Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Uyu ndiye freedom fighter 💪 🙌 ❤❤❤ love u Mr Chisale
Iwe ndidolo kamodzi kkkkkkkk fire fire Mr 🔥
Akamuna okonda dziko lawo Anomanitimakukondani❤❤
Powerful message bwana Chisale ❤❤❤
Thanks Mr chisale kuyankhura chilungamo mopanda kuphyatira ife ngati nzika tikumva kuwawa
More fire Chisale auze dziko latonse ili palib zoopsezan akufa bwanji maunyolo alimthumba hehehehehe😂😂😂😂😂😂heyiiiiii
Yes chisale good massage
Long live Mr chisale Awuzeni ma savejiwa
Iweyo ndiwe galu kwabasi mulonda Ngati iwe 💪💪💪💪💪💪💪💪
Zoona big man mr chisary
Power power 💪 chimwendo akuzolowera
Chimwendo akudzolowela
Akulu akulu ndithu Chisale ndi chikatundu 💪💪. Mau ambir ndilibe.
Chisale ndi the bodyguard from Beijing,, ali ndi 3rd Dan black belt in kioshin 2nd black belt in Judo 🥋 ndipo anagwira ntchito ku military ngati 2nd lieutenant ku airborne. Ndipo akunenazi ndizoona apweteka anthu chisale.
Viva bwana chisale ulemu wanu amcp atizuza mokwana pano tatopa nawo
Achimwendo koma hayayi eeee atasa zedi ngati dziko ndilake bwanji mmmm its too much mr chidina man
Umakwana chisale ❤❤❤❤❤
Normally chisale his freedom fighter ❤
Yes mumakwana achsare
Chisale bravo, this government ikutiwonjeza heavy and akutinyasa ati obowa a boma la mcp
More fire mr Chisale🎉🎉🎉🎉
Mr chisale osataya khawa ubwino wake wamkuluyo wayamba kele kufa chiwalo chimodzi chimodzi akufa mpopanopa
😂😂😂
Anthu azikhalako achilungamo wezii love you dady
D.P.P knows what Malawian wants
Dpp fanz we love you so much guyz
We proud of you boss
Chisale umakwana iweyo. ❤
Amene anakaotchanso office ya ku 24 amangidwe iwe chisale you are a good man freedom fighter
Uyu ndye samanyekerera iponde chisale😅
Iweyo nde ukhare president 2030
Uyuu too emotionalSangakhale leader 💔🙌
Ndi leader kale wa youth iwe sukuziwa
Mr Chisale umatiyimilira MULUNGU akudalitseni
Chimwendo akuziva kwambili
Mwa chisale leadership mulibemo
God bless you chisale❤❤❤❤
Ndipo namachende chimwendo kaya amazimva chani kaya
Long live mr chisale❤❤❤❤
Norman chisale is mr Hit man
Inu munamumenya Brian Banda
❤❤❤ takudalalani bwana chisaleh
Mmmmm ADPP mmamenya atolankhani nanunso
Look at the fellow team Ndiyamanyazi 😂😂kut koma uyuu 😂
Koma ichi chimang’alura eeeh!
Luwemba ndiwe wabodza iwe tikuzuwa from Biwi. Ngati kuli munthu mbava ndiye ndiweyo Luwemba
Mr man sopano🙏🙏 😂😂 uwuze ndi ana sakuziwa kalikonse ayi iwo koma kudya ndalama bas kkk
Chisale bravo
Mr chisale ndinu munthu wamkulu
Osaopa Mr,,chisale,,tli pambuyo panu
❤❤ Apm my vote
Apm my vote
Chisare on fire iye ndi monitor wa central region
❤❤❤❤ ulemu wanu sir
Bwana chisale
We love you mr chisale
Dolo kwambiri Chisale
Eyah chisale wanena zanzeru and asiyedi kukumanga ndi hatred ya mtundu wanji 😂😂😂😂😂
Boommaa iiillooo❤❤
My vote ❤❤
Chimwendo banda akudziyesa mulungu dziko laufulu ngt ilili kupusa galu
Ndip kwambr
Ulemu wanu mr chisale mumatimirira
Komano thawi yanu anthu atatemedwa ku blantyre azanuwa akuyakhula inu mudali chete thawi imeneyo osaonetsa kukhudzika . Azitsogoreri mukukolezera ziwawa chifukwa anthu simmukumawauza kt ali ndi ufulu osakha kapena ku joina chipan chilichose chomwe iwo asakha posatengera chigawo chakomwe atsogoleri achokera. Komaso kt alemekeze ufulu wa wina aliyese chifukwa cha zokhumba zawo.
