 2 роки тому +7

    Bambo ngati kalankhulidwe kanu mumaganiza kuti ndikachikoka aaaaaiiii ndithu sinthani kalankhulidweko thats my opinion

  • @harrymaganga5977
    @harrymaganga5977 2 роки тому +2

    Muthuyu ndi luso lake Koma Muthu akatchuka kapena kulemela anthu amamukamba Koma skeffa usaoke ndithawi yako nyimbo zako Ife dzinatisitha

    • @macdonaldkorea2928
      @macdonaldkorea2928 2 роки тому

      Amalawi tili ndi bvuto mchifukwa ambiri tili osauka mpaka panopo komano kusaukaku ndi kwammutu mwathu, tikadzalemera mmutu pamaganizidwe tidzayamba kutukulana tokha tokha like Indians......
      Ukatukuka akuti walowa satanic, ukasauka akuti anasemphanitsa chizimba, umphawi udzatipha kwabasi.....sinthani maganizidwe potero kuti Mulungu atisinthe nafe

    • @AishaChibwana-b8o
      @AishaChibwana-b8o Місяць тому

      Koma ife tikulondoloza kalata ya Grace Chinga

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 10 місяців тому

    Nthawi yotsiliza ino Satana akugwira nthito kwambiri ndi anthu omwe mukuti ndi alusowo, Tamawelengani za kutha kwa nthawi ya pansi pano , komanso mudzisegula ma website ena mudzaseguka m'mitu mwanu, Inenso ndinkamukonda koma zomwe ndinapeza ku ma website ena zinandipangitssa kufuta nyimbo zake zonse komanso si yenkhayo ayi, alipo kagulu moti ena amati ndi a gospel koma akutumikila satana kuseli , inu simukuziwa komanso mwini wakeyo sangavomere ayi. Chomwe mukuona inu ndi nyimbo basi

  • @kinlosmachemba5046
    @kinlosmachemba5046 2 роки тому +1

    Amalawi tidzitha kuyamika mzathu akachita bwino.Uyu ndi mmalawi akuyimba ku malawi akutukula malawi.Chonde tiphunzire kuyamika zimene wina wachita.

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 місяці тому

    Oyimba ambiri nimasataniki uyuso sikefa nisataniki grace chinga anaurura kare

  • @GraceTandani
    @GraceTandani 6 місяців тому

    Watching live from United States

  • @EliseuMoffatliver-vn1xg
    @EliseuMoffatliver-vn1xg 7 місяців тому

    Musatinamizepo apa it's only God who knows everything

  • @rasheedmalunga9212
    @rasheedmalunga9212 Рік тому +1

    Watching from UK

  • @lastonnthenda2309
    @lastonnthenda2309 Рік тому

    I lke that guy n he is so humble from thyolo

  • @RaffiqMahmoud
    @RaffiqMahmoud 2 місяці тому

    Akapusise azibale ako,ngati siiwe WA satanic why uli ndi page ya illuminat pa Facebook?? Wayiwala zomwe umapanga post pa FB zija,mavuto ogulisa zipewadzo ndizomwe zinakupangitsa kut ulowe ma cult opanda pake

  • @mlezanyirenda2815
    @mlezanyirenda2815 2 роки тому +3

    Oyimba ambiri akwathu ose awonongeka ndi usatanic vuto asogoleri nde akakuwuza kut ulowe
    Umarowa u satanic kwathuko sakubisa kharidwe lonyasa

    • @graciousrobertrobert6928
      @graciousrobertrobert6928 2 роки тому

      Its true hé is thé satanic one

    • @ipyanamwanyongo4169
      @ipyanamwanyongo4169 2 роки тому

      you're speaking the truth my brother all of them Malawian musician alowa usatanic, chifukwa anampha uyimba but we need to pray for Malawi that God most delivered this country from powers of darkness,

    • @christopherbadson699
      @christopherbadson699 2 роки тому

      Inu mumati angavomere kuti iye ndi wa satanic?

