Grey uyende uyende pamene utaziwe kut KUTALI by Fada Moti ndi HIT kwambiliii nde umwe gin uku chili pa speaker aaaaah musamangovela mma headset nyimboziii
Late Martse also used same verse two songs, yina ndi Akitivi, ina ndaiwala koma ku hip hop "Mulungu analenga iwe kungokuona ndikupenja ine" etc.........................
Now you have mentioned one song I like the most. Asibe Happy
Grey uyende uyende pamene utaziwe kut KUTALI by Fada Moti ndi HIT kwambiliii nde umwe gin uku chili pa speaker aaaaah musamangovela mma headset nyimboziii
listen on 18:38, what do you hear?
😂 zeze ndi gate keeper olo fadah atamudutsa motan 😂😂
Fada MOTi wayamba kuonela kwambil mashow a yung stuna
Late Martse also used same verse two songs, yina ndi Akitivi, ina ndaiwala koma ku hip hop
"Mulungu analenga iwe
kungokuona ndikupenja ine"
etc.........................
Ife ndye tnaonela. I watch every show ya Kabza de small
koma abulandoni chizungu ndipanja komanso mumasokoneza show yanzanu be like humble ras
Ati you have a point ngati game ya draw😂😂🙌🙌 Adani tsopano , dauloooooo kwambiri
Hip hop uliku lilongwe ku 25
Get on up is the movie
Mr Adani
❤❤
Kodi aGray nkhani izingopita kubanja? 😂😂😂😂
Watching live koma tipatseni Jersey
😊😊❤
Am watching it koma guys u wasted time zinthu zopanda nzeru koyambililako aaa improve
Adan okuda pompo patiii❤
Adana okuda
A yesu athesa show🤣🤣🤣🔥
Benisamu pa tuno mwanama😅
makape
Ati miss gry
Fada ndi katundu