Thanks for the history koma mabodzawa muchepetse i e kut kamuzu amapha munthu akapezeka akudya mpunga tsiku lot sila xmas thats a total lie bwana infact ur information is always biased
@@HamdanMasuku-db1zq sitinabadwe lero amkolo mu leadership ya kamuzu takhalamo much as we appropriate kt mavuto analipo what about Bakili Bingu J Banda n Peter?
I just believe it might be true. During the foundation of MYP, rice was the main crop grown and indeed was regarded,even up now rice is regarded one of the highly valued food. Remember MYP was Kamuzu's personal security organisation
Bible silimasinthidwa rather kutanthauzilidwa kuchokera ku chiheberi kupita kuchilankhulo china. King James version kuti idzikhala Authorized King James Version nchifukwa choti iyeyo anaika lamulo ndi chitetezo chokhwima kuti litanthauzilidwe bwinobwino kupeleka tanthauzo lake lenileni mmene zinalili mu chiheberi nkana ili version yodalilika Atsogo
Kondi achristu a ku Europe amapa a yuda chifukwa ciyani? Yesu ndi m`yuda Kondi analowelelapo bwanji monga ndim`bale wawo? Koma ciku`oneka kuti ndi properganda chabe kuti antu awakonde, chifukwa gati bible yawo'yi imanena zoona ndiyekuti ali ndi mulandu waukulu. ISAAH amati muphulumutsi ayenela kufa, tsono gati ayenela kufa bwanji pakha lelo ayuda safunika?.
Amwene mumakamba history mokondera why 75% of your stories mumakamba za kamuzu mosinjilira? Mwina muzinamiza ana amasiku anowa kapena anthu osantha kuwelenga...kodi simungakambeko za njala ya 2001 nthawi ya kamuzu inali yabwino kwambiri kwa anthu amene samapanga za ndale. Tasiyani kunamiza amalawi inuso ndi m'malawi.paja anzanthunu munakulira ku mudzi nde zonamizidwa nzambiri Funso langa ndi ili, ndi chifukwa chiyani numadana ndi akhristu, ayuda Komanso kamuzu nanga kodi munakulira kuti?
Tatiuzani anapha Robert Chasowa ndindani? Nanga sukamba bwanji galu iwe za anthu omwe anaphedwa ku mphoto pa ziwonetselo za ufulu wawo munthawi ya Bingu munthalika ndi DPP? Bwanji sukamba za abale athu amaphedwa ngati dzombe aja nthawi ya DPP ndi Peter Mumtalika? Bwanji sunena za kuphedwa mwankhaza kwa Issa Njaunju yemwe anaphedwa ndi Peter Mumtalika ndi DPP? Ndichifukwa chani sukamba za kuononga dziko komwe anaononga Peter Mumtalika ndi DPP. Galu iwe ingoyamba ndale za DPP izo basi. Ndipo iwale zoti Peter Mumtalika ndi DPP azalowaso m'boma anatizunza kwambiri.
Iwe wa MCP pantumbo pa mayiako ukudzatani pano iwe osapanga channel chako uwawuze anthu za abale ako anafawo bwanji, ukufuna uzionesa ngati umadziwa zinthu. Galu ndi amayiako usamachite ma cpmment opusa pano wanva panyini pako wanvaaa
Proud of you big brother love you from Lusaka Zambia
This is a brilliant research ever, proud of you brother Man 🔥🔥🔥🔥
Watching live and direct from Washington DC pa boma penipeni
Watching from mpumalanga south Africa ulemu wanu big pitilizan
Big up Bwana Bakili Muluzi TV. May God keep blessing you
Be safe and give us more details
Ndinali munthu osakonda social media koma inuyo biggy mwandipangisa kuikonda heavy big up boss
Am watching from Heaven.
We are proud of you here. Keep up
watching from south Africa Benoni
Proudly Watching from the beautiful city of lusaka zambia
Keep it up my brother and have more long life brother
Idya amin anali munthu wabwino koma azungu ndi amene anamuipisila mbiri
Always waiting for your new
Respect my journalist
Remember we really appreciate
Your job
God protect u sir mumativesa kukoza kuno kumal6
Thanx for giving us a good history.
