DPP ndi UTM alliance itha kukhala yamphamvu bwanji?..HOT CURRENT 26/05/2024.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 25 тра 2024

КОМЕНТАРІ • 31

  • @AdamMpalira
    @AdamMpalira Місяць тому +3

    Amnyamata inu mukugwila ntchito yabwino chifukwa kuona bwino bwino mkati mwa chimalawichi dzikoli nde lafika penipeni moti we need God's intervention

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs Місяць тому +3

    Kumalawi ndalama zapweka ndithu zaniff ay zikomo

  • @Happ2y
    @Happ2y Місяць тому +3

    Mr kunkunyu ndi muthu oipa kwambili chifukwa ndi opanda chisoni ndi amalawi ndi muthu wakupha that's why akamalakhula amalakhula mopanda manyadzi

    • @jennyx6914
      @jennyx6914 Місяць тому +1

      anaphunzira from the best teacher MCP kunkuyu nkhaza chipongwe satanic mind evil thoughts in his small head like tortoise

  • @AdamMpalira
    @AdamMpalira Місяць тому +1

    Mesa kodi pakumvakaso kuti u vice president akuoneka kuti suli ndiphindu sukufunikilaso nde kodi it's game played

  • @elijahausi2274
    @elijahausi2274 Місяць тому +1

    Aaaaa uku ndiye kuzipangilira zipani zoti zichite

  • @aminrajab5482
    @aminrajab5482 Місяць тому +4

    Ife adpp ayi utm yo

    • @user-qn2nu4xs9i
      @user-qn2nu4xs9i Місяць тому

      Aaaaa... za utm ndiye ayi....zimenezo ai tisamve..

  • @mavmsusa1310
    @mavmsusa1310 Місяць тому

    Odillo, ndi Clement Kafuwa, milandu yawo inalowa ku court bwinobwino mpakana anapatsidwa court bail.

  • @chimwemwechiundira6002
    @chimwemwechiundira6002 Місяць тому +2

    No sound

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 5 днів тому

    Gwirizzano wabwino ndi opysa kwambiri,,Dpp,udf and afford

  • @KassimmwStevenetc
    @KassimmwStevenetc Місяць тому

    Joka ndi joka singasithe mawanga achilima akuyenera kuganiza mwazeru

  • @innocentkandulu2825
    @innocentkandulu2825 Місяць тому

    palibeso za alliance chipani chilichose chiime pawokha

  • @yamikanifischer
    @yamikanifischer Місяць тому +1

    Sound yabwera

  • @chrispinechirwa2655
    @chrispinechirwa2655 Місяць тому

    Osati chilima ku dpp ndiwakuba uyo aaaaaa

  • @Happ2y
    @Happ2y Місяць тому +2

    Naose chakwera anapanga nawo katangale palibe kuzemba Ai

  • @user-nx7yz4qo8f
    @user-nx7yz4qo8f Місяць тому

    Adpp musayelekeze kupanga ngwilizano ndi utm anthu akusani kudpp ko,better udf n aford,not chilima ndiyemwe wasaukisa malaw,coz anthu ambiri anamukhulupilira

  • @user-mj3ms4jt3b
    @user-mj3ms4jt3b Місяць тому +2

    Kuti DPP ndi UTM apange alliance chimenecho ndiye. Kulingati kuwanga amalawi ngati zitsilu. Onsewa analephera kukwanilitsa malonjezo awo omwe anatilonjeza mu chaka cha 2014 up to 2020 which is 6 years. Ndiye tingeso olephera ndi olephera aphatikizani tingamayembekezele chanino? Pamenepotu ndiyekuti tiyembekele kulephera x2. Ndiposo banja likatha mkukhalilaso limodzi, timati kubwelelana osati alliance. Boma ndilomweri la tonse alliance basi. Ndipo amalawi singavoteleso munthu ndi chipani chake chomwe tinachiona kuphera kwa kaleyi. Ngati zitatero ndiyekuti amalawi tachitika misala tonse

    • @user-tk6wf2eg4z
      @user-tk6wf2eg4z Місяць тому

      Panyapako ase mboli yaki plus iweyo bdi chakwela panyero pako

    • @user-ck6ij6bj5n
      @user-ck6ij6bj5n Місяць тому

      Mwalusatu biggy😂

  • @jelsonmlowoka8611
    @jelsonmlowoka8611 Місяць тому +1

    Where have you put sound 🔊?

  • @kennedygama8939
    @kennedygama8939 Місяць тому

    Neef is really a sucess story indeed

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 5 днів тому

    Utmost it's fuck it up already.

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o Місяць тому

    Hehehe nde agogo azawina popanda mgwirizanio😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @chrispinechirwa2655
    @chrispinechirwa2655 Місяць тому

    A msiska nanunso mwafanana ndi a kumkuyu kusintha mayina kamba koti muli ku south 😂😂😂😂😂 inu musakhare a ndevu za mwayi ayi. A kumkuyunso akhare chabe a chaba monga mwa mfunda yawo kukonda kubisala bwanji?😂😂😂🎉

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 Місяць тому

    Dpp and utm alliance can never be.....oil and water

  • @louisgolden
    @louisgolden Місяць тому

    Koma phindu la ngwirizanowu amalawi tikupindulanji? Fuso

  • @jameschiziwa
    @jameschiziwa Місяць тому +1

    No sound😂😂

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 5 днів тому

    UTM NDI DPP ANS IS ZERO

  • @yamikanifischer
    @yamikanifischer Місяць тому +1

    Copy yavuta apa

  • @JustinPhiri-kq2bb
    @JustinPhiri-kq2bb Місяць тому

    2025 elections % ndi iyi sizizasithaso MCP 35%,UTM 25% DPP 45% and Chihanna18% PP10%