Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Asiye kulandla ndalama kuchokela kwamkayo ayambe 7 days fasting and prayer Ambuye akumasulan
Choyamba apemphera,chachiwiri asalekudya mawa, masana nd madzulo kupemphela komanso 12 o'clock usiku adzidzuka kupemphela chifukwa nthawi imene Santana amagwiritsa ntchito kuzoza anthu pachilichose aike chinkhwulupililo pa mulungu
Ndipemphelalo ndi pembedzelo mulungu ndi chida thandizo lathu amen
Only God is d answer
Only God is the answer, ask God first he will able
Kkkkkkkkkk komatu mmmmm anthu mukumananazo muleke kususukq azibambo
Prayer is only weapon
Mulungu nd wamkulu mubwerako bwno kulabour in the name of Jesus Amen
Choyamba mulape pamaso pa Mulungu musambisile Mulungu kathi muzikhuthule kwatunthuOsaleka kupemphela inu eni Mulungu ndiokhulupilika akukuyankhani
Ndipo adzachipezadi chomwe akuchifuna azibambowa,akapezavuto ndipamene amabwera anga abwino
Mungopeza muthu wa Mulungu akuthandizeni mapephero
Mulungu ndiye nthandizo muitaneni akhale nthandizo lanu pabanja panu ndipo musaope mulungu alinako kuthekera kokumasulani ndipo asakuopyseni dalirani mulungu
Choyamba zipereken kwa Mulungu nokha sister then muitane amene ndiokhulupilila mawu kupanga prayer intersection devil will surrender in the Lord Jesus Christ
Ndinakakonda anakautchula mzimuwo mwina akuononga azibambo ambiri koma osaziwa tinakauwona nawo ife pa tiktok mwina ndi friend timutuluke mwansanga
Kuzuza munthu wachete azibambo dekhani plz
Kukhulupilika pabanja ndicithu cokhaco cimene chimasamalila banjalo
Ndipo chilungamo ❤
Akunamatu ameneyu mulungu si munthu kazi yu akachila bwino bwino kuja kuno kuli mulungu ikani mulungu patsogolo zipelekeni mwathuthu kwa mulungu zintha zimenezo
kumapephelo bass ambuye azayakha
Komanso zalakwika kuti mnzimayi wabkisidwa dzina chifukwa awononga anthu a mbiri
Manyenganyenga amunawa kukanika kt mkadzi modzi yenkhayo kumangomusamala basi
Kothawila ndi kwa mulungu yekha basi
Mupeze mbusa wamphamvu amene amathana ndi ziwanda.
Koma anthu opemphera alipotu ndipo pemphero silinama
Ameneyo asamile mulungu
Mama Mulungu anakupasani mphanvu yoponda pazinkhanila tawasalileni kudya amenewo mupambana, Mulungu salephera, eeeiish Koma a man wa nthawi Zina mmmm
Mmmmmmm
Khalani ndi nkaziwanu kuli ngozi kunjaku
Yoo zovuta ndithu😢
Pemphero ndi chida zotheka ndi Mulungu
Ambuye akhale yankho ku banja lanu
Good leader
Pephelo ndi chida chogonjesela zonse
Chenjezo kwa anyamata anzanga achichepele ofuna ma sugar mumie phunzilani kena kake apa
Mmmh
Iiiih koma kukuchitika zinthu
Ysamilani pa mkono wayesu
Koma ndizovyta
Nkhani yakula iyi
Dziko lapansi ndiathu ake
Eeee zoopsa
Mulungu nde yankho
Mulungu ndye yankho ya zotse
Yaweh nde yankho
Mmmmmhu
Apite Kwa twaibu
Ndipo
Zina ukava
Zovuta
Zovuta kusimba
Zovuta kwambili
Asiye kulandla ndalama kuchokela kwamkayo ayambe 7 days fasting and prayer Ambuye akumasulan
Choyamba apemphera,chachiwiri asalekudya mawa, masana nd madzulo kupemphela komanso 12 o'clock usiku adzidzuka kupemphela chifukwa nthawi imene Santana amagwiritsa ntchito kuzoza anthu pachilichose aike chinkhwulupililo pa mulungu
Ndipemphelalo ndi pembedzelo mulungu ndi chida thandizo lathu amen
Only God is d answer
Only God is the answer, ask God first he will able
Kkkkkkkkkk komatu mmmmm anthu mukumananazo muleke kususukq azibambo
Prayer is only weapon
Mulungu nd wamkulu mubwerako bwno kulabour in the name of Jesus Amen
Choyamba mulape pamaso pa Mulungu musambisile Mulungu kathi muzikhuthule kwatunthu
Osaleka kupemphela inu eni Mulungu ndiokhulupilika akukuyankhani