Thanks for the video we have been waiting for this boss continue with this excellent work
Our home of history, God bless you big man ❤
I respect this big man
🎉🎉🎉❤❤
Ndiye bwanji osanyonga chakwera please kamuzu machende ake inu😢😢😢
Azungu si azibale athu amatinyoza over😢😢😢
Amene amadana ndi America amankhala dictator
May God bless you all the time for your good job and protect you .
Thanks man we need more stories za ku mcp part because young ones they should to know mcp ndi anthu ake😢
🎉 May God continue to keep u self Boss
GOD bless you our journalists
Salute bmtv
Salute bro..
Bwana ndinu munthu amene mukuyenera ulemu wanu koma sindikudziwa ndizaku onani Allah allamu
Mmakwana big chilungamo chiziyenda ngati basi okwiya akwiye oseka aseke koma chilungamo chisabisidwe ayi yimakumyadirani big
This is the best man ever
Nice one.
Oh Allah give him piece for ever. We know now history from you big man
Ngati kuli munthu oyipa padzikolotse lapansipano ndi pastor chakwera yomwe akufunisitsa atapha amalawi otse
Our best Tv
Kunana zoona azungu ndi anthu oopsa
Ayi ndi anthu abwino bwino 😂
Big man proud of u always
Nice job brother keep it up
Iweyo ndi dolo aise💪💪💪😊
Respect Boss
Mumatha bro I appreciate you
Thanks for the history koma mabodzawa muchepetse i e kut kamuzu amapha munthu akapezeka akudya mpunga tsiku lot sila xmas thats a total lie bwana infact ur information is always biased
@@MavutoChauma vt kumva nd kuvetsetsa nd zndu ziwiri zosiyana
@@HamdanMasuku-db1zq sitinabadwe lero amkolo mu leadership ya kamuzu takhalamo much as we appropriate kt mavuto analipo what about Bakili Bingu J Banda n Peter?
Big love brother ❤❤❤❤❤❤❤
❤such fantastic
I always feel proud of you, brother man!!
THE WINNERS
Ndadziwa lero kuti Kamuzu si dzina lake leni leni komanso sadali mMalawi. Ma underground movement amene akhala akupanga azungu ationongera zinthu zochuluka
Am listening
Iweyo ndi dolo wa history yoohhh
Ulemu wanu brother
Were born 11 children in our family,munthawi yakamuzuyo,
aye sowona anthu ambili mulungu akala ndizoyipa somwe akupanga
❤❤❤
𝐌𝐮𝐦𝐚𝐭𝐡𝐚❤❤
❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤
❤❤❤❤
Taziwa zambiri guchoka kwa Inu osasia timakunyadirani
our heroe in history 🎉🎉
Ulemu wanu nthawi zose sir
Zidapita ndipo zilibe kupindula kwa munthu wamoyo
Mmm ok takunyadilani bro
Big timafuna mbiri ya king leopard yoo
Subhan Allah 😥😥
Zoona big man
Never give up bro ❤
hello how you feeling
Eeee kunali nkhanza😢
💥
❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Exactly
You are my favorite
Pena pakeditu koma kulandila ufulu kumapangisa anthu azipanga zofuna zawo moonjeza...anthu amakhala n mantha indee koma zinthu zina zimayenda...taonani ndi maiko angati Aku Africa amene Ali paufulu odzilamulila okha Ali oidziimila pawokha posapempha kwa azungu chithanduzo ?so tikamati tikufuna ufulu bweziso titapeza njila zotukulila maiko athu mopanda kukapempha ngongole ngati zilikunozi..ngongole ngambwingambwi koma dziko anthu mkumadya chitedze,nde pamenepo tinene kut ufulu ukutipindulila?Mudzatipaseko mbiri ya Aldof Hitra kapena ilipo kale
Ma president oyipa
✍️🙏👏💯
Koma amwene mukumachedwa kubwera pa online bwanji timaderatu khawa
Mumakamba ngamo yokhayokha biggy
🤗
Ya apa tikumaona kumene nkhanza zikumachokera
Abwana tipasireni mmene zikuyendera ku ucraen
First to comment
Thanks
Ndiwe dolo ase
Please can you join anyone who is fighting with this useless chakwera government, on street am sure you can help Malawian's
Pitilizani brother
Umakwana bigy
This guy has talent 💪💪 appreciate
Ulemu wanu big
So sad
We want updates fo Palestine
Dolo
Takumvan bwana
God protect you sir we real love you and we appriate your good work, God bless you
Koma bro inuyo mumakwana
Asamasowa pliz
Umana kwambili iwe
umakwana
Lots of inaccuracies in this reporting! No one was getting arrested for eating rice. Don’t damage your good reputation.
