Khani iyi inenso inandi chitikira 24 yrs ago but l thank God me and my girls we bounce but after matatalazi Anawa ali ndi tsogolo labwino ambuye awathandize ndi kulanga makolo akhaza akuchimunawa ndipo it's my prayer asamwalire asanaone ukulu wa mulungu pa ana wa
So painful, Lord have mercy on them
So touching story😭
Khani iyi inenso inandi chitikira 24 yrs ago but l thank God me and my girls we bounce but after matatalazi
Anawa ali ndi tsogolo labwino ambuye awathandize ndi kulanga makolo akhaza akuchimunawa ndipo it's my prayer asamwalire asanaone ukulu wa mulungu pa ana wa
Amabungwe alowerelepo athandizidwe anawa nkhaza zimenezo ana akuvutika bambo awo atawasiyira chuma kuyipa kwambiri
Eish nkhani yosautsa
Ife as we're taking tikukangana ndi abale akuchimuna,nkhani ya nyumba
Komaaa zachisoni my dad a kumpoto mayi Aku south andilanda farm 67 hectares aaa Aphoka ufiti mkati
Eeeesh musandikumbuse ccter wanga waziona 2yrs ago kulandidwa nyumba yot amamanga onse ndalama akalandila aliyese kusokhelan kumamanga nyumba koma zachson bamb kumwalira ccter wanga kusowa mtendere mmmm athu akumpoto siwathu or
Apite kumabungwe owona za ufulu wa ana
Km2 zovutatu
Nkhan ndiyovuta kwambili
Zosayenda murugu awatandize
Eeee koma ambuye mitima yachiwembuyi ukuchulukira dziko lathu chilungamo chidatha pano anthu akuona khope yandalama bas
Sambi
Zovetsa chisoni
Anzathu akuponto ndi anthu obvuta ndichifukwa safuna kukhalala ndi mitundu ya anthu ena
Siwose zilipalipose omwe amapa ximenexo ndimbuli osati munthu wozindikila