Wakuba Iwe, 1.7billion komanso magalimoto 87 ubodigadi wake uti chumachosechi, umamubera mbuyawako uja
Press conference ya ma wounded soilder...Chisale you think you are more powerful than all malawians koma ukunama ifeso sungatiopsyeze mmaso mwako
Umatiyimilira Achisale ,tcheu sisunga kape .
Kodi Mesa akuti munayankha achimwendo pafon Kuti ndizanu zomwe zisakhudze? Zakumbowe?
Kasamben inu
Mr chisale mumatiyimilira ndinudi soldier weni weni
Inuyo bakili muluzi uja mumkamumanga uja samkava kuwawa
Fact 😢
Ndinu akape bambo mmesa bakili muluzi adaba @@LongmansLandscaping5
Chisale ❤❤❤❤❤
Mbava iyi aaaa 2:39 😮 2:49 2:54
Please mukamapanga zanuzo Qur'an yo muziyisiya kutali because you do not know how to hold it, so please u can use pakamwa panonopo
Is this press conference or kuopseza mburi zandale
Paja kale munalikupanga zomwezo mafuta munali kwatenga kuti kungoti inuyo adpp mulindintopola nthawi ija anzanu anali kunja kwaboma sanali kupanga chonchi inuyo mulindivuto mavoti mukufuna kuwatengera makani mulindivuto kwambiri
Aaah tapita uko iwe,unganene Chani chomveka mmakutu mwa anthu za MCP anthu ndkumva,tazingoliliran ambuyanu
Angoni ❤❤
❤❤❤❤❤❤Respect
Ingaluleni achisale atikwana anthu oyipa amenewa
Umatha chisale
Chisale analankhuladi zomwe Chimwendo anaulura za Chisale. According to his speech it is showing kuti Chisale anayankhuladi zomwe chimwendo anaulura
Fundoso mulibe mwalephelaso ku court za kusintha kwa kalembela amane mnayamba nokha zama registration 2012 panu mkuti asinthe.bwanji osanena za banja la tambala mnawawo ncha aja Nkhani yaku Israel wina alise amapita ndikupanga apply yenkha munthu chisale panja chamba chimakuphwetaka huh
Sarary ya mlonda wa president ndi zingati chisale anaba ndalama za misonkho ya a mlw
Akuva kuwawa ku opposition
Ichi chinabwera😂😂😂❤❤
Big up Chisale
Maboma ndiangati. Malawian, zikuomeka kuti ma camp ndiambiri.
Mkwiyowutu ukanalipo mpaka 2030 muphulika ndithu
❤fact up
Akuyankhura ndi mkwiyotu chisare mmmm😢
Boma ilooooo
Bravo chisale
Kkkkkkkkk akuti anthuinu nda abale asatana bwanji
Nanga mwalemba bwanji kuti Bodyguard wa a Muthalika.
Eya, anayankhuladi wina wake zimenezi
Kodi ku dpp wazeru kuribe chifukwa tikungova mbwerera zokhazokha popanda fondo
chisale kuyankhula mopusa unayambirsa wekha ndiye anakuyankha usapse mtima, usamadzitenge nangati dolo oti tizikuopa, tiye nazo usanati iweso ndi kalongonda yemweyo akukuyankhulitsa mopusa mwakomo!😂😂😂 tiye nazo anyamata akowo kutimana nawo kumalizila iweyo
Akusakani kukumenyani muzimvetsanso chisoni
Kubwebweta konseko 2000 basi? Mupindulanji ndi ka 2000
@@VictoriaWilliam-ms2ft 😆😆😆😆aaaaa kumenyana nkhani yake? ayelekeze!!!!!!!!!!!!
ndi amanye achisale mbowe ndichani nkhani munaotcha banda la kadambala muyankha chani manchende anu agaluinu
Inu a Chisale ndi DPP nose agaruu muuzane
Lamulo likusateni basi mulibe umunthu inu a Chisale
Inuyo mmakwana ma hope tiyeni tiyeni tiyeni
Zoona ulemu , mtendere zikufunika osati nkhaza Kwa Malawi's.
Chimwendo Banda vuto ndi umbuli and I don't know kut Chakwera akumuopa chyn ?
Chisale akuyakhula zoona
koma yah🎉😂
A MCP mwatimangilad achisale kokwana nw its enough dzikoli siyanu lokha ...
