Beracah - M'manja Mwanu (Music Video)
Вставка
- Опубліковано 3 гру 2024
- Stream & Download on push.fm/fl/mma...
Lyrics:
Yense osambitsidwa ndi mwazi wa Yesu
Ndimwazi wa Yesu
Ali mmanja mwake
Palibe dzina lina lomwe ndingafune kutsata
Ndipo palibe kwina komwe ndingafune kukhala
Kuposa mwandiyikako kutsata mukuchitazo
Ufumu wanu ndilondola till the day that you return
Palibe chondikopa
Palibe chondisuntha
Mwa inu muli zonse
Author and the finisher
Ukulu wanu ndi osatha
Ufumu wanu wamuyaya
Chondilimbitsa you're above it all and I'm so thankful
Tili m'manja mwanu
m'manja mwanu m'manja mwanu
Ndine wanu
Tili m'manja mwanu
m'manja mwanu
Ndine wanu m'manja mwanu
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu yeah
Chikondi chanu ncholemera
Chindichotsa manyazi
Ndili kutali munabwera kundikokera nkati
Yesu my solid ground
No one can hold me down
No one can wear your crown
You're so profound
Palibe chondikopa
Palibe chondisuntha
Mwa inu muli zonse
Author and the finisher
Ukulu wanu ndi osatha
Ufumu wanu wamuyaya
Chondilimbitsa you're above it all and I'm so thankful
Tili m'manja mwanu
m'manja mwanu m'manja mwanu
Ndine wanu
Tili m'manja mwanu
m'manja mwanu
Ndine wanu m'manja mwanu
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu yeah
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu (mwanu mwanu)
Mwanu mwanu yeah
Yense osambitsidwa ndi mwazi wa Yesu
Ndimwazi wa yesu ndimwazi wa Yesu
Yense osambitsidwa ndi mwazi wa Yesu
Ndimwazi wa Yesu ali mmanja mwake
Beracah fans gather here🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉Ife nganga manja mwanu
International standard amwene❤
The best male gospel artist of our land......inu mumatha Chief. Koma nthawi inayake try and feature Theresa Phondo and any rapper on your song, it will be fire 🔥
And a hit🔥
I can't wait for that banger 😂❤️
Live and direct
Blessed love ❤.. tonse tili manja mwake
Lots to be grateful for ❤
Koma achinyamata tikunjoya mwa Yesu iiiih.🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Dolo mwa Yesu🎉🔥🔥🔥
Beracah. .. I understand 25% of your songs (the English lines).. The rest just makes sense on its own.. 😂.. Much love from UG🔥.. We need songs with 75% English.. Bless us too😭
I hope you and pompi 🇿🇲 can work on something soon to minster to the continent and the world at large
Beracah is who he thinks he is.Dolo mwa Yesu🔥🔥
Please just release the album already 🥹😭. Love from Zambia 🇿🇲
This man is a blessing in the body of Christ. Enjoying the music from Zambia🎶🎵🎶
Beracah you are really a man who they say you are, a great gospel artist❤🔥❤🔥❤🔥
Adha inu muli mu zone yanu yanu🔥🔥🔥🔥🎧
Nyimbo yokoma kwambili🙏🏿🙏🏿
Another masterpiece from great artist,... Can't believe Malawi is still sleeping on this genius
Beracah never disappoint🔥🔥🔥
Ending this year ndili m'manja mwanu❤🎉
👏🙌amen 🇿🇲
Shasha kangapo🥰👏
May the good Lord increase you
Watched it the first time. I came back to watch it again❤❤❤
Quite a way to Wrap up 2024, a beautiful tune🔥🔥♥️
Beracah iweyo ndi machine. Nde ukatengana ndi Kelvin Sings imakhala collabo yoopsa. Tamenyani collabo ina guys
Wow !One day I know I will sing like that,🙏🙏🙏
Nyimbo ndi izizi 🔥🔥🙌
ndipo sitingamvelenso zina
God bless and keep enlarging you territory, may HE fill your cup until it overflows. 🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤
You are a blessing to me personally Beracah. Keep up the good work. Nyimbo zako ndimazikonda heavy: they really bless my soul 😇😇😇
Best Gospel Artist Malawi has ever seen
This song is giving 🎉❤
I love you beracah 🙌❤️🩹 spiritual songs for real 🤍✝️
Luso la nyoooooo🥳
Palibe chondisuntha🔥❤️
Nyimbo 💯🔥
Your music is so unique🔥your songs have been on repeat 🔁
Beracah 😭😭😭♥️♥️♥️♥️
Zambia is locked in 🔥🔥🔥🇿🇲❣️
Love from Kuwait 🇰🇼💯😎
Who else is watching this beautiful piece from Zambia🇿🇲 ?