    • @alexbanda4982
      @alexbanda4982 2 роки тому

      Kaya abale Inu

    • @ishmaelchiponda7806
      @ishmaelchiponda7806 2 роки тому

      Koma ndinu omvetsa chisoni, satanic kulibeko ku malawi...

  • @cktutorials7998
    @cktutorials7998 2 роки тому +1

    Skeffa is a blessing love from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲

  • @sesfikileshop7344
    @sesfikileshop7344 Рік тому

    Komatu zoti ndi Billionaire mukumulakwira inde ali ndi kanthu koma zoti ndi Billionaire mukuzitenga kuti? Mu list yama Billionaires m'Malawi muno iyeyo mulibemo

  • @dicksonphili3466
    @dicksonphili3466 2 роки тому

    Sikefa kaya ndiwa sitac zilibe kanthu ine nyimbo zake zimandisintha

  • @mwayikayuza8164
    @mwayikayuza8164 Рік тому

    I like chimoto so much

  • @clementbanda1137
    @clementbanda1137 2 роки тому

    Watching from Port Elizabeth South Africa,,

  • @MarhaKamowa
    @MarhaKamowa 2 місяці тому

    ndiko lamalawi linachuluka kaduka kwambuli kaduka akuchedwetsani amalawi mulungu amadalitsa kwaolimbikila bwana skeffa ulemu wanu chanu sikanga chanu ndichanu bas

  • @blessingsmtambalika358
    @blessingsmtambalika358 2 роки тому

    Sikefa chimoto
    Amadidalitsa ndi nyimbozake

  • @TaitusNyamula-iv2mr
    @TaitusNyamula-iv2mr Рік тому

    watching from kenya

  • @HestingsChapola
    @HestingsChapola 6 місяців тому

    Ndichifukwa chake amatilimbikisa kwambiri munyimbo zake

  • @agnesssomaliland
    @agnesssomaliland Рік тому

    Koma tone ya voice mukanasitha please news zanu sizikubeba zuoneka ngati kukakamiza zithu kumangolakhula voice yanu bwanji😂

  • @ntchindikondowe643
    @ntchindikondowe643 2 роки тому

    Amalawi nzanu asachite bwino ndekuti ndi wa satanic inuyo mumayankhula chonchonu mumafuna kusauka mulinakoko ngati ndi wa satanic Inu mukulekelanji kukalowa kuti nanunso mulemele tamango kandani anthu opanda tsogolonu

  • @ajisonchimombo88
    @ajisonchimombo88 2 роки тому +4

    Jealous people always loose

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 2 роки тому

    Nthawi zambiri chifukwa cha kulephera kapena kufooka kwa munthu mapeto ake wina amayamba kuda anthu ena posafuna kuvomeredza kulephera kwake

  • @miracleeneah5861
    @miracleeneah5861 Рік тому

    Komaso alibe Galimoto registered number skeffa 1

  • @FinishB
    @FinishB 3 місяці тому

    Zonse aziwa ndi mulungu siyeni muthu

  • @miracleeneah5861
    @miracleeneah5861 Рік тому

    Palibe chomwe mudziwa inu za skeffa aaaaaaaa dzina lake lenileni ndi joviara moti simuzidzuwaso

  • @ruthtimothy9583
    @ruthtimothy9583 2 роки тому

    Watching from Cape town

  • @albertinamartins2593
    @albertinamartins2593 2 роки тому +1

    Ndimakukondani achimuene

  • @dorafaartsigns6188
    @dorafaartsigns6188 2 роки тому

    Vuto lakwathu kuno ku Malawi timadana ndi wolimbika ndipo wolimbikayo akalemera amampatsa nickname yotchedwa satanic.

  • @alfredbanda1732
    @alfredbanda1732 2 роки тому +2

    Suziwa kumasulila nkhani ataaaa

    • @manuelmakonda2324
      @manuelmakonda2324 2 роки тому

      I think better mukanapanga zanu tione, than kuti mukhale wazelu pazomwe wina wachita,

    • @ConcleyManeya
      @ConcleyManeya Рік тому

      Osamadana ndi anthu olimbika pogwila ntchito .

