JOYCE BANDA WANG’ALURA CHAKWERA NDIPO WATI MU NTHAWI YAKE ANTHU SANADYE CHITEZE APA NDIYE KWACHEMA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 81

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc Місяць тому +7

    This lady is better than chikangawa 😅

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 Місяць тому +8

    Mbava yayikazi....kwanu ku zomba anthu akudza chitedze utaba ndalama unathawila jozi lero wasauka wayamba kulankhula ngati saint
    Mbuzi ndife amalawi

    • @vitujames53
      @vitujames53 Місяць тому +1

      Kumalankhula ngati oduka mutu bwanji..Amagawa chakudya ku Zomba simunawone???

    • @JhadahLeafs
      @JhadahLeafs Місяць тому

      Zilibe nchito zimenezo a wawa ndiokuba ​@@vitujames53

    • @JulieNdekha
      @JulieNdekha Місяць тому

      Vuto amalawi kusachedwa kuiwala ngati mbuzi😢

    • @Cammie921
      @Cammie921 Місяць тому

      Oops! I didn’t know that 😅

  • @HaliJana
    @HaliJana Місяць тому +4

    Koma kusiya za ndale pa chilungamo joice banda sangafane ndi chakwera joice banda amakonda amalawi ndipo pa saizi yake amayesesa zovuta sizilepela koma mayi uyu sangafane ndi mr chikangawa chakwera is

  • @kumbukanikafwafwa
    @kumbukanikafwafwa Місяць тому +4

    I love this woman. Amafotokoza mbali zonse.

  • @peterthawi
    @peterthawi Місяць тому +1

    this woman is a hero...she ruled MALAWI WITH empathy...and money was circulating with a free fall😂😂😂

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Місяць тому +2

    Aaaaaaa Mai tukumvani koma inuyo muli guru limodzi ndi chakwela musapusitse a malawi 🇲🇼 chonde, amalawi akuvutika, zoti muzaputsitsa a malawi 🇲🇼 moyo yathu ikumawa ,iweyo uli limodzi ndi chakwela so please usalowetse athu tchile muopeni mulungu

  • @vitujames53
    @vitujames53 Місяць тому

    Nkhani ndiya straight mukunena Amayi..you have passion for the people

  • @UthandekireSibande
    @UthandekireSibande Місяць тому +1

    I love you amayi Joyce Banda

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 Місяць тому +1

    Amayi salankhula mwa direct kudzudzula Boma akulankhura mozembera monyengelera,azilankhura mobaya ngati achina Inock Chihana

  • @JulieNdekha
    @JulieNdekha Місяць тому +1

    Koma amalawi adah kkk kuombera mmanja ndizophwisa zomwe😢mudakanika kale inu tiyeni uko...never again get out

  • @MaggieMbewe-qu5lt
    @MaggieMbewe-qu5lt Місяць тому +1

    Ndi zake wa chakwera uyuu akunamizira samalani anthunu afuna kunamizira ngat sali limozidzi ndi chakwera

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 Місяць тому +1

    Joice Banda osamukhulupilira akugwira ntchito ndi Chakwera uyu mkaona misonkhano yake ikumaulutsidwa pa MBC pomwe zamsonkhano wa UTM,DPP ndi Afford simungamve akukamba nkhani zao pa MBC unless zikhale zofuna kuwanyozatu

  • @JohnMota-jd1gt
    @JohnMota-jd1gt Місяць тому +5

    Onse amene akudziwa kuti anapezako.bwino chifukwa Cha ndale kapena boma adzilima osati mudzingo loza boma lolamula nonse amene mwakhala mulamula ndinu olephera manyazi mulibe njala musaitenge ngati chopangira kampeni zimatiwawa

    • @GiftJulius-gx2kb
      @GiftJulius-gx2kb Місяць тому

      Aaaaa inu joyce kuthandiza anthu simunganame amalipilila sukulu ana angati mziko muno wamanga amanyumba angati aa anthu ovutika osamayamkhulila zinazi ndale

