Koma steve konda banda uli ndi ulemu ndi amalawi osati galu chawezi kodi mwamuyitanilanji kùmibawa akufuna anthu azida ndi mibawa tv yabwino chawezi usamale usamapite pa pa tv utaledzela panya pako
Mmm koma konda Banda ndiwa mcp kuyambila kale kale nthawi imeneyo mukukhala kuchiwembe. Nde zomwe mumayakhula zopepelazi pena ife sitimadabwa nanu😂😂😂😂😂😂😂
Achawezi mukuti akunyasidwa asamaonere uko nde kuononga bznes yaeni, Zina kulibwino osayankha simufa be professional my brother. Izi zomati siyani kuonerazi mmmm doesn't sound professional
Good keep on sharing New invents
Bola inuyo osati garu chawezi mbuzi yamunthu sapota wa mcp otukwana amalawi
Komanso APM BOMA 2025
Palibe WINA
APM my vote
Koma steve konda banda uli ndi ulemu ndi amalawi osati galu chawezi kodi mwamuyitanilanji kùmibawa akufuna anthu azida ndi mibawa tv yabwino chawezi usamale usamapite pa pa tv utaledzela panya pako
Chawezi awononga tv yanu galu ameneyu
Apm boma
Follow how professional times tv is with it's kwagwanji and hot current osati zoyankhula ngati program mumapanga kuti muzionera nokha
Inu ndiye mumaima pa chilungam km si galu uja Chawez ndi nyani wachabebr
Chawezi ❤❤❤❤umatha kulankhura mwachifundo mwachisoni mwa bwino momveka bwino
Good message guys ❤
I like you guys ♥️♥️♥️♥️
Yah but forget about mcp 2025
Dpp vote
Zoona amadziwa akakavota 👍
Akuluakulu chilungamo chiyende ngati madzi kaya wagwilidwa ndi amuna kaya akazi lamulo ligwile ntchito basi mavenda enieni amadziwa poyala katundu wawo
Aaaa Shame guys penapake tadzilankhulani pozindikira kuti kuliso mawa. Ngati anthu ambiri akudandaula munthu mmodzi zoona inu osadzifusa kuti why munthuyu? Chawezi mukapanda kumuchotsa zionetseratu kuti inuyoso mwagulidwa ndi mcp paja mcp iripa plan yogula anthu media
Ali zunguli zunguli ntchalitchi atavala jejete Yolanda 😂😂
Apm boma ine kuno ku south Africa ndi magulisa agalu koma anangondiuza malamulo amagulisidwe akhe sanandilande
Ine ndi mkona sindimavera program yanu
Ndichifukwa chake dziko la Malawi silimatukuka chifukwa Cha m, sanje ndi khaza
Mmm koma konda Banda ndiwa mcp kuyambila kale kale nthawi imeneyo mukukhala kuchiwembe. Nde zomwe mumayakhula zopepelazi pena ife sitimadabwa nanu😂😂😂😂😂😂😂
Kondwa Banda ndi wabodza mukunyadila ndalama zangongole muzabweze ndinu pamodzindi ana wanu amenewo akazachokapo 2025
Ndende ya ku south Africa akayidi amalowa mbulanda Koma anthu amalowesabe mafoni kudende
DPP My vote
Zowonadi
Timava kukoma
Ndi mibawa t/v
Banda banba ndakuthokodza kwambiri ife maveda
Kambani zoona tifuna chilungamo
Mumakwana ndi Gwedegwede
Koma chawezi muchose
Ndimadabwa ma grass a Maso alikuti
Iwe umakamba chilungamo
Mbambande inuyo
Achawezi mukuti akunyasidwa asamaonere uko nde kuononga bznes yaeni, Zina kulibwino osayankha simufa be professional my brother. Izi zomati siyani kuonerazi mmmm doesn't sound professional
Mcp 2025 boma kale
You mad
Ukulota Dzuka uliko😂😂😂
Kweni iwe
Zakutulo ase
DPP my vote 💙💙💙💪