I just believe it might be true. During the foundation of MYP, rice was the main crop grown and indeed was regarded,even up now rice is regarded one of the highly valued food. Remember MYP was Kamuzu's personal security organisation
@@AiwaMedia-sh6vx educate yourself
Bible silimasinthidwa rather kutanthauzilidwa kuchokera ku chiheberi kupita kuchilankhulo china. King James version kuti idzikhala Authorized King James Version nchifukwa choti iyeyo anaika lamulo ndi chitetezo chokhwima kuti litanthauzilidwe bwinobwino kupeleka tanthauzo lake lenileni mmene zinalili mu chiheberi nkana ili version yodalilika Atsogo
Kondi achristu a ku Europe amapa a yuda chifukwa ciyani? Yesu ndi m`yuda Kondi analowelelapo bwanji monga ndim`bale wawo? Koma ciku`oneka kuti ndi properganda chabe kuti antu awakonde, chifukwa gati bible yawo'yi imanena zoona ndiyekuti ali ndi mulandu waukulu. ISAAH amati muphulumutsi ayenela kufa, tsono gati ayenela kufa bwanji pakha lelo ayuda safunika?.
Amwene mumakamba history mokondera why 75% of your stories mumakamba za kamuzu mosinjilira? Mwina muzinamiza ana amasiku anowa kapena anthu osantha kuwelenga...kodi simungakambeko za njala ya 2001 nthawi ya kamuzu inali yabwino kwambiri kwa anthu amene samapanga za ndale. Tasiyani kunamiza amalawi inuso ndi m'malawi.paja anzanthunu munakulira ku mudzi nde zonamizidwa nzambiri Funso langa ndi ili, ndi chifukwa chiyani numadana ndi akhristu, ayuda Komanso kamuzu nanga kodi munakulira kuti?
Ndipo inu kukondera basi
Tatiuzani anapha Robert Chasowa ndindani? Nanga sukamba bwanji galu iwe za anthu omwe anaphedwa ku mphoto pa ziwonetselo za ufulu wawo munthawi ya Bingu munthalika ndi DPP? Bwanji sukamba za abale athu amaphedwa ngati dzombe aja nthawi ya DPP ndi Peter Mumtalika? Bwanji sunena za kuphedwa mwankhaza kwa Issa Njaunju yemwe anaphedwa ndi Peter Mumtalika ndi DPP? Ndichifukwa chani sukamba za kuononga dziko komwe anaononga Peter Mumtalika ndi DPP. Galu iwe ingoyamba ndale za DPP izo basi. Ndipo iwale zoti Peter Mumtalika ndi DPP azalowaso m'boma anatizunza kwambiri.
I think something is wrong ngat panalibe comment it better osalemba
Inu smuziwa chomwe mufuna coz it seems u have information nde ufunaso chan😂😂😂😂
Comment yakoi ikuchita kuonetsa kuti ndiwe mfana wakudambwe zoba iwe
Iwe wa MCP pantumbo pa mayiako ukudzatani pano iwe osapanga channel chako uwawuze anthu za abale ako anafawo bwanji, ukufuna uzionesa ngati umadziwa zinthu. Galu ndi amayiako usamachite ma cpmment opusa pano wanva panyini pako wanvaaa
Ndichisilu uyu kwambiri
Iwe zopanda ntchito zomwe ukunena,uzawanthu zot ziwathandize osat zau silu zomwe ukuchitazo zopusa
this is false about idi amin
❤