Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
From Mozambique Apm my vote ❤❤❤❤
Super angoni osawopa ndichibadidwe chanthu
You're the best one Mr Norman Chisale 🔥🔥🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪
Chisale muli spirit ya Chilima ndiolimba mtima keep it up good work 😇
Awuze chisale long live ❤achisale mudziyenda mmalele bwana
Mr chisale your number one ❤
ilike this guy Norman chisale please Chisale madzilo mapemphero akakhale mu malilime kuti uzakondwr nawenso kupemphera motereMandelele ramantaka raboshika mantalaba powers are changing hands kkkk
Chisale we are together.me too am a Chisale
Good Mr kisari congratulation good speech
Norman usaope, ussanjenjemele,usafoke dzikoli ndi lathu cikangawa asatiopyeze APM akubweleranso tidzidyanso ka 4 pa tsiku osati izi mahule, mbava ndikupha ndizomwe akudziwa a mcp.Ndizoona pali a police 4 amenewa sadzifunila zabwino asiyeni ifenso tinafa kwambiri.
i love this guy too much
Chisale ng, alula more fireeeeee
Mwina samakuziwani kuti nanuso mudagwirapo ntchito ya u army bwana Chisale koma ndaona sopano DPP iri safe ndi Norman chisale kp it up
Fire 🔥 mwana wakwathu ❤❤❤❤
KomaMrChisale kkkkk yes dziko limafunika kumakhala ndi anthu olimba mtima. Dziwani kuti tonse ndife a malawi... Dziko ndilathu ili tonse
Achisale umuuze Mutharika akapezekeko ku ma demo chonde asaope. Chakwera aziwe kuti amalawi akuvutikadi kuti otiombola alipo.
Long live Norman
Usandikumbutse kumudzi Norman. Akhakhakha, abwampini,agurukunyinda.kwathu kumangoni. Chichewa chonveka bwino
Chisale alibe nzeru za utsogoleri koma ntudzu ndi ndewu sangathandize dziko awa, nzeru za utsogoleri zili mwa Peter basi
🎉 Malawi ndi nsima osati pakamwa Po Wawa po
More fire 🔥 guys 🇲🇼 👦 dpp is my vote 🗳 2025 boma and adad woyeeeeee
Viva mano nomani. I respect uuu
Noman chisale mbava yachabe chabe iyi.akupanga ndale za mkwiyo
Mr chisale❤❤
Achisale mkulu wanga mesa ku Mchinji m'mati tizikaona inu bwana? Lelo kwa chisapo mukuti tizikaona Adadi. Kwenikweni tizikaona ndani?
Adha awa loyalty ilimo yatho... Amafunika ku chipani chathu cha UDF
Inuyo Mr chisale mumakwana musazafe muzangosowa
Chisale ndi pangolin 🎉🎉
Wandikumbusa chilima chisale ndine wanu ku dpp
❤❤ km gangata ai thanks
Ameneyu angothokoza kuti Saulos Chirima kulibe mphata umenewu bwenzi akumayankhulira kundende
Inu ndopoila et
Big man chitsale ulemu wanu
Kodi Norman Chisale ndi munyamata kkkkkk koma ku DPP nkhalamba zikuzizuzatu
APM my vote
Uyu alibe zake
Mukufunsa kuti amadalila cani simaziwa kuti cisale ndi msilikali
Peter munthalikatu akhodza kumatelo komano inuyo ozendeweranu kuuuuuuuba cholinga mumutukwanitse,,,,,,,,nonse osatilanu ndnu mbava
Chisale woyeeeeeee slaimani woyeeeeeee peter muthalika woyeeeeee imfe pheee kumasitandi mvote tangoisunga ya peter enanu tazingodikilira kukadyesa ng,ombe iyaaaaa
Good advice to them they misleading Malawi
Dzoona bwana palibe dzonyengelelana inafu idzinafu agulukunyinda ena ake amaziva amaona ngati dzikoli ndilawo okha
Chisa2lil❤is good nice alike
Kkkkkk koma norman chisale simunthu wamba
Chilima 2
Uyu alindi phuzo 😆
ine ndimadanwa kuti akufuna kumfufuza kuti ngati ali ndi mfuti, kodi ndi tchimo kspena cholakwika pokhala bodyguard wa presudent angakhale alibe? malaei chibwana kuno south africa mfuti ndiye amayenda naxo ngskgale ma taxi driver olo wapnjinga yemwe
