Sukulu za Secondary zinayamba bwanji ku Malawi? Geoffrey Colby; The Development Governor

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 7 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 97

  • @MuhamadiIbraima-dr3lz
    @MuhamadiIbraima-dr3lz 7 місяців тому +4

    One of the best 👌

  • @christophermkhize1991
    @christophermkhize1991 7 місяців тому

    Our big brother tsopano ine phe!!! Kumangomva kukoma may Allah protect you brother

  • @HusseinMachemba
    @HusseinMachemba 7 місяців тому +7

    Kod bakili muluzi TV award inawaphonya kamba kachilungamo chani 🎉🎉🎉🎉❤❤❤

  • @KwestalanjesAjangale
    @KwestalanjesAjangale 3 місяці тому

    God be with you boss man

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 7 місяців тому

    Respect bg mn 👏 very true iweyo makwana bakilli

  • @princechimtengo4793
    @princechimtengo4793 3 місяці тому

    Very educative

  • @michealchaomba9761
    @michealchaomba9761 7 місяців тому +2

    Big up osafuna kumva asamve koma inu mumanena zokhala ndi umboni

  • @user-fe2sc7hq7q
    @user-fe2sc7hq7q 7 місяців тому

    The king of history mafiru bro ❤

  • @Bishopmagombo
    @Bishopmagombo 7 місяців тому

    Your brave enough to sharpen our brains

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 7 місяців тому

    Truth❤. King

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 7 місяців тому

    Big up broz kungoti chilungamo ena chimapweteka🔥🔥🔥🔥

  • @FatimaKazembe-ot1os
    @FatimaKazembe-ot1os 16 днів тому

    Best tv

  • @yammiejaymakawa5067
    @yammiejaymakawa5067 7 місяців тому

    Much love always

  • @user-nn9mx5tt6d
    @user-nn9mx5tt6d 7 місяців тому

    Best TV in Malawi

  • @RaphickBanda-hz4gx
    @RaphickBanda-hz4gx 7 місяців тому

    History Legend

  • @user-eo7xt1ft3q
    @user-eo7xt1ft3q 7 місяців тому

    Thanks. Nzeru nkupangwa

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 7 місяців тому

    Nice👌

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 7 місяців тому

    Yes mr perfect!!

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 7 місяців тому +1

    You always talking true we love you so much brother

  • @user-ub6di9em6g
    @user-ub6di9em6g 7 місяців тому

    Iwe ndiye 1

  • @user-iu2tx2gg3m
    @user-iu2tx2gg3m 7 місяців тому

    Ulemu wano big ❤

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 7 місяців тому

    Looking for another one for filip kisekedi

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 7 місяців тому

    Big ndakunyadilan pondiuza zomwe anapqngapo Mr kanyqma analibe sankho bwezi akqnqmqnga ku nkhata

  • @farookousmane715
    @farookousmane715 7 місяців тому

    Let us those who watched this 2 times gather here..😊

  • @chipiliromalola6380
    @chipiliromalola6380 7 місяців тому

    Umatha brother big up❤❤

  • @daviebanda5098
    @daviebanda5098 7 місяців тому

    Big up bro u r de best

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 7 місяців тому

    Koma akulu inuyo mmmmm MULUNGU akudaliseni mukutivesa kukoma ineyo ngati NTUMBUKA ndikamava kuwotchedwa kwama book achitumbuka ndikudanilathu kamuzuyo ngati kuli munthu anabweresa umphawi kuno kwathu ndi chigawengachi chotchedwa am strong kamuzu anapondeleza eni nthaka kupha wose 😢

  • @JamesImran
    @JamesImran 7 місяців тому

    Your number one bro

  • @user-dx4zu1wv4q
    @user-dx4zu1wv4q 7 місяців тому

    Number one man

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 7 місяців тому +1

    Haaa chakwera ndi osekesa kwambiri bwanji, basi ife tili pa mbuyo pa bakili muluzi TV

  • @molicieeosama8877
    @molicieeosama8877 7 місяців тому

    ❤❤❤❤❤❤

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 7 місяців тому

    Kaya Peter Mutharika apangacampaign kaya ayi inde ndidzamuvotera iyeyo basi.

