CHAKWERA KUTI AMVE ZOMWE CATHY MAULIDI NDI NZAKE ATOKOTA LERO KU KONVESHON YA UDF NKHANI ITHA KUVUTA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 2 жов 2024
  • CHAKWERA KUTI AMVE ZOMWE CATHY MAULIDI NDI NZAKE ATOKOTA LERO KU KONVESHON YA UDF NKHANI ITHA KUVUTA
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

КОМЕНТАРІ • 21

  • @McdonaldChirwa
    @McdonaldChirwa 2 години тому +1

    Cathy Maulidi number one Reporter from times TV, I like the way she reports without bias

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 3 години тому +1

    Kom ndimvuseko bigu anachokera kut mukuiwalatu kom bakili mulusi adapasa bingu chifukwa chake athu akuwopabe mwinaso asagulisa chipani bibgu poyamba analiwa UDF

  • @InsideMalawiUSAnews
    @InsideMalawiUSAnews 2 години тому

    MCP and UDF will form alliance. Bad news for USI. Bad news for Chakwera. Atupele will create chikangawa for Chakwera. UDF will be back in Government.! Congrats to UDF.! 😂

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh 2 години тому

    Ma speech onse ndawavera sadaipitsepo mcp

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh 2 години тому +2

    UDF + mcp gwirizano mark my wd

    • @AmoTiamo
      @AmoTiamo 38 хвилин тому

      Ngati ziri choncho tinene Kuti a UDF akuganiza mwa chikapekape samayenera kuphatikana ndi chikangawa zipani zosusazi zimafunika ayisiye MCP iyende yokha ngati chiyenda yekha

  • @grantjossam
    @grantjossam 3 години тому +1

    Chakwera watha basi 😅😅

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 години тому

    UDF is going to MCP bas. Ma speech awo akulowera konko😂😂😂😂😂😂😂

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama 2 години тому

    Udf isiyeni ikalowe ku mcp ikufunako ndiyamanyi koma ine vote yanga sadzayiwona ngakhale ndili wa udf

  • @MorrisTsoka
    @MorrisTsoka Годину тому

    Chipani cha UDF ndichaminyama chikapanga ngwirizano ndi chipani china chipanicho chimalephera....

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Годину тому

    Apanga alliance ndi kongolesi awa period ,ofunika kuyamba kuwapanga unfollow awaa mxeuii

  • @ClementsKamanga
    @ClementsKamanga 38 хвилин тому

    ❤Sangawine or kma ayesetse kut adzakhala nomber 2 adzakhala vp

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza Годину тому

    Atupere amaoneka kuyambira kale koma ngati zili choncho nde kuti anthu ambiri ayitulula udf

  • @martinchimoyo208
    @martinchimoyo208 Годину тому

    Family politics comes in because of money. If they had money, they could have challenged them.

  • @Majorleman
    @Majorleman Годину тому

    Koma mayiwa awona zoona zonse zimene akukamba apa zachiziwikile kt udf anthu ambiti ayenela kuchimva kt atupele ndi WA MCP pamodzi ndi bambo ache

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 51 хвилина тому

    Tikudana ndi chakwera ndi hule komaso ndi chigawenga

  • @ChristopherChapeta
    @ChristopherChapeta Годину тому

    A mcp akatero amafuna kugula omwe alephera ku convetion

  • @ClementsKamanga
    @ClementsKamanga 35 хвилин тому

    Zake zimenezo akatelo udf yatha

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama 2 години тому

    Maiuyu ndiwa.mcp mwamuwona mene walakhulila akuti dzabwino dzapnga mcp iyeyu dzapitilizda yapanga chani mcp kumalawi kopotsa kupha athu 9 kuchikangawa

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 49 хвилин тому

    Komaso inu anthu akumpoto osavotela UDF mwaona nokha angovotelana ayao okha okha mbuzi dza anthu

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh 2 години тому

    Atupere ndi kape