Zinalanga. Jawadu. Majidu. Kumuzi. Kusalima ndiriosangararakwambiri. Pamenemwatenga kurai. NdibaYibulo
Uyu ndiye freedom fighter 💪 🙌 ❤❤❤ love u Mr Chisale
Iwe ndidolo kamodzi kkkkkkkk fire fire Mr 🔥
Akamuna okonda dziko lawo Anomani
timakukondani❤❤
Powerful message bwana Chisale ❤❤❤
Thanks Mr chisale kuyankhura chilungamo mopanda kuphyatira ife ngati nzika tikumva kuwawa
More fire Chisale auze dziko latonse ili palib zoopsezan akufa bwanji maunyolo alimthumba hehehehehe😂😂😂😂😂😂heyiiiiii
Yes chisale good massage
Long live Mr chisale Awuzeni ma savejiwa
Iweyo ndiwe galu kwabasi mulonda Ngati iwe 💪💪💪💪💪💪💪💪
Zoona big man mr chisary
Power power 💪 chimwendo akuzolowera
Chimwendo akudzolowela
Akulu akulu ndithu Chisale ndi chikatundu 💪💪. Mau ambir ndilibe.
Chisale ndi the bodyguard from Beijing,, ali ndi 3rd Dan black belt in kioshin 2nd black belt in Judo 🥋 ndipo anagwira ntchito ku military ngati 2nd lieutenant ku airborne. Ndipo akunenazi ndizoona apweteka anthu chisale.
Viva bwana chisale ulemu wanu amcp atizuza mokwana pano tatopa nawo
Achimwendo koma hayayi eeee atasa zedi ngati dziko ndilake bwanji mmmm its too much mr chidina man
Umakwana chisale ❤❤❤❤❤
Normally chisale his freedom fighter ❤
Yes mumakwana achsare
Chisale bravo, this government ikutiwonjeza heavy and akutinyasa ati obowa a boma la mcp
More fire mr Chisale🎉🎉🎉🎉
Mr chisale osataya khawa ubwino wake wamkuluyo wayamba kele kufa chiwalo chimodzi chimodzi akufa mpopanopa
😂😂😂
Anthu azikhalako achilungamo wezii love you dady
D.P.P knows what Malawian wants
Dpp fanz we love you so much guyz
We proud of you boss
Chisale umakwana iweyo. ❤
Amene anakaotchanso office ya ku 24 amangidwe iwe chisale you are a good man freedom fighter
Uyu ndye samanyekerera iponde chisale😅
Iweyo nde ukhare president 2030
Uyuu too emotional
Sangakhale leader 💔🙌
Ndi leader kale wa youth iwe sukuziwa
Mr Chisale umatiyimilira MULUNGU akudalitseni
Chimwendo akuziva kwambili
Mwa chisale leadership mulibemo
God bless you chisale❤❤❤❤
Ndipo namachende chimwendo kaya amazimva chani kaya
Long live mr chisale❤❤❤❤
Norman chisale is mr Hit man
Inu munamumenya Brian Banda
❤❤❤ takudalalani bwana chisaleh
Mmmmm ADPP mmamenya atolankhani nanunso
Look at the fellow team
Ndiyamanyazi 😂😂kut koma uyuu 😂
Koma ichi chimang’alura eeeh!
Luwemba ndiwe wabodza iwe tikuzuwa from Biwi. Ngati kuli munthu mbava ndiye ndiweyo Luwemba
Mr man sopano🙏🙏 😂😂 uwuze ndi ana sakuziwa kalikonse ayi iwo koma kudya ndalama bas kkk
Chisale bravo
Mr chisale ndinu munthu wamkulu
Osaopa Mr,,chisale,,tli pambuyo panu
❤❤ Apm my vote
Apm my vote
Chisare on fire iye ndi monitor wa central region
❤❤❤❤ ulemu wanu sir
Bwana chisale
We love you mr chisale
Dolo kwambiri Chisale
Eyah chisale wanena zanzeru and asiyedi kukumanga ndi hatred ya mtundu wanji 😂😂😂😂😂
Boommaa iiillooo❤❤
My vote ❤❤
Chimwendo banda akudziyesa mulungu dziko laufulu ngt ilili kupusa galu
Ndip kwambr
Ulemu wanu mr chisale mumatimirira
Komano thawi yanu anthu atatemedwa ku blantyre azanuwa akuyakhula inu mudali chete thawi imeneyo osaonetsa kukhudzika .
Azitsogoreri mukukolezera ziwawa chifukwa anthu simmukumawauza kt ali ndi ufulu osakha kapena ku joina chipan chilichose chomwe iwo asakha posatengera chigawo chakomwe atsogoleri achokera.