Honourable Chisale i solute you
DPP yomweyo/chisale ndimbalizina
Mungomanyoza m'malo mot muzikamba zachitukuko
Amadalila ndalama zakuba zija
Nkhondo timenya a chisale
Chisale woyeeeee
Angoni satha onse😅
Dpp kuti Wawa 2025 moto kachikena
Kakambani fundo zachitukuko izo mudzachitile anthu mukadzalowa boma osati mangoti mung'alule chilakhulo chakut chimenecho
Jezebel , chimwendo banda , zikhale ng'oma
Long Live
Koma bwana chisale mumatha kuyankhula
Norman chisale uli bho
Ndiye mu MALAWI mose apolisi 4
Umakwana mr chisale
Wanyoza chani pamenepa? Musakhale amangawa osathandiza dziko
Soldier chisale ndili kwa iwe
❤❤❤❤❤ Form Durban
Me 2 Durban Phoenix
Mumakwana
Dpp boma
Chisale mumakwana
Koma ndiye nkhwimbi la anthu DPP BOMA
Wakwiya ndi mfiti
Mbambande chisale
Koma nkuluyi mmmm ndilibe naye mau
Apm ❤🎉🎉🎉
Mulungu azikudalitsani
Kod akudziva mphavu kapena akupanga campaign
Akukuza chilungamo mesa
Chisale ndi dolo ka 100
Tili limozi timenyana nawo
Agulukunyinda yomweyo chisale
Mbabva iyi bvuto uchitsilu a Malawi olo bava timasapotabe
Anakubela Machende ako? Mbuzi iwe
💙💙💙💙💙💙
Evasi mereka
Zoona
Chisale umakwana,ulemu wako
💪💪
Oh yes
Kusowa fundo uku tsiku ndi tsiku zandewu
😂😂😂😂😂😂
From kep town
Pobwela tangodya chiteze kuli mavutotu
Mukhale ndifindo musamango likakhala dziko zaka 5 munapangapo chani pano mmukusowa fundo kumamkamba zandewu
Eti aise
😂😂
Eeeeeeeeeee
From Mozambique Apm my vote ❤❤❤❤
Super angoni osawopa ndichibadidwe chanthu
You're the best one Mr Norman Chisale 🔥🔥🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪
Chisale muli spirit ya Chilima ndiolimba mtima keep it up good work 😇
Awuze chisale long live ❤achisale mudziyenda mmalele bwana
Mr chisale your number one ❤
ilike this guy Norman chisale please Chisale madzilo mapemphero akakhale mu malilime kuti uzakondwr nawenso
kupemphera motere
Mandelele ramantaka raboshika mantalaba powers are changing hands kkkk
Chisale we are together.me too am a Chisale
Good Mr kisari congratulation good speech
Norman usaope, ussanjenjemele,usafoke dzikoli ndi lathu cikangawa asatiopyeze APM akubweleranso tidzidyanso ka 4 pa tsiku osati izi mahule, mbava ndikupha ndizomwe akudziwa a mcp.Ndizoona pali a police 4 amenewa sadzifunila zabwino asiyeni ifenso tinafa kwambiri.
i love this guy too much
Chisale ng, alula more fireeeeee
Mwina samakuziwani kuti nanuso mudagwirapo ntchito ya u army bwana Chisale koma ndaona sopano DPP iri safe ndi Norman chisale kp it up
Fire 🔥 mwana wakwathu ❤❤❤❤
Koma
Mr
Chisale kkkkk yes dziko limafunika kumakhala ndi anthu olimba mtima. Dziwani kuti tonse ndife a malawi... Dziko ndilathu ili tonse
Achisale umuuze Mutharika akapezekeko ku ma demo chonde asaope. Chakwera aziwe kuti amalawi akuvutikadi kuti otiombola alipo.
Long live Norman
Usandikumbutse kumudzi Norman. Akhakhakha, abwampini,agurukunyinda.kwathu kumangoni. Chichewa chonveka bwino
Chisale alibe nzeru za utsogoleri koma ntudzu ndi ndewu sangathandize dziko awa, nzeru za utsogoleri zili mwa Peter basi
🎉 Malawi ndi nsima osati pakamwa Po Wawa po
More fire 🔥 guys 🇲🇼 👦 dpp is my vote 🗳 2025 boma and adad woyeeeeee
Viva mano nomani. I respect uuu
Noman chisale mbava yachabe chabe iyi.akupanga ndale za mkwiyo
Mr chisale❤❤
Achisale mkulu wanga mesa ku Mchinji m'mati tizikaona inu bwana? Lelo kwa chisapo mukuti tizikaona Adadi. Kwenikweni tizikaona ndani?