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u Місяць тому

      Mwana wa chikangawa sasowa, njala ikachitika president lolamula ndi yemwe amayenera kulankhula ndi kutenga mbali ku anthu ake, koma ambuyakowo kukayendera ng'ombe pomwe ngakhale ambuyako omwe adabeleka ambuyako sadadyepo kapena kumva zoti anthu akudya chitedze, mpamene chikangawa akukanamiza anthu za mafuta agalimoto 😂😂😂😂 president wanuyu eeeeish wachita za chilendo ku dziko la malawitu, scandal after scandal ya a president 😂😂😂😂😂

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie Місяць тому +1

    Mayi oyipitsitsa dziko lonse iwe galubwako

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Місяць тому +1

    Wakuba uyu, angofuna kupusitsa amalawi, izi ndi ndale koma kunena zoona ali limodzi ndi chakwera amgofuna mavote. Anasakaza mu nthawi yake uyu, kugulitsa ndege, cash gate nkati. Zaka ziwili koma ku sakaza. Pitani mukalele zizukulu amai.

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 Місяць тому +5

    Cash gate womani mbava

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Місяць тому +1

    Chakwela watinyoza kwambili amalawi

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p Місяць тому +1

    Onse amaba koma ada alipowa ndi over

  • @GladysndilimbiraBonongwe-g6c
    @GladysndilimbiraBonongwe-g6c Місяць тому +1

    Kodi amaiwa akuti chani, poti ndi crew ya chakwera

  • @vitujames53
    @vitujames53 Місяць тому

    Ambuye azikudalitsani Mama JB..chikondi chanu pa a Malawi sichizatha mpaka kalekale

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g Місяць тому

    Ndiye azipani za mcp wo akutani ndipo muligulu limodzi ndi chakwera

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON Місяць тому +1

    Uyu nde samachedwa lugulitsa zithu ndichimodzimodzi mr chikangawa yooo

  • @happynyirenda8790
    @happynyirenda8790 Місяць тому

    Boza lokhalokha apa awa! Mulandu was cashgate unatga bwanji kubera ife amalawi nde lero kuzang'alura boza lokhalokha! Mungosiya kachipani kanuko! Mzimai iwe unaba kwambiri in 2years yokha

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb Місяць тому

    Inu eti akututumuka ndi oti adela thanks Rodwell

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Місяць тому +1

    Mahule akulu akulu ativuta ma girlfriend achakwera 😂😂😂

  • @Christopher-xc2ey
    @Christopher-xc2ey Місяць тому +1

    Wabodza uyo
    Hle

  • @DysonTummiesSajiwa
    @DysonTummiesSajiwa Місяць тому +2

    Koditu iwe sudakhalepo president m'Malawi muno nthawi imene ija umadika siwa usayiwale

  • @CosterMustafa-m6h
    @CosterMustafa-m6h Місяць тому

    Koma chandiqaza chojambulira foni yombanda moto aaa bt anyway ❤

  • @JohnMota-jd1gt
    @JohnMota-jd1gt Місяць тому +1

    Viva bushiri waonesa ntima osamala aMalawi thawi yanjala amai wanu munda ulipo?

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 Місяць тому

    Nawo mayo Joyce Banda atothandiza bwanji,payment iwoao Ali gulu lomwelo,chifukwa akufuna ma voti nde akhale ngati atithangata?

  • @FranksonKennethChipande
    @FranksonKennethChipande Місяць тому +1

    Amai awa timawapasa ulemu koma akayamba kunyoza anzawo tiwasika chifukwatu APM anawachosa m,Boma mosavuta koma pa Chakwera pakhala kulimbana MCP is stronghold from background

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 Місяць тому

    amai woyeeee

  • @MphatsoIshmaeladam
    @MphatsoIshmaeladam Місяць тому

    Ma president onse opuma kuyambila bakili muluz, bingu,Joyce and Peter ayi ndithu mbali yawo adayesetsa chifukwa amaba koma anthu amapeza mpumulo,koma zaka 4 for nothing chikangawa Palibe cholodzeka

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani Місяць тому

    Pamene ndimamukwatira mkazi wanga, salary yake inali ili pa mwk14000, within 2years ya mai uyu inafika pa 75pin, koma atalawa madala aja mmmmm nanjinanji lero kkkkkkk, ndalama zikungopita kuma delegates 😅😅😅😅

