CDEDI YAVUTA NDIPO CHIMWENDO BANDA AKHALA MMAVUTO AKAPANDA KUFOTOKOZA BWINO POSAKWERA NDEGE |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 16 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 128

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam 3 дні тому

    more fire chilungamo chiziwike cdedi god may continue kukudalitsan pa moyo wanu watsiku ndi tsiku🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @user-ig9qk6gi6g
    @user-ig9qk6gi6g 6 днів тому +8

    MCP, Chimwendo zimuvuta heavy.

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh 6 днів тому +5

    Anthu a mcp akutiyesa ngati makape awo sakudziwa kuti tikulilira mmimba,ndiye tsiku lozatulutsa mau kudzkhala ngozi

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 6 днів тому +8

    Koma guys omwe timanyozafe muziganiza anakakhala bare wanu. Kt simunakafuna chilungamo. Onse anja si abare anga koma anafa imfa yowawa .

  • @MuhamadYassin-ye4hn
    @MuhamadYassin-ye4hn 5 днів тому +2

    Anamiwa mulibwino ine ndilinanu ❤❤❤

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt 5 днів тому +1

    Osawanyengelela ma gangster a MCP Mr Namiwa more 🔥🔥 🔥.

  • @BrightonKamwendo-db1ci
    @BrightonKamwendo-db1ci 6 днів тому +3

    Chimwendo anenebwino komaso Mr mwayamba bwino zomwe timasowa kunva ife ndizo izi musalore chonde kuti paloweso chinyengo mulungu azakulipilani moyo wautali plz

  • @IanKajiso
    @IanKajiso 4 дні тому

    Watching from France

  • @charleskwawani9095
    @charleskwawani9095 2 години тому

    Bravo 👏 to the cided 🔥🔥

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w 6 днів тому +3

    More fire namiwa azajaira

  • @RICHMANCHIMWAZA
    @RICHMANCHIMWAZA 5 днів тому

    More Fire 🔥 Mr Namiwa.

  • @HowardTchauya
    @HowardTchauya 4 дні тому

    Proud of you Sir..

  • @mphatsomonjeza4371
    @mphatsomonjeza4371 4 дні тому

    Keep it up CIDED

  • @yohanekipandula5197
    @yohanekipandula5197 6 днів тому +1

    Thanks very much atsogoleri athu proud of you,,

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 5 днів тому +1

    Akulu nkhani mukuyitenga bwino kwambili ndipo osabwelela kumbuyo plz plz bwana namiwa

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 5 днів тому +1

    Tikudikira ma yankho anyoooooo!!!!

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 5 днів тому +1

    angomangidwa basi onse kukuyu chakwera varentino phiri onse apite kundende basi akolowe basi zoonadi osachedwa ma comrade

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 2 дні тому

    You are the real person

  • @RukayaIssah-h7t
    @RukayaIssah-h7t 5 днів тому

    Atolankhani kumangofunsa zopepera basi 😂😂😂 CDedi more fire

  • @user-xt2gu9yt9q
    @user-xt2gu9yt9q 6 днів тому +2

    Koma tidziyang,ana kochoka 2020 kufikila pano asdiki miya anafela ndale chilima anapita ndiathu ena 8 popandapo wina aliyese wa mcp zinatheka bwanji kapena panali line yanji a mery chilima amaenda ndiamuna awo thawi zose anawalesa ndani komaso chimwendo anawalesa ndani kuti asapite oooooooo palikathu mcp ititha tose

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo 6 днів тому +1

    Pamenepo ndipomwe amalawi tiziwe kuti achakwera anapha chilima😭😭😭💔

  • @MuhamadYassin-ye4hn
    @MuhamadYassin-ye4hn 5 днів тому +1

    Komad nhimomwemo Anene bwinod

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 5 днів тому +1

    Ipondeni fadah tikuziwa kt ikubwera gear 3

  • @LinlyMkunghudzakadzuwa
    @LinlyMkunghudzakadzuwa 5 днів тому

    Ndipo sitizamvesa mpaka kale atiuze basi😭😭😭

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 2 дні тому

    Ajayila anthu amenewa
    Chilungamo chiziyenda ngati madzi akulu akulu

  • @edwinearlkachiwala3070
    @edwinearlkachiwala3070 5 днів тому +1

    Bwana namiwa tili nanu limodzi tikufuna kumva zoona zokha zokha pa nkhani iyi

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 6 днів тому +1

    Anangopakilamo a UTM okhaokha ndikukawataya kuchikangawa.
    Maudindo anawakomela a MCP afika opera anthu