Adha awa loyalty ilimo yatho... Amafunika ku chipani chathu cha UDF
Inuyo Mr chisale mumakwana musazafe muzangosowa
Chisale ndi pangolin 🎉🎉
Wandikumbusa chilima chisale ndine wanu ku dpp
❤❤ km gangata ai thanks
Ameneyu angothokoza kuti Saulos Chirima kulibe mphata umenewu bwenzi akumayankhulira kundende
Inu ndopoila et
Big man chitsale ulemu wanu
Kodi Norman Chisale ndi munyamata kkkkkk koma ku DPP nkhalamba zikuzizuzatu
APM my vote
Uyu alibe zake
Mukufunsa kuti amadalila cani simaziwa kuti cisale ndi msilikali
Peter munthalikatu akhodza kumatelo komano inuyo ozendeweranu kuuuuuuuba cholinga mumutukwanitse,,,,,,,,nonse osatilanu ndnu mbava
Chisale woyeeeeeee slaimani woyeeeeeee peter muthalika woyeeeeee imfe pheee kumasitandi mvote tangoisunga ya peter enanu tazingodikilira kukadyesa ng,ombe iyaaaaa
Good advice to them they misleading Malawi
Dzoona bwana palibe dzonyengelelana inafu idzinafu agulukunyinda ena ake amaziva amaona ngati dzikoli ndilawo okha
Chisa2lil❤is good nice alike
Kkkkkk koma norman chisale simunthu wamba
Chilima 2
Uyu alindi phuzo 😆
ine ndimadanwa kuti akufuna kumfufuza kuti ngati ali ndi mfuti, kodi ndi tchimo kspena cholakwika pokhala bodyguard wa presudent angakhale alibe?
malaei chibwana kuno south africa mfuti ndiye amayenda naxo ngskgale ma taxi driver olo wapnjinga yemwe
Honourable Chisale i solute you
DPP yomweyo/chisale ndimbalizina
Mungomanyoza m'malo mot muzikamba zachitukuko
Amadalila ndalama zakuba zija
Nkhondo timenya a chisale
Chisale woyeeeee
Angoni satha onse😅
Dpp kuti Wawa 2025 moto kachikena
Kakambani fundo zachitukuko izo mudzachitile anthu mukadzalowa boma osati mangoti mung'alule chilakhulo chakut chimenecho
Jezebel , chimwendo banda , zikhale ng'oma
Long Live
Koma bwana chisale mumatha kuyankhula
Norman chisale uli bho
Ndiye mu MALAWI mose apolisi 4
Umakwana mr chisale
Wanyoza chani pamenepa? Musakhale amangawa osathandiza dziko
Soldier chisale ndili kwa iwe
❤❤❤❤❤ Form Durban
Me 2 Durban Phoenix
Mumakwana
Dpp boma
Chisale mumakwana
Koma ndiye nkhwimbi la anthu DPP BOMA
Wakwiya ndi mfiti
Mbambande chisale
Koma nkuluyi mmmm ndilibe naye mau
Apm ❤🎉🎉🎉
Mulungu azikudalitsani
Kod akudziva mphavu kapena akupanga campaign
Akukuza chilungamo mesa
Chisale ndi dolo ka 100
Tili limozi timenyana nawo
Agulukunyinda yomweyo chisale
Mbabva iyi bvuto uchitsilu a Malawi olo bava timasapotabe
Anakubela Machende ako? Mbuzi iwe
💙💙💙💙💙💙
Evasi mereka
Zoona
Chisale umakwana,ulemu wako
💪💪
Oh yes
Kusowa fundo uku tsiku ndi tsiku zandewu
😂😂😂😂😂😂
From kep town
Pobwela tangodya chiteze kuli mavutotu
Mukhale ndifindo musamango likakhala dziko zaka 5 munapangapo chani pano m
mukusowa fundo kumamkamba zandewu
Eti aise
😂😂
Eeeeeeeeeee
Kakambani fundo zachitukuko izo mudzachitile anthu mukadzalowa boma osati mangoti mung'alule chilakhulo chakut chimenecho