I am
@@GrowAfricaGreenZambia Awesomness
Love from Zambia 🇿🇲❤️.
Madhala 🔥🔥🔥🙌
from welenga to Mmanja mwanu 🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Beracah my dwag 🥰
You'll forever be my fav gospel artist Beracah
Wow! Nyimbo yasamba heavy🔥
You're very gifted ❤, may the Lord grant you grace to sustain this gifting and you minister to us.
God bless you Beracah
Limoblaze should send you a dm ase. Ndiwe dolooo
Beracah for a reason 😚💗💯📌📌
Dolo 😎😎
I really love your music 🎶 ❤❤you got a gift love from 🇿🇲 zambia
U dnt disappoint bro 🔥🔥🙋♂️🎧🎤🥁🎶🎵
Any translations please
This is so beautiful 🔥
Munthu kuchita kumveka kuti akudziwa chomwe akuchita.
This one really knows
You've been my fav artist..especially for Munkhale song. You're great.
One of our few real top layers in music industry of Malawi ❤️...the song is beautiful
Kunjoya mwa Yesu...🎉🎉
🇿🇲 do something with Abel Chungu❤
Exactly 💯🔥🔥🔥
Iyiyi ndi hit🤩🥰💥
Beracah 🥳🎉🎉🎉
If not him then who else❤
Beracah❤🎉🔥🔥
Ndili manja mwanu Yahweh 🎉🎉 nice song
MASSIVE SONG!! BLESSED!!! 🙏 MAY GOD KEEP YOU SHINING BROSKI
❤❤❤❤❤❤❤@Beracah ...
Iwe ndi one🎉🎉🎉
Shasha kwambili iwey🔥🔥🔥🔥🔥
💪💪💪💪 manja mwanu
Dolo Ka fili handede🔥🔥❤️🔥
Umfumu wanu ngosatha 🙏🙏 Tili mmanja mwanu 🙏🙏❤❤
Beracah ndiwe dolo aise 🔥🔥🔥
I love your vibes king beracah 🎉😊
Beautiful piece of art Beracah, watching from Zambia.
🎉🎉🎉i like your songs beracah
Beracah❤😊
Amene tikuziwa tili manja mwake tilikuno
Tili mmanja mwanu ambuyee
I love it!! Much love from Zambia 🇿🇲
Kuno kuno🔥🔥
Shasha kwambili 🔥🔥🔥🐐
Tili mmanja mwanu ndine Wanu Mwanu Mwanu 🔥🔥🔥🔥🙌🙌🙌🙌
Dolo🔥🔥🔥
Palibe chondikoka🔥🔥🔥this is huge
Mmanja mwanu.... So Powerful
Mmanja mwanu...🔥🔥🔥🔥
My favorite artist ❤❤please drop album
Lovely song bro🔥💯 🇿🇲👏🙌
Oh this is heavenly!!! 👏🏽👏🏽👏🏽
Nice tune madhala 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Tigona pompa 🎉
Nyimbo iyooooo🔥🔥🔥🔥🔥
Dolo kangapo 🎉
Luso🇲🇼🤝
shasha mwa Ambuye umatikwanila
Come on now🔥. To God be the glory.
On repeat 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Tionjezere pa fav playlist paja🔥🔥
Am ur biggest fan ❤😊
Beracah Peatry Jr Gem 🙌🏽🙌🏽🙌🏽
Dolo katatu uyu 🔥
Abusa ❤🇲🇼🔥🔥🔥🔥🔥
Imma leave this here🔥🔥🔥
What a hit song 🔥❤️🔥🥵