  • @TimeMbona
    @TimeMbona 7 місяців тому

    TV iyi umakwana true story 🙏🙏🙏🙏

  • @user-uc6uc5pc8q
    @user-uc6uc5pc8q 7 місяців тому

    Big up mr

  • @juniornkhata2518
    @juniornkhata2518 7 місяців тому

    Kamudzu banda only knew how to organize old Mama's from all over the country to dance for him, while inspecting with litchowa in his hands.
    Koma Ada bakili pa Masafu pokha anakonza. I remember moving from under the tree to a new built classroom.
    Koma uyu amene alipo uyu Nchifukwa chake akumaponyedwa miyala😂.

  • @kasupeowenpaul
    @kasupeowenpaul 7 місяців тому

    Big up

  • @elizamaster2168
    @elizamaster2168 7 місяців тому

    Mumatiyimila bwana, mwayinu muli chlungamo chokhachokha🎉

  • @user-mz4tk1pw3f
    @user-mz4tk1pw3f 7 місяців тому

    Big inuyo timakunyadirani kwambiri mulungu azikudalizani kwambiri

  • @chigokhalid9420
    @chigokhalid9420 7 місяців тому

    The best TV in Malawi

  • @timothychilwe5231
    @timothychilwe5231 7 місяців тому

    12:23

  • @GeorgeGeorge-bu6cy
    @GeorgeGeorge-bu6cy 7 місяців тому

    Ulemu wanu brother

  • @gradsonmayira9336
    @gradsonmayira9336 7 місяців тому +1

    Madala inu mumatha kufukula history

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 7 місяців тому

    Amalawi tikanakhala a nzeru bwezi titagwilizana kuti mcp yithe chifukwa ikutisupula mabala omwe situzaiwala please amalawi tiyeni tigwilane manja mcp yithe kusazamvekeso za mcp

  • @SamsonMtengula-fl6yl
    @SamsonMtengula-fl6yl 7 місяців тому

    Mr man mumatha

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 7 місяців тому

    Komanso anabwerako ndi zithunzi zonjambulitsa ataima ndi aZungu basi.

  • @ApocheC
    @ApocheC 7 місяців тому

    mukapita kwanuko, mukagwetse kwacha ndi 44%

  • @timothychilwe5231
    @timothychilwe5231 7 місяців тому

    Zowona Timakukonda komaso umayankhula chilungamu

  • @georgeabigailmaseko-ts3fq
    @georgeabigailmaseko-ts3fq 7 місяців тому

    🎉🎉🎉❤❤

  • @user-jm8ft5dt9n
    @user-jm8ft5dt9n 7 місяців тому

    Bwana wathu ndiinuyo

  • @farookousmane715
    @farookousmane715 7 місяців тому

    Extraordinary narration! ❤

  • @user-dk6yc8pl2m
    @user-dk6yc8pl2m 7 місяців тому

    Mulungu azptlila kukupasa zobiska nfkukilimbikisa mtima ndmava kukoma nd anthu olimba mtima ngat inu nd kalindo

  • @chrismakhela7133
    @chrismakhela7133 7 місяців тому

    Chakwera uja alibe mzuru

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 7 місяців тому

    I'm the first to comment bwana❤😂

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 7 місяців тому

    Kkkkkk koma yah

  • @user-to4lf5cr5v
    @user-to4lf5cr5v 7 місяців тому +1

    Chakwera wopanda mzeru kupita kamereka kuapempha kukwesa kwacha

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 7 місяців тому

    Chakwela abwelele ku mpingo basi

  • @sharrifgwape7169
    @sharrifgwape7169 7 місяців тому +1

    Madala sopano

  • @matembamadadada8291
    @matembamadadada8291 7 місяців тому

    🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤

  • @MathiasJoseph-ot5bf
    @MathiasJoseph-ot5bf 7 місяців тому

    Mumatha

  • @Bishopmagombo
    @Bishopmagombo 7 місяців тому

    Umakwana

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 7 місяців тому

    Ena alipompa akususaso ,hiiiii sakuona et

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc 7 місяців тому

    Chakwela ndi munulo nzelu zawo ndizofanana

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 7 місяців тому

    Mbambande bwana

  • @nyararaishumba9288
    @nyararaishumba9288 7 місяців тому

    Chilungamo Ichi maulendo 100 opanda phindu 😂😂😂

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 7 місяців тому

    Mr devaluation president sir panyapake ndithu chakwera fertilizer pa 4500 passport 14 sauzande kkkkkkkk