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s 5 днів тому

    Agwadila iweyo,,,Iweyo mene ukuvekera lilime lakolo unayamba wavoteloko chakwera cibadwileni akutuma adpp

  • @CharlesMukona
    @CharlesMukona 5 днів тому +1

    Zikuoneka ngati zocheza koma tsiku lophilika chithupsya likakwana tizachotsa mutu . Palibe ntsogoleli amene anabadwila kusanjika timachita kukuikakoni kukuchotsaniso ndikwaife 7 days ikwana tigwetsa babulo

  • @Cubotenterprise
    @Cubotenterprise 2 дні тому

    Usi usanyere bwana❤

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 День тому

    Zimenezi mudzimuwuza Billy malata ndi mzake Bennie Longwe ndi Redson Mulo kapena agape khombe ndi mbuli za ant

  • @EdwardMorris-pf3ue
    @EdwardMorris-pf3ue 5 днів тому +1

    MCP ikuwona ngati ndi nthawi yakale yongopha anthu mwachisawawa ndi galu wanuyo

  • @AdamUsufu
    @AdamUsufu 5 днів тому +1

    Namiwa moto kut bbbbuuuuu

  • @MARAQUICHACANA
    @MARAQUICHACANA 6 днів тому +1

    chakwerayo akumpatsa phavu zompusa nyusi wamozambiki wakupha akuchezerana akupha athamangitsidwe chakwera kumalawi

  • @FisherAction
    @FisherAction 5 днів тому +1

    Pitirizani big

  • @BerthTHOMASS-fc1qc
    @BerthTHOMASS-fc1qc 5 днів тому

    Chakwela Ndi chimwendo banda ndi azakewose akwezedwe boti mukawataye pakati panyanja tiwone ngati angapulumuke agalu amenewo amphedwe

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc 6 днів тому +2

    Agalu akupha mcp ma devils okha okha ndi useless chakwera

  • @Aishahimulan
    @Aishahimulan 5 днів тому

    Ambuye akudalitseni ndithu izizi ndizoona amalawi fe tikuyenela kudzuka ndi kuthandizana nao chifukwa sintchito yophweka iyi we have to help them ❤❤❤❤❤

  • @RukayaIssah-h7t
    @RukayaIssah-h7t 5 днів тому

    Abd and funso lina ndi lakuti a president antiuza kuti akupita ku Mozambique ndi zimbabwe koma anapitilira kukafika italy ndi jermany bwanji atolankhani sanafunseko zokhudza mayiko awiriwa kuti tidziwe chimene amakachita

  • @user-oc8nj3or6y
    @user-oc8nj3or6y 6 днів тому +1

    Tinachotsa Dpp ndi mademo then iwoso adzachokamo ndimademo ngati 😅😅😅

  • @Gilbert-bk9ml
    @Gilbert-bk9ml День тому

    Mafunso bwana simukumayankha mukuchulukitsa kulankhula zolankhula zizibwera after mwayankha

  • @user-iv4dj1pi3b
    @user-iv4dj1pi3b 6 днів тому +1

    Congrants mr NAMIWA

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 5 днів тому

      Mbuli iyi kupanda kutero sakadya kunyumba or dzina lakero ndi LA milandu basi

  • @denniskalambo-fv4ou
    @denniskalambo-fv4ou 6 днів тому +1

    We need such checks on these people they are running the gvt as if its their own bussiness entity.
    Chimwendo banda is more powerful in mcp than chakwera