  • @kelvinmwasinga1706
    @kelvinmwasinga1706 2 роки тому

    Watching from Namibia

  • @AmosMalikebu
    @AmosMalikebu Місяць тому

    Amen

  • @AlfredbensonaogagmMunthali
    @AlfredbensonaogagmMunthali 6 місяців тому

    Vuto a Malawi munthu akayiphula amati ndiwa satanic

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 2 роки тому +1

    Inu taziyankhulani bwino bwino apa.

  • @Rabeccah-m2q
    @Rabeccah-m2q Рік тому

    I like Driemo cfkwa sapanga nao

  • @mwale1154
    @mwale1154 Рік тому

    Wa was wa akulu akulu!

  • @benjaminjobo3525
    @benjaminjobo3525 Місяць тому

    Grace chingas letter dont forget you are included there so y are you saying you dont belong to the MARK OF THE BEAST 👹👹👹👹

  • @EliseuMoffatliver-vn1xg
    @EliseuMoffatliver-vn1xg 7 місяців тому

    A Malawi ambiri mukutiopsa kwambiri mwasintha modabwitsa koma Bible imati mwini nyumba akadadziwa kuti mbala ldza boola nyumba si bwenzi ata gona koma akadadikirira kuti mbala lsa boole 'koma a Malawi mwataya chamoyo mwatola chakufa

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu Рік тому

    Sangavomeredze olo ali wasatanik kma akudzuza ndi mulungu ekha basi

  • @PhatsoKapheta
    @PhatsoKapheta 9 місяців тому

    Munipatseko nambar achimoto skef

  • @b.i.gndunab.i.gnduna7441
    @b.i.gndunab.i.gnduna7441 2 роки тому

    Ai ndiwasataniki skefa yo guys

    • @rainfordisaacs6789
      @rainfordisaacs6789 2 роки тому

      Muli ndi umboni inuyo?

    • @victormsika1538
      @victormsika1538 10 місяців тому

      Wasatanic yo ndi iweyo ka. Ukhalilanji ndi nsanje ngt siiwe wa satana. Mfiti yachabechabe

  • @ericndizeye9490
    @ericndizeye9490 Рік тому

    ooohhhh

  • @willsonmzumala
    @willsonmzumala Рік тому

    Akutameni

  • @masterevanschomora
    @masterevanschomora 2 роки тому

    Vuto anthufe sitikufuna kuyesa zinthi kuti tiziwe mataleti athu mara muzati in ineso Wa Sataniki koma tikuyambila apa movutikira 👉aaronnemarere TV watch muone mmene timavutikila kuyamba zinthu

  • @vettasanga3876
    @vettasanga3876 Рік тому

    God bless you mr

  • @Adelaidebasera08
    @Adelaidebasera08 Рік тому

    Ndi n'daliso wake basi

  • @stainmilanzi5293
    @stainmilanzi5293 2 роки тому

    Palibe chilipo pamenepo guys

  • @NespoliNanganga
    @NespoliNanganga Рік тому

    Ndiwe dolo

  • @yamie1
    @yamie1 2 роки тому

    Munthu ndi olimbikira uyu

  • @henzomanzo9158
    @henzomanzo9158 2 роки тому

    You are the best skeffa not this guys gwambizo fukolo man

  • @hopekandle6707
    @hopekandle6707 2 роки тому +1

    🤣🤣🤣🤣 koma adolo inu nde mmadziwa kulongosola nkhan eti

  • @dondream5021
    @dondream5021 2 роки тому

    🙉🙉🙉🙉

  • @modyanthuachino2074
    @modyanthuachino2074 2 роки тому

    Ndi wa satanic uyu luso lake ija anakagulitsa kwa satana pano saimbanso bwino
    Mumuuze mmaso mwake skeffa yo

  • @snetawailiyasa3215
    @snetawailiyasa3215 2 роки тому

    watching from jamaica