WAIMASURA UDF NDIZOTSATIRA ONSE_MULI KACHILUNGAMO UMU_ISAIAH SUNGANIMOYO 25/12/24

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 1 січ 2025

КОМЕНТАРІ •

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 8 днів тому +1

    MWAYANKHULA BIG MAN KOMANO DZIWANI KUTI KU UDF ANTHU ALIKO VUTO ATUPERE WADZIONONGA YEKHA PANKHANI YOMWE IMAMVEKA KUTI WAPANGA UBALE NDI MCP PAMENEPO MPAMENE ANTHU AKHALACHETE NDIPO SAKUDZIWAKUTI ALIPATI

  • @KamaradaHamuza
    @KamaradaHamuza 7 днів тому +1

    Mawu amenewo

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 7 днів тому +2

    Atupere muluzi anarakwisa ku join mcp basi chipani cha Udf chata chifukwa cha nsogoreli

  • @MuhamadMpate
    @MuhamadMpate 7 днів тому +1

    Uchitsiru iyeyo payekha sangalimbe mtima sizingatheke

  • @PhiriVictor-e9l
    @PhiriVictor-e9l 7 днів тому +1

    Koma mukunena zowona.zokhazokha zikubvuta pafunika kukonza convention unatha tsopano tivale zacampaign

  • @NancyChimoto
    @NancyChimoto 7 днів тому

    Aaaaa 😮😮

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 7 днів тому +1

    Big dzitavuta, dzitatani Atupele sangatenge boma 2025 cifukwa wanena kale kulibe akumuthandizira nkhondo yoti ndikuwina dzisankho ndiye yekha ali bize ndicipanici ikutenga boma ndi dpp anthu mufune, musafune 2025 APM boma.

  • @ChingaipeBoss
    @ChingaipeBoss 7 днів тому +1

    Umandiwadza aise

  • @Felie-p7l
    @Felie-p7l 7 днів тому +1

    Ndipo ndizoona kuchipani Cha atupele aphungu ake sakumaenda kumakapangitsa misokhanodi

  • @WilfredKazembe-i6q
    @WilfredKazembe-i6q 7 днів тому +1

    Ndipo chipani chimenechi ngati anachikhwimila mavuto wokha wokha

  • @StevenMasamba-y1p
    @StevenMasamba-y1p 4 дні тому

    Atupere alibe Kuthekera Kwa usogoleri komanso amalawi tisachedwe naye alibe nzeru

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 7 днів тому +1

    Uli ndi dzina labwino m'bale ndalikonda

  • @BashiruAdamus-l2b
    @BashiruAdamus-l2b 7 днів тому +1

    Ndipo ndi zowona

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 8 днів тому +1

    Ndipo pano atupele watha ndimbili yake yoka joina mcp

  • @chikumbutsomatias1117
    @chikumbutsomatias1117 7 днів тому

    Zaziiiii

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 7 днів тому

    Siyani nkhani zandale zimapha ndale

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 7 днів тому

    olouli,iweyo,nzako,kunpatsa,udindo,emweyo,nkukumwngitsaso,ugayendenayeso,

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 7 днів тому

    dpp,ikhaulitsa,udf,,atupele,olo,atati,wayamba,khunyu,sangayende,ndi,dpp,

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 7 днів тому

    otsutsanu,mukufuna,mayiko,omwe,akuponya,mavoti,asamawine,olamula,km,otsutsa,nde,muzisangalala,mukunama,akati,npikisano,sichoncho,

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 7 днів тому

    Kodi anthu simungawafunile aMalawi umoyo WA bwino chimene mumaziwa Ndi ndale basi

  • @saidimwanyali8969
    @saidimwanyali8969 7 днів тому +1

    Mwayita big

  • @MphatsoChilangiza
    @MphatsoChilangiza 6 днів тому

    Atupele dyera kwambili koma mwanayu adzamva chipani Cha udf China onongeka atupele atabweleraso pali mayi patero udf inayambaso kuoneka komano awa ango bwera awonongaso

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 7 днів тому

    chipani,akayendaso,limodzzi,ndi,dpp,amulanda,MA,mp,ose,akhala,yekhayekha