President atakhala The Dc.... Vice president Ntanyiwa... Nduna ya dziko Bakili TV wallah malawa akadakoma cz ma guys awawa umunthu alinawo kwambiri, poti munthu umachita kusintha koma dziko lathu likadakhala lokoma... Babu Jr from polokwane Jon's 🇿🇦🇿🇦🇿🇦🇿🇦🇿🇦
A police ambili ndi amowa akazapanga zawozo tizikapondela ku mawa komwe kumukoka kukamutaya kunja zikatelo thatana naye asiyeni ambili asiya Ana ndi mabanja awo pa umasiye 2025
Powerful 💙 iwe mtanyiwa ndi dolo kwambili 🎉
Salute comrade
President atakhala The Dc.... Vice president Ntanyiwa... Nduna ya dziko Bakili TV wallah malawa akadakoma cz ma guys awawa umunthu alinawo kwambiri, poti munthu umachita kusintha koma dziko lathu likadakhala lokoma... Babu Jr from polokwane Jon's 🇿🇦🇿🇦🇿🇦🇿🇦🇿🇦
Sitiopa mfuti, Yehova ndie mfuti yathu
Chilungamo chimamasula😢 zinthunzi zimatengedwa ngati zocheza koma apapa zafikapo 😠😠😠😠
100% agreed comrade smart matic isagwilisidwe tchito mademo acitike apo biiii mavoti alepheleke.Dzikuonetsa kuti ngakhale bambo ake a chikangawa analinso akuba ndichifukwa chikangawa ndi mwanayi akungoba bambo mbuu! Ana mbuu.
16:35
😢😢😢😢😢
A police ambili ndi amowa akazapanga zawozo tizikapondela ku mawa komwe kumukoka kukamutaya kunja zikatelo thatana naye asiyeni ambili asiya Ana ndi mabanja awo pa umasiye 2025
❤❤❤❤❤
Mumatha mr
Mungoti pheee muoneeeeee 😫💔⚰️
Koma ntanyiwaaaa aaaaa umazitengakuyi zinsisi zimenezi
Chakwela akanagotulapasi udindo kiri zikhale ndi ulem
Chakwela wationjeza kwambiliiiiiiiiiiiiiii km guys mmmmmm palibe njila yachidule kd guys taonan talima opanda feteleza mmmm
Kodi kasinja mutengo wake ulibwanji? Mr
Ngwirizano wa zipani 9 unaphetsa anthu 9 mcp chipani choipa kwambiri mizimu wa chilima usawasiye amenewa
😂😂😂😂😂 komatu ntanyiwa
South africa wa police aliyese ali ndi mfiti koma ife sitingaope mfiti ife kumata wa police so kumafa
Mifuti imeneyo sigwila tchito tiwanda ndikuphela omwewo