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu 5 днів тому +1

    We independent investigation about Chilimas plane clash

  • @waltermoyo-z8u
    @waltermoyo-z8u 6 днів тому +1

    Chikangawa chikangawa

  • @WorriedNdhlovu
    @WorriedNdhlovu 5 днів тому

    Opposition kukanakhala anthu angapo ngat nkulu ameneyu bwez zinthu zilibwino

  • @Gilbert-bk9ml
    @Gilbert-bk9ml День тому

    Funso ngati sayankha mupanga chani,

  • @user-rn7wv8ze3v
    @user-rn7wv8ze3v 5 днів тому +1

    Mukapana yumozi or awiri azaulura chisisi

  • @CatherineMunthali-r1f
    @CatherineMunthali-r1f 6 днів тому +1

    Hmmmmmmm may those who perished in that tragic accident restwell till the truth comes out for the nation to be at rest

  • @JamesMpinda
    @JamesMpinda 2 години тому

    Atiwuze chilungamo

  • @Sophisticate230
    @Sophisticate230 5 днів тому

    Namiwa akufunika asilikali phwamwamwa. Atetezedwe. Anthu achilungamo ngati awawa amasowa

  • @mandelahindu9226
    @mandelahindu9226 6 днів тому +3

    Anamiwa Moto tili limodzi tiyeni Malawi akufunika anthu ngati inu big up

  • @VanPaul-sv9yx
    @VanPaul-sv9yx 6 днів тому +1

    Ndipo ng'ombe zija ndizawo anakayendela Achakwerazo ife monga aku banja takana ng'ombe sizanthu

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 6 днів тому +1

    Kwayaka.moto kkkkk 😂💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s 5 днів тому

    Iweyo gwapewe uyende sinanga magogo aja akunyemera ,,apule mtima phee!!!

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 4 дні тому

    Mulungu ndi woopsa zoona zeni zeni pa nkhaniyi ziziwika no secret under the sun

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 5 днів тому

    🔥🔥🔥

  • @NZERUMBAWIRIJEFFAT
    @NZERUMBAWIRIJEFFAT 6 днів тому +2

    Truth

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 6 днів тому +1

    Zambiri zidziwika za imfa ya Biyeni

  • @andrewmtendere3167
    @andrewmtendere3167 5 днів тому

    Namiwa✊

  • @ScrarNation
    @ScrarNation 6 днів тому +1

    Chakwera a anaphadi Chilima

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g 6 днів тому +2

    Chakwera anapa chilima

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 5 днів тому

    The truth must be reviewed

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g 6 днів тому +1

    Thilimozi basi❤

  • @FrankGeoffrey-r6o
    @FrankGeoffrey-r6o 2 дні тому

    💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🇲🇼

  • @ChiyembekezoCharles
    @ChiyembekezoCharles 6 днів тому +1

    tithandizeni pankhan imeneyi

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 5 днів тому

    Munalibe olo modzi wa mcp Mundege

  • @ChavukaGumbo
    @ChavukaGumbo 6 днів тому +1

    Tiyeni naone agalu awa

  • @DavieKachiwala
    @DavieKachiwala 5 днів тому

    Ndiye kuti mu ndengemo munali anthu 10 kale okwereratu amene andunawo akuwadziwa

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 5 днів тому +1

    Zaziii mukungochedwa nazo zopanda pake inuyo ngati mukuwona palichinqchake chinachitika inuyo bwanji osapeza anthu ena oti akuthandizeni tiziwe chowonadi osati kupita uku kupita uku bwanji nanuso pezani yankho lanu timve

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s 5 днів тому

    Kodi iweyo akutuma kuti maliro ayiniake upangire kampeni magogo aja

  • @ZephMbeleswa
    @ZephMbeleswa 5 днів тому

    Pathako pako iwe cholinga akuveni ndani or mutatani simdzakhala oramura

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 5 днів тому

    Zoona zake

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 5 днів тому

    Zikusowani zolankhura inu kodi kufa kwamoyo wamunthu mulindibuku la mumalawi wina aliyense yonse munthu azafa inuyo pangani nzeru kuti mupeze lipoti lenileni mukunena zang.ombe inuso ngati ndi kampeni yikuvutani ndithu pano dairy nkhani zopanda pake uposichoni wanu ikuvutani ndithu

  • @JuniorJone-v1g
    @JuniorJone-v1g 5 днів тому

    😢😢😢truth chilungamo

  • @RukayaIssah-h7t
    @RukayaIssah-h7t 5 днів тому

    Dziko ndi lanthu ili asatiopseze

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 5 днів тому

    Chimwendo us you can see the truth is coming out

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h 5 днів тому

    Tiyeni tili pa mbuyo pAnu

  • @DalisoulThom
    @DalisoulThom 5 днів тому

    Zabwino zonse anamiwa komaso mayi wa malemuwa akueneleka kufusidwa ndi chifukwa Chan sanakwele ndege?

