Nanunsowangokhala osaganiza Bo koma akunenaz nzoona cuz being opposition leader na pamene wafika Moyo pamalawi mmm amayenera kukhala active kuimira anthu akupsinjikawa koma wangot chete ngat Ali lolamula naye then mawa adzibwela mufuna vot ya anthu asakuwayilirawoso
Auze Mangochi kuti azitsogoleri onse azipani za opposition akapezeke ku mademo chifukwa mademowa ndi azipani a Namiwa paja nawo timadziwa kuti ndi a DPP pajatu amagwira ntchito ku STATE HOUSE nthawi ya DPP. Ndiye tikufuna Peter 'Namkhumwa ' Atupeleyo and Kabambe Osamangoti aNamalomba tiyeni kumademo kukanunkhe mphira .Mugobisala mnyumba kumangofunsa zili bwanji kumeneko otumidwawo akungokhapidwa uku.
Kkkk koma ndaseka aaaa cholinga anthu azidana mmakwalalamu bwanji osangopita direct kwa Atupeleyo? Nkhani mbweee aaaaa tikhale ndi mzeru koma.Nkhani tipange plan yowina basi koma kukamba ichi ayi kudambwe ayi chimwendo ayi smatmatic machine ayi mwana wa Tembo aaaa let's plan kupanga zowina basi
Chifukwa chake chipani cha udf ndi machinga ndi mangochi chifukwa kuli mbuli zambili mukawone mupoto alibe nazo ntchito zoti kuli aford chifukwa ambiri ndi anthu a nzeru hevy
Powerful advise from Lyton Mangochi, proud of you always ❤❤❤❤
Great advise mr ❤❤❤
😂😂😂😂😂😂😂😂 wina amuchindila mkazi kkkkkkkkk Richard chimwendo Banda kuchinda 😂😂😂😂😂
Muwuzeni ameneyo ifetikufunakut atenge pandoumenewu ndeakupanga zachibwanaso aaaa ifetimalikondatu bomalimeneri❤❤
Atupele wapangatsa mangochi kuyankhula chizungu kkkk mr lyton mangochi ur the true free speech 😂😂😂😂
Good advice 💪💪💪💪💪
I 100 %agree with Lyton mangochi
Atupere ndiwodzikonda ngakhale kwawo kumachinga analephera kusankhidwa u mp
Malawi anthu azerudi osawopa alipo big up amfumu 🙏
More fire comrade mangochi
Osaopa osatopa osafooka Allah alipo Mr
Musalile munafuna Nokha kusakha chakwera musatukwane atupere
Inu apange chiyani Mesa anatichenjeza kuti mukavotera mcp muzalira nde Leroy mukumuda
Dpp or utm kungiwina azisogoleri ambiri a mcp ambiri azamwa tameki
Atupele nimnthu wadzelu sangafanane mbuzi ngati iwe chisilu iwe
It's true
😅😅😅😅😅😅😂😂😂Atupele koma ukumva uliko 😅😅😅😅😅😂😂😂yomweyo Chikangawa party
On point
More fire Layton chemangochi
Atupele ndi Kape weniweni zoti anthu akuvutika he doesn't care
Good massage
Soona
Why forcing Atupele to do the things in your way if you want to fix things just do it the way you want
Oooh yes Comrade Mangochi Osaopa,osatopa and osafooka
Lero wafunika Atupere? Mmesa munkamunyoza atapanga Alliance ndi Dpp, muchisankho cha 2020 nkumakuuzani za zoipa za MCP, munkamutenga tenga ngati openga lero ndi izi, musiyeni anthu opanda pabwino iya.
Anthu awa ndi otembeleledwa kamba ka uchimo wa kaduka ndi msanje komanso tsankho kotero sawona komwe akupita
Tsankho
Kkk zaziii akulira chiyani kodi awa
🎉🎉🎉🎉🎉🎉
To the honest Atupele ndi opsesa mtima aaaa😢
❤❤❤ Layton mangoch nakutaya kma lero ndaonela video yako zoonad ATUPELE ndiozikonda mmm ndiokwana kmaso amene amakakamila ATUPELE NAO AMAKHALA ALIBE CHOCHITA
Atupele ndi amene adayenda Kona ndi kona kuwuza anthu 2019 ndi 2020 uja kuti musavotele nonsense alayansi kapena MCP koma inuyo mumkamutukwana munampatsa mayina osiyana siyana onyasa please lero muyende ndiinu Atupele musiyeni
😂😂😂😂 Comrade Mangochi woyeeeeeeeeeeee❤❤ awuze
Chilungamo chokha chokha Comrade Layton Mangochi ndipo tonse tigwirane manja ndicholinga tikwanitse kuchotsa agalu amenewa m'boma.