  • @MakufaTrading
    @MakufaTrading Місяць тому +1

    Koma munagulisa ndege dollayo ndkuiba et😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @Blessings31
    @Blessings31 Місяць тому +1

    People still have trust in this woman.
    Zomwe anapanga within 2 years zija sizawamba

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Місяць тому

    ❤❤❤❤❤mau Mai

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska Місяць тому

    JB analamulira bwino anali wachikondi vuto anampanga chipongwe ya cash get zakaso zinali zochepa,chakwela waononga Malawi vuto la sopano la JB ulilimozi ndi chikangawa

  • @FelistusTaulo
    @FelistusTaulo Місяць тому

    Ng'ombe yanga ya nkaka yagwesa ma billion inalemedwa

  • @AlfredChimijo
    @AlfredChimijo Місяць тому

    nothern region tikumane pano

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v Місяць тому

    Mesa muli gulu limodzi la chikangawa Mai oyipa uyu

  • @PhilbertoChaimah
    @PhilbertoChaimah Місяць тому

    Mawu amenewo mai

  • @FelistusTaulo
    @FelistusTaulo Місяць тому

    Amaiwa ndi izi zikulamulira panozi bolaso amai

  • @Blessings31
    @Blessings31 Місяць тому +2

    Palibe pomwe JB wangalula Chakwera apa.JB wangokamba zomwe amatha iyeyo andzimene anapanga.Stop infuriating violence amongst and between leaders

    • @CrifordKamalez
      @CrifordKamalez Місяць тому

      Choka hule iwe

    • @Blessings31
      @Blessings31 Місяць тому +1

      @@CrifordKamalez Hule ukanene amako chule

    • @FranksonKennethChipande
      @FranksonKennethChipande Місяць тому +1

      Kodi Olo atati amung'anule Chakwera amutha????? A satana onse alira chaka chamawa chi vote yanga ndikusunga ndikufuna satana aliyese azachite manyazi komaso azalire

    • @Blessings31
      @Blessings31 Місяць тому +1

      JB sapanga ndale zonyoza munthu ndipo she has respect for Dr Chakwera..sangapange nsonkhano kukanyoza president wadziko

    • @Mavisbunny346
      @Mavisbunny346 Місяць тому

      Kodi ya ndege ndi cash gate anabweza?

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Місяць тому

    Joyce Banda bolako kusiyana ndi chakwela

  • @swinibanda5412
    @swinibanda5412 Місяць тому

    Mai chashgate tinakutulukani

  • @thomluciouss7360
    @thomluciouss7360 Місяць тому

    Mai fundo zabwino koma amalawi kusava izi zingowalowa uku kutulukila uko pamawa azakukumbukulani fundo zabwino izi

  • @SydneyDrinkson
    @SydneyDrinkson Місяць тому

    Musafooke ,mama

  • @HawaSadiki-m9w
    @HawaSadiki-m9w Місяць тому

    Mai uyu amatha pomanga manyumba

  • @ZikhonaPantshwa-qs6jn
    @ZikhonaPantshwa-qs6jn Місяць тому

    Mfiti ndi mfiti.

  • @sylvesterzangalama6451
    @sylvesterzangalama6451 Місяць тому

    😂😂😂😂😂koma amene tikumva mau ochemelera ndi ana okha okha kkkkk zipo

  • @MillicaBanda
    @MillicaBanda Місяць тому

    Mbavq wakuba iwe sitingakuselere kachigeti iwe

  • @HaleemaAllie
    @HaleemaAllie Місяць тому

    Ndifitiso iwe fiti yayikazi chatafu

  • @HawaSadiki-m9w
    @HawaSadiki-m9w Місяць тому

    Zomba sisunga kape

  • @bazalikasokomera
    @bazalikasokomera Місяць тому

    Kkkkkkkk very pathos koma Malawi Ali pamoto mwa dzina lake

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Місяць тому

    Koma kuli zinthu

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev Місяць тому

    Zadziiii