  • @user-pn7cj9hb3t
    @user-pn7cj9hb3t 7 місяців тому

    Iwe ndi oopsya ase

  • @dannymangawa7511
    @dannymangawa7511 7 місяців тому

    Za mphamvu

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc 7 місяців тому

    Osafowoka tili limodzi bro

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 7 місяців тому

    Kusonyeza kuti anthu ena mu malawi alimo osakondela za mutundu

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 7 місяців тому

    Koma chakwela watitola kwabasi ndi mukaka wake

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 7 місяців тому

    Bro mumatha koma musamasowe chifukwa tinazolowera, tatiuzani ya pa red sea ya America ndi Yemen

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 7 місяців тому

    Kkkk koma chakwela ndi opwambwana kwqmbiri

  • @Justman34_dislike
    @Justman34_dislike 7 місяців тому

    Kubweretsa zitukuko zenizeni

  • @humairamalombe295
    @humairamalombe295 7 місяців тому

    MCP kuinvesa kuning'ina😂😂😂

  • @user-qj6lp8ff8t
    @user-qj6lp8ff8t 7 місяців тому

    Boss inuyo mumakwana inuyo bc ndilipo pitilidzani big ifeyo tilipano kukusatani bc ukali wanu inuyo

  • @user-mi5pe3wd6d
    @user-mi5pe3wd6d 7 місяців тому

    Bakili muluzi ili bhobho kwambili

  • @user-xf4nh3tl3l
    @user-xf4nh3tl3l 7 місяців тому +1

    Bakili muluzi ndi katundu

  • @PatrickLimiton
    @PatrickLimiton 7 місяців тому

    Iponden fada

  • @tamimudaudisaikonde5624
    @tamimudaudisaikonde5624 7 місяців тому

    Chakwera ndigalu

  • @user-qq3ip1od6i
    @user-qq3ip1od6i 7 місяців тому

    Kuchintekete

  • @user-sb4om5pw2h
    @user-sb4om5pw2h 7 місяців тому

    Ulemu wanu madala

  • @janenkhoma6447
    @janenkhoma6447 7 місяців тому

    Zamphavu umaitha

  • @musaphiri317
    @musaphiri317 7 місяців тому

    Zoona vuto makani azaziona

  • @leepaul1826
    @leepaul1826 7 місяців тому

    Koma awaso bodza amaonjeza bwanji? Kungodana naye kamuzu ndiye basi kufuna kufuta mbiri za kamuzu? Simuikwanisa kuononga mbiri ya kamuzu

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 7 місяців тому

      Ngat akunena bodza tiuzeni inuyo zoonazo time.

    • @user-hd7wq2yc6m
      @user-hd7wq2yc6m 7 місяців тому

      Awaso ndi agalu kamuzu olo Chakwera anapangapo zanzeriu ntchito yikhale yosintha maina azitikuko za anzawo akunena zoona zokhazokha Bakili Muluzi TV continew Bakili TV to educate and to wake up Malawians

    • @kennedychinguwo1640
      @kennedychinguwo1640 7 місяців тому

      Kamuzu mbava yochokera ku Ghana,kubwera kuzazunza anthu kuno,mbuzi ya munthu

  • @leepaul1826
    @leepaul1826 7 місяців тому

    Ndiwe galu ma secondary 250 anamangidwa kuti? Ndiwe galu kwabasi muti ouma ngati njerwa wo chisiru chamunthu iwe

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 7 місяців тому +1

      Pepa ndi munthu si galu, ngat akunama tiuzeni inuyo zoonazo, ife timve.

    • @ApocheC
      @ApocheC 7 місяців тому

      kupepela basi, ukatero akunyozera mbuzi ya 44% ndiye zawawa

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 7 місяців тому

    man muzi gotiuzako za history osati kuyipisa chipani kape muthu oti anamwalira karekare timayamika zambili mumatiuza zinthu zabwino koma mukumadana kwambili ndi chipani

    • @kennedychinguwo1640
      @kennedychinguwo1640 7 місяців тому

      Sakuyipitsa chipani koma akulongosola mbiri ya dziko yomwe ili attached ndi utsogoleri wa chipani chomwe chinkalamulira pa nthawiyo

    • @ChristopherKabanga
      @ChristopherKabanga 7 місяців тому

      @@kennedychinguwo1640 ok koma zikuonjeza kalindo kuti anthu ayambe kumutuluka amayankhura zosemphana ndizomwe zikuchitika mdzikomu o

    • @amabhohlela.3492
      @amabhohlela.3492 7 місяців тому

      Tapitauko iwe,,,Galu "iweyo ngati zimakunyatsa kulibwino usamamvere BAKILI MULUZI .ndipo upange unsubscribe..

  • @DickMdala-pn4pd
    @DickMdala-pn4pd 7 місяців тому

    Best tv