Anakuwuza Galu iwe Kut MCP siyabwino inu munavotabe atupelu ozindikila oziwa akuphen kumene atupele alibe vuto,koma inu athu kusava ulila sunat
Ndipo ananena mr Atupele loud n clear 🎉vuto nditokhadi
Viva Layton mangochi 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Chilungamo ndipo live
❤❤❤❤
Muuzeni zowona zake Atupere ndikutha kuwona kut simunthu wakut atha kuthandiza dziko ayi ndiwofoyila
amangochi inu😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Aopposion ndi ogona kwambiri adzalira Mcp itadzadutsanso
😂😂😂😂 Atupere anafansa kwambiri usogoleri palibe paja
Ife ndi ma savage 😂😂😂😂😂 eish
Atupele ndiwe chisilu 😅😅😅😅
Lero limenelo ndikupepha mulungu akhawulise Malawi MCP ipitilile kulamula atupele mpaka abambo ake anatiwwza Za MCP lelo limenelo lero,lero limenelo lero
Zopanga za usiluzi ndi inu nomwe ankhalamba pitani muzikalera zi dzukulu
Chakwela wapeleka mimba 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Kkkk koma mcp imaziwa kuchinda
Lytton ukubwela bwino God
God bless lyton mangochi
Mmm yooo
Why bihevu puraudi? Heee
Atupele muluzi Peter munthalika inock chihana dalitso kabambe onsewa tikuwafuna ku mademo
Tamuuzen ameneyo asamzimve ngat Ali ndi nzeru😂😂
😂😂😂😂😂😂😂 koma zoona indee baba chilungamo 💪💪💪
Apa pangofunika mademo kapena nkhondo basi..coz apapa ndiye palibe chilipo
Iwe ndie palibe chanzeru basi maganizo ako ali pa chisankho osati kutukula dziko?Zazi moyo angofuna akuuononga dziko
Kodi Galu iwe ukufuna apange zosangalatsa iwe😂😂😂 koma ndalama zikulowa kwambili
Nanunsowangokhala osaganiza Bo koma akunenaz nzoona cuz being opposition leader na pamene wafika Moyo pamalawi mmm amayenera kukhala active kuimira anthu akupsinjikawa koma wangot chete ngat Ali lolamula naye then mawa adzibwela mufuna vot ya anthu asakuwayilirawoso
AMALAWI UYU NDI KAZITAPE WA UTM ATUPELE MULUZI AKUDZIWA CHIMENE AKUCHITA BWANJI SAKUTI KABAMBE KAPENA MUTHALIKA UYU ASIYE ZOLIMBANA NDI UDF APANGE ZAKE
@@symoldickyatupele muluzi ndiozindikila komanso si leader of opposition komanso si mp mukufuna atani
Ndiwe chisilu kwabasi lyton
Kod mademo akungokanika kma mcp ndkatundu tiyen tizingokhala bas mademo sangachitike kkkkkk😂😂
😅😅😅 mademo adapita
Misala iyi Atupere walakwa chani
Eeee!!!! Mukutiyimilira Loyton mukuyitha Allah akhale nanu populumutsa Malawi kuti abwerere mwakhale
This Lyton is bitter coz of poverty, He makes lot of noise for nothing
Ulaliki uwu eeeeh😂
Ineyo mkuona kwanga ndikuona ngati akuluwa akufuna kupita ku mcp thats y sakulankhula lankhula
Odo ukooooo
Munthuyu siwa UDF ai kodi mademo azipanga achipani msyesa ngati ife tili pamavuto ndivoti yikubwelayi ku malawi kwa chuluka anthu ofuna kudya kamba kamilomo yakutwa ai modyapo kwavutadi achikulile kupemba mokwanila wakuba uyu nzina la zzUDF
😂😂😂😂😂zoona bwana we the savage😅😅
Atupele is not agood leader ndiwamatama komsnso ndi wozikonda kwambili
Ulibe mphavu zakakamiza munthu iweyo ngati ukufuna pitako wekha mukhaula .kachaso wakupweteka
Dzukani aopposion chonde dziko la malawi laola
More fire layton mangochi chilungoma basi
Audzeni
Atupele asazapite Ku mademo chifukwa dziko la Malawi ngati Pari munthu wa ndale amene amawopedwa ndi Atupele kotero kupita ku Mademo idzangokhala njira yofuna kudziyipitsa yekha komanso ndi onse omwe amamutsatira.
