Very informative. Its crazy i don’t know most of the artists mentioned above😢Please Malawian lets do something about recovering the old music this man has been describing above.
Khalidwe longa ili ndilimene lidapanga expand mngakhale mma Radio station mwathu momwe. They promote ma artist akunja instead of local artists. Chodabwitsa mchakuti Kuti akuwerere nyimbo ndi ndalama uwapatse ma DJ, nanga R Kelly ndi DJ Tira komaso Rick Ross amakuma naye Kuti kuwapatsa ndalama Kuti adzimuikira nyimbo program yonse kutha zakunja zokhazokha.? Maiko anzathu tu sungamve nyimbo za Ku Malawi pa radio yawo. Especially mudzapite Ku south Africa then mukumvere ma Radio station awo.
Very informative. Its crazy i don’t know most of the artists mentioned above😢Please Malawian lets do something about recovering the old music this man has been describing above.
Zoonadi big man. Thanks for the info.
This gentleman deserves respect
Well explained brother open years for ama2000
"John bwelera," what a reminder❤
Well explained
I hope someone has written this important history on music in Malawi.
Poor man's soup 🍲😂😂😂 big Up brothers
This history of our dry music past without infusing our own traditional dances can assist our youth into driving music onto the world map
Khalidwe longa ili ndilimene lidapanga expand mngakhale mma Radio station mwathu momwe. They promote ma artist akunja instead of local artists. Chodabwitsa mchakuti Kuti akuwerere nyimbo ndi ndalama uwapatse ma DJ, nanga R Kelly ndi DJ Tira komaso Rick Ross amakuma naye Kuti kuwapatsa ndalama Kuti adzimuikira nyimbo program yonse kutha zakunja zokhazokha.?
Maiko anzathu tu sungamve nyimbo za Ku Malawi pa radio yawo. Especially mudzapite Ku south Africa then mukumvere ma Radio station awo.
Akunena zoona ndinamva nyimbo za Aran Namoko ku Kenya koma mu language yakomko. Ndinadabwa.
Angakhale Jetu amayimba za ku South Africa
Apa ndiye afotokoza bwino kwambiri ndipo ine ndakhulupirila
mbiri yokoma ndthu zapamwamba izi pitilizani kufukula mbiri
ziri bho kwambili
Zilibwiino kwapili kwajema Malawi watuu ❤❤
Why hands keep on trembling
Akutsatira zomwe kamuzu Banda ankachita
He has a neurological condition called Essential Tremor.
This is sickness
The gentleman is a real historian
This condition is called Parkinson's Disease. It is uncontrollable although there are some drugs to reduce the tremor.