Ngakhale tinkavutika, padali nkulu wanga yemwe adali my late father's younger brother George Sly Dambula. Anandiphimba umphawi wanga kundipatsa zosowa zonse mpakana laptop pa Chanco. He was my role model. Rest in peace uncle Geo. Nanenso ndidzabwera konko to join you and we shall be together for eternity my brother, my uncle, and my best friend. I can't wait for that reunion uncle Geo!
Pa tsikulo ena azati Ambuye tidachita zozizwa mu Dzina lanu. Tidachilisa odwala Koma Ambuye adzati, Sindikuziwani. Eeeeh. Point iyiyi Mama you've awaken my Spiritual life.
Amai akwathu ku Dowa! your songs maka maka ija yotchedwa Nthawi yakwana,,, my friend likes it, but first she thought it is a male voice but after i told her that it is a female voice, she listen to your songs almost every day! proud of you Mama.
Wow listening to her story , what she've been through just like shes telling my story yet I wouldn't imagine she went through this mush a d still humbly so talking about it proudly, such an amazing woman may God protect you mother. NB how can one get your original DVD Videos ?
eeish koma ndinamva chisoni kuti akuti it was not easy to go out and mingle with friends for fear of being ridiculed because of poverty. Inenso ndinakula moyo oterowo, moti atsikana ankatikana chibwenzi akuti ndife osauka.
But i thought your there to preach the Gospel for the salvation of mankind are you there for money ... Is it God who call you to be apostle??? Or is the Bible school that gave you that title apostle .???
Ngakhale tinkavutika, padali nkulu wanga yemwe adali my late father's younger brother George Sly Dambula. Anandiphimba umphawi wanga kundipatsa zosowa zonse mpakana laptop pa Chanco. He was my role model. Rest in peace uncle Geo. Nanenso ndidzabwera konko to join you and we shall be together for eternity my brother, my uncle, and my best friend. I can't wait for that reunion uncle Geo!
She has a very interesting personality, so genuine and cool, with a very welcoming smile..God bless her beautiful soul..🇬🇧
Thats my mom with a very inspiring background history. Be blessed mom
Umboni wanu Mai, wandipatsa msozi zisanaoneke! i remember myself as well kugona pamodzi ndi Mbuzi! but there is God in Heaven!
I love your voice mama chitheka I wish I could sing like you
I love this woman ❤️
❤
God bless this woman........she has been my moms favourite since i was born....and her songs are also my favourite🙌♥️
God of miracles am happy for her testimony
Pa tsikulo ena azati Ambuye tidachita zozizwa mu Dzina lanu.
Tidachilisa odwala
Koma Ambuye adzati, Sindikuziwani.
Eeeeh. Point iyiyi Mama you've awaken my Spiritual life.
Apostle Enesia Chitheka Lewis, ndinu chi Vibe of glory
Wow I love this women of God her life is a living testimony 🙌 🙏
Amai akwathu ku Dowa! your songs maka maka ija yotchedwa Nthawi yakwana,,, my friend likes it, but first she thought it is a male voice but after i told her that it is a female voice, she listen to your songs almost every day! proud of you Mama.
Am so touched ..may God see me through.
Zikomo kwambili potigaira mbili imeneyi Apostle E Chitheka L 😢 😅 Zandisuntha zedi 👏👏
♨♨♨♨❤❤koma chibade tamusowa kwambiri yesetsani big Man
Love you lots The Chitheka's nyimbo zanu sizimandisiya chimodzimodzi
My favourite,,Ilove you so much❤❤
Very interesting and sad background but God is good all the times.
I love this woman nee😍.......Life is indeed a Mystery😑
I like the chitheka's family
life is a real journey. God bless you Mana
Praise God 👏
So encouraging,God is good
Wow what a humility lady
Following from Capetown
Mwazi nda ima
God's ways are not our way. He takes those who are down and put them on top.
Wow listening to her story , what she've been through just like shes telling my story yet I wouldn't imagine she went through this mush a d still humbly so talking about it proudly, such an amazing woman may God protect you mother. NB how can one get your original DVD Videos ?
Following nice interview
God bless you mama 🙏
WONDERFUL
Dzikomo kwambiri, koma ine ndikulakalaka kuti siku lina ndizadziwe cruise5 yainu big Man mr Joab
Kkkkk komadi
Inu nde nde nde nde ndi zimene ndimalingalira ine. Ndimafuna nditadziwa za mkulu ameneyu kwabasi
Ineso🤚pangani zotheka mr Chakhadza
eeish koma ndinamva chisoni kuti akuti it was not easy to go out and mingle with friends for fear of being ridiculed because of poverty. Inenso ndinakula moyo oterowo, moti atsikana ankatikana chibwenzi akuti ndife osauka.
Amém mamãe
Powerful testmony mama ndi mulungu wosathera pa njira am blessed with your testimony uhmmm
Ndanyadira kwambiri ndizomwe mwanena mu background yanu mama ndipo ndatengapo phuziro
Koma amayi inu ndiye ndiinu okongola bwanji
Osamachedwa this is Tuesday eti
Joab za chimbudzi wazikakamira bwanji kkkk bg mn
koma mulungu wanthu ndi mulungu wazichomu kulingalila komwe tachoka kufika lero lino ambuye asintha nyengu zanthu ndipo ndi umboni waukulu amama
Komano inde mumabweletsa madolo, anthu ambiri yawo mu programmeyi koma na IWENSO Joab ndikatundu mmmmmm
Palibe chimene MULUNGU amakulora kuti udutse popanda umboni wawukulu
Next time tikufuna Thomas chibade 😂
not only him but also Zebron Kankhunda
Zilibwino
@@idrissamalinga3175 even gwaladi 👏👏👏
Umboni uwu
But i thought your there to preach the Gospel for the salvation of mankind are you there for money ... Is it God who call you to be apostle??? Or is the Bible school that gave you that title apostle .???
Kkkkkkkkkkkkkklkkkk
Ndanyadira kwambiri ndizomwe mwanena mu background yanu mama ndipo ndatengapo phuziro