Paribe chinthu chomwe atupele amachita kapena kulankhula popanda kutukwanidwa kunyozedwa ndi kudzudzuridwa angakhale zochitazo ziri za bwino
Akanakhara Atupele osauka kapena akuchokera kubanja lanjara.kalekale atarowa M.boma .kapena ndale zake bwezi zili zoravula moto.koma iye aliphe osarankhura komaso kudzudzura
Inaliposo nthawi Malawi tisanadziwe za Multiparty ambiri timakana koy Muluzi atawina tonse Tina vomereza lero machine a smartatic sitikudziwa tikagwirirsa ntchito. Tonse tidzavomereza kotero Atupele ndimamunamuna a genuine democracy
Zoona atupele uyuyu otherwise sazapeza vote kunyada kwambiri ngati iyoyo nde bwana wanthu
ATUPELE amadziva, ine ndinamuona kale ameneyo
Kkkk muwuzeni amvese sumunamupempheko ndalama simungamupemphe ndipo simuzamupempha kkk
Leave him alone akukambilana ndi MCP uyu.
Akukula mtima ndi chakwera ndamene akutuma zonse
Kodi uyu ali kumalawi? Nanga bwanji samamanga?
Auze Mangochi kuti azitsogoleri onse azipani za opposition akapezeke ku mademo chifukwa mademowa ndi azipani a Namiwa paja nawo timadziwa kuti ndi a DPP pajatu amagwira ntchito ku STATE HOUSE nthawi ya DPP. Ndiye tikufuna Peter 'Namkhumwa ' Atupeleyo and Kabambe
Osamangoti aNamalomba tiyeni kumademo kukanunkhe mphira .Mugobisala mnyumba kumangofunsa zili bwanji kumeneko otumidwawo akungokhapidwa uku.
Kodi anzanu muwatukwanawa opusa zitsilu iwo alibe ufulu wao tikuonga dziko Ana athu adzakhala pa mavuto akulu aziona kuti munthu kusiyana naye chipani ndiye kuti ndichitsilu uku ndikulakwitsa komabe ndi ufulu wanu lakhulani
Apa next year kulibe chisankho chakwera atilamulebe
Chizungu chayankhulidwatu
Atupele ndiodzikonda
Atupere ndiwozindikira inu, mbuzi iwe palibe chomwe ukulakhulapo apa, ukufuna apanga za umbuli ngati iweyo. Nkuona Malawi sikupita patsogolo chifukwa mbuli za anthu ndizomwe zikumalakhula zopanda mitu,
Atupele ndi mpongoz wake wa tembo and Anabel ndi mla wake
Panyopako mangichi usaveji iyambitse wekha usatume anzako chikala chobe mwana wakwa shonongo.
Mangochi ndi wamisala
Atupere ndi wanzeru sati usilu uwu
Ulemu wanu wakulu muuzeni amvetse
Kkkk koma ndaseka aaaa cholinga anthu azidana mmakwalalamu bwanji osangopita direct kwa Atupeleyo? Nkhani mbweee aaaaa tikhale ndi mzeru koma.Nkhani tipange plan yowina basi koma kukamba ichi ayi kudambwe ayi chimwendo ayi smatmatic machine ayi mwana wa Tembo aaaa let's plan kupanga zowina basi
Koma anthu a misala t@chuluka eee kod mukufuna munthu atan
Komadi guyz atupele akugonadi tulo
Mau
Misala awa bissinesi yatha mwayamba kutukwana anthu ndinu zisilu ufuluwo amapanga chochi chihana naye misala yokha yokha kutukwana simngawi e ayi
Mukulamuliridwabe ndi ng'onazo iwe ukhala choncho ufaso choncho
Aziliman amangochi kkkkkkpangani zanu ndale SI gulu la 21 vote kkkkkk
Atupele.ndi munthu okonda za iye yekha ndiye munthu wa nzeru sangamusatile amasatila atupele mukati muwone ndi mbuli zokha zokha
kod amchita kukakamizana kuchita mademo koma ndiye kumnyozako akumvele
izi zomangotokota social media tatopa nazo pangofunika mademo basi
Ndipo inu inuu Atupere kuli ziii
Kkkkk koma man awa
Atupele wangoti pheeee..nde u president mungakwanitse kulamula dzikoli?
Chizungu chikuveka ngat........ Ndiwe mbuzi yeni yeni anthu osaphuzira kwawo ndikusokosera ngat mene ukusokosereramu mbuzi yamunthu iwe
Utsogoleri ndikudekha komaso kuona poyankha komaso kuyankhula umayenera uganize usanayankhule
a lyton nanu zitokotan ku mzzdyesa mimba zan msatipusise mumadyela momwemo yaaa
Chifukwa chake chipani cha udf ndi machinga ndi mangochi chifukwa kuli mbuli zambili mukawone mupoto alibe nazo ntchito zoti kuli aford chifukwa ambiri ndi anthu a nzeru hevy
This so called Atupele is pompous and self centered