GWEDE-GWEE _KU UTM AKUSUMIRANA__21 November 2024

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 25 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 45

  • @SkeffaKaifa123
    @SkeffaKaifa123 5 днів тому +4

    Mwayi kuziyana kabambe Ali ndimwayi ochokela kwa mulungu ❤

  • @PempheroAmos
    @PempheroAmos 5 днів тому +4

    Gwede gwede followers let's gather here

  • @FelixGambiza-fp7tn
    @FelixGambiza-fp7tn День тому

    Creative tht dazzle

  • @KondwaniPatson
    @KondwaniPatson 4 дні тому

    Wa usilu mutumbuka Uyo
    Akuona Ngati angawine

  • @LucyKuchete
    @LucyKuchete 5 днів тому +1

    Steve ndi Selina mumakwana guys keep it up,auzeni

  • @lasmoboko5989
    @lasmoboko5989 3 дні тому

    Mwachidule ku KENYA zinthu sizikuyenda bwino

  • @SueWahna-y8m
    @SueWahna-y8m 5 днів тому +3

    Tingochosa 150 ,150 ,150, wa kabambe tiwapase athu aluzawa ndiye kut kaliat ikhala 171 wina 172 wina 176 kabambe atsala ndi 186😅😅😅😅😅

  • @khaleedsaidi6232
    @khaleedsaidi6232 5 днів тому +2

    ❤❤❤ inuyo munabwela bas

  • @TyconSululuwa
    @TyconSululuwa 4 дні тому

    GwedeGwede, Munabwera km bola asakuguleni pajatu oyankhula chilungamo ngt Inu akumakugulani

  • @watsonmatewere6170
    @watsonmatewere6170 4 дні тому +2

    Komatu DK mmene amkalowa mu convention muja,mmene anthu ana sangalalira kukuwira muja,zimachita kueonetseratu kuti awina

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 5 днів тому

    Viva philp nyolo arc Bishop mutengele chitsanzo aku malawi nu

  • @enockchauluka6800
    @enockchauluka6800 4 дні тому

    😂😂😂zamanet zisiyike😂😂

  • @JosephineLongweSelolwane
    @JosephineLongweSelolwane 4 дні тому

    At the end of any election,there must be one winner...The gap is just too much for one to complain,ayambira pati????Just accept and move on together,there is still next time..Akuluakulu anati "Kumayang'ana pomwe wagwera"Those who didn't make it just do a self assessment and work on that, chonde thandizanani ndi a Kabambe may be next time you might win,who knows??

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 4 дні тому

    Musadandaule, ndimayesa mfiti yanu Chakwela mumati ndi m'busa wa Mulungu ndikumpangira campaign pomunyoza Peter Mthalika. Mulungu akutilanga kudzera muzofuna zathu ngati dziko. Ma judge, Army, Police, HRDC ndi Timothy Mtambo akunjoya poti zinthu zinasintha. Zikomo.

  • @shotsfired588
    @shotsfired588 4 дні тому +1

    Mafuta akusowa ku Malawi chifukwa aluya sakufuna kumuthandiza chakwera chifukwa ndi m’busa amene wasankha kusapota kupha kwa anthu ku Palestine. Wasankha mbali ya Israel m’busa amene akusapota kupha kwa ma Muslim ndi a khristu mdziko la Palestine. Connection palibiletu apa.

    • @CharlesBanda-kv8bh
      @CharlesBanda-kv8bh 4 дні тому

      Aluya adayamba okha nkhondo ndi Israel chakwera kudalibeko ukaziputa limba chakwera sasowa mafuta koma iweyo ndi ine ndife tikhaule

  • @IreenMwachande
    @IreenMwachande 4 дні тому

    Azibusa Anamosa pano ndi Njoka zimenezi

  • @JestonTengeletu
    @JestonTengeletu 4 дні тому

    Amandibowa kumangosrka mozelezekera

  • @ThozaChilinjasanena
    @ThozaChilinjasanena 5 днів тому

    akukakamila zozizila ,kodi munthu wakuberani bwanji pamenepo,mukusiyana ndi mavoti ambili mmmm,mwandidabwisa anthu oterenu ndiaja mukufuna nanu mukabe misonkho,bwanji osavomereza nkugwira ntchito limodzi ndi akabambe.inu ngati munaona kuti mwawina bwanji amakunamizanio mukangotenga munawapasazo,

  • @baison3648
    @baison3648 4 дні тому

    ASK THE 265 N TIMES TV MEMBERS TO BROADCAST IN ENGLISH THIS KIND OF PROGRAM OR EITHER POLITICAL STORIES. LET OTHER NATIONALITIES & OTHER COUNTRIES IN THE WORLD SHLD KNOW WHAT IS HAPPENING IN MALAWI, NOT ONLY FOR MALAWIANS. THEY CAN BROADCAST HALF PART IN MALAWI LANGUAGE & OTHER PART IN ENGLISH.

  • @EsnartKamwendo
    @EsnartKamwendo 5 днів тому +1

    Ndipo live akwanadi kkkkkkk za ma net agreen

  • @LerinaKatuli
    @LerinaKatuli 4 дні тому

    Ubwino he was there

  • @BoycraKachiyata
    @BoycraKachiyata 5 днів тому +1

    Munabwela kudzakhala

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 5 днів тому

    Kkkkkk mwawalangiza wakumva wamva basi

  • @BoyneMalenga
    @BoyneMalenga 5 днів тому

    Auzeni mabishopu akumalawi sakulabada ngati momwe amachitila kale alekeni tife tonse kumalawi aziza busa mbuzi osati ife amalawi

  • @StevenFombe
    @StevenFombe 4 дні тому

    Can this current LG of police be taken to task after his expired term due to lack proffessionalism?

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 5 днів тому +1

    More fire bamboo 😂😂😂

  • @ChrisPeter-q4g
    @ChrisPeter-q4g 4 дні тому

    Koma Ku convention nane ndikukayika kuti zinayenda bwino

  • @RaphaelKatimba
    @RaphaelKatimba 5 днів тому

    Mipingo yatha mphanvu chifukwa chadyela. makamaka ma Bishop ndi Ansembe a Roman Catholic ndi anthu opanda chilungamo dyela ndi ndalama komanso bodza limene amawauza a Malawi 🇲🇼 .Roman Catholic it was before not nowadays. Thanks

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j 5 днів тому

    Ma candidate onse anali ndi ma monitor awo

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 4 дні тому

    Or akakamile koma adziwe kuti anthu sanankonde avomeleze

  • @MUSSAHCASIM
    @MUSSAHCASIM 5 днів тому

    Kukhalangati akumadyako kwambili azaumoyowo

  • @kittymalambo1853
    @kittymalambo1853 5 днів тому

    Kkkkkk koma Steve ali ndimwano azaumoyo ndi ma net yagreen

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 4 дні тому

      Chilungamo pajatu ndimwano,zatopesadi zoona

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 5 днів тому

    Ndipo adzikhala serious di akuonjeza ma guys wa

  • @hastingskaira324
    @hastingskaira324 5 днів тому

    One of the leading causes of neonatal mortality is Malaria. Zama Net zofunikirabe kkkkkk

  • @FrankSued
    @FrankSued 5 днів тому

    Net ya green yandiliza.kkk

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 5 днів тому

    Nkhani ya mafuta boma la Chakwera lilikuti

  • @hastingskaira324
    @hastingskaira324 5 днів тому

    One of the leading causes of neonatal mortality is Malaria. Zama Net zofunikirabe kkkkkk