    • @kennymwanyongo8165
      @kennymwanyongo8165 5 днів тому

      Mai wa Amalemu sanakwele nawo popeza kuti anali atangofika kumene pa ulendo wautali waku South Korea komwe iwo pamodzi ndi Malemu anakayimila ziko latu.
      Ngakhale malemuyu anali be chikumbokumbo potengela kuti iyenso anali otopa, koma kuti mwinamwake anakakamizidwa kuti akawonekele mwalo mwa Boma potengela kuti a president amati anali ndi ulendo waku Bahamasi. Koma nkhani Zake.. 😪🙆

  • @FredrickSongwe-xc6bw
    @FredrickSongwe-xc6bw 6 днів тому

    Mkaka is playing the card.,

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm 5 днів тому

    Km big awa amadziwa kukamba nkhani

  • @solobertkamunga2826
    @solobertkamunga2826 5 днів тому

    Inu report simunawerenge

  • @morsonmhone
    @morsonmhone 6 днів тому

    Bwanji osakawafunsa a times kuti nkhani iyi iwo adayitenga kuti nkhani?

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 5 днів тому

    Zoona

  • @crytoniegrantliffa2431
    @crytoniegrantliffa2431 6 днів тому

    Chimwendo banda!!! 😂😂😂😂😂

  • @StuartGondwe
    @StuartGondwe 5 днів тому

    Namiwa machine

  • @RauryneBishop
    @RauryneBishop 5 днів тому

    We need atsogoleli ngat Namiwa

  • @EdwardMorris-pf3ue
    @EdwardMorris-pf3ue 5 днів тому

    ndi zigawenga koma anapanga mwa umbuli chuwuluka chimatera kuchenjera ndi kupusa zinawandikana

  • @BashielSalade
    @BashielSalade 6 днів тому

    👍

  • @munyenyembe
    @munyenyembe 6 днів тому

    Tili limodzi guys we want the truth through commission of enquiry

  • @GiftKgomongwe
    @GiftKgomongwe 6 днів тому

    Tiyeni nawoni agaluwa

  • @RuthTimothyChirwa
    @RuthTimothyChirwa 6 днів тому

    😂😂😢 truth

  • @sabinaphili
    @sabinaphili 6 днів тому

    zigawenga za M C P

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 5 днів тому

    Kamufukuleni chilimayo ngati anali mulungu wanu ndi ngozi imeneija basi ngati chimwendo anapulumuka ndi mulungu yemwe bwanji nanga mary chilima nayeso anasintha ulendowo nthawi yathayitha inu ndi mbuli bwanji anapita basi kenako ndinu mwamva

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc 6 днів тому

    Agalu mcp aku gahenna awa

  • @OscarKJekapu-t3s
    @OscarKJekapu-t3s 6 днів тому

    Tiyen

  • @StainDandize
    @StainDandize 6 днів тому

    Tien nayo mkhan mpaka tidziwe zoona zen zen

  • @PatrickMtira
    @PatrickMtira 6 днів тому

    Tikumvera nawo basi

  • @shephardlonex3371
    @shephardlonex3371 6 днів тому

    Namiwa ndi zibwezi zake ziwili akaliza akazi phwale

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 5 днів тому +1

    khaniyi anamiwa ife tilinanu pamozi ndizona ziko si lilibwino pakhani ya ndege komaso athu 9 tiziwe chilungamo chenicheni chifukwa a ndizonyasa izi tikuziona apa nda mcp abwele ayakhule komwe anazitenga khanizo chifukwa akunena zoti ife amalawi tikulephela kutengapo mtu