Komaso kt alemekeze ufulu wa wina aliyese chifukwa cha zokhumba zawo.
Wakuba Iwe, 1.7billion komanso magalimoto 87 ubodigadi wake uti chumachosechi, umamubera mbuyawako uja
Press conference ya ma wounded soilder...
Chisale you think you are more powerful than all malawians koma ukunama ifeso sungatiopsyeze mmaso mwako
Umatiyimilira Achisale ,tcheu sisunga kape .
Kodi Mesa akuti munayankha achimwendo pafon Kuti ndizanu zomwe zisakhudze? Zakumbowe?
Kasamben inu
Mr chisale mumatiyimilira ndinudi soldier weni weni
Inuyo bakili muluzi uja mumkamumanga uja samkava kuwawa
Fact 😢
Ndinu akape bambo mmesa bakili muluzi adaba @@LongmansLandscaping5
Chisale ❤❤❤❤❤
Mbava iyi aaaa 2:39 😮 2:49 2:54
Please mukamapanga zanuzo Qur'an yo muziyisiya kutali because you do not know how to hold it, so please u can use pakamwa panonopo
Is this press conference or kuopseza mburi zandale
Paja kale munalikupanga zomwezo mafuta munali kwatenga kuti kungoti inuyo adpp mulindintopola nthawi ija anzanu anali kunja kwaboma sanali kupanga chonchi inuyo mulindivuto mavoti mukufuna kuwatengera makani mulindivuto kwambiri
Aaah tapita uko iwe,unganene Chani chomveka mmakutu mwa anthu za MCP anthu ndkumva,tazingoliliran ambuyanu
Angoni ❤❤
❤❤❤❤❤❤Respect
Ingaluleni achisale atikwana anthu oyipa amenewa
Umatha chisale
Chisale analankhuladi zomwe Chimwendo anaulura za Chisale. According to his speech it is showing kuti Chisale anayankhuladi zomwe chimwendo anaulura
Fundoso mulibe mwalephelaso ku court za kusintha kwa kalembela amane mnayamba nokha zama registration 2012 panu mkuti asinthe.bwanji osanena za banja la tambala mnawawo ncha aja
Nkhani yaku Israel wina alise amapita ndikupanga apply yenkha munthu chisale panja chamba chimakuphwetaka huh
Sarary ya mlonda wa president ndi zingati chisale anaba ndalama za misonkho ya a mlw
Akuva kuwawa ku opposition
Ichi chinabwera😂😂😂❤❤
Big up Chisale
Maboma ndiangati. Malawian, zikuomeka kuti ma camp ndiambiri.
Mkwiyowutu ukanalipo mpaka 2030 muphulika ndithu
❤fact up
Akuyankhura ndi mkwiyotu chisare mmmm😢
Boma ilooooo
Bravo chisale
Kkkkkkkkk akuti anthuinu nda abale asatana bwanji
Nanga mwalemba bwanji kuti Bodyguard wa a Muthalika.
Eya, anayankhuladi wina wake zimenezi
Kodi ku dpp wazeru kuribe chifukwa tikungova mbwerera zokhazokha popanda fondo
chisale kuyankhula mopusa unayambirsa wekha ndiye anakuyankha usapse mtima, usamadzitenge nangati dolo oti tizikuopa, tiye nazo usanati iweso ndi kalongonda yemweyo akukuyankhulitsa mopusa mwakomo!😂😂😂 tiye nazo anyamata akowo kutimana nawo kumalizila iweyo
Akusakani kukumenyani muzimvetsanso chisoni
Kubwebweta konseko 2000 basi? Mupindulanji ndi ka 2000
@@VictoriaWilliam-ms2ft 😆😆😆😆aaaaa kumenyana nkhani yake? ayelekeze!!!!!!!!!!!!
ndi amanye achisale mbowe ndichani nkhani munaotcha banda la kadambala muyankha chani manchende anu agaluinu
Inu a Chisale ndi DPP nose agaruu muuzane
Lamulo likusateni basi mulibe umunthu inu a Chisale
Inuyo mmakwana ma hope tiyeni tiyeni tiyeni
Zoona ulemu , mtendere zikufunika osati nkhaza Kwa Malawi's.
Chimwendo Banda vuto ndi umbuli and I don't know kut Chakwera akumuopa chyn ?
Chisale akuyakhula zoona
koma yah🎉😂
A MCP mwatimangilad achisale kokwana nw its enough dzikoli siyanu lokha ...
Zinalanga. Jawadu. Majidu. Kumuzi. Kusalima ndiriosangararakwambiri. Pamenemwatenga kurai